December, 2003 when i was in Standard 6 is the time this famous album of him was released. Tigwilane Manja. I loved every track from this legendary album but this song still stands out above them all. My mom passed away and this song carried me throughout my school years. This song made me the man i am today. Ankasa pitilizani kuyimba nyimbo za malangizo chonchi. You are the best Mr, i love you.
MADALITSO OCHULUKA APITE KWA ANUWAKE SITE IYI.INEYO WANGA NDI UMBONI WAKUTI SINDIMAGONA TULO POGANIZA ZA KATUNDU UYU WA NYIMBO KUTI KODI NDIDZAMUPEZA KUTI.CHIFUKWA OLO PA INTERNET SAMAPEZEKA AYI.NYIMBO IYI NDIYOOPSYA PA MOYO WAMUNTHU YEMWE SAFUNA UPANGILI WA MAKOLO AKE.AMENI AMBUYE AZIMUDALITSABE M',KHASA.AMENI AND AMENI

Motivated brother
azakutola ndani pano makes more sense than before 🤣🤣🤣
ndipo apapo ndipomwe yonse imalowezeka bwino🙌🙌🙌🙌ndakhala nduyisaka koopsya nyimbo iyi😂😂🙌
Pamenepo bola ukanaziwa nychito yamanja ❤❤❤ ndikonda pamenepo
Joseph Mkasa remains my best artist
Nkasa uzimba koma nyimbo iii unafasa uremu wako ❤❤❤❤
I remember this song in 2003 I was in form one, respect nkasa
Nyimbo iyi ntaivera ndiliku secondary school inandipangisa kuyamba kulimbikira
To take your time listen to and understand what this song tries to portray its wisdom on it's own. Bravo Mkasa you have served many
Just pure talent..... live long fadah pano ndnakula ndpo nyimbo iyi imakhalabe ikulira mmutu mwanga
Indeed this man is a prophet.
It reminds me of my late father who used to put these songs on his playlist
May he rest in peace
Nkasa you are the best artist nyimbo zatanthauzo
Very touching and educating......maso ali psuu ndi utsi wa chamba
This song reminds me my late bro Bahati mmmm my bro continue resting in peace
MADALITSO OCHULUKA APITE KWA ANUWAKE SITE IYI.INEYO WANGA NDI UMBONI WAKUTI SINDIMAGONA TULO POGANIZA ZA KATUNDU UYU WA NYIMBO KUTI KODI NDIDZAMUPEZA KUTI.CHIFUKWA OLO PA INTERNET SAMAPEZEKA AYI.NYIMBO IYI NDIYOOPSYA PA MOYO WAMUNTHU YEMWE SAFUNA UPANGILI WA MAKOLO AKE.AMENI AMBUYE AZIMUDALITSABE M',KHASA.AMENI AND AMENI
Nkasa ndi machine eeeh ulemu wanu
pure music. very educative. bravo Nkasa
Nyimboyi amandikumbusa mayi anga akudwala ndipo ndimangozililila ndekha
Greatest of All Time
Louder and crea moot adzakutora ndani moyo wawulesi
Nyimbo iyi olo mwana wanga ndimuyimbira
Eeiishh I remember when I was in Lilongwe 2004 hustling
I remember my father akundiuza kut uzikhala bwino ndi anthu.
Was looking for this one, thanks
My song when I was teenager more fire
Katswiri 🎉
A prophecy being vindicated..
Full of malangizo ,powerful
I remember this song before my uncle dead he said I must work hard in my life
This song reminds me about a certain location in mzuzu around four ways mma 2005 ndli std 2
❤❤❤ we love bg boss mn
Dzuwa salozerana awa chauta anawadalitsa pa luso loyimba nyimbo zatathauzo
I love songs from mkasa ever and ever
Nyimbo izi mpaka muyaya
These were prophecies to some people 2003,2004 it was beautiful & remains a beauty 02/2024
Powerful message
Nice one🔥🔥🔥
My favorite song
❤❤❤phungu
My favourite song ❤❤
very powerful massage
This song makes sense
My favorite song l never forget this song
Legend ❤️
Ndavera ka 10 day imodz yandikhudza
ndekuti iwe umatibula anthu eti
It gives advice to children my behalf
Ana ovuta kulera mumakula moyo ovutika
Muzanga 🎉🎉🎉🎉🎉
2003 when I was in grade 11 I love this song
Nice one
Izizi ndizonyimbo not zomangolozazi sha😅😅😅😅
Legendary ❤
one chifundo ku CK andala 2002 production fadah
Nice 🎉
Machine
Kodi mkuluyu alipo
❤❤❤❤❤
Phungu indeed,
Mbambande Nkasa
In love with.
Amen
My song
Perez Paul Garcia Barbara Garcia Brenda
😂😂😂
Mbambande Nkasa
❤❤❤