That's our beloved president, president for the poor always guided and protected by the living God, long live our president, we poor citizens loves you more, the Dddddd Cccccc!!!!, the senior pangolin 🔥🔥🔥🔥
Komano Kodi anthu osawukawo mukumawauza kuti azipangako chani kuti mu umphawimo adzachokemo. Chifukwatu kulimbana ndi BOMA sizingasinthe status ya osawukawo koma zitha kusintha status yanu. Mukalimbana nalo BOMA chonde tilimbikitseniso kuchita ma business chifukwa chete chete sautsa nyama
Men ma business wo mupangira kutiko?dZiko silikuyenda bhoo amayenera kumadzuzula kut amalawi wo azikhala pabwino...ngongole Zama business mutenga kut?Amati mukonze chapansi kut chapamwamba chikhale bhoo...
Ngati Satan simumuziwa melowere ku state house Satan amakhala kumeneko pamodzi ndi Angelo ake azikhale ng'oma ,,kunkuyu ,,,mkaka ,,Monica,,chityola ,,nick amenewa nde Angelo asatana
Concerned malawians let's gather here apule anu alakhula mbali yakuno
Power to people malawi
This guys, is a strong man, he hasn't any fear and all time he fights for Malawians.Lets fight hand on hand guys Dzikoli ndilathu ndithu tisaope.
Kalindo I lv u I'm in studio now do your special song u de best fada 🔥🔥💪🔥💪🔥💪🔥💪💪💪
Proud to be Mangochi❤Welcome to Mangochi bon
Izo padela Koma Ife tungofuna Kuti utipelekeze Kwa sing'anga amene iwe unapita fukwa ameneyo ndikatundu ndisaname
😅😅😅😅
Kkk awa akuiputanso mlandi ina kķkk komabe akunena chilungamo sure inuyo soja WA mphawi mwatenga dzina la lucius
😂😂😂😂😂
Si zachilendo izi azanu a Mntambo ankatelonso tinakutulukani
Mtambo sanamangidweko sanamveko zowawa
@@KimJime-d9k kumangidwa ndikumeneko koma ndi anthu aja ongofuna zikawayendela basi kwinako ziiii
Umakwana ukufunka kuno kalindo uzachangamuse Ntcheu ❤
Born kalindo is my eff
Adzafera mbendera iyi kuti?
Sakugina mizimu ikumusaka.. ndndende Macbeth
Hahaha Kodi muputanso ina bigy milandu 😂😂😂
That's our beloved president, president for the poor always guided and protected by the living God, long live our president, we poor citizens loves you more, the Dddddd Cccccc!!!!, the senior pangolin 🔥🔥🔥🔥
Zoonadi ine ndi mboni kundende kuli anthu osalakwa
Theeee DC iweyo ndi one zomwe umanena zimachitika🇲🇼✊
Akuti mademo tsopano tizipanga bwino....The DC ✊
Booooooon kalindo the comred💥💥💥🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Booooooniiiiiiiiiii kaliiiiiindooooooo! Katundu osamangia unyolo koma chulungamo 😅😅😅
Salute my homie 🔥
Kkkkkkkkkkkkk koma amalume😅😅😅😅😅😅
😂😂😂😂😂😂😂🙌
Koma Kalindooo
Ma background music wo akuononga zinthu fix that guys ... almost ma videos Anu got the same prob
Live from south Africa cape town
Bon Kalindo The DC ofunika azikhala ku State House ndipo tikamuthamangitse Satana Ali kumenekoyo
Vuto umaphatikiza za zelu ndi zofoila zomwe nde makhala kaye ndi zofoila zakozo
Booooonnn Kalindoooooo 🔥
Apolice onse aja? Amabwelela ineyoooo🤪🤪🤪 akut pozamutenga Bon kalindo pazikhala kasinja
Kalindoooo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Komano Kodi anthu osawukawo mukumawauza kuti azipangako chani kuti mu umphawimo adzachokemo. Chifukwatu kulimbana ndi BOMA sizingasinthe status ya osawukawo koma zitha kusintha status yanu. Mukalimbana nalo BOMA chonde tilimbikitseniso kuchita ma business chifukwa chete chete sautsa nyama
Men ma business wo mupangira kutiko?dZiko silikuyenda bhoo amayenera kumadzuzula kut amalawi wo azikhala pabwino...ngongole Zama business mutenga kut?Amati mukonze chapansi kut chapamwamba chikhale bhoo...
