Amalawi tidatani Kabambe wakhalapo Reserve Bank Governor osathandiza zeruzo zaoneka Lero Amalawi ndi otemberedwa Kaliyati yemweyu wanyoza akulu enandiena lero akuchuluka zeru. U T M Ndiya olemekezeka a vice president a Dr Usi komanso olemekezeka Akambala omwe mophatikizana ndi okondedwa athu Dr SKC mzimuwawo uuse muntendere ana panga United Transformation Movement (UTM ) asakunamizeni a Kabambe abwera Kuti DPP isavutike kupanga mgwirizano NDI UTM. Kuba mbava izo a Malawi osanamizidwa.
Anybody joining UTM should go to the branch and area and constituency. Nobody should enter at Central executive level. Ngati uli umphawi ndi wanu. UTM youth should not accept corruption, mediocrity and rubbish.. The UTM youth should protect the party for greedy leaders.
Dzikomo a Kabambe chifukwa chokumbutsa bodza lomwe tinalandira pomwe UTM inali limodzi ndi Mcp. Anthu azadya katatu pa tsiku Koma anthu kusowa ndi phara lomwe. Kulemba anthu 1.000.000 pa Chaka, Koma anthu amaphunziro awo kukharira maganyu m'ma Town ndi m'minda ya anthu. Chonde Manfestar amenewo chotsaniponi angationongele Chipani chathuchi. Amenewo ndi amene alepheleka kale. Bodza limenelo tiyeni tiwasiyile Eni ake a Mcp
Welcome to UTM Bwana kabambe , the only beloved and trusted party, thanks for choosing wisely 🔥🔥🔥🔥
Welcome to the family Dr Kabambe
Amalawi tidatani Kabambe wakhalapo Reserve Bank Governor osathandiza zeruzo zaoneka Lero Amalawi ndi otemberedwa Kaliyati yemweyu wanyoza akulu enandiena lero akuchuluka zeru. U T M Ndiya olemekezeka a vice president a Dr Usi komanso olemekezeka Akambala omwe mophatikizana ndi okondedwa athu Dr SKC mzimuwawo uuse muntendere ana panga United Transformation Movement (UTM ) asakunamizeni a Kabambe abwera Kuti DPP isavutike kupanga mgwirizano NDI UTM. Kuba mbava izo a Malawi osanamizidwa.
Exactly 💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯
Munthu osankhidwa ndi Mulungu amampatsa nzeru zakuya zoyendetsera dziko koma so amakhala ndi maso mphenya losamalira anthu m'dziko tipelekeso ulemu kwambiri inu mayi kaliyati mlelankhugwa amayi osategeka ndi dziko kuti zili uku ,Mulungu akuonjezeleni madalitso ochuluka pantchito yomwe mwaidwira koma so mwasankha mtsongoleni oyenelera
😂😂😂😂😂😂 mwabadwa liti kod inu
Ok@@GeraldChisamba
@@GeraldChisambamusiyeni sakudiwa kanthu za kaliyati kusintha zipani koseko sikutengeka kodi 😅😅😅😅😅
Anybody joining UTM should go to the branch and area and constituency. Nobody should enter at Central executive level.
Ngati uli umphawi ndi wanu. UTM youth should not accept corruption, mediocrity and rubbish.. The UTM youth should protect the party for greedy leaders.
Kod amadikila kt achilima atisiye kaye kenako azibwela nkuzapanga join UTM,bodzatu ili akusaka mpando onona mkuluyu,akuluakulu a UTM mukapanda kusamala muononga chipani
Ku utm timapitatu ku conversation musayiwale sitipeleka mpando pa tebulo
Zaziii izo mukukamba utm si ya masavechi kuti ingangopereka mpando mophweka
My vote
You r welcome bwana Kabambe.
Achimwene anga ndasangalala kwambiri chifukwa cha chisankho chanu choyenera nanenso ndili m, mbuyomo ndikupezani
Koma mr kabambe dzalemekezeni mzimuwachilima pls mubwelendintima ofuna kudzathandiza dziko kuti kuwala kwachilima kudzapitilile
Welcome bwana
Good mayi❤
Umakwana katswiri engineer bk tv
😂😂😂😂 Tinabwela timasakasaka mpado wonona 😂😂
Dpp ndiyochenjera kutumiza nyambo ku utm cholinga asavute kupanga alliance kabambe skut wongobwera tiziona kothera .
😂😂😂
Dzikomo a Kabambe chifukwa chokumbutsa bodza lomwe tinalandira pomwe UTM inali limodzi ndi Mcp. Anthu azadya katatu pa tsiku Koma anthu kusowa ndi phara lomwe. Kulemba anthu 1.000.000 pa Chaka, Koma anthu amaphunziro awo kukharira maganyu m'ma Town ndi m'minda ya anthu.
Chonde Manfestar amenewo chotsaniponi angationongele Chipani chathuchi. Amenewo ndi amene alepheleka kale. Bodza limenelo tiyeni tiwasiyile Eni ake a Mcp
Man inu simukudziwa kuti zimenezo angalonjeza ndi kathyali wa Miyambi uja zonsezo
Koditu manifesto mwanenadi idali yathu ife a Utm . Koma tiziti siidatheke chifukwa kum'phika sikudali ife.
😂
Mwagulitsa chipan kwa kabambe
Amazwa ndale sangadabwe ife eni ake tkuzwana
Congratulations .
Amen
Foundation ya tsogolo lowala layambika
Kutha chipani kumeneko 😂😂😂😂😂
Mumva pain simunatiii
@@manfredzalirabetha2440you’re the one who will suffer akadzakupusitsa
Fundoless ungobwera basi inuyo better be bank governor
Inatha UDF kulibwanj UTM 😂😂😂😂😂
🎉
Imposter... A good one though 😂
U T M mpaka kale apa yanyamuka wina alira
Anthu adpp anthu oipa kutereku mwasangalala ndiifa yachilima mpaka kutumana Kuti kabambe Jayenge utm
Eti eti
Mauwo nga UTM koma mtimawo ngwa DPP
Bvuto palibe
Welcome Mr kabambe
Vuto akusaka saka mpando wawu President osa komedwa
Bodza ilo
Mr Kabambe mukulankhula ngat munthu wamayitu mwatan kod kkkk
Ndipo ineso ndimava ngat Joyce 😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
Apa mwaliwa chipan cho ganiza bho hev
Exactly
Zilibwino
Mai mumakwana inuyo
Kabambe u need to polish up ur political speeches 😢
Koma ndiye kukakamulatu kkkkkkk
Ganizo lanzeru la munthu ozindikila osati mbuli zopita kusukuluzi
Koma kabambe kkkkk. Anyway politics ndizovuta kuzitsatila bwino. Asamale a UTM akakomedwa APHA chipani mophweka in the name of kulemekeza nzimu WA skc
Exactly
Manyazi DPP. Apa dpp watha
Apa ndiye yikhala ndi mphavu kaya ukuwona ngati kabambe wabwerera utm
Lol too much talk is unnecessary 😁
😂