ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Nyimbo iyi yikundikumbusa my brother amayikonda so much continue rest well my brother Frank phiri
This was a special Request. We are preparing to throw the whole album. Stay tuned 👍🏽
Okay
I was looking for this song 😅😅🙌
Please I need Joseph nkasa kulira kwa amphawi, please
0:22
Help me with Jimmy T (James Tsamba)'s songs of Malume and Zabwera Nkhoswe please.
Justice for mkasa nkhani iyi sinathetu😂😂😂😂
Hahaha ndipo he needs his car😅😅😅
@jamestewesa1046 ndpo live 😆
2024 still a hit nkasa ndakamuna
Anava yomweyo even panopa chakwera anatilonjedza zambiri koma mmmmm ambiri anava❤❤❤😂😂😂
Kunoso ku Chimvano ku Ntcheu tinanva ndithu
Hahaha ifeso balaka tinanva😅
Nyimboyi yandikumbutsa ndukhala ku Bangwe/namatapa a landlord amasewera album yonse coz amaphikako mowa😂 nde dailytu and mkasa mnamudziwira kumeneko eeeee yandikumbutsa kale
Nkasa ali Nkasa nthawi imeneyo
yine nyimbo yimeneyi yimandikumbutsa transporter wina 2003 anandilonjeza kuti anditenga kupita ku joni ndimpatse 3000 kwacha kuti 4000 kwacha ndikampatsa ndikakyamba ntchito ndiye ndinagona kunyumba kwake kutacha anandiwuza kuti sanditenga chifukwa ndalama sikukwana
Mmmm nkhaza.. kma munafikako ku South ko?
kkkkkkkkkkkkk akutitu by requeast, ife nde tinkaifunatu nyimboyi tisaname, mesa promise inali yawo a president wo
Promise is a credit, if this could be true still Muluzi has a debt to be given back to Nkasa period 😂 😂
Ndipo zimamuwawa😅😅😅
Nyimboyi yimandikumbusa mzanga wa ine akayikonda zedi
I love phungu Joseph nkasa
My favourite song I remember 2003 I used to sing this song the time
True
My artist of all the time
Mutch respect to your soul Jimmy❤❤❤
Koma kale anthu amapha sound ❤❤
Nkasa your just my all time best ❤
Uyuyu ndioyimbadi mmmmm
Nice one been looking for the whale ulbum
Best of the best wise man
Anikumbutsa ndukhala ku ndirande Ma bar akumeneko usiku onse nyimboyi kuchedzera koma sitinkagona ehhh
🤣🤣🤣🤣osamasewela NDI oyimba amayaausa mophiphilisa .nde kwalelo Atha iukuyalusa mmpiano kkkk
Muli bho.am waiting for ndimukonda bwanji mdani
Uyu siwamasewelatu amapeka nyimbo kkk
Ndye atsogoleli akumalawi amenewo,amakhuluilira bodza
Nice song the King of Malawi
Mbambande anava
That was in 2003 when I was in Std 4😊How time flies!
Exactly
Timayendera limodzi eti?😅
Pano uli std chAni😂
Ku Ekwendeni nafeso tinamva
Bakili analonjeza Galimoto because he was very excited 😊, Never make promises when ur very happy
OF COURSE BUT ITS GOOD TO FULFIL OUR PROMISES
@@GreciousNkhomandipo straight
It brought me back to 2003
Masiku amenewo
Akuti anamupatsa koma anaimwera mowa
Ndesakanatulutsa song Nkasa ndumudziwa
Anthutu mukumulakwira zedi sanalandireyi n pa interview anayakhulanso
This time was at ekwendeni, was in standard 3 koma 😂😂😂😂 nthawi nkachitsiru ndithu kkkk
Good Messnge mukasa
Akuti anamupatsa kma anaimwera mowa😊
Zabodza
Andale ndi aboza
Koma nkuluyu anamulakwila kwambili to be honest 😢😢😢
Kale Langa ❤
Uthenga kwa bakiri muludzi kasa akudandaura
Vunga zambilizo bro watikumbusa chikale
Koma ndiye amudandaula bakili mpaka kumukumbutsa kut anthu onse anamva😂😂😂 ife amatinamiza kuti lero mudya galimoto yachimanga ikubwera ilimunjira basi bakili amangiyankhula zomwe aganiza basi😅😅😊😅
Broh tikufuna choti didididididi!!!chizimveka
Munthu wamkulu ameneyu
Koma nyimbo tinaivina iyi kalekale mmmmIkundikumbusa ndilikwanthu kumachinga !Nditangoyamba kumene kukhala ndi chibwezi😂😂😂😂😂😂😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
.....
Ukanatimveseresaso speech ya ntundayo😂😂😂.. Muluzi has never been serious even today
I like this song 🔥🔥🔥
Kkkkkkkkkkk eya mwina wayiwalaka
😅😅😅😅😅
Mpasenj galimoto yake bwana😂
The best lyricist
Bakili please give him his car abeg😂😂😂
Umaitha bro, keep it up, nkasa ali ndi mfundo😅😅
Nyimbo imeneyi izausankhan
Ndili form 3
Osamapanga chibwana ndi Nkasa 😂😂😂😂😂😂
Still waiting up to now,, don't be tired chief
Plz throw the whole album
Anamva chikangawa
Nkasa ndi akatundu guys muluzi mpase chokwera chake legendary yu please
Help me with James Tsamba (Jimmy T) songs especially Malume and Zabwera Nkhoswe
Nkhani ija pano ndi nyimbo yobheba
Indeed tinava
Promise is a credit give him please
ati chikumbumtima chikugwireni🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mpatseni Galimoto inu fumu ya dziko
Mesa ati anagulusa kkkkkk
Chamuma 2004 umo eish
Mkasa kukakamira 😂😂😂😂
Akathundo
Kma Mkasa 😅😮
Bakili suwomutengela nane anandilonjeza sapato atakhala present anakana adati size za sapato sangaziziwe zatonse😂😂😂😂
Bigy nkasa
Km adalandira😢😢?