Pa ma china pokhapo nde wabayatu driver, operator gad zose zikugwilidwa ndi ma china lebala wawo ndi bwana wa anthu aku malawi.
Inuyo ndi 1. More 🔥🔥🔥🔥🔥
You are welcome in mangochi bon kalindo
Munyengo ya ku ng'alula
Number one kalindo
Iwe ndi nyooo ndikukudziwa bwino bwino
Oipayo alephera yekha
Ngati Satan simumuziwa melowere ku state house Satan amakhala kumeneko pamodzi ndi Angelo ake azikhale ng'oma ,,kunkuyu ,,,mkaka ,,Monica,,chityola ,,nick amenewa nde Angelo asatana
T/A MABUKA 😂🔥 AND THE LAST MAN STANDING ✊🌹
Chi booooniiiiii kalindo 🤣🤣
Kutchaya kugwetsa, shatapuuu!
Ati ine ndiye ndi "kusendendani" uyuyu sakuwopa eeesh 😂
Uyuyu mmmmm koma yeah
Cd2d❤
Akut koma chino sichimakpa kumangidwa😜🤪🤪🤪 ochatsika siyani kuononga ndalama zathu pa nkuluyu mungoziyipisila mbili
Sichimaopa
Bon Kalindo the DC
Ife timakukonda bon Kalindo
Boma lopusa
Chilungamo sichimabisika
Ndalama zolipira Lawyer ndilibe ine
Uyuuuuuu ase ati chiboni kalindo😂😂😂😂
Zaphavu zmenez
Uyu ndi woopsaaa kwambiri ‼️🤣😂
Eeeeh !!! Uyuyu anatopa
Akut atamangidwe ndamako😂😂😂
Uyuyu ndi makina😃😆😃😆😃😆
Eeeh kom ichi
UTM president
Ine ndine nyooo,too much drama.
Chibooooon kalindooo
Koma boma muthu uyu kungomusiya basi sidzoona paka apolisi 200 kuononga misomkho ya anthu
Joab tachezaniko ndi bodyguard wa kalindo bwa?
Kasunja woyeeeeeee!!!!!!
Makosana nanu mwati mudyele ma views pa speech ya nzanu nanu yakhulan yanu mupange post bas Khan ya straight
😂😂😂
Umakwana bale
Koma yh ,,,ichi nde Kaya😂💔🤣🤣😳
Inu ndi one😂
Ka instrumental kabpansiko kaksomoneza olo mukatsitse kwambiri😅
Dc nkatundu uyuuuu
😂😂😂Kalindo
this is born kalindo 😂😂😂🎉
Inu makosana stop kuika ma instrumental si nyimbo izi mixieew tonse ndi oimba?
Musatitopese
The DC mumakwana inyo
Komchi
Kom ichiii inu 😂😂😂
W
Kkkkkk yeah
Koma ichi 😂😂😂😂😂
Koma ichichi eeeeh 🙌😂
Kma. Ichi🤣🤣
The DC
Koma ziliko 😹😹🏃
Kuli zinthu ku 🇲🇼😂😂😂😂💔
kuyaka
Koma akulu awa
🫡🫡🫡🫡🫡🫡🫡🫡
Chatokotatu ichochi ndichooopsa🤣🤣🤣
Komatu nde watokotatu
Kkkkk koma the DC
Zowonadi tikudikira za ifa zimene zija.
Akuti pa mdipiti okamutenga kalindo mudziikaposo kasinja😂😂😂
😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣kasinja
Wayita m,bale
What's with the useless background songs ?
Inde Nyo!!!!... lol
😂😂😂😂
Chiphe😆😆😆
A Kalindo mukuimira ndani bwenzi mutapita kwanu ku Mulanje muzikapanga campaign muzaimire DPP yomwe ija muzapeze chochita panopa sizikuthandizani izi muzafa osauka ndithu
Boooooooooooooooooon kalindo
Kkkk
😂😂