I grew up in Chilobwe & went to school at Naotcha Primary School.. ifeyo tili ana nthawi yeneyo, kunabwera azungu ku soche mountain amene ananena kuti anthu asamuke chifukwa mu soche anapeza kuti muli napolo wa mitu itatu ndipo ma tauni woyandikira azawonongedwa ngati anthu sasamuka.. That was around long time ago beyond 2013 & finally now it’s when we’re experiencing this type of devastation.. Praying for beloved people aku Southern region. One Malawi. One People
I grew up in Chilobwe & went to school at Naotcha Primary School.. ifeyo tili ana nthawi yeneyo, kunabwera azungu ku soche mountain amene ananena kuti anthu asamuke chifukwa mu soche anapeza kuti muli napolo wa mitu itatu ndipo ma tauni woyandikira azawonongedwa ngati anthu sasamuka.. That was around long time ago beyond 2013 & finally now it’s when we’re experiencing this type of devastation.. Praying for beloved people aku Southern region. One Malawi. One People
Keep on updating us mumakwana malume
Mumayitha bwana!! Pochita zinthu mumakhala nazo chidwi , komanso tikumva nkhani mosavuta timakudyadirani Boss man. Big up yourself man!!
Well bg thanks for your update
You are a very good narrator Sir.
Thank you very much Sir.
Am proud of Gabriel kamilomo
Excellent analysis sir this is quality information, we look forward for any update from Russia Ukraine war, and Ramzan Cadrof from chechiniya
Big man timafunanso titadziwa kusiyana kwa kagwiridwe ntchito ka ma department awiri awa FBI ndi CIA
Great job mr kma muzaponye pic yanu tizakuonen mumakwana here in cape town umandimvesa kukoma
Mumati vesa kukoma brother timaziwa mbiri zakale kwainu 💪
Your so intelligent mr
You're a hero
Inu mumatimvesa kukoma, daily timayesesa kuti pa channel yanu kuti pali chiani, big up
Muzitero mkulu timamva kukoma komanso timadziwa zobisika
Thanks BG man
Thanks big next time muzatipasireko mbiri ya Brenda Fassie
Well done king of history in Malawi kma tikufuna update yaku Ukraine chifukwa tikunamizidwq
Simunasazikesotu boss
Ambuye atichitile chifundo
Tiuzeni zoonadi amene amapereka mainawo amadziwipo kanthu
Ciclone saliwoyenera kumupatsa dzina la munthu koma azipatsidwa dzina malinga ndi tchito yake
Timakudalirani potifufuzira zinthu zosiyanasiyana
Koma mayinawa ena asintha mayina awo kamba ka history 😂 yanu bwana, ine ndaziwilako sindinkaziwa kuti mayinawa anayamba bwanji? Well done brother
Yes it was true that why these scientists didn't give the names like Johnson, Hamilton, Morrison, Ibrahim, Ivanovic, Muhammad etc.
Mumakwana Inuyo bigy
Ndakutayìlan ka mtengo
RIP all people we lost
Takunvani Big timakunyadilani Mumakwana inuwo.
Excellent
Mumakhwana big
Mumakwan abwana
We need update Ukraine conflicts
I stand with you
Greetings from London UK 🇬🇧 USA has sent its weapons to Poland declared 3rd world war including Germany.
But its still mother nature NOT FATHER NATURE.
Russia 🇷🇺 is losing
Big wanga zili pati ku Ukraine and Russia pano please big 🙏
Update on Russian invasion and an agreement to abandon use of us Dolla
Always the first one
Ine ndikuona ngati mayinawa amapelwkwdwa kuchokela ku kagulu kena kake kaku sataniki
Bon kalindo wapita ndimadzi
Koma tatifufuzilen kut kod anamondwe amenewa samatheka kuapezela njila yokuwasokonezela kut asaononge kwambili
Ndizosatheka kutembenuza mwa njila ina iliyonse ndizachilengedwe pasi
Cyclone Laz.Chakwera.
Nkhondo ya ku Russia vs Ukraine 🇺🇦 update please
Rest in peace all people we lost 😭😭😭😭
Mitengo ya ma blue gam izidzalidwa kuti ichepetse madzi
Pakana Ellen my name kkkk
Timudziwed yemwe amapeleka mayinawo timvaso kut cyclone Chakwera
Always I'm second
Mumayitha inuyo
Koma cyclone Cecilia asadzabwere coz ine makonda anthu nde dzina linga lisadzaononge anthu komaso ndine ofatsako😅
Afiti akupereka mayina.
Koma sizinakhale bwino
Ada inuyo mumakwana
😂😂😂 ndipo my qquestion too kuti where do these names come from
Napolo president said its 99 people dead only.
Zamadays omaliza izi mateyu 24 ves 5
Mwathandiza tidziwitseni
Mulungu atichitile chifundo
Timathokoza kwambiri big
Mumativesa kukoma
Timakupasani ulemu nthawi zonse achikulire
Cyclone chakwela
Improve on your presentation skills.
6:36 6:37
Cychrone Izeki kkkkkk
😢😢😢😢😢😢
Bush cycron
Rest in peace
Kanyimboka kalibwino