The Citizen S01 EP3 - Sex Worker

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 20 ธ.ค. 2021
  • Today I talk to a full-time sex worker based in the city of Blantyre. We talk about their day-to-day life and the risks that come with the job.

ความคิดเห็น • 43

  • @chrispinchikakula2293
    @chrispinchikakula2293 ปีที่แล้ว +1

    😆😆😆🙌🙌 akuti kunazolowera, kuwawa nje. Rodwell my classmate at Athens, salute!

  • @tchanganiskitsmalawi5067
    @tchanganiskitsmalawi5067 2 ปีที่แล้ว +5

    We need channels like this in Malawi

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว +1

    Komaso iweyo ndi hule mapeto kukhara choncho bwanji ukufuna brother rodwell amve bwanji ukukhanyula choncho bwanji😂😂😂

  • @gomezganiphiri2446
    @gomezganiphiri2446 2 ปีที่แล้ว +3

    Okay, this is a gem

  • @christofagolden1595
    @christofagolden1595 ปีที่แล้ว

    2022 kalikose tikaonadi 😂😂😂😂😂😂

  • @luciusjoseph7552
    @luciusjoseph7552 ปีที่แล้ว

    kkkkkk koma guys ....SIBWINO.... MWINATSO BANJA LINATH ACHIFUKWA CHA UHULEO

  • @ireenkaiche4038
    @ireenkaiche4038 ปีที่แล้ว +2

    Muzandilembe ntchito zizafunsa mafunso anyoo nane 🤣

  • @bettymwale2515
    @bettymwale2515 ปีที่แล้ว

    Awe mumaphuzisa ba malawi mwandi,but mwamene nizibila ine mulungu sanapasepo munthu chito zoipa,tonse banatipasa vochita nanzelu,pepani aneba achimwene,am from Zambia

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว

    Mwana wa njoka iwe uli ndi masiku owelenga.....kulephera kugwira ntchito kufuna kudyera thupi mmmm ndalama zimenezo udzazisiya

  • @wapenyapatali5849
    @wapenyapatali5849 ปีที่แล้ว +1

    Atisokonezara mabanja amayi awa kkkkk!

  • @aishachisale4267
    @aishachisale4267 2 ปีที่แล้ว +2

    Koma guys 🤣🤣🙌

  • @kededychiwanda9116
    @kededychiwanda9116 2 ปีที่แล้ว

    kkkkk iiiii ayi ati ndinazolowera sidziwawa

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว

    Brother rodwell mumaziwa kufunsa mafunso inuyo ndi one😂

  • @happymakhalira5460
    @happymakhalira5460 2 ปีที่แล้ว

    🤣😆😆😆😆😆😆 koma Rodwel umatha ase

  • @promise3693
    @promise3693 2 ปีที่แล้ว +1

    Mtsikana iwe ndiwe okongora usiye uhure Uzipemphera Mulungu akupatsa Mwamuna wa serious

  • @CharlesJackson-fb9os
    @CharlesJackson-fb9os 9 หลายเดือนก่อน +1

    Palibecholakwika chomwe ndikuwona ine apa enanu muliso ndimachimo bolaso iyeyu amuna ambili pano ndimahuleso

  • @thecross9297
    @thecross9297 2 ปีที่แล้ว

    Finally

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali1489 ปีที่แล้ว

    Kalikose tikawona basi Mustafa kkkk

  • @sharonjalamu8657
    @sharonjalamu8657 ปีที่แล้ว

    Mwana wasatana ikufunika deliver

  • @brendadumisan2526
    @brendadumisan2526 ปีที่แล้ว

    Koma nde eeee nkani banja linawavuta kusakhutisidwa mayi landila yesu

  • @unstorice4045
    @unstorice4045 2 ปีที่แล้ว

    Koma guys 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 ปีที่แล้ว

    Brother man mumafusa bwino kwabasi

  • @EmmanuelKamsale-ph1nr
    @EmmanuelKamsale-ph1nr 11 หลายเดือนก่อน

    mavalidwe ake amenewo??

  • @stevekananjisenior2575
    @stevekananjisenior2575 2 ปีที่แล้ว

    Kuyankhula mkaziyu amadula dula

  • @christinakalulu2952
    @christinakalulu2952 2 ปีที่แล้ว +1

    Eee....🙌

  • @aliciabanda3656
    @aliciabanda3656 ปีที่แล้ว

    Mau aliyese ndi woipa anthu akupanga zinthu zonyasa kunjaku

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g 6 หลายเดือนก่อน

    mkasa anaimba uhule si business alibe family uyu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @Hamidaimran-ob2it
    @Hamidaimran-ob2it 3 หลายเดือนก่อน

    Zimangochitika chabe poti aliense alindimakonda-makonda, ntchitoi Mmmmm.....imachosa umunthu

  • @juniormaononga99
    @juniormaononga99 2 ปีที่แล้ว

    Kalikonse tikaona

  • @stainermaguire3501
    @stainermaguire3501 ปีที่แล้ว

    Koma guys

  • @scottgillhedricko2260
    @scottgillhedricko2260 ปีที่แล้ว

    Uhure Ndmtima,

  • @hopembendela
    @hopembendela 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkk koma dziliko mpakana kunazolowela

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 ปีที่แล้ว

    Mulungu taonani ananuwa

  • @arfredidamuson1864
    @arfredidamuson1864 ปีที่แล้ว

    Koma D.K udapeza yopanda mpambatu

  • @samuelchimimba2966
    @samuelchimimba2966 ปีที่แล้ว

    Za ulendo uno kkkk

  • @macdonaldmtengula6475
    @macdonaldmtengula6475 2 ปีที่แล้ว

    Zina ukamva 🙌🏾

  • @calebghama3213
    @calebghama3213 2 ปีที่แล้ว

    Simunamufunse kuti banja lake Linatha bwanji

  • @memorykilofasi1165
    @memorykilofasi1165 8 หลายเดือนก่อน

    Ai zikomo

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda4192 ปีที่แล้ว

    Uhuu

  • @alicekhalokhela1461
    @alicekhalokhela1461 ปีที่แล้ว

    70i0l

  • @DoreenDzuwa
    @DoreenDzuwa 18 วันที่ผ่านมา

    Hule losamba

  • @marychinkhuntha6726
    @marychinkhuntha6726 ปีที่แล้ว +1

    Please sister you make money but soon Jesus Christ coming Repent