And madam Patrucia Kaluati being the leader of utm presidential.candidate.cos she is has got experience of leadership.by profession she is a teacher and again she has experience of political leadership.she was in dpp .wurh Bingu wamutharika and peter mutharika
Nkhani ikhale UTM , AFORD ndi UDF apange alliance, president achoke ku UTM ndekuti azapeza ma vote Ku north , central pang'ono koma ochuluka ku southern nde kuti azaiphula bho bho
A UTM panokhs simungalamule dziko ndpo position yanu izingokhala 3 or 4... Koma chifukwa chot ndinu okulamtima mumadzimva ngat muli nkuthekera... Kachipani ka ma MP 4 koma matama thooo🤣🤣🤣
UTM ISAPHATIKIZANE NDI DPP CHIFUKWA MKAZI WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POTHAWA MOTO KU SODOMU..PAMENE NGELO WA AMBUYE ANAWAUZA KUTI ALIYENSE ASAYANG'ANE MBUYO. KOMA MKAZI WAKE WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POGANIZIRA MOWA WAKE WOMWE ANKAPHIKA KUSOMUKO NKUMAGULITSA. IYEO ANASANDUKA CHULU CHA MCHERE. SO UTM NSO MUKAPHATIKANA NDI DPP MUSANDUKA CHULU CHA MCHERE.MUKHALA STUCK AND DORMANT DEAD WOOD .!!!
A Kalindo zindikirani ichi dziko la Malawi ndi latonse, is not about resignation of its members in government positions. Stop misleading people, eg Usi won't resign cos he is serving Malawians not MCP.
UTM back to DPP never we r on our own🔥🔥🔥🔥🔥
Koma fact ndiyakut apapa a UTM mwaphunziladi angakhale achedwa koma this is brave idea , tili ku mbuyo kwanu .
UTM should first stand on its own. Build the party
❤❤❤This guy he's genius Ndipo amati fightiler kwambiri 🔥
From town centre Mitchell's capetown bon ndimakudyadilan kwambili God ahead u bro
Uyuyu a Malawi ambr mmamupeputsa ,.koma nthw idzakwana ubwino wake muzaudziwa
Chitsime chimaoneka chokuya madzi akaphwa
Asiyeni a UTM apange zomwe agwirizana
Ndale zokha zokha,mwasiya masewero abwino, ndalama iwonongesa mbiri
Kalindo salimoyesa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉👍👍👍👍💯
Mumakwana Mr DC
Kkkkkk Manganya adali Yudasi zoona, bwato satsilana pakati pa nyanja kkkkkk
Iwe ndi machine🔥🔥🔥
The DC is right
UTM welcome back to DPP family
Mupwetekana
God first
Ubwino wake ovota ndife, and kalikonse kochitika pansi pathambo Mulungu amachionetsa poyera
Fakafaka mumatiimilila braz
Kalindo the man of the momenti %100
Eeeh ndine bon ...... 😂😂😂 Kuipatsatu fireee
Mission possible
Utm bwelenani ku dpp kuti udzamange amene anapha chilima
Chikati hahahaaa Ndipo chimaseka modelela Chi Born Kalindooooo
Mr bon kalindo thanks live on zambia Lusaka
Boooooooooon Kalindo!🔥
Mr DC hohoho🔥🔥🔥
Born kalindo ndakamuna
And madam Patrucia Kaluati being the leader of utm presidential.candidate.cos she is has got experience of leadership.by profession she is a teacher and again she has experience of political leadership.she was in dpp .wurh Bingu wamutharika and peter mutharika
Uthenga ukupita kwa Michael Usi aka Manganya
Mawu a Bon sapita pachabe nd Yosef mwana wa maloto😅
Nkhani ikhale UTM , AFORD ndi UDF apange alliance, president achoke ku UTM ndekuti azapeza ma vote Ku north , central pang'ono koma ochuluka ku southern nde kuti azaiphula bho bho
So good 👍
Well did
L
Pangolini tsopano
Born kalindo akamuna bambo
This is the truth utm plz bwererani ku dpp
Mmakwanila big
This is boooooooorn Kalindo🤣🤣🤣💯🔥
Good
Ku dpp tikataniko? Chilima anatulukako ndipo sanabwelere mpaka kufa kwake ndiye ife tufuna mufuna mzimu wake utikanthe?
