Chifukwa cha chipongwe chomwe a MCP anapangitsa kuti ambiri ife tiyambe ndale chonde kwa m'mene zinthu ziliri apa tiyeni tipange Ndale muno M'malawi.UTM never forgotten.
Mai kaliyati mupitilize kupephelela mukanafela limodzi ndi Achilima moti Chikangawa zamavetsa kuti ina kuphonyani pati moti ntima umamuwawa b kuti simuna kwelenao ndege ija Mulungu apilize kukutetezana kungona
Ndipo ndi Mulungu ekha akanakhala ali limodzi. Ndipamene anthu akanalira kwambiri ndipo tsogolo la UTM likanakhala lokayikitsa kwambiri. Because Madam Kaliati she is very strong woman.
Malawians busy crying for someone that didn't even know them😂😂😂😂😂 he was enjoying his life didn't even care for you fam ....you have never even cry like this all this month's kwa abale Anu....stop putting politicians on top of the elephant selfish people 😢
Chakwera ndi Oyipa ndipo ndizokayikisa Kuti angapange zoyenerera pa kafukufuku wa ngozi ya Ndege chifukwa chomwe chinachitika Ku Chikangawa akuchidziwa
Kandiverere adanena za mumaluwa koma aliyense akudziwa ndi kuwona zomwe MCP members omwe ndi akulu akulu kuyambira president amachita kuyenda tsiku lilironse kuwonongetsa chuma chanthu. Tiyeni tizichotse mu Mbavazi.
Akupanga dala bcoz president ali ndi mphamvu zambiri. Ndi zija Chilima amkati mphamvu za president mzofunika kuzichepetsa bcoz amazipanga abuse mkumaswa nazo malamulo. Afa ndi chikumbumtima makamaka akazaluza azalira zenizeni kuti adapha anthu ulele
Chifukwa cha chipongwe chomwe a MCP anapangitsa kuti ambiri ife tiyambe ndale chonde kwa m'mene zinthu ziliri apa tiyeni tipange Ndale muno M'malawi.UTM never forgotten.
Do it kwanuko ndi abale ako.... leave Chilima to rest in peace guys
Chakwera chiwanda cha munthu
We don't do the politics in such way to dismiss the importance people in order to get power this What chakwera did is stupidity and useless mission
Chamba 😅😅😅
@FrankAdoniswatanichakwera-zl6qc
Kaliati ndimakukonda kwambiri ndi mtima wanga onse.
This message must go to chakwera and his government
I will vote for UTM
Speech yolilitsa anthu akulira chikumbumtima chawapeza 😢😢
Musalole kuti imfa ya Chilima ipindulire Chakwera. Chakwera ndi mfiti.
Exactly
True
The struggle continue we need to change the system of government otherwise will continue suffering as foreigners in our own country.
Ndipo ndava chisoni kwambili ndakumbukadi vula ikubwela koma wose anali pa nsewu kupulumutsa dziko m'maja kwa zisenga zitatu (DPP) lelo zooowona mwamupha nzanu ndalila 😢😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
😭😭😭😭😭😭 misozi yosatha chilimawanthu ngati boza ukanyowa tsiku limene umazapanga kampen kudera lathu kuti galuyi awulawe mpando kut umakomabwanji panu ndiyemweyemweyo wakutumizira zifwamba kukupha ngati chigawenga😭😭😭😭 mulungu akuone chikangawa kumeneuliko😭😭😭😭😭😭😭
Sitikulora .amakana kupanga searching chifukwa amafuna anthane nawo Kaye akamaliza mmpamene azinena kuti pitani koma asaiwale mulungu si amai awo. Ndimulungu wa yakobo ndi Isaac ndeno asayiwale . One-day is coming
❤❤❤❤ nkhani yokhuza Report atiuze bwino chakwera Chikangawa komwe aliko
The problem with you is, you have not read the report. You're just getting it from other dunderheads. A Malawi yinatani?
@@georgechifundochiwaula3846koma ase uil ndivuto muzionera plane crush ngati kumatuluka amalipoti awiri akukunamizani kut litulukaso kumakhulupirila kut report ilmatuluka kwari
But the nature will going to its Job softly😭😭😭😭 we still remember him up the end of this world of sadness.
Mwalakhura Bambo inu Ambuye akudalitseni koposa akudzenso malire a Moyo wanu😭😭😭😭😭
Eshiii mwandililisaso bwanji🙆🙆🙆🙆
Matthews Mtumbuka is very intelligent. You have my tevo
I like him too
✅
Ndizongofunika inuyo a UTM kupamga kafufuku osati omwe anachita chiwembu akafufuze okha penapake a Malawi tikulephera
All in all glory to be to God who knows everything than us.
