Umboni - za mkwatulo komanso zina zowalepheretsa anthu pa mkwatulo komanso

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 14 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 8

  • @shadreckthandaza1059
    @shadreckthandaza1059 ปีที่แล้ว +1

    Uthenga wolasa uwu eee it is indeed a warning message. My God bless brother Twaibu amen

  • @AaronMakoni-r2w
    @AaronMakoni-r2w ปีที่แล้ว

    Tikukupemphani kut muzitumizabe mawuthengawa ...yehova akudalisen azichimwene...tikufunaso kuti uthenga wa mr twayibu uziponyedwabe pls anthu amulungu

  • @braveshugah-fm7nv
    @braveshugah-fm7nv ปีที่แล้ว

    Ndilape chimalizilo chafika

  • @Sonye-h9f
    @Sonye-h9f 7 หลายเดือนก่อน

    Uthenga wabwino ambuye akudalitsen

  • @robertbanda765
    @robertbanda765 ปีที่แล้ว

    Brother Twaibu alikuti munthu wa mulungu tamusowa ngati sakudziwa umboni wao ukutembenula miyoyo ya anthu ambiri kulapa machimo kubwera kwa yesu khristu ine pano ndine mmodzi wokhudziwa.

  • @upene253
    @upene253 ปีที่แล้ว

    Koma munati zii tinakusowan muzibwelabwela

  • @marychilenje4769
    @marychilenje4769 2 หลายเดือนก่อน

    Zoonadi mkwaturo ulipo chofunika ndikusintha makhalidwe athu oipa

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 ปีที่แล้ว

    Mulungu akhululuke machimo athu