Ndeee kupusako do you think kut utm payokha ingagwetse mcp yotiiii ili m'boma inuyo dziko lanu simulikondayiiii amkolo chilima ananena yekha kut ku dpp anachokako analibe vuto lililonseee ndee inu ndare simuzidziwa Bola mungokharah chete ngt muganiza kut mungazawine panokha kuchotsa chipan cholamulachi
A UTM panokhs simungalamule dziko ndpo position yanu izingokhala 3 or 4... Koma chifukwa chot ndinu okulamtima mumadzimva ngat muli nkuthekera... Kachipani ka ma MP 4 koma matama thooo🤣🤣🤣
Kkkkkk
Pakhala mabvuto olimbilana utsogoleli APA ifee phee Ku MCP basi
Propaganda at its peak. Ife anthu osauka takana kuti ndiwe president wathu
Born💥💥💥
Pangolin iweyo the DC
Chilungamo kalindo
Munyengo yong'alula🔥
We don't have opposition in Malawi
UTM ISAPHATIKIZANE NDI DPP CHIFUKWA MKAZI WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POTHAWA MOTO KU SODOMU..PAMENE NGELO WA AMBUYE ANAWAUZA KUTI ALIYENSE ASAYANG'ANE MBUYO. KOMA MKAZI WAKE WA LOTI ANAYANG'ANA MBUYO POGANIZIRA MOWA WAKE WOMWE ANKAPHIKA KUSOMUKO NKUMAGULITSA. IYEO ANASANDUKA CHULU CHA MCHERE. SO UTM NSO MUKAPHATIKANA NDI DPP MUSANDUKA CHULU CHA MCHERE.MUKHALA STUCK AND DORMANT DEAD WOOD .!!!
Born!!!!!!!!!!!! Kalindo!!!!!!
Dolo kwambiri bonte kalindo😂
The DC 💥💥💥💥💭
Carry on pangolin
UTM 🕊️🕊️🕊️
🔥
Ichichi chinabwera🔥🔥🔥.
Tiuze zoona ife tiri nga nga pa mbuyo pa DC
Mwana wakwathu DC tie nao kung'alurako
The fact is Kodi Njoka kudulidwa Mutu ingayende?
Akuti anzanu wo anavota kale😂😂
Inu kusokoneza basi
The DC Born Kalindo
Booon kalindo ❤❤❤❤
Zimene ukufuna iweyo abwelere ku Dpp ....
Thawi yong'alura 😅😅
The DC
Zikomo kwambiri azaona chomwe Chinameta nkhanga mpala mcp palibeso
Kkkkkkķ tiligu mwati
😂moyo moto Aye!
Apa mwapala, za alliance so ayi
Akakhala okha olo atapanga bwanji olo atatani sangawine ndipo akazabera dziko lizakhala mmanja mwa chinyamata
😢😢😢😢
Kung'alura bas
Kkk
Tidzavote popanda ID plz
Manganya 🚮🚮🚮
Tisasogoze kukangana tieni tione patsogolo...
Mau bg kkkkk😂😂
Ichi chimaseka udyo..
Munyengo yong'alula
Correction utm has vast followers so let utm.stand alone..and its gonna win with the majority.nos
Bwana kwambr😂😂
Uyu ndi neneri ndithu
We are not going for coalition again
Musiyeni Manganya asangalale ndi mdalitso wake, ndi Mulungu adalola kuti akhale pa mpando umenewo. Sizoti iyayi wa UTM weniweni apange resign, kuti chani? Kulephera kwanu musade nako anzanu amwayi.
Hehehehehe kweeee ulira sunati
Koma chikuseka😅😂🤣🤣
Emrove
Boooooooooooooooooon kalindo the DC
kung'alura
Nde dpp zabwino?
zoona kalindo chilungamo
Boooon kalindo
😂😂😂
UTM chipani cha pa social media🤣
Chayankhula bwinotu
Komatu ndiye kuli kung'alula🤦
Utm
Uyuyu ndi 🔥🔥🔥
Uyusotu amangolubwa

😂😂😂😂