Kakkkkkk A LUTA CONTINUA ,imatanthauza Kuti
Nkhondo ikupitilira
😭😭😭😭😭 zolirisa kwambiri mm
More fire utm
❤❤❤❤my vote
Inu boma satengera poipitsa wina tamangopangan zanu bas mukuganiza kuti mukupangazi mungatipange ife kusnthaa maganizo kuti tisamuvotere chakwera never mukunama 💪💪......mcp boma
Nchimbawako uzionatukoma
Ineso singasinthe maganizo kamba kazopusazo zimene akuyankhula zamanyi awo
Olo wekha ukudziseka comment yako yuduka Mutuyi
😢😢😭😭😭 Yehovah tichotsereni fiti izi
UTM moto 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🥰🥰🥰🥰❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndipo Chakwera mwatilanga Mulungu akuoneni ndithu mukutililira ife tsiku ndi tsiku yoooooh Chakwera kuiwala zoona kuti pa mpando mulipo anakuikani ndi Chilima 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Chilima anafa ifa yowawa 😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Nice speech 😢😢😢
Sitiopa. , mpaka chakwela afe.
😂😂😂😂😂😂 Koma ndaseka, mpaka afe😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
😂😂😂 uyu afa ndithu
RIP SKC YOUR LEGACY WILL LEAVE LONG BIYENI ANALAKWANJI Analakwachani mwanawamunthu anaanjoka inu!
Pajatu anati we can find independent pple to do the investigation
Iiiiih koma chilima abale inu eishiiiiiiii misonzi imagwa ine mkaona pic ya chilima ndiponso moyo wanga umayamba kupweteka iiiiih Chakwera anatilakwira anthufe kwambi mai ineeeeee 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Chitukuko NDI chomwecho deile nkhan yake imeneyo ai zikomo siyani nzimu wa chilima uwuse muntendele 😭😭😭😭😭😭
Kupusaa iweeee 😢😢😢😢
Ause mumtendere mutamupha mtendere wanji mbuzi iweeee
Sinanga mudamupha mukhoza kulankhula ngati mukulankhulira kuphazi zimatiwawatu ,kupusa
Kuputsa eti
Kulira salesana iwe ngati watopa khale chete
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 SKC Rest well 😢😢😢😢😢😢
😢😢😢😢😢and he's gone for good ndmangt azabweraso😭😭😭
Ndife Malawi so osagwilitsa ntchito chilankhulo Cha kumozambique
Mathews Mtumbuka takulandirani
Charcoal is still smoldering
Azingokamba fundo zogwira mtima osati zamaliro achilima mpaka lero aaa
Mama kaliyati timakunyadirani mulungu azikutsogolerani
Ang'alule akuphawa
May I beg you all political party leaders in Malawi to hold a canvass to safeguard us from the current massacre and miscon ceptions.
Replies
kapolo,iwe uzingolemba atwork bas.osati recording yakoyo
Mai kaliyati mupitilize kupephelela mukanafela limodzi ndi Achilima moti Chikangawa zamavetsa kuti ina kuphonyani pati moti ntima umamuwawa b kuti simuna kwelenao ndege ija Mulungu apilize kukutetezana kungona
Ndipo ndi Mulungu ekha akanakhala ali limodzi. Ndipamene anthu akanalira kwambiri ndipo tsogolo la UTM likanakhala lokayikitsa kwambiri. Because Madam Kaliati she is very strong woman.
You guys must have your own private security special agents all the time....dont expect protection from your devorced husband
Kod sound mumaikonda bwanji pamene ife timakuzani kut muchotse
Malawians busy crying for someone that didn't even know them😂😂😂😂😂 he was enjoying his life didn't even care for you fam ....you have never even cry like this all this month's kwa abale Anu....stop putting politicians on top of the elephant selfish people 😢
More 🔥🔥🔥
Olo kulikana kapena olo kutani,siziphula kanthu izi.....Tiyeni tizingolira ,Mulungu ndiye odziwa zonse.....
More 🔥 🔥 🔥 🔥
All the best
Anakuuzani kuti mumpeze wofufuzayo, ndye mpaka pano simunampeze? kapena mwaywala kut anatero? 😂😂😂
Koma or ineyo imfayi iyiyi imandiliza kwambiro or apapa misoz m'maso mwanga yatsikira😢😢
Kubeleka ndikumozi diii 😭😭😭😭😭😭😭
AMALAWI KUPUPULUMA TAONANI TSOPANO ZOVETSA CHISONI MWATILILITSA.
