Utumiki wa a Twaibu - 'kupembedza' Mulungu koma uli mu uniform ya satana, usayembeke mayankho

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 23

  • @MatiasHambulo
    @MatiasHambulo ปีที่แล้ว +2

    Zikomo kwambiri mutumi wamulungu potusegura manso ndine Matias hambulo ku Zambia amen

  • @ShieldHenryHills-nm2wt
    @ShieldHenryHills-nm2wt 7 หลายเดือนก่อน

    How i wish to see you sir am apostle evangelist shield henry PHIRI in Zambia..i love you so much in CHRIST JESUS...mumandilimbikitsa kooposa mchikhristu changa🙏

  • @stewartkazembe1174
    @stewartkazembe1174 ปีที่แล้ว

    AMEN AMEN ABUSA MWAYAKHULA CHAPAMTIMA PA YESU ONYOZA ANYOZE KM TRUE PASTOR, HALLELUJAH CHILUNGAMO CHIMAWAWA

  • @JosephNdenga-jl2lm
    @JosephNdenga-jl2lm ปีที่แล้ว +1

    Amen so powerful thank you

  • @markbanda7434
    @markbanda7434 ปีที่แล้ว +1

    Chilungamo chiyankhulidwe, Amen abusa

  • @shakiraamin625
    @shakiraamin625 ปีที่แล้ว

    Amen man of God continue doing good work

  • @TrynesMenia
    @TrynesMenia ปีที่แล้ว

    Zikomo kwambiri popitiliza kunditsegula maso ndilolola kumanenedwa otsalila wachimizi koma zinazi ndasisiyilatu zikomo God bless you

  • @Sonye-h9f
    @Sonye-h9f 8 หลายเดือนก่อน

    Uthenga wabwino ambuye akudalitsen 🙏

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 ปีที่แล้ว

    😂,😂😂😂😂😂😂 iiiii koma balee akuti upakiza ma diledi

  • @GrevanzioShaba-u6l
    @GrevanzioShaba-u6l ปีที่แล้ว

    Ine ndye ndikudalisika. Km Link

  • @JacobowazaSabe-cb4hx
    @JacobowazaSabe-cb4hx ปีที่แล้ว

    Mulibwanji
    pasta
    Wanga
    Ku
    Malawi
    Ko?

  • @eleckmasoshomakalani6471
    @eleckmasoshomakalani6471 ปีที่แล้ว

    KkkK Devi sabwela

  • @delisntawa
    @delisntawa ปีที่แล้ว

    Zamphabvutu izi

  • @AshrafuBwanali-qi3my
    @AshrafuBwanali-qi3my ปีที่แล้ว

    Munthu wabodza uyu zongolota bs

    • @Yahiya-wm8nd
      @Yahiya-wm8nd ปีที่แล้ว

      Zongolota zonse usatelo ase zoona amena mkuluyu

    • @JerryNcube-gt3te
      @JerryNcube-gt3te ปีที่แล้ว

      Koma inu mukukananu mkanakonda mukanangokhala Chete osaikilapo mulomo wabodza ndiinuyo Kaya atwaibu amanena zoona ndipo akukamba zoona zenizeni

    • @esthergweje4038
      @esthergweje4038 ปีที่แล้ว

      Mulungu akudzudzule wamva!!!!!mkuluyi akunena zoona

  • @eleckmasoshomakalani6471
    @eleckmasoshomakalani6471 ปีที่แล้ว +1

    Link please ya whatsapp grou

  • @victoriabanda7828
    @victoriabanda7828 ปีที่แล้ว

    Tipasen link Whatsapp group