Kwabasi and ndimadabwa kuti anthu aku Malawi sanadzegukebe mmaso why, bushiri ndi wa satanic ndiopa heavy, Chakwera, Joyce Banda ndi asatana awa, anthu amati Bushiri alindi ndalama koma sungaloze church yoti anamanga ayi
Ana Amma 2000 mumangosatira zili zonse. Makolo ankanena Kuti MCP ndi yoipa munkachita makani. Koma dziwani Kuti makolo athu anazunzidwa ndi chipani chimenechi.
@@EdwardDixies Makolo kumene amanena Kuti ma card anali okakamiza mayi oyembekedzera amatha kuchilira pa njira kukanizidwa kudutsa kamba alibe a ndalama can you emergin ufiti ndeno ndi izi
Ana ama 2000 musamangiwanamizira ,ndi angat anakavotera MCP 2020,, your failure to confront the current problems its not as a result of a certain group that you see so fragile to attack,,kakonzenitu inuyo ama 80s n 90s pomwe analakwisa ama 2000po
Grace Chinga . May your soul continue resting in peace. U said it, but people ignore that, and Joyce Banda and Bushiri indeed are included as you said earlier,,.. Where do Malawi going to,, we need to Pray hard against this satanism political party,,. Kulibe kanthu konse komwe yehova adzabisire Ana ake
Ndipo olo ena akamati bola dzikoli akadalamulira ngt president Bushiri ine ndimangotseka a Malawi kutengeka ndikusamudziwa zintchito zake Pali mau amati: Kusadziwanso ndi kufa komwe. Osadabwa munthu opanda chisoni chifundo eeeeh kungoti zoopsa km
Mmmmm koma nde eeee ziliko ndpo zikuchita kuonekelatu kt Chakwera ngwa satanic no Wonder zintchito zake za umve zikuoneka...ndpo zoti bushiri akuyendetsa naye boma kwa ine sizachilendo ..a satanic inu koma tsiku ndili modz mzayankha pamaso pa mulungu
respect the MAN OF GOD bushiri. i know a prophet is not respected by his own city or family but remember he brought millions to Christ and saved thousands of souls. if he is a Satanist then what are you? Satanism is done in secrecy so what were you doing to notice his satanism? on behalf of millions of his followers, we are not moved not even a single inche.
Zaugalu mukapangana kuti mupeleke mangadzi ndiye chifukwa kumalawi kuli mavuto ambili zingodzi tikuziwonazi musokhane nose mupeleke ana anu nosenu mbiri yabushiri mukuyiziwa mukusithanisa ndi magazi anthu moto wamulungu ukufikileni nonsenu nema of jesus fair
Ndi uchitsirutu umenewo kumaipitsa mbiri za anthu iwe ndi galu kobas ukanakhala dolo unakajambula video coz umboni ulinawo koma ka audio kakoka kaonetseratu kut iwe ndi mbuli komanso ulibe mzeru, Kapolo ngat iwe udzafa mphawi chomcho, mabwana wawatchulawa angakumane ndi iwe Kapolo iwe, Chitsiru Cha Munthu.
Continue exposing each other... Malawians we need to stand in prayers against spirit of accident.Holy spirit will take control in Jesus Christ name.
Ameeen mulungu atithangata tonse Malawi, ameeen
Amen
Amen
Ndipo apa ndipang'ono zikubwera Zina zoposa apa coz kumene aliko ndiye akutenga mphamvu zochuluka Malawi tikapanda kugwada pasi kupephera zolimba titha ndithu komaso chomwe mungaziwe tili mu thawi yakumapeto Yesu akubwera posachedwa
Yah thus true akukatenga mphamvu zina
@@PeterMPWWailes Zoona coz Apapa nde tili pamoto ndipo tilira mpaka Yesuyo afika
Coz step watenga pano kukhala ngat wabalalika Koma chomwe akuchita akuchidziwa
"Malawi tipemphere bas Kwa Mulungu kt chikho ichi chitipitilte"
Amen
Ambuye chikho ichi chitipitilire😢😢😢😢
I don't believe this is true
Mwati amkaka nawonso analipo pa meeting? Ndichifukwa ankati ndale zawo amapanga usiku eti yooooh 😭😭😭 Shalom Malawi shalom
Is true bushiri akutha anthu Ku Malawi Kuno ndipo wokonda iyeyu ndi mfitiso
Eti esh
Koma😢
Exactly eshiii 😢😢😢
Kwabasi
Kwabasi and ndimadabwa kuti anthu aku Malawi sanadzegukebe mmaso why, bushiri ndi wa satanic ndiopa heavy, Chakwera, Joyce Banda ndi asatana awa, anthu amati Bushiri alindi ndalama koma sungaloze church yoti anamanga ayi
Finally yafika pambalambanda audio
I got it December 2023😅
Groly to almighty God
Ana Amma 2000 mumangosatira zili zonse. Makolo ankanena Kuti MCP ndi yoipa munkachita makani. Koma dziwani Kuti makolo athu anazunzidwa ndi chipani chimenechi.