Timapanga ziganizo tili ndi mkwiyo zosakhala bwino
Biyeni anafa mopweteka😢
Music
Imfa yachilima ndiye ikhare kampeni awawa fundo palibe
😢😢😢😢😢😢
Opha mdzake ndilupanga, adzafatso ndilupanga lomwelo
Mcp ndiyakupha chilima sikuti ndi oyamba tiyeni titenge Action mcp yapha ambiri koma vuto timangoyankhula no action nothing can change
Osaopa,osatopa
Tifinya korona zenizeni
Nde mukatelo mupeza mavoti kkkkk mavoti sichipepeso ai
Agalu amenewa aziona mwina amamphuzira kumpha anthu anakafusa kaye tembo asanafe
Munamuphela njiru Chilima munalakwa koma Ambuye ali nanu ntchito 💔
Ndipo mwa nkhaza😢😢😢
😢😢😢😢 ishii zithu zokhudza kwambir
Moti campaign yawo izingokhala yokhudza maliro basi Awa ndizitsiru za anthu.....
Aaah iwe choka iwee
Iweyo nde chisilu choyamba
Rest well Biyeni.
Chakwera ndi Oyipa ndipo ndizokayikisa Kuti angapange zoyenerera pa kafukufuku wa ngozi ya Ndege chifukwa chomwe chinachitika Ku Chikangawa akuchidziwa
The background music is so disturbing
Rip SKC😢😢
Dr mathews mtumbuka takulandilani tikuvotelani muyimile
Ndipo chakwera asapeze mpando oloko wa opposite hiyaa 😂😂
You have to done it yourself musadikile kut apange chikangawa zimenezo chifukwa iyeyo akukhuzidwanso so mfiti ingakasake mankhwala italoza yokha munthu sizingatheke komano muwapemphe kut akupaseni mpata kut inuyo nokha mukhazikitse commission of enquire please please we are waiting for UTM PLEASE PLEASE TITHANDIZENI ANTHU ONSE MWATCHULAWO ALIBWINO KWAMBIRI KUPATULA CHIKANGAWA BASI 🔥 🔥 UTM
Why my eyes are shading tears?😢
More fire 🔥
Kulankhula kwabwino kwambiri wakumva wamva ndithu....chatsala ndi kuchita ndi kukwanilisa zomwe zalankhulidwadzi.
Osamu tchula Chakwera Kuti bwana kumu honga Galu ngati ameneyu mbolo ya make Chakwera kupha Wanthu osalakwa,msambi, Munthu woipa kwambiri Chakwera Panyero pa Make,wosamu nyengerera Chakwera wapha Saulos Klaus chilima ngati Galu
Ikhale independence commissioner's of equally
Ipondeni fada mpaka wina apenge misala
makosana, unneccessary background audio chi sound mmaikacho simatisokosela plz zichotsani chimenecho too noisy, chimabowa
Oooh my l always shade tears guys
Zovetsa chisoni kwambiri 😢😢
Atidura mutu ife eisheeeeee
Chomwe mungaziwe munthu sazisumila yekha , ife a Malawi tingopanga zoti tithane ndi Boma ilipoyi basi, Ndipo chilungamo chizaziwika trust me.
Kandiverere adanena za mumaluwa koma aliyense akudziwa ndi kuwona zomwe MCP members omwe ndi akulu akulu kuyambira president amachita kuyenda tsiku lilironse kuwonongetsa chuma chanthu.
Tiyeni tizichotse mu Mbavazi.
Inetu ndi wa UTM ineso ndikulira nao kma anthu mukundinyoza it's okey
mbuli za utm chipani chawanthu ozungulira mutu
Mtumbuka viva
Ndipo chakwera mmmmmh
Chilungamo chizadziwika next year akachoka pampando
Mcp paulendo basi
Fire director
Chakwela uzafa ifa yowawa anthu tikudandaula mulungu akulange chakwela
Tiwaswaaaatu awa achepa akuopaaa
Komaso UTM siyidzawinapo
Zandikhuza😢
ng'ona zomwezo sizikugonatu ng'ona sizikugona zikufuna kugula ma mp onse
Apanga bwanji komisho of inkwayare poti amupha ndiyemweyo chakwerayo mukutuma munthu amene akubelani kuti akakusakireni yemwe akubelani
Akupanga dala bcoz president ali ndi mphamvu zambiri. Ndi zija Chilima amkati mphamvu za president mzofunika kuzichepetsa bcoz amazipanga abuse mkumaswa nazo malamulo. Afa ndi chikumbumtima makamaka akazaluza azalira zenizeni kuti adapha anthu ulele
Zoona
SKC 💔😭😭😭😭