Kuganiza mwakuya Maso anga adali kwa a Chitsi sindimadziwa kuti angapange Khomani!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Kunena zoona nthawi yatha tisamachedwe ndi kukokana
Mu dziko lino lapansi tili ndi soka lalikulu! We will surely die in the way zamasiku otsiliza... Ndilibe kanthu ndi munthu , ndili ndi kanthu ndi moyo wanga ndi onse akumvera chenjezo la Mulungu ndi kuyenda m'menemo! How would you say inu ndi Mulungu! Just worried of asking this such question
Manganya you are , a best actor , you impat knowledge and wisdom to Malawians.
Vp inu one lkkkkkk munava mwambo
Ine kuno ku Moçambique ndaphunzirapo.
Full of sense, wisdom and knowledge.
Keep it up Guys ❤
Manganya mngochenjera angogwiritsa ntchito amzake😮 Poteteza mpando wake ilisi Sewero la Tikufelanji km La Tonse alliance
Ngati bodza
Good advice my VP
Inuyo zoti ndi a honourable sizimadziwika munthu odzichepetsa koopsa I 👍 you Dr manga
Akuchimbukwa tulikwalolela naga akawe chalew^e... Khomani!!!❤❤
Very nice point, Mr. Manganya like
Blees up sir👌
Bravo manganya utumbuka sungathe🎉🎉
Watching from Johannesburg olifantsfontein
watching from Capricorn Cape town
Manganya is good at this koma ku ndaleku aaaaa ndimaona kuti sakumasuka bhobho 😊
Mkazi samalawidwa kkkkk,Manganya mwaphunzitsatu
😂😂😂😂 Ndaone mochedwa atakhala kale pa vice president. Anyway u perform well
Kajambuleni kawiri we want the real tikuferanji not politics
Kkkkk 😂 so ❤ zakwathu more nice 🇲🇼👊🤞
DR MANGA MY VP MUMAKANA
Manganya sewero labwn bwn wayamba kulowesa ndale
A Namalawa 😅😅😅 great piece of advice
Watching after he been made Vice President
Kkkķkkk mmakwana madolo inuyo more respect
Mlelemba akukwatanitsa Nkhwasala😂😂😂
😂😂😂😂 manganya anakonza nthawi Zina zimamveka zongosekesa chabe koma ayi ndithu zili ndi thandauzo
My best ever
My home boy
Live Long sir usi
You're coming old manganya just because muli m'boma
Ine pano supporting the vp🎉🎉❤
Ulemu wanu avep
Kuganiza mwakuya Maso anga adali kwa a Chitsi sindimadziwa kuti angapange Khomani!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Kunena zoona nthawi yatha tisamachedwe ndi kukokana
Manganya those were the days kale lathu 😂🎉
Achisi ndimangoti alankhula zosanveka.
Ndale zoli apo manganya amatha kuyambila kale koma uwu unali msonkhano wa ndale
Paja nae alikomweko akudya nawo
Manganya
Km manganya mmmm iwe anakoza
Manga you're one
Kakakakakakak ndaswekaa koma manganya kkkkkkk
Kkkkk❤❤❤❤ more
Panotu akuti vp koma kkkkkkk
Salute
Manganya iweyo umakwana
😂😂😂Manganya ndigalu kwabasi
Palibe ndatola ky ndikuuma mutukwanga ky😂😂
Komano ndiye muzitipangirabe sewelo Dr Manga
Mumakwana inuyo ❤❤❤❤
Zopusa izi ndale pasewelo
Manganya ipatseni moto
Zopusa basi ndare pa sewero
Riiiiiiih khomani😂😂😂😂
Tinkawakonda amanganya km pano kkkkkkkkkk anatha analowa ndare opusa iwe manganya
Anamalawaaaaaaaa!!!!!!!!!