@@EdwardDixies Makolo kumene amanena Kuti ma card anali okakamiza mayi oyembekedzera amatha kuchilira pa njira kukanizidwa kudutsa kamba alibe a ndalama can you emergin ufiti ndeno ndi izi
Ana ama 2000 musamangiwanamizira ,ndi angat anakavotera MCP 2020,, your failure to confront the current problems its not as a result of a certain group that you see so fragile to attack,,kakonzenitu inuyo ama 80s n 90s pomwe analakwisa ama 2000po
Heeeeeee mulungu ndiwamphamvu 🙏🙏🙏🙏 tamvako zisinsi yoooooo 🙆🙆🙆🙆🙆
Ndpo nkhan imneyi yandikumbusa muthalika akumukana kt bushir azagawe chimanga ndpo boma la dpp linkaziwa kt bushir ndi wa magaz eish 😢😢
Yaap
Eyetu Peter amamudziwa bwino Bushiri koma timkamutukwana lero tazindikika kuti anthu adyelawa amkangowona za mpando wa u president lero ndi izi
Anakanadi
INU AMENE MUKUTSUTSA NKHANIYI MITUYANU SIMAGWIRAYI , MUKUONA NGATI UYUYU ANGANGOZUKA NKUMAKAMBA IZIZI? DZIWANI KUTI PALIBE CHOMWE CHINGABISALE PANSI PATHAMBO ILI KUTI SICHIDZAULULIKAYI MULUNGU AMADZERA MWA ANTHU KUTI CHINSINSI
CHIDZIWIKA NKHANIYI NDI YOONA MUKANE MUSAKANE WAYANKHULAZI NDI ZOONA VUTO A MALAWI SIMUCHEDWA KUIWALA KUTI MUKHULUPIRIRE MUKUMBUKIRE ULOSI WA MALEMU GRACE CHINGA MZIMU WAKE UUSE MUMTENDERE , MALAWI ATHA UYU TIKUPEMPHA BUSHIRI KATENGENI CHAKWERA NDI BANJA LAKE KOMANSO ABALE AKE CHIFUKWA KUMENE MUNKAPANGANA A MALAWI AKUFAO KUNALIBE MALAWI NDI OKOMA 😅😅😅😅😅
@@HalisonSolomon Ndipo inu angozifera Malawi
Mulungu awakanthe
Kkkkk kumbukirani Grace chinga mai ake
🤞🤞
Koma Mulungu inuyo ndiokongola 🙏🔥
❤❤❤
Kkk ndowokongoladi tugwirizana
Ndipo ndiowaladi MULUNGU
Allah atimenyera khozo kuti zonsezi zithe
Mulungu mulikodi kumwamba izizi zikuonetsa kuti mcp ikuthela pompa, chonde amalawi tisazavoteleso mcp izi simoyo koma malilo okhaokha 😢😢
Mulungu siwamasewera, zakumidima zayamba kuululika, ndalirira Malawi wanga
Big Amen
Koma DPP singawineso zosatheka
Amalawa vuto boza nde nde timalikhulupila heavy
Man Khan iyi njowona for some reason
Eeeee inu ameneyooo?????
