I am completely convinced with this leader how I feel the majority should see the same as some of us are seeing in him...May the good Lord direct him more to build this nation
This guy wasemphana ndi Chilima anakavana hvy ndipo dziko lino tinakaliva kukoma.....komabe Mulungu salakwitsa APA nduu wabweretsaso Chilima wina,, ndag WA naye mchikondi Munthu amenei
As good citizens this is our chance to change our Malawi. Once we support this GUY and his team technically we have joined the GAME CHANGERS TO THE WINNING TEAM. BRAVOOOO!!!
Osamangoti skc chilichonse ngati kuti inuyo you were genuinely loving him.This guy has got good ideas which is needed to be taken seriously koma aMalawi gullibility imatipweteka ,kutengeka ngati kuti brain zanu munagulitsa, stop kumangotengeka ndale will never help single you kutukuka work hard atati alowe m'boma he will be advised and will forget everything he's saying now I tell you, Our late professor ngwazi Bingu Wam'thalika was a man koma lots of you simnamuonetu ,he was man I was telling my fellas akumavomeleza panopa chikufunika NB: n'kuzasintha government system everything will change thus all .. I like this guy but I already lost hope in policians, maybe tingapeze ozamuvotela next yr amenye campaign...tizamuone next yr..✊
Zinakati maphunzilo athu amakhala mchilankhulo chathu bwenzi dzikoli liri la chuma ndi kulemera koopsa. Phunzilo ili ndilovuta kwambiri mchingelezi koma apa olo nkhalamba ya zaka 80 itha kunvetsetsa.😢😢
Derete ua comment..mesiah ndi Mulungu in humana flesh don't compare Him with anybody else..mind you tinabadwa through brood shareling while the Messiah was born through the Word power of God@@fleshar-j6i
Anthu ngati awawa ndi chiombolo cha dziko, (akundikumbusa ndi Bingu nkuluyu) chifukwa amayendesa dziko ndi mutu wawo monga akuonera pa ground osati kumangosatila ndondomeko zoti zinapangidwa kale ndi azungu. Koma kuti ayamba zandalezi payekha sizingatheke ndipo sangazakhale president mpaka kalekale.koma angochita kutengedwa ndi chipani chomwe chili chothekera kuwina mosavuta ngati DPP ija monga anachitila Bakili 2004 kungomutenga Bingu ku convention kuti ndi amene azaime ngati president wa chipanicho basi.
Vuto ndi lakuti anthu Ngati awa satengedwa serious,, anthu amakonda ndalama, ma t shirt ndi munthu wamolaro not nzeru,, Koma if party's like DPP, or UTM atamutenga zingathandize Kuti akalowe mu parliament
Uyuu katundu tiyeni timulange sponsor muwone agwetse yekha chakwera😂😂😂😂😂😂 I will I will be minister of finance in his government kungotero ma youth ntchito 5 million azipeza 😂😂😂😂 tiyeni timisapote nfanayu❤❤❤❤
Akuluwa alibwino kwambiri,...Nzeru zomveka bwino ngakhale ma system azungu ndi amphamvu,....Pamodzi ndi achina Julius Malema,Bobi Wine,Ibrahim Traore nzotheka. Nkhani ndi zakazo chisankho chikubwelachi sangakwanitse kuima.. Ndulingalira ataenda ndi Martha Chidzuma ngati president,..zitithandiza. Bravo DMNk,... Mitu
He must talk and enlight the youth about pacts and treaties also signed by our government officials behind doors without consult the pple... IMF AND WORLD BANK
I was skipping this post but I took a few moment to listen to this video,there is wisdom in the guy,i thought tinathera pa Chilima but the guy is a genius.
This guy is brave man ,genius ,I second this brilliant idea, I even read a quote from the bible ,"come let us reason together and make one thing" indeed just like Ibrahim Traore 35yrs he is leading BUKINA FASO ,young man 33yrs leading SENEGAL , why not Malawi ? Lets change our Nation with Servant leadership
I just like the guy's MFUNDO. Ndiwachichepere, koma wamva maitanidwe muutsogoleri wa dziko lino. Sikukulamulani aMalawi amnzanga makamaka inu achinyamata, let's give a guy much support. Timupatse sapoti yambiri, kuti Mulungu apitirize kumutsegula maso, komanso akhale nawo omuthandiza kukwaniritsa komanso kufikira masomphenya, for the betterment of ifeyo aeni ake aMalawi....