Manganya kumtima mbee...😂
Ayambitsa nyimbo asa kudabwa2 ine
🎉🎉
Kkkkkkkkkk mmmmm manganya wadiwonjeza mpaka akapa iwe tikumana tikalowesa zoma lathu ndilinawe ntchito
😂😂😂😂 ndiye mwati knomani?😅😅😅😅😅
Ai zikomo
Yomweyoooo 🎉
Mfumu kadzi ndawonatu ananyoni
Ruth similar AKA make sikono
Eeeeeee ziliko
Manga umakwana 😂
Come on Mr VP we proud of u not chakwera
Kdi ndye paulo atulukira liti😊
Ili sisewele la tikufelnji koma kuteteza udindo wanu nkulu mukuononga drama group ndi ma politics anuwo moya
timakusatani mwalowesa ndale😊
Bring back ma sikono
kapeni for tonse
Akuluwo kd saima kuvuna nao aaaaa
Munalowetsa ndale akulu inu
Waikamo zandale basi ingotsiyani amaganya
😂😂😂😂😂😂 koma
Mwazilowesa ndale
Ndipo kwabas ya week ino yalowa ndale zedi
@@user-ly6eg7zk1s ndipo sizinabebe taaa
Title ya njimboyo ndichan ine imandisangalatsa
Anali kale awa
Abale Nyoo Ali kuti???
"Munthawi yosiliza" 🤔
Zopusa zeni zeni
Tikufelanji anasiya kubeba ndale too much
Bamboo a sikono ajaa
Mmmm zalowa ndale
🔥
Kutsegula comment box kufuna kutitapa mkamwa😏🙄
😂😂😂😂😂 tikuferanji kapena nsonkhano wa ndale
Ndimaganiza ngat nduwona ndekha
Msonkhano ndipo azathuwa sakuona vto poti akudya musavutikila ngat ife ife timagobola basi
Ndale
Mbola
Where is Mr nyo
Mukuononga mbili yanu chifukwa chandalama
Koma mikuluwiko ili umu eishií
bwana Michael usi ndi group yanu ai ai mumatha. ❤️❤️❤️❤️
watching from Capricorn Cape town
Gindee
Mimba nkagunde chigololo salawa
😂😂😂
Koma Honourable Manganya
Alinse Ali ndi mutu wachewache achinyamata musamale
Boma losaopa Mulungu, zitheka bwanji kuti Ampingo alowererepo, kodi akanena chilungamo mungakhonze kuchimvera ? Atanena kuti Mulungu akuti president aime , chakwerayo angaime? Kumbukilani Mfumu Ahabu ... Adauzidwa ndi mneneri Mikaya zooona zake zomwe Mulungu wanena koma adasankha kusamvera , ndiye mundiuze inuyo kuti chidamuchitikira Mfumu Ahabu ndichiyani ! Adafa chifukwa chonyoza mau a Mulungu! Momwemo the current government will surely die 😢
Ndipo sikutiso angawavele apingowo ayi kma kuwasakaso kt awamange ati akutsutsana nawo iiii😢
Inu ndi mulungu?moti zinthu pano zikuvuta dziko lose simukudziwa?muziwerenga bible zamasiku otsiliza
Mu dziko lino lapansi tili ndi soka lalikulu! We will surely die in the way zamasiku otsiliza... Ndilibe kanthu ndi munthu , ndili ndi kanthu ndi moyo wanga ndi onse akumvera chenjezo la Mulungu ndi kuyenda m'menemo!
How would you say inu ndi Mulungu! Just worried of asking this such question
mangqdyq and mulemba don't talk nonsense musazitenge Malawi ndioupusa
Akudya bwino akalephele kusangalala😢
Ipatse motooooo
This is tikuferanji or politics??? Stop talking abt politics plz, sewero munaliyamba bwino koma mwalowetsanso ndale
I think it's better to stop acting tikuferanji not boring like this.we don't need ndale tikufuna tikuferanji yachikale yokamba Za HIV and AIDS