Muzasalatu inu
I remember Grace chinga zimene Anafotkoza asanamwalire
Grace Chinga . May your soul continue resting in peace. U said it, but people ignore that, and Joyce Banda and Bushiri indeed are included as you said earlier,,.. Where do Malawi going to,, we need to Pray hard against this satanism political party,,. Kulibe kanthu konse komwe yehova adzabisire Ana ake
Tipephere amalawi timugwetse bushili afe ndithu, Allah tithandinzeni rabi rabi rabi 🤲🤲🤲🤲
Mmmmm musamapemphere chonchi mulungu simunthu
It's only believers who understand the current situation.The end is near musawasokoneze anthu kaganizidwe ayi
All
Allah make Easy this difficult things for us we can't do nothing it's only your
Power chosani zoyipa zonse
History is the best teacher,kwa amene muri mburi pa tsogolo la dziko ndiomwe mukuwononga dziko. Afiti
Best teacher bwino 😂😂😂😂
Ndipo olo ena akamati bola dzikoli akadalamulira ngt president Bushiri ine ndimangotseka a Malawi kutengeka ndikusamudziwa zintchito zake
Pali mau amati:
Kusadziwanso ndi kufa komwe.
Osadabwa munthu opanda chisoni chifundo eeeeh
kungoti zoopsa km
Zoona
Ambuye mulungu bwerani mudzakanthe ana a njaka Abuka nmalawi wiwa iyhoooo malawi wanga
Chipani cha magazi ananenakale grace tchinga
Yes eshii ananenatu mchifukwa chake anamuphaeshiii
Koma a Malawife kusamva😢
MCP inakhalako asanabadwe grace
Chakwera mutu sukugwira angoyenda ngati zisiru ena ndi awa angodya nsima mma restrant ngati munthu wamba mwazi wa Chilima muyaluka agalu inu
Dramatic vice president 😊
Grace Chinga,ananena kale zadzimenezi ,,,😭😭😭😭😭 GRACE.ANZTIFELA IFE A MALAWI
Ife tidzavotera mcp ndipo uyu amalankhulayu ndiwabodza komaso siiwe wamcp . Galu wabodza iwe. Or ngati akuwuza kuti uzinama zimenezi kadeti iwe ungodzivuta. Mcp tikuwinaso ngakhale mayi ako akudziwa zimenezi. Akuluakulu koma mcp simukugona nayo tulo eti? Simunati mpaka 2050 wooo
Basi mungotenga magazi a chakwerayooo ,,,kusiyana mkutenga magazi aanthu osalakwa,,
Ndipo ngozi zosayamba dairly hmn 🙌
Simmene kuliri 😂😂😂
Malawi the warm heart of Africa ❤
zosayenda
Joyce,bushiri ndi chikangawa tamuoneni chimutu gwape iwe okumwa magazi inu dzisilu inu
Jesus is the king ✝️🙏🙏🙏
Grace chinga asanamwal8re ananena kuti pakubwera chipani koma chamwazi apa mpamene anthu akungofaku.
shalom shalom Malawi ndili ku USA inee 🙌
Ndikumbuka yesu anati ndalama iyi ndiyandani yakayesara paseni mwini wake zamumulungu ndiye zanthu amalawi lero kayesara akufuna zake😂😂😂😂
No wonder ngoz zkuchtikaz ....God protect us
That's why APM amamukana
Mukulakwisa mukupha nazo anthu osalakwa km Mulungu ndi wankulu magazi ameneo musanza muzipha ana anu agalu inu
Uyuu ndi wa bodza akanagokamba za dale zakezooo osatii aipitse anthu ena fotseki
God is watching this and he will rescure as from this,lets pray hard a malawi😢😢
Munthu sangangozuka nkumanena izizi mukuziwana
Akuziwana bwino
Ndipodi muthu ungayambile pati akudziwanadi sungadzuke mkumanena izi usakuziwapo kathu
@@user-bd7nr1vm4u Kodi mesa akutero ndithu
Anachitira meeting akuti Ku Pretoria
Kumeneko ndikomwe kumakhala munthu wawo wankulu (mfiti yaikulu)
Zoona akudziwana
Magaziwo azibweza akutunthu kwawo yemweyo galuyo la 40 lakwana bs eshiii ambuye atopa nawo anthu amenewa mmnn🙆🙆🙆
Chokani inu nditi ndinu, anthu osokoneze mabodza basi
Tsono ngati nkhani ndi imeneyo magaziwo akuwafuna lero bwanji zausiru basi
I remember he said that "I will shed blood "
"Ndikhetsa mwazi"
😭😭
Komabe Mulungu Wathu Ali maso
Aaaaah koma guys bodza linali mukuonjeza mmmmm
Anthu mkuvutika panopa kumbuyoku kunali ziiii koma ndale eeee kufuna kuwina mpakana kumapangisa anthu ena ngati siabwino and zimenezoso muluza nazo chifukwa mulungu akuwona zose
Open your eyes,pray hard fear God brother
Remember kalata ya grace chinga
Ndipo grace chinga amkanena zoona
Asiyeni amene akukanirawa azavomereza Ali kati mwa poto akupsa, tiyeni tipephere molimba dziko laipa ili
Zikamugwera pabanja lake ndipamene azaziwe kuya kwa chisime
Osati kuonong'a chipani koma kuonong'a dziko lero ndiizi chipani cha MCP ndi cha satanic simwazimvera nokha
Mmmmm koma nde eeee ziliko ndpo zikuchita kuonekelatu kt Chakwera ngwa satanic no Wonder zintchito zake za umve zikuoneka...ndpo zoti bushiri akuyendetsa naye boma kwa ine sizachilendo ..a satanic inu koma tsiku ndili modz mzayankha pamaso pa mulungu
Koma zikufika Malawi gozi ndi deile 😮😮😮
respect the MAN OF GOD bushiri. i know a prophet is not respected by his own city or family but remember he brought millions to Christ and saved thousands of souls. if he is a Satanist then what are you? Satanism is done in secrecy so what were you doing to notice his satanism? on behalf of millions of his followers, we are not moved not even a single inche.