Very constructive ideals of the national transformation for the betterment of all.Much interested in educational part.Indeed education can be another form of slavery.The only mindset to embrance as a nation.Much thanks to u brother for ur courage.
Next time Africa will become super power , Let's focusing minerals on that we have , we will have better Africa . Butter exchange is good ldea . We have lntergent people .
This guy is most Genius. Congratulations Mibawa TV shame to mother Medias they can't cover this.
Bravo Mibawa Tv
This is ideal. Bravo the president to be
MBC feed us fake information...let them go to hell
❤❤❤❤❤
I am completely convinced with this leader how I feel the majority should see the same as some of us are seeing in him...May the good Lord direct him more to build this nation
Wow. Wisdom of Solomon. God has revealed the leader we have been searching for. How i wish SKC was around to groom this "born leader".
Ndipo eeeeeeish
He could differ even with SKC
This guy wasemphana ndi Chilima anakavana hvy ndipo dziko lino tinakaliva kukoma.....komabe Mulungu salakwitsa APA nduu wabweretsaso Chilima wina,, ndag WA naye mchikondi Munthu amenei
Perfect hope mr president has listen this
Good man
Eyetu china chikamafa china chimakhala chikubadwa misozi yanthu yazala chinthu china
Tili limodzi.. bwerani ku utm
Very true@@StellaCharmer
Man u are brilliant than any president of malawi u need to be respected
Seems to be Malawi's Ibrahim Traore
As good citizens this is our chance to change our Malawi. Once we support this GUY and his team technically we have joined the GAME CHANGERS TO THE WINNING TEAM. BRAVOOOO!!!
He sounds genuine, I think God does not run out of ideas,SKC is gone but look at this khang'a now, so powerful
Exactly skc still exist
Kwamunthu yemwe analowako mkalasi kumva mfundo izi mkosavuta,koma munthu wakumudzi yemwe akangopeza tima handouts amangoti MY VOTE😢😮😮.Bwana Dennis muli mmaganizo abwino ndithuu....
Ndipo ndi zoona zake,Koma mkulu wa Ku chikangawa sangamve izi
SKC spirit big up
Osamangoti skc chilichonse ngati kuti inuyo you were genuinely loving him.This guy has got good ideas which is needed to be taken seriously koma aMalawi gullibility imatipweteka ,kutengeka ngati kuti brain zanu munagulitsa, stop kumangotengeka ndale will never help single you kutukuka work hard atati alowe m'boma he will be advised and will forget everything he's saying now I tell you, Our late professor ngwazi Bingu Wam'thalika was a man koma lots of you simnamuonetu ,he was man I was telling my fellas akumavomeleza panopa chikufunika NB: n'kuzasintha government system everything will change thus all .. I like this guy but I already lost hope in policians, maybe tingapeze ozamuvotela next yr amenye campaign...tizamuone next yr..✊
@@InnocentMtafya khala serious bro disflareting politic ndi game yoopsa take care
Guys this is our guy let's support him
The one who might win presidency should include this guy pliz he has strong upstair
Akaonongekako let him be as he is with his team. The most important thing to do is to support him and his team.
Tamutchulen dzina timupange follow 💥💥💥 the guy is just extraordinary 🎉🎉🎉 The Dawn is just Here 🤟
Ichichi ndicholombo guys,we need people like this
This is the leader we expected to have in this country
What about aisenhowa mkaka and his friend bwanji are not good
Uyo ndi big man ❤❤ lets hope the born kalindo akuva kuti amumenyere nkhondo uyu akhare president 😂
This is powerful lecturing and mind blowing
Honestly the guy is genius,all the way from Mozambique adawa ndi dolo
Iweyo ase watenga vote yanga basi
He's from Mozambique?
No Malawian @@limbikanil.i.mmtewa7595
Zinakati maphunzilo athu amakhala mchilankhulo chathu bwenzi dzikoli liri la chuma ndi kulemera koopsa. Phunzilo ili ndilovuta kwambiri mchingelezi koma apa olo nkhalamba ya zaka 80 itha kunvetsetsa.😢😢
Am agree with you
Of course bro
Pamenepo
Very true.. most Asian countries are successful because they make everyone understand issues or concepts in there local languages.