Koma a muluzi munamulakwira nkasa bwenzi mutapatsa kena kake kaya azikakha
Thanks Bro, just keep on uploading many
It was true story tell us😅
@@kingmshanga342It was a true story . I know the story 😅
Ndinkhani yazoona anamulonjezadi then osamupatsayi mpakana Lero
Za vuta bwana
Kkkk kma mkasa
Joseph khasa sorry bakirimulus boza
Thnxxxx
❤
I wish I could give him a car if I had money but I'm broke
Km messeng yabwino
😂😂😂
😂😂😂😂
Nyimbo iyi yikundikumbusa my brother amayikonda so much continue rest well my brother Frank phiri
This was a special Request. We are preparing to throw the whole album. Stay tuned 👍🏽
Okay
I was looking for this song 😅😅🙌
Please I need Joseph nkasa kulira kwa amphawi, please
0:22
Help me with Jimmy T (James Tsamba)'s songs of Malume and Zabwera Nkhoswe please.
Justice for mkasa nkhani iyi sinathetu😂😂😂😂
Hahaha ndipo he needs his car😅😅😅
@jamestewesa1046 ndpo live 😆
2024 still a hit nkasa ndakamuna
Anava yomweyo even panopa chakwera anatilonjedza zambiri koma mmmmm ambiri anava❤❤❤😂😂😂
Kunoso ku Chimvano ku Ntcheu tinanva ndithu
Hahaha ifeso balaka tinanva😅
Nyimboyi yandikumbutsa ndukhala ku Bangwe/namatapa a landlord amasewera album yonse coz amaphikako mowa😂 nde dailytu and mkasa mnamudziwira kumeneko eeeee yandikumbutsa kale
Nkasa ali Nkasa nthawi imeneyo
yine nyimbo yimeneyi yimandikumbutsa transporter wina 2003 anandilonjeza kuti anditenga kupita ku joni ndimpatse 3000 kwacha kuti 4000 kwacha ndikampatsa ndikakyamba ntchito ndiye ndinagona kunyumba kwake kutacha anandiwuza kuti sanditenga chifukwa ndalama sikukwana
Mmmm nkhaza.. kma munafikako ku South ko?
kkkkkkkkkkkkk akutitu by requeast, ife nde tinkaifunatu nyimboyi tisaname, mesa promise inali yawo a president wo
Promise is a credit, if this could be true still Muluzi has a debt to be given back to Nkasa period 😂 😂
Ndipo zimamuwawa😅😅😅
Nyimboyi yimandikumbusa mzanga wa ine akayikonda zedi
I love phungu Joseph nkasa
My favourite song I remember 2003 I used to sing this song the time
True
My artist of all the time
Mutch respect to your soul Jimmy❤❤❤
Koma kale anthu amapha sound ❤❤
Nkasa your just my all time best ❤
Uyuyu ndioyimbadi mmmmm
Nice one been looking for the whale ulbum
Best of the best wise man
Anikumbutsa ndukhala ku ndirande
Ma bar akumeneko usiku onse nyimboyi kuchedzera koma sitinkagona ehhh
🤣🤣🤣🤣osamasewela NDI oyimba amayaausa mophiphilisa .nde kwalelo Atha iukuyalusa mmpiano kkkk
Muli bho.am waiting for ndimukonda bwanji mdani
Uyu siwamasewelatu amapeka nyimbo kkk
Ndye atsogoleli akumalawi amenewo,amakhuluilira bodza
Nice song the King of Malawi
Mbambande anava
That was in 2003 when I was in Std 4😊How time flies!
Exactly
Timayendera limodzi eti?😅
Pano uli std chAni😂
Ku Ekwendeni nafeso tinamva
Bakili analonjeza Galimoto because he was very excited 😊, Never make promises when ur very happy
OF COURSE BUT ITS GOOD TO FULFIL OUR PROMISES
@@GreciousNkhomandipo straight
It brought me back to 2003
Masiku amenewo
Akuti anamupatsa koma anaimwera mowa
Ndesakanatulutsa song Nkasa ndumudziwa
Anthutu mukumulakwira zedi sanalandireyi n pa interview anayakhulanso
This time was at ekwendeni, was in standard 3 koma 😂😂😂😂 nthawi nkachitsiru ndithu kkkk
Good Messnge mukasa
Akuti anamupatsa kma anaimwera mowa😊
Zabodza
Andale ndi aboza
Koma nkuluyu anamulakwila kwambili to be honest 😢😢😢
Kale Langa ❤
Uthenga kwa bakiri muludzi kasa akudandaura
Vunga zambilizo bro watikumbusa chikale
Koma ndiye amudandaula bakili mpaka kumukumbutsa kut anthu onse anamva😂😂😂 ife amatinamiza kuti lero mudya galimoto yachimanga ikubwera ilimunjira basi bakili amangiyankhula zomwe aganiza basi😅😅😊😅
Broh tikufuna choti didididididi!!!chizimveka
Munthu wamkulu ameneyu
Koma nyimbo tinaivina iyi kalekale mmmm
Ikundikumbusa ndilikwanthu kumachinga !
Nditangoyamba kumene kukhala ndi chibwezi😂😂😂😂😂😂😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