Kulibe mcp so ku malawi kuno izo musazinamize
A Malawi ambiri mwasowa zochita ndithu. Don't hate Bushiri for nothing. Mutha nonsenu, ife ndiye sitili ku Malawikoku, munya muwona
Kkkkkkkk iwe usandisekese
Titha phiti ku Malawi 🇲🇼 Boma ili ndila ma Satanism ♥️
Zoona Koma anthu amanena timati bodza
Mzimu wake uutse mu mtendere Grace Chinga
Mulungu wathu ndi wolungama sangalore anthu ake azingolira
Koma titha ndithu onani panopo ngozi dairly athu kuphedwa osaverana chisoni
Is malawi heaven????????
A DPP mukusowa zoipitsa pezani njira yabwino osati zoopsa mukunenazo!
Koma picture mwaikayo mwaganizabwanji kkkkk😮enawo alindinyanga pachipumi😅😅
Aaaaa pezani zochita abwana
Ukunamatu kadet bushir ndi mcp zikugwirizana chyani galu iwe mabodza akowo siya
Mmmmm ndi chifukwa ngozi zikuchitika daily eee ambuye atithandize ndthu'
Kodi anthu inu mukamanama mumapindula Po chani? Audio ya 2016 iyi
A Malawi kulani osamangokhulupilira nkhani za boza izi aaaaaaaa kkkkkk
Ukunama iwe, MCP 2025 boma! Udatani kuzitulutsa pachiyambi pomwe.
Nkhani iyiy inatuluka PA ka nthaw ndithu I think wina wangopanga repost koma zinatuluka 2023
Yeah ATI akubwera lero ndi maboza Ake Kuti apusise Ife apa Kwa ineyo wakanika ndi boza lako tenge ena awo Amit iteta
Nanga zakuchikangawazi mukanaso?? Mcp boma boma Malawi wake uti?? Muona
Yakale khaniyi ndekuti unalibe fn nanga even grace chinga ananena zimenezi
@@SuzgoMkandawire-ss4khndipo inu tingovota mawa atuluka okuphawa
Zaugalu mukapangana kuti mupeleke mangadzi ndiye chifukwa kumalawi kuli mavuto ambili zingodzi tikuziwonazi musokhane nose mupeleke ana anu nosenu mbiri yabushiri mukuyiziwa mukusithanisa ndi magazi anthu moto wamulungu ukufikileni nonsenu nema of jesus fair
Achisiru inu mwasowa zochita sizikuvekat zimene wakambazo panyopako garu ukuona ngat mcp tiisiya mbuzi👊👊
Muli mbali iti mama?