Munthu ameneyu akhale otetezedwa chifukwa dziko limadana ndi month wanzeru ngati ameneyu amaziwa kuti atisegula maso timuteteze
Adah awawa akuganiza ngat Ibrahim Traore the captain
Ndipo heavy
Kwambili he needs our support
Tiyeni tiyetseko achinyamatawa
Uja nd messiah
Derete ua comment..mesiah ndi Mulungu in humana flesh don't compare Him with anybody else..mind you tinabadwa through brood shareling while the Messiah was born through the Word power of God@@fleshar-j6i
Anthu ngati awawa ndi chiombolo cha dziko, (akundikumbusa ndi Bingu nkuluyu) chifukwa amayendesa dziko ndi mutu wawo monga akuonera pa ground osati kumangosatila ndondomeko zoti zinapangidwa kale ndi azungu.
Koma kuti ayamba zandalezi payekha sizingatheke ndipo sangazakhale president mpaka kalekale.koma angochita kutengedwa ndi chipani chomwe chili chothekera kuwina mosavuta ngati DPP ija monga anachitila Bakili 2004 kungomutenga Bingu ku convention kuti ndi amene azaime ngati president wa chipanicho basi.
Vuto ndi lakuti anthu Ngati awa satengedwa serious,, anthu amakonda ndalama, ma t shirt ndi munthu wamolaro not nzeru,, Koma if party's like DPP, or UTM atamutenga zingathandize Kuti akalowe mu parliament
Bingu Wamthalika anayesesadi chilungamo zinthu zimayenda bwino njala inatha ndithu Malawi nthawi ija
DPP ndiyophangila Peter sangalole kumupatsa ufulu munthu wina koma zangovuta wasephana ndi chilima 😢😢😢😢😢
Akakhala bakili anali wachikondi coz anapanga zimene zija kumutenga bingu
I'm totally impressed with this guy... We need such leaders in our country
Kupasidwa ngongole koma anthu kudukula kutsala pang'ono kudula chiwuno kusangalala 😂😂
Kkkkkkk
Uyuyu nde president
Even though he is young and inexperienced. He carries my vote, experience aipezera pawu presidency pomwepo
Aaaah guys this is extraordinary , join forces,you and kabambe ,I love this ideology,we can move forward with him
Zoona man
Mudima umadana ndi kuunika
May Allah grant much protection to my brother let's support him guys we need talented youth like this one
Lets make this person known
Guys let's support this man ... He is a genius
Nthandwe your advice is effective to transform Malawi , your are like Ibrahim troei of Burkina Faso Kee it up brother
skc is back akuluakulu they cant stop us the reader is here
If ur leader was dinning with puppets then also he was ...May his soul rest in peace.....
I will vote for him
Here is another Bingu,,,welcome bro,,,mdziko muno tikufuna anthu ngati inu🔥🔥🔥🔥
She deserves to be a leader
She????😂😂😂😂😂
Uyuu katundu tiyeni timulange sponsor muwone agwetse yekha chakwera😂😂😂😂😂😂
I will I will be minister of finance in his government kungotero ma youth ntchito 5 million azipeza 😂😂😂😂 tiyeni timisapote nfanayu❤❤❤❤
Graat man we need people like you lets work together to change our country
Big man Muthu ameneyu akuyankhula zanzerukwabansi
Akuluwa alibwino kwambiri,...Nzeru zomveka bwino ngakhale ma system azungu ndi amphamvu,....Pamodzi ndi achina Julius Malema,Bobi Wine,Ibrahim Traore nzotheka.
Nkhani ndi zakazo chisankho chikubwelachi sangakwanitse kuima..
Ndulingalira ataenda ndi Martha Chidzuma ngati president,..zitithandiza.
Bravo DMNk,...
Mitu
That's great news, God should guide you and protect you from all evils.
❤
The guys has good basis more especially on economics which is every key to development, however am still following him
Replacement for chilima, Mai kaliat wapedzeka munthu uja chitanipo kanthu
Ngati Martha Chizuma ananena live pa maso pa president kuti ndikugwilizana ndi maganizo a DENNIS MAHATA ineso I will support you brother..
I love this guy kanduthu pachuma❤this as solution 😂
He must talk and enlight the youth about pacts and treaties also signed by our government officials behind doors without consult the pple...
IMF AND WORLD BANK
Now I think we hv our own traore in Malawi
This guy very interingent
Its true brah
Traore ? Who is he ?
New revolutionary leader of burkinabe state and his full name is Captain Ibrahim Traore@@limbikanil.i.mmtewa7595
@@limbikanil.i.mmtewa7595president waku Burkina Faso akatundu
This man is upful and creative!!.
This is wat Malawi needs in a leader...
