Ku Malawi Kuli Mitundu Inayi Pa Ndale - Richard C Mphepo
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 5 ก.พ. 2025
- In Malawi, we have four political groups representing the four regions of the country: the North, South, Central, and Eastern regions. These groups are often characterized by the following traits:
Pride
Selfishness
Tribalism
Arrogance
Ku Malawi, tili ndi magulu anayi a ndale omwe akuimira zigawo zinayi za dziko lino: Kumpoto, Kumwera, Pakati ndi Kum’mawa. Magulu awa nthawi zambiri amakhala ndi makhalidwe awa:
Kunyada
Kudzikonda
Kusankhana mafuko
Kudzikuza
#malawi
Silani anthu odziwa kutsitsa fundo Ngati sir Beni longwe
Makwana arichard
❤
Phavu ya president ichepesedwe please ikhale phavu ku wanthu please
iweyo,ande,suwakwanitsa,ingosia,kulankhulako,
Inu mwasara pang'ono kuti tikusikeni tiyambano kukonda Ben longwe chifukwa ndiye akubwera bwino atupere sangatithandize ndiye bolanso kabambetu olo zitavuta zitatani na pagwirizanopa atupere ali kutali kwambiri kukhala pa tsogolo tikayerekeza n kabambe or chihana APM N pasogolo mufune musafune
Ur right 🎉
Machende anu achawa mbuli za anthu
ife,tizikukumbutsaniso,mukamakamba,mokondela,nkhani,za,anthu,ameme,anaphedwa,ndizipani,,zathu,,zose,
Izi mwayamba ma activist kumachita side ndi munthu ndi zopanda ntchito. I think as activists just tell us qualities of a good leader otherwise mukuchitaya. Iweyo kavotere atupeleyo coz ndamene ukumufuna. Cuikhumbo chako si cha amalawi onse.
kuno,kulibe,nkhondo,bwanji,,,kd,
Point yako tayidziwa udf nthawi yake inatha udziwe zimenezo Atupere wakoyo sizingatheke mwawi anauphonya
nkhondoyo,sili,kuno,
What abad tribalistic approach from a worst analyst.
musamaphatikize,ulamulilo,wakamuzu,ndi,wa,chakwela,,chimodzimodzi,osaphatikizaso,ulamulilo,wa,bingu,,km,wa,pita,muthalika,nthawi,yapita,muthalika,alobino,amaphedwa,azibambo,adazi,amaphedwa,,utiuzeko,athu,amenawa,samaphedwa,mwankhaza,kapena,akamaphedwa,enanu,mumaseka,kutanthauza,,kt,amaphedwa,mwantendele,eti,kapena,amaphedwa,ndi,MCP,ndi,,,,athu,km,amaphedwa,ndi,dpp,siathu,ndichifukwa,simukuliuza,dziko,km,amene,m,bale ,,,,wake,anaphedwa,ndi,dpp,ngakhale,mcp,amakumbukilabe,lt,chipani,chidandiphela,abale,anga,olo,dpp,muibise,
mukamakumbutsa,zakuphedwa,kwaanthu,mudzikumbutsa,anthu,amene,anaphedwa,ndi,mcp,komaso,amene,anaphedwa,,ndi,dpp,ndi,amene,anaphedwa,ndi,,UDF,pamapeto,pake,dziko,lizivetsetsa,zomwe,mukufuna,kutanthauza,zot,,,UDF,imapha,azimai,amabele,akulu,akulu,sukunena,bwanji,abale,awo,amafuna,uzakumbutsaso,,abaleyake,alobino,,,naoso,amafuna,mudzakumbutsaso,kt,azikumbukila,kt,dpp,idawaphela,abale,awo,osamango,nena,za,mcp,yokha,ayi,,enawoso,anali,anthu,
iweyo,ande,suwakwanitsa,ingosia,kulankhulako,