The story of a man with a broken spinal cord who is confined in his bedroom for 8 years

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 33

  • @user-tu8yx2on1r
    @user-tu8yx2on1r 5 หลายเดือนก่อน +2

    God bless you bro ukugwira tchito ❤

  • @stantchualex3883
    @stantchualex3883 ปีที่แล้ว +2

    Oooooohh My God!!!! Full Of Tears In Eyes 😭😭😭😭😭😭😭

  • @marykaunga-cm1dd
    @marykaunga-cm1dd ปีที่แล้ว +3

    Ayi ndithu dziko lamalawi umphawi ngosayamba 😢😢

  • @rosebanda3613
    @rosebanda3613 ปีที่แล้ว +3

    Boma apapa litengepo mbali limuthandize m'baleyu apite ku South Africa akayetse mwina angakapeze thandizo. Ku South Africa amayetsadi nkhani yolumikiza mafupa

    • @VictoriaWilliam-gn1xw
      @VictoriaWilliam-gn1xw ปีที่แล้ว

      Brother wanga wavulalanso spinal cord konkuno ku SA Watha 5 months ali mchipatala kunkuno pano basi kumunsi kunafa zakanika kuti ayendenso

  • @user-wv7mh9yf7t
    @user-wv7mh9yf7t ปีที่แล้ว +1

    This is very sad. May the healing powers of the Most High touch you brother

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f ปีที่แล้ว +3

    Ungokhala president Rodwell bas

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh ปีที่แล้ว +1

    God bless this guy he got hat of gold

  • @mphatsnellymalemia3926
    @mphatsnellymalemia3926 ปีที่แล้ว +2

    munthuyu ngwamtima wabwino eeeee, kumumvera chisoni bwana oti adamuthawa... Ambuye amuone

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 3 หลายเดือนก่อน

    Nthawi Zina chilango timachilandila pasi pompano kuthawa munthu ovulala osadziwa kuti naweso ukadutsa momwemo mwina akanati sanathawe sakanachita ngozi abwanawo ambuye akukhudzeni mwapadela achimwene 😢

  • @hugaallan-yw8fi
    @hugaallan-yw8fi 6 หลายเดือนก่อน

    😔😔😔😔moyowu pena.... so much left unsaid

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 5 หลายเดือนก่อน

    Ooh pepani brother tipemphe ambuye akhale thandizo lanu
    Akukhuzeni ndidzanja lake lamphamvu lamachiritso 😢😢
    Kodi kukachere amalipira?

  • @scottgillhedricko2260
    @scottgillhedricko2260 ปีที่แล้ว

    Eish!!!! Nkhan yosakhala bwino mkomwe, we should know kut pomwe tilnd umoyo wamphanvu, chilichonse chtha kuchtika,like m'bale wathuyu, MULUNGU ekha ndiemwe amatitetezera,ndiemweso amachiritsa,we are together in prayers,GOD will heal u,sachedwa safulumira,

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว +1

    Zomvesa chison kwambiri ambuye akukhuzen ndi zanja lamachiliso

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f ปีที่แล้ว +2

    Chonsecho ma MP alikomko koma osatengapo mbali kut apeze thandizo lochokera ku boma,shame

  • @gracelimani1526
    @gracelimani1526 ปีที่แล้ว

    Mr rodwell vuto limenero mwana wanga anapanga ngozi nayeso anamukankha azake pa fourth floor kusweka spinal cord amphangako operation ku south africa koma amatha kusutha ndi kuima koma ndi chilumba ndithu analumala basi kunthunda kumagira ntchito koma kumunsi miyendo ayi nada ambuye okha ndamene angachize spinal cord mavuto adzakhalapobe moyo wawo wonse

  • @NaomiMashapi
    @NaomiMashapi 10 หลายเดือนก่อน

    God have mercy on him

  • @user-ez5ug9dx2p
    @user-ez5ug9dx2p ปีที่แล้ว

    Nkhani yomvetsa chisoni mmmmm mulungu alowelelepo ndithu

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev ปีที่แล้ว

    Sorry braz nane ndiwakomko kwa mgwira kma Allah akufungatilen baas

  • @user-wd4yi3ol8l
    @user-wd4yi3ol8l 11 หลายเดือนก่อน

    Go to Kakande in Uganda

  • @catherinemkondana751
    @catherinemkondana751 11 หลายเดือนก่อน

    Zokhudza kwambiri 😭😭😭

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 ปีที่แล้ว

    Zosayenda pepani pepani ndothu

  • @chimwemwemajor4578
    @chimwemwemajor4578 ปีที่แล้ว

    This is heartbreaking eeeeh eeh

  • @marthacassam
    @marthacassam 11 หลายเดือนก่อน

    Mmmm very sad😢

  • @Ishmaelmsash5598
    @Ishmaelmsash5598 ปีที่แล้ว

    Mmmm zosayendaa 💔

  • @estherkapesi6261
    @estherkapesi6261 ปีที่แล้ว

    Mmm koma abale😢

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh ปีที่แล้ว

    Kumalwi ayi ndithu dokotola alikoyenda 3 morths

  • @agnesnyirenda4955
    @agnesnyirenda4955 ปีที่แล้ว

    This life

  • @edgarmax-pi1bx
    @edgarmax-pi1bx ปีที่แล้ว

    Abwezi apadziko

  • @josephchikweni1857
    @josephchikweni1857 ปีที่แล้ว

    Kma guys eeeish

  • @edgarmax-pi1bx
    @edgarmax-pi1bx ปีที่แล้ว

    Dziko lapansi mavuto

  • @user-gu7rx1bo5j
    @user-gu7rx1bo5j ปีที่แล้ว

    Zosakhalabwno