@@OdettaLowrenceokupha awa
Zabodza izi bushiri atani bushiri ili muboma zazi
ife tilipambuyo pa mcp yomweyi chakwera mupaka 2030 wooooooo
Mbudzi iwe
Mcp kuwinaso kumalawi kuno AMALAWI tizatha ndithutu mmm
Anthu mesa ndi opusa akuti mcp ikulamula bwino chifukwa akudya ndalama sakuwelenga zamiyoyo ya mzawo
@@GiftJulius-gx2kbndipo live maka pa central region nde mmmmm ayi azamuvotera ndithu😢😢😢
Ndiwe wopusa kwambiri.Mulungu akukhululukire
Oooh akanalola kupanga mademo cholinga mwaziwo ubwezedwe bwno patsikulo? Mmm km dzkoli ayi Malawidi anakonza
Palibe cisisi pansi panthambo, Mulungu sadzasitha adzakhala iyeyo paka kale
Vuto la sosho midiya wina amangokhuta mowa wache nkuyamba kuyankhula, kwachuluka masewero kwambiri
Musiyeni munthu wa Mulungu Bushiri sakupanga nawo zandale ngati mulibe chonena kulibwino kukhala chete.
Malawi wanga ukupita kuti😭😭😭😭😭😭
Uzikanamiza ana ako zimenezo
abwere poyera timudziwe ndindani ,zabodza basi wagwa ndi iyeyo ,or MP amene akunena izi angawine kwawo? asandikwiyitsenso ndinkhani zopanda mutu wake ngati..
Achitsiru awa
Muzasala inu 😂😂😂😂 muli mbili yakale ana ama 2000
Izi ndizoona kuti Bushiri alimo machakwela koma bushiri upole moto because ndalama ndizanu, koma inuyo mumalawi muno simukhalapo mutendele
Koma GUYS iii
Zovuta kwambiri ndithuu 200%
Komatu abale midiatu iyi ena mupezanazo mavuto wosatha inu ,bwanji wosamangodzigwilila ntchito panokha mkumadzipezela eeee!
Munthuyu angolankhula yekhayekha sizopeka izi
Zopeka kumene wasowa zochita. He doesn't know what tomorrow will bring
The guy has a particle of truth....he is not mad. Take it or leave it
inuso galu munali kt thawi yoseyi chisiru 😂😂😂😂😂😂😂😂
Gays uyutu siwamisala oloso anthu inuyo pena muzitha kuona mene zithu zikuyendera koma ngati munaputa bushier mumila bushili simunthu wamba
Ndi uchitsirutu umenewo kumaipitsa mbiri za anthu iwe ndi galu kobas ukanakhala dolo unakajambula video coz umboni ulinawo koma ka audio kakoka kaonetseratu kut iwe ndi mbuli komanso ulibe mzeru, Kapolo ngat iwe udzafa mphawi chomcho, mabwana wawatchulawa angakumane ndi iwe Kapolo iwe, Chitsiru Cha Munthu.
Ndimadabwatu nkhaza chikangawa
Guys musamawapepeletse anthu pano pa social media, izi ndzabodza mwangokonza ka Audio
Koma bushiri nisataniki yoophwa chakwera nisataniki yoophwa amangogwesa vula.nikupha anthu nichifukwa chake anamuthamangisa ku joni bushiri Kamba kausataniki wake ife tikufuna dpp osati mcp ayi
Koma ngati zili zoonadi kumwamba kulemekezeke ndinthu pakuti Mau amubulu lopatulika amanena Kuti zobisika zizaulika Kuti ukulu wamulungu uziwike
Mesa bushiri ndi satanic nde tiziwona tithilabe nsembe ya magazi
Amalawi tilindivuto munthu akankhala ndi ndalama mukuti ndi wasataniki koma bushiri akuyesesa kumbali yake
Pangani bwino kampeni inu osanamiza ife ngati ndife ana ai pitani uko ndi maboza anu
Mwachende ake Chakwela apeleke magaz ake
Agalu nonse munavotela chakwela munatipwetekesa
Amumwe chakwelayo,,, coz alindimagazi abwino,
Ine2 kudabwa chibweleleni bushili zikoli ngozi 2much eshii disaster Yehova mpothawila panga
Chakwela you mast go
Mkani zepeka izi, zopusa zenizeni
Amalawi ndizimenezotu azabweza magazi
An old audio which was circulating in the past but now resurfacing due to current events but there is sense in this nonsense
Shalom malawi shalom 😢😢😢
Kulila gauys sukutithandiza koman tiyen tizipephera basi athuwa achok
Magazi ake ndi amene akubwezawa ngozi dairy
Eeetu koditu or president ndiwakare koma chilungamo ndi chakut 2025 mcp kulibe kuwina
Malawi Malawi alipamoto dziko lija latha basi chakwera munthu oipa kwambili satana ameneyi
Inu mawu awa sound familiar