Eee koma man-wa I think sapindula chilichonse kulimbana ndi Chakwerayu ndie popeza aliyense ali ndi ufulu wake mmm pitilizani man koma palibe chomwe mupindule ndimomwe ndikuonera sure!!
@@Musa1828-l5dkutukwana sikupindula kalikonse man, awa ndi andale omwe ali ndi zidani inuyo mukungotsatira za ziii pangani zoti zikuthandizeni not kunvera anthu ama activities-wa man bliv mi
Congratulations to Malawi first, you are endeed fighting for the vulnerable people
Much appreciate the Dc💪💪💪💪
Good example Malawi first team
amalawi if they are giving u money 💰(mcp) receive it and don't tell them who u going to vote 4..so chop their money and don't vote for them 2025 🎉
❤🎉
Komatu winiko za marry chilima akunena zoona ngati sachenjera team iyiii itha
Anthu akumalawife ndionvetsa chimoni kwambili bon adayambila muja opanda akunva eeeee ai zikomo ndalema ndiine
Siyeni mwana wakwathu mukufuna aphedwese .Ali ndi mwana wang,ono need to b cared for .Ndale is not priority musiyeni for now .
Chiganizo chabwino kwa anthu owopa Ndikumudziwa Mulungu❤😊
Tiyeni tigwilane manja, zonsezi zizakhala mbili yakale. Rest in peace SKC
Thé Dc Bon kalindo good message number one ❤
Congratulations to Malawi first team
Bon Kalindo keep it up ALLAH bless you
Our president timakunyadirani
Abale anga ndikufuna number ya The DC please please please
Bon kalindo mulungu adzikudalisani
Mary chilima❤
Mary can't have strength to do campaigns now
Mulungu azikudalisani koposa bwana mfundo zoona zokha zokha tililimozi bwana DC ❤
❤❤❤❤ lweyo DC ambuye azikudalitsa
marry chirima take over to be president
Congratulation Malawi First.Unless we are able to differentiate between politics and development, Malawi will never be transformed.
Can I have DC'c cell number
Tiyamike kumwamba chifukwa Cha inu abonieeee kalondo kuti miyoyo yanthu ambili ikupulumuka chifukwa warm Cha inu osati namanyonyolo akuyenda muulendo ngati kuti alibe udindo ngati kuti iyeyu bambo wqdziko lamalawi amene malingalilo ake Ali pa ndalama amene waiwala kuti afike pomwe alipo ndi voti ya anthu amene lelo akunvutika ndi njala akufa ngozi zosiyana siyana zomwe iyeyo akungoyang'ana ngati kuti naye ndimulendo
Asandiyakhulitse pachabe zoona ng'ombe zake akngwilitse misonkho ya BOMA ,ayini ake akufa ndinjala iye kukayendela ng'ombe ,ayi zikomo ndipo mulungu odziwa kudalitsa ndikupeleza zomwe iye afuna ,amudalitse chakwela ameneyu ndi nkanzi wake ndithu ndipo amuike pomwe akupafuna atakhala
Bravo Malawi first
Well done the DC🙏
Ya Mary Chilimayo please speak it loud mpaka abwera tikumufuns
Bon kalindo ALLAH azikudalisa
Aninjury to one is aninjury to all congratulation the DC
nfundo yabwino mumatiimilila a born kalindo
Koma chomwe sitikuva bwanji? Zowonadi Mai Chilima ofunika aimepo tikuziwa akundutsa mu zowawa.koma apange zomwe amafuna Biyeni.
Anakuuzaniko kut mary ndiwandale n amafuna atapanga za ndale??
Kachamba nama drama iwe leave marry alone iweyo unakasiya galimoto ku dovic pita kayimile utm
Iweyo ukufuna kut upite kwabusa oky muziyangula bwino
Tipatseni number yo nafe titumize 5 pin yokha
Sorry mr Dc zulo sinavele audio yanu koma osadandaula ng'alulani koma umakwana ulem wanu
Dzoveka DC number ndipaseni
Eee koma man-wa I think sapindula chilichonse kulimbana ndi Chakwerayu ndie popeza aliyense ali ndi ufulu wake mmm pitilizani man koma palibe chomwe mupindule ndimomwe ndikuonera sure!!
Iweso ukuganiza mopusa
Ku wati nawe chakwela wakoyo
I don't know why malaw face these challenge God forgive us if we have done wrong to you
Mumakwana the dc
Kamuna Iweyo Bigy 😅
Aaaaa. Mtumbuka. Usanamize. Amalawi. Hahahaha. Ulibe. Mphatso. Ya. Utsogoleli.. Ungozikakamiza. Tikakuvotere. Poti. Unali. Nzake. Wa. Chilima. Ayi. aa.... Komanso. Uzatiwonesa. Ngati. Za. Mcp. Mbola. Singangozuka. Kwanuko. Kumati. Uzakhale. Presdent. Wa. Dziko.... 😂😂😂
Number yotumizira
Zoonadi the Dc
Zoona boma ili lapanoli ndi agothi ndithu
The dc number yanu tipaseni
Mapazi ako
Dc
❤❤❤😂😂
Nosence
Nonsese mkuthako kwa Chakwera mesa pamtumbo pakoso wamva chitsiru iwe amakuitana ndi ndani apa galu fiti
@@Musa1828-l5dkutukwana sikupindula kalikonse man, awa ndi andale omwe ali ndi zidani inuyo mukungotsatira za ziii pangani zoti zikuthandizeni not kunvera anthu ama activities-wa man bliv mi
Anthu oipa inu, abale anthu kumadya chitedze osamva chisoni koma kusapotera nyasi. Amalawi tafika pomakhala ngt obadwa kwa nyama
DC Number yanu tipaseni