ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

Ku Rumphi

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ก.พ. 2023

ความคิดเห็น • 26

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282 2 หลายเดือนก่อน

    Malawi kulakwilana kumeneku sikwabwn ay kuzuza azanu chochi zonkhuza

  • @kettiemnthali9483
    @kettiemnthali9483 ปีที่แล้ว +1

    Komatu zongoganizilana sizabwino,,, anthu enawotu akuyenela kubweza zinthu zomwe zaonongeka. Akubanjawo ndamene agwidwe ndamene anavulaza munthuyu. Akuzengeleza pati

  • @collinsassenga3711
    @collinsassenga3711 ปีที่แล้ว +1

    Pepani asowoya, mulungu akupatseni mphamvu

    • @eliasmtonga8900
      @eliasmtonga8900 ปีที่แล้ว

      Mmmmmm Malawi sazatheka ndi nkhani za ufiti

  • @jeffreyjeffrey8829
    @jeffreyjeffrey8829 ปีที่แล้ว +2

    Koma anthu akulakwa kwambiri sing'anga amanama amangofuna kuwadyera ndalama basi pepani ambuye akhuzeni

  • @magretkalimba-ov6kn
    @magretkalimba-ov6kn ปีที่แล้ว

    kunganizila muthu sibwino aiii uyoo singa' nga akugofuna ndalama ooooooh God have mercy on this family

  • @hanafi4766
    @hanafi4766 ปีที่แล้ว

    Omwetu Amati ujeni ndi mfiti nayeso ndi mfiti dzikoli kulibe atsogoleri ikanakhala nthawi ya kamuzu ndipomwe zafika leroli kamuzu akanapanga chiganizo Kuti Malawi alongosoke osati mbuzi zikutitsogolera zaka zinozi

  • @sarahmughogho8127
    @sarahmughogho8127 ปีที่แล้ว +3

    Koma mtolankhani wachitumbuka kulibe? Chifukwa aliyese amamasuka kuyankhula chiyankhulidwe chake.

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 8 หลายเดือนก่อน

    Hooo!!! Nkhani yolilitsa kuti Kodi dziko lathu lokondedwa likupita kuti. Anthu opemphera koma osaleka kukundika dzitsa panjira ya anzathu, akuzunzidwilanji anthu awa? Mwina munthuyu nkupezeka, adzitani? Osathamangira kuweruza chonde!!! Zikomo Achitetezo, Zikomo Atolankhani chifukwa cha ntchito yayikulu mumayigwira.

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 ปีที่แล้ว

    Zosakhalabwino amabungwe tapitaniko ku rumphi mukawa thandize anthu amenewa abweleleso kunyumba zawo

  • @user-wn4cr9nx7b
    @user-wn4cr9nx7b 9 หลายเดือนก่อน

    Koma amalawi

  • @mbawabuliyan9704
    @mbawabuliyan9704 ปีที่แล้ว

    Inu atola Nkhani muzithaso kutitengela kumbali ya Anthu amene adapanga zimenezo chifukwa ufiti ulipo ameneyo ndi mfiti

  • @georgemsangu
    @georgemsangu ปีที่แล้ว

    Ndimwe zimakhalila Mu Dziko losauka ndichoncho .Ine Dziko la Malawi aaaaa kalanga ineee maiyi Wawayeeeeeeee

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 ปีที่แล้ว

    Koma dzikoli likupita kuti iiiii

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd ปีที่แล้ว

    Nde pot aboma amati ufiti kulibe bwanji lero apolisi akuvomera kut anthu yawa azivutika bwanji osawamanga anthu awo akuvutisa anzao ndi asing'anga awo nanuso munalandira ndalama kod

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 ปีที่แล้ว

    Apolice amangofuna ndalama ndikuona ngati alandila chibanzi kuchokela kwa athu achiwembuwo amangidwe basi chifukwa akuzuza athu osalakwa

  • @kaisiyassin4138
    @kaisiyassin4138 ปีที่แล้ว

    Mmmmm nkhaza tizasiya liti amalawi komanso kusaphunzila chifukwa izi kumaiko anzathu kulibe

  • @markchimpeni7819
    @markchimpeni7819 ปีที่แล้ว

    Ambuye awamenyere khondo chilichose chikhara bwino pepani kwambiri

  • @ChristineKafuka-xu5pm
    @ChristineKafuka-xu5pm ปีที่แล้ว

    D. Pi

  • @janetnpaul426
    @janetnpaul426 ปีที่แล้ว

    Muziika mitu bwinobwino nanga kungoti ju rumphi

  • @josephineringstone7489
    @josephineringstone7489 ปีที่แล้ว

    Kulibe ufiti kumalawi boma imatero ndiye apa boma mangani omwe akusowesa ufulu wa anthuwa

    • @lovebinta6863
      @lovebinta6863 ปีที่แล้ว

      Mmmmm kma amalawi chomwe mukunzunzira anzanu ndichiyani nkhani yopanda umboni mmmmm kma apolice mugwile ntchito yanu ndpo katundu wa anthu aphwanyayo abweze

  • @austingondwe5192
    @austingondwe5192 ปีที่แล้ว

    Sorry for that family

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 ปีที่แล้ว

    Koma kumalawi penapake sutili serious tikulimbana ndi zakuufiti boma likanatengopo gao ndithu pokuthana ndiizi

  • @euniceflash5612
    @euniceflash5612 ปีที่แล้ว

    Zosakhala bwino 😏