Kodi ine ndifuse nawo pepani wa mavuto kodi ifa yili kumwela okha okha?kodi njala yili komweko kokha? kalindo lero wasuta poison waja koma kumbukila ngati iwe ukunena kuti ndi agalu iwe ndindani galuso or who
Eya southern region anthu akufa coz central region inapatsidwa ma phone olandilira ndalama from 5hundted thousands to 1million from Chaķwera whiĺe southern ŕegion samalandira nao , people.are starving to death..and also remember that most parts of the southern region Minda was destroyed ndi Freddy cyclone .That's natural disaster ..komanso omwe akulandira ndalama za Chakwera ku central sionse akulandira nao Ena akuzunzika
munthu aliyese akadya chakudya cha poison amafa ndithu ndichifukwa chake ana a ku south Africa amwalira nkhani yake kudya chinthu chimene chili ndi poison ndiye zilizonse tisamagoti boma mmmmm guys
A Malawi. Let's all repent, follow Daniels prayer, Daniel 9 v 4-9. Tinamufuna tokha uyu, MCP kukana chisankho cha Mulungu. Nkhondo iyi siyakuthupi, so talking alone will not work, the host of this channel please let people of malawi know that we have to pray for God to forgive us for choosing what we want. We didn't see the heart of the sheep in wolf's skin. Ephesians 6 v 10 -12. The way ppl were praying and even fasting for in 2019-2020. We must go back there and reverse that curse. Other wise. We will be surprised to see this MCP BACK IN POWER. We must start now if we really need change.
Keep it up
Kwathu kumachinjiri mmmmm😢😢😢😢
Makape amenewa akuonjeza
Keep it up bona ili mmmm Manyaka,boma lopanda Admarc
Ndipo kwakameza tithandizeni mr DC talima almost 30chakuti yrs lero akuti chokani mpaka kutithira ma teargas please tithandizeni matithandiza tikalima chokudya komaso mafees amachoka momwemo
Ulemu wanu the DC ❤❤
Makwana Mr president ❤
Mmm Koma born kalindo ndiye amayakhula thawi zose Koma boma ili NDI losava akudikira Kaye athu akafa ndiye azikqpereka no chakudya
Zosayenda ku Malawi, Michael Usi apite kumeneko kah
Ignore Kalindo at your own peril
The DC mumatiimiliratu,ife chete kudikira inu😂😂😂
Zoona Misokho ya malawi ovutika kumagula anthu oimbaa, 😢😢😢pomwe Anthu akufa ndi njala mdziko muno, Mulungu akuona bwino zonse, SKC and 8 others Mhsrip😭😭😭
Next to my house anthunso akumazakumba but they said it's poisonous zimafunika kutaya madzi when boiling...so sad to see our country like this.
Koma athu ndikumaombela m, manja athu akuphawa ambuye atithandize ndithu
Mwana oopsa kwambiri booooooni kalindoooooo the DC
Ndege ija inaonongeka ku chikangawa, ikanagulitsidwa bwenzi iikanagulira chimanga😭😭😭😭😭
Hy ndiwe one boni
True story
Kodi dziko lonziwa Mulungu lomeneri?Abale chonde Mulungu wathu tithandizeni !!!
The DC more fire
Ndipo dziko lino latembeleledwa , atsongoleri apima , ofunika kuwaphikila masamba.
💔😭 may their souls rest in peace
Koma mmene achulukira police traffic munseumu tiyankhulireni kuchoka pakachere kukumanga nawo kayatu mmm zaonjeza
Koma mpaka ana kumwamwalira aboma Ali momu koma Mr chikangawa akuganiza bwanji kapeyo
May there souls rest in internal piece
Ndipo zikundiopya za njala eeech mulungu atisongolele
Boma la chikangawa lationetsa zinthu😭😭😭
Mmmmmmm zamumvuta kulamulila anthu kumafa kambakanjala aaaa nanga tikafika February kukhala zotani 😮😮😮😮
Allah atichutre cfundo nditu 😢
No vote for MCP, never again
The DC
Ine ndinazililira nditaona ana atamwalira motelomo,koma Ambuye atithandize ndithu boma limeneli lichoke
😂😂😂😂😂 koma nkulu uyuyu zangovuta kut support ikusowa koma ma demonstration ameneyu atha kulanda bom😅😅
Ndipo ndi afisi koopsa the DC
Alick kapapa pwara rako iwe ukukoza osagwirizira ukufusa Fuso ramanyi pakwinya pako iwe wa MCP ulinawo limozi ndichifukwa ukufusa
Chopelekela misokho ndichani tiyamba kusiya kupeleka kumaba ndrama basi
Muchoseni chakwera yo!!