You are so genius you deserve to be a reader of our country malawi
He's good with his brains 2030 constitution ikadzalola we will vote for his fundo...
We need his friends too coz he seems to have good friends who can also assist ...
I this this guy is good at economics
Chilima's resurrection, i am ur prospect #my vote
this guy anasowa pakatipa I used to follow him ngati nsakulakwisa Ali ku bunda... he I genius...this 2024 let's listen to him
You have my vote sir🎉... May God prosper you..
Koma chonde add GYM in your daily routine..
You deserve to be a president, go ahead God almighty is with you my dear
This young man I respect him
Let's Support him please 🎉
You suppose to be a president I think you can change Malawi
Powerful my brother 👏🏿👏🏿👏🏿
My bro keep it up we need to change Malawi atikwana anthu Okubawa
This is powerful indeed , he deserves to lead Africa .....
Actually one of the source of finance is Seigniorage finance and the government we can use it because we in trouble now
I was skipping this post but I took a few moment to listen to this video,there is wisdom in the guy,i thought tinathera pa Chilima but the guy is a genius.
This guy is brave man ,genius ,I second this brilliant idea, I even read a quote from the bible ,"come let us reason together and make one thing" indeed just like Ibrahim Traore 35yrs he is leading BUKINA FASO ,young man 33yrs leading SENEGAL , why not Malawi ? Lets change our Nation with Servant leadership
I like this way of thinking. Keep up man u have the vision
Kuli mfiti 400 Malawi chikangawa party izakuphani baba.
Be careful
😂😂😂😂Ndipo mmmmmmmm
He has inspired me, very genuine person. My vote
Uyuyu ndi traore wakumalawi may God protect him and make his dream come true for the better Malawi in future
I swear this is the type of people Malawi needs....:: You have worn my heart my guy, vote ndakusungira!!
I'll vote this year only for you mr President
I just like the guy's MFUNDO. Ndiwachichepere, koma wamva maitanidwe muutsogoleri wa dziko lino.
Sikukulamulani aMalawi amnzanga makamaka inu achinyamata, let's give a guy much support.
Timupatse sapoti yambiri, kuti Mulungu apitirize kumutsegula maso, komanso akhale nawo omuthandiza kukwaniritsa komanso kufikira masomphenya, for the betterment of ifeyo aeni ake aMalawi....
This guy realy he knows Economics wow big brains working ahead.
Very constructive ideals of the national transformation for the betterment of all.Much interested in educational part.Indeed education can be another form of slavery.The only mindset to embrance as a nation.Much thanks to u brother for ur courage.
He deserves my vote
Uyuyu ndi mphwake wa chilima....you touched
This guy has that thing 🔥🔥...my vote
Ayime uyu we can support him i love this guy
Am not an economics but this is 100% true
We need this kind of people in to rule our country ❤
So much wisdom in his sayings and needs much support for this thinking to be fruitful ..azungu anatipweteka 😢
Chilima wadzuka Amwene ehhh mulungu 🙌
Powerful I need to meet this guy.
Another SKC. The blood of SKC will not go just like that. God will raise more people to change Malawi for the better
You will be my president
Please someone like my comment, tomorrow must watch this again
Our own genius
Well said boss...
Uyuyu next year akuyenera kukhala pa ballot paper 👍
Amkhomerera
Eeeeee zoona amukhomerera
Information iyitu anyamata tidzuke tiyeni.... powerful eye opener
The Rising of second
Skc
True this
UTM leaders this is your vessel
I know this guy anali president, pa NRC ndikatundu
Dennis Mahata?
Mcp ilipamoto kuchotsa chilima kubwelanso wina ntchito ilipo
Kkkkkkkkk
Ndipo Ngati achinyamata tikuyenera Ada awawa tiwapatse molaro
Kkkkk
😂😂😂😂😂😂😂 weniweni
Bwino abusa angakuphe anapha chilima samala m'bale
Next time Africa will become super power ,
Let's focusing minerals on that we have , we will have better Africa . Butter exchange is good ldea .
We have lntergent people .
Koma Denis iweyo Mulungu azikudalitsa. That's an eye opener
I like this man for the change may God protect him
Wow!we need this knowledge in our generation agenda
Dolo Kwambiri... I like his way of thinking
Munthuyu ndiwa nzeru ndthu ❤even syllabus yathu I wonder generation after generation with the same syllabus ayi szoona izi
I wish you well Thandwe ndakumvetsetsa mfundo zako, you were born to lead this country
Finally someone who gets it, I was beginning to think I was alone