Thanks you talk through answer I believe you help us to malawian people I like your answer talking you can open Jude 1vs24-25 please you can remember always God bless you but remember you talking day and night I'm Lonald E mumba I'm preacher for Last church of God his Christ international I support you
I liked UDF especially when it was led by Bakili Muluzi. He used to handle things with maturity. Buy now from what our current president is saying l have some reservations because he makes unstable critical decisions at certain times.Well let's pray for the party to move in the right direction
Mavutowa alipodi koma vuto atupele simungakhale presdent izi muchedwa tiyeni tizipita ku DPP. Anthu maso ali pa DPP, UDF yagudwa ife zimenezi tikudziwa
awa sangatithandizde akungofuna kupitiliza kusamala chuma chawo chifukwa zikuwoneka kuti akufuna kuphatikira ku mcp kuti chuma chawo chipitilire and kunena kuti akagwiririzana ndi chipani akhale torch bearer akungofuna kuti adzawapatse u vice president rather than u minister okha kkkkk ndani angapange ubale woti iwowa akhale torch bearer?

finally you showed up, where were you all these years, let me vote 🗳 in advance AMP 💙
I liked UDF especially when it was led by Bakili Muluzi. He used to handle things with maturity. Buy now from what our current president is saying l have some reservations because he makes unstable critical decisions at certain times.Well let's pray for the party to move in the right direction
My vote ☑️
Sakuyankha according to the questions
That's true mr president
Ngati peter muthalika anatibela panopa akufuna atipusitseso
My vote 🗳
Brian Banda anali kuti aaaaa akanapanikiza pusiyi apa
That's dreaming!!!
UDF payokha sidzaphula kanthu ndipo alliance imene munapanga ndi Dpp ndiyimene inakakuthandizilani kuti mwina nkudzakhalako mtsogoleri koma payokha udf olo mutasintha ma presidential candidate motani ndipo nthawi olo yayitali bwanji simungawine
Komaso uyu ndiopusa mene anadayambila kuyakula muja ku dyila iwe ukutandauza chan iwe bambo Ako alibe nyila
Sakuyankha mafunso Atupereyu
Koma wasemphanadi ndi funso uyuyu.
Atupele ndi wabwino koma zikuyenera aganize bwino coz tikapusa ku opposition sudzawina ngati sapanga umodzi
Exactly
Mwanayi alibe nzeru wangokula mutu basi akuyakha zosiyana ndi mafuso
Sakuyankha nkomwe ndipo akungofotokoza basi. Komaso zimene akufotokizazo sizikukhudzakosi olo pang'ono pamafuso amene akufunsidwawo.
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mukunama bakili muluzi zangapereke mwanawake kungo ona
Tsongoleli ndi uyuyu osati ndale zomangonyozana
There we again
Mcp oyeeeeeeeeee❤❤❤❤❤❤❤
Wakufunsa ndani pano
Vote yanga straight yizapita kwa atupele muluzi koma chonde musayelekeze kulowa mcp bwana tupele mutikhumudwitsa kwambiri
Zero marks zikuvuta pati iwe atupele kuyankha .wadya ndalama za chikangawa party Kani?
& there is UTM political party & it's candidates are more serious than all these candidates
Mavutowa alipodi koma vuto atupele simungakhale presdent izi muchedwa tiyeni tizipita ku DPP. Anthu maso ali pa DPP, UDF yagudwa ife zimenezi tikudziwa
Zobayu sakuyankha mafunso
Tiona m'mene alili chifukwa anasowa zedi, Tupele more fire
M'bale wanga, dzichepetseni kuti alliance ikhalepo ndcholinga chongochotsa MCP pa mpando bas zinazo zioneka coz mukaima panokha muli zero
Panokha simungawine inu asaa
Kkkkkk sukunma sangawine
Hope yasala kumalawi ndi atupele basi koma anthu samadziwa kakaka ndi zakubazi ndizi tikuvutika kudziko lathu tiyeni lipase mpata mwanayu ndithu m'malawi tizazimba lokoma
Carthy ,ndevu zamwayi ,pankuku komaso Brian,,,iyiyi timayitchula moyinyadila kut big 4 team ya chabe kwambili
Ndipo ngati mukufuna gwilizano immediately mupite ku dpp
IWE SUNGAWINE PAWEKHA KOMA UPANGE MUGWIRIZANO NDI DPP APO NDIYE UDZALOWA MUBOMA KOMA PAWEKHA UKUNAMA 50+1 SUNGADUTSE PA WEKHA
Uganizi bhobho zagwilizano bg boss
Kodi ameneyi ndi opusa eti Mesa anati wapanga retire
Ganizanu bwino nkhani ya alliance please 🙏
Akuti ikhoza kupanga Boma that means their faith is too small.
Ai tamiveseleni kaye atupele akunenazo
Udf ikulowa ndi MCP ndithu
Sakunena strait uyu wadya za Chikangawa
Awa sangakhale a President azikhala minister basi.
Bwana atupele tili pambuyo pano 2025 boma
Bwana atupele timakukondani kwambiri ndipo chembekezo chathu chili painu koma tikuchenjezeni kuti musayelekeze kugwilizana ndi mcp choooooooooonde
Atupele ndiwabwino koma panopa akuoneka ngt wadya ndalama za MCP
Nkhani apa siya MCP. nenani zomwe akunena Atupele. Andale musaiwalire kuti anthu okhwima mnzeru tinasankha munthu amene tizavotere
Amagubila DPP awa
Atupele udf panokha simupata kanthu anta musakule mtima
Atupere alibwino, ndidekha, ndiolemera kale, wachinyamata, ogniza mwachangu
Yellow payokha siyidzalowa mmboma ayi
Zowona ndiwosaba ameneyo amalawi timupase voti yathu tayesapo zinazi
Indedi tiyesedi imeneyu mmalo mwachilima
Mau ogwila mtima bola ngat zili zoona zimenezo
awa sangatithandizde akungofuna kupitiliza kusamala chuma chawo chifukwa zikuwoneka kuti akufuna kuphatikira ku mcp kuti chuma chawo chipitilire and kunena kuti akagwiririzana ndi chipani akhale torch bearer akungofuna kuti adzawapatse u vice president rather than u minister okha kkkkk ndani angapange ubale woti iwowa akhale torch bearer?
Ngati kuli kopita mupite ku dpp
🇲🇼
Sangawine uyu olo zitatani
Usapite ku Dpp paja adakuberani kale Boma wa dpp wa
Chimutu ngati mapwala a mbuzi
Aganize bwino za mgwilizano
Ndiwe wabodza palibe amene amapita kundale kukagwira ntchito ulere, aliyense akamagwira ntchito amafuna phindu koma vuto andale, too much kuba
❤❤❤ 17:06 17:09
Palibe chomwe angapange awa🤣🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂😂 atupere
Mabig atupele tiyeni tipaseni sapoti mwina mwamwayi zikolinja lizayenda bwino kwambiri