Koma nkhani zobweleza bweleza zisamachuluke plus osamachulukisa kuseka kumakhala serious osamawonesa ngat ndi Comedy kwenikweni Tizingoziwa ndifeyo tikamawonela kut ndi Comedy koma inuyoo Muzingokhala active bas for sure Zizikoma kuposa apapa koma zili sharp ndithu ndala Jay
Pitilizani guy always bg up jay jay cee 👌🇲🇼
Who noticed kusintha kwa pa sitting room😅
Kambodya 🎉🎉🎉🎉
😂😂😂😂kambodya mwez siunathe tchito ilimba km
SHOW FUDZE COMEDY
Kkkkk za nice
Muli bho kwambiri 🔥🔥🙌
Kkkkkkkkk uwawuze kuti ndili ndi wina wake ochita bwino
SHOW FUDZE COMEDY
Kkkkkk kom yhaa big up guys
😂😂😂😂 nzanga ndi ochita bwino
Ase ukubwela bhoo ❤
Fere 🔥😂❤❤❤❤❤❤❤
Kkkk yeah moyo ngat uli ndi achibale umabeba moyo kuzi njoya nda chibale
SHOW FUDZE COMEDY
😂😂😂😂😂 km ndaseka
Kaziyo akuonesa kuuma wez bat angokoza akhale womasuka mwaukazi
Nice one majidaz
Zili bho kwambir❤❤❤ kmno Mr kambodya u have to change voice yo sili bho
Ali Ndi Nyumba 😂😂
Pena ngat bwana ndi @ACE KAY kkkkkkkkkkk mene wauswela jekete eeeh zinazaketu
Ndiye mwati nyimboyi anaipha ndindani
Kkkkkk pajatu mabwana sakokomeza ulusi kkkkll
@HenzoniceMW kmabe amawiika pa level kah kumaonesa kma siiizi eeh
Nice one guys mumayitha
Khenge hvy tazifira
All Zambians gather here ✍️🙏
SHOW FUDZE COMEDY
Amathadi ndikudziwa bwino, Khethiwe yo 😂😂👍
Ndidzasankha konkuno kkkkkkk
Ikuchita kusangalasa nice one koma mumantha
Kambodya wachamba akukanika kuyankha😂😂
Nice tune man Joy
Maintain this guys mukutha heavy
😂😂😂😂😂 koma iyi ichema🎉
Zili bho kom kumangobwerezabwereza nkhn ndili ndi ndlama ine mose mwayambila mutu wakhan sukuziwik
Anthu akumasokosa panjawo simungamaauze akhale chete
Mulibho guyz
Kambodya acting ngt asodo kkk
kodi adah awa si aja anafikila pakhonde mkumati ndikufuna nzanga then atatuluka anangoti iwe sukundidziwa
Pajatu ananena kut ndkufuna ganyu😂😂
Kambodya wangomutenga Isaac ndendende
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤Twepano
Kkkkk bwana wakeiya2
SHOW FUDZE COMEDY
Yatha fast Koma ili bho kwambili 😂😆😆🤣
Ndimuyimbile ace kay
Koma nkhani zobweleza bweleza zisamachuluke plus osamachulukisa kuseka kumakhala serious osamawonesa ngat ndi Comedy kwenikweni Tizingoziwa ndifeyo tikamawonela kut ndi Comedy koma inuyoo Muzingokhala active bas for sure Zizikoma kuposa apapa koma zili sharp ndithu ndala Jay
Kambodya vep ilibe xogolo
Ati zasakha kokuno😂😂
SHOW FUDZE COMEDY
Koma kambodya aaah!!
SHOW FUDZE COMEDY
kkkk koma yachema kkkk
Komano kambodya yo acting Samantha nanga adzingoti ndili ndi ndalama ine, ndili ndi ndalama ine
@jay jay cee ati ndili ndalama ine😂😂
Gyz iyi video Yi ndimbola Yolanda voliom
Kkkk ndi wolemera ndidzanga kkkk kkkk kkk unene kut ndidzanga
Mwabebetsa gaezi
FIRE
Ili bho ❤❤❤
Zayamba bwino kwambili 🔥🔥
SHOW FUDZE COMEDY
Mumakwana inuyo anyamata akambonja
Taponyani pat 1 zinalo motan
😂😂😂😂😂 km kambodya
Kambodya 🤣🤣
Good acting Mr kambodya
Kkkkkk km kambodya sazatheka😂
🎉🎉🎉🎉 fire 🔥🔥🔥🔥🔥 guy
Kambodya 😂😂😂😂
SHOW FUDZE COMEDY
Nice
SHOW FUDZE COMEDY
Mwakomesa kambodya😅😅
🔥🔥😁😁😁😁
😂😂😂😂😂 fouls of kambodya😂
Wamasuka mnyamata kkkk
Nice gyz
Ase wachotselanji chi pic cha mwini wake ngat nyumba ndi yako kkkk kma iww
koma anamelera akenso
Mumakwana
The girl coordination
Next please 😂😮
Nyimboyi anaipha ndindani mwati???
Spy t
@@ticksymk1149 wow okay
Uli ndi ndalama iweo😂😂
?Nyumbamo i think muli camera
Next
Mukuveka inuyo
Next guys you started very well I hope you'll never disappoint us as your followers
Warrior❤❤❤
Waiting
😂🙌
Mmmmm komakaambodya🤣🤣🤣🤣
Za dolo
❤
Guys muzipanga story otherwise muzionela noka
😅😅😅😅😅
Nice, koma dressing yapa sitting room yasintha from no where boss..
Kod nd nyumba ya JJC??
size yabwino madolo koma voice yanuyo muziyikoza cz mumarakhura ngt mwarezera bwanji kape zamba zinakupwetekani
🤣🤣🤣
Kulemela moya
There is room for improvement on your acting skills.
Km guyz
Komatu zovakazo ai zikomo
Next time learn how to hide phone kutimisawoneke Kati waidula take note bro 😂😂😂😂 big up km
Zilibho
Tikufupika
😂😂😂😂
Nyamata
Koma zlikoliko 🤐
Kkkkk
You can do better than this
Kambodya 😂😂😂
Next
😂😂😂