No vote for mcp at all
amene akusapotabe mcp pano ndi mfiti
Tithane nazo Chaka chamawa😢😢
Bon, keep it up telling them the truth
Kodi ine ndifuse nawo pepani wa mavuto kodi ifa yili kumwela okha okha?kodi njala yili komweko kokha? kalindo lero wasuta poison waja koma kumbukila ngati iwe ukunena kuti ndi agalu iwe ndindani galuso or who
Muzipemphera amwene mulungu akuchitileni chifundo ngati umaganiza bwino
Eya southern region anthu akufa coz central region inapatsidwa ma phone olandilira ndalama from 5hundted thousands to 1million from Chaķwera whiĺe southern ŕegion samalandira nao , people.are starving to death..and also remember that most parts of the southern region Minda was destroyed ndi Freddy cyclone .That's natural disaster ..komanso omwe akulandira ndalama za Chakwera ku central sionse akulandira nao Ena akuzunzika
Abwanyanga ziwanda
alick kapapa ndiwe galu wachabechabe in other words chidzete chamunthu wungomwalira iwe munthu wopanda phindu padziko lapansi nzeru zako zopusa
Mesa akafuna atiphe ndinamondwe apa atipha ndinjala
Kung'alula kung'alula basi
Ambuye mundikhululukire chifukwa ndinali mmodzi mwa athu omwe ndinasankha nawo lazaro Chakwera kukhala president wadziko lino lero ndi izi ana kms abale athu ambiri akufuna ndinjala kamba ka chisankho cholakwika chomwe ndinapanga 😢
Tinaika pa mpando chigwenga ambuye atithandize ndipo atikhululukire
@@MariaNyamwera Ndipo zoonadi sister tinasankha molakwika Eish!
Ndiye Titani?
The DC awuze mbuzi Za anthu
Aaa zako izo Ife sizikutinkhudza zomwe.ukuyankhukazi aise, zankutu
Uli ndichiwanda chachikulu .sukumva Chisoni ndixomwe xikuchitikilamu?
The Dc Bon Kalindo tiye nawo amenewo paka asiye zoputsa zawonzo
uchira!!!!!!!
Wulemu wanu abon
munthu aliyese akadya chakudya cha poison amafa ndithu ndichifukwa chake ana a ku south Africa amwalira nkhani yake kudya chinthu chimene chili ndi poison ndiye zilizonse tisamagoti boma mmmmm guys
Boma ilili latizuza kwambili
A Malawi. Let's all repent, follow Daniels prayer, Daniel 9 v 4-9. Tinamufuna tokha uyu, MCP kukana chisankho cha Mulungu. Nkhondo iyi siyakuthupi, so talking alone will not work, the host of this channel please let people of malawi know that we have to pray for God to forgive us for choosing what we want. We didn't see the heart of the sheep in wolf's skin. Ephesians 6 v 10 -12. The way ppl were praying and even fasting for in 2019-2020. We must go back there and reverse that curse. Other wise. We will be surprised to see this MCP BACK IN POWER. We must start now if we really need change.
Chakwera sali bwino ena mkumati boma ndilomweli za ziii
Boma lako lagawako chani galu iwe pita ku Tikufelanji azimayi aja akukudikira uku
Koma yah
Boma ili laonjeza, akatero azing'amba kukamwa kumati Boma ndi Lomweli..... Mfiti za anthu zikungoba ndalama kumapita kunja chigulu cha anthu.... Busy kupasa ndalama Oimba malo moti apeleke zosowa kwa osauka kuti azipeza mphamvu zopitila ku sonkhano wanu wa ndale..... Amfiti inu opanda chisoni.... Agalu 🐕🦺🐕🦺
Zombvesa chisoni boma ili abale, ali busy kugula anthu, pamenepo nde mukudziwonetsera kuti mulibe di mzeru palibe amene angakumbvotereni anyani inu munya muwona Mulungu akuwona zonse mukuchita la 40 likukwanilani pompano,
Wakupha uyu
Chakwera is evil
Chikangawa party ndi zintchito zake
Kodi uyu president wa anthu osauka bwanji naye anuwake sakutigawira chakudya
Tauzeni makapewo
Tingodikira 2025basi
The DC woyeeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Chipani chapatumbo cha MCP mbuzi za anthu
Eeeeee mpaka kukachotsa mimba kunja, km timvazinthu
zovuta
Kumangolankhula ngakhare thumba limodzi osathandizako pamalirowo
Boma ili ndilafiti
Zoona guys 😢
Koma anthu tikumvutikadi eeeeeish.....Ayi Zikomo
Vuto amalawi kaya ndi umbuli wanj, tikuvela achina chimwendo banda, zikhale ng'oma, chawez kut dziko likuyenda bwino, pomwe amalawi ambiri ma millions akuvutika uko, boma ili komanso anthuwa ationelera kwambiri ndipo Atitola zedii kut ndife zitsilu, mbuzi za anthu, akudziwa kut tikavotelanso
Koma Malawi wafka poti eeee mphaw slibeso kothawila
Kma to say the fact zafika posauzana eish Malawi wakale uja tamulira kma ambuye atichitire chifundo ndithu
The DC ❤️🔥
Iwe chichewa chako sichikumveka bwno ,ukufuna uyankhule motani ?
Tayankhula chiyankhulo chomwe umayankhula ur mother tongue .
Anatilodzayo ayindinthu adatilakwira
Kumwerako mukufa ndi njala chifukwa chakudalira
The DC more fire
The DC