ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Chisale aliphe his actions speaks volumes komwe aliko ntchito zawo zikuwachitira umboni
May God bless you forever Mr chisale❤❤
Chisale amandiwaza kwambiri
Dziko la Malawi likufuna anthu ngati amenewa
Ineso ndimamunyadila silikali ameneo siwakwathu koma zomwe amachita Pali athu ambili andalama koma sathandiza ana amasiye koma achisale God bless you
Kwawo kutì big ameneyi
Koma ndi zoona uyu ndi munthu wamkulu na pachitukuko ndikuthandiza anthu akwao.
Kwawo chitukuko zabwino
Achisale. Woooooyeeeeeee mp chaka chamawa
katswiri chisale long live💪