Ben Longwe Kuyankhula Za Ku Chikangawa - Part 3

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 13

  • @allieadam3235
    @allieadam3235 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Sir professor Charles Ben Longwe ,
    We are following U,

  • @BlessingsNgomba
    @BlessingsNgomba 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Am beginning to like ur commentaries once more.. bravo on the insight

  • @PeterMorgen-k4b
    @PeterMorgen-k4b 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Chakwela did a foulplay😢😢

  • @EladiChabe-d4w
    @EladiChabe-d4w 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Mukukwanila a beni osaopa chikangawa koma chilungapo🔥🔥🔥🔥🔥

  • @frankmanda639
    @frankmanda639 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    It's true what Ben longwe had said anatiphela vp wanthu chifukwa chakusasamala

  • @ZigeMposa
    @ZigeMposa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Osaopa tatopa naye bwana chikangawayu ife

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Tisataye nthawi ndi uyu akhala akusapota MCP nthawi yaitari pano akulubwalubwa chani apa

    • @ZigeMposa
      @ZigeMposa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kulankhula kwabwanji uko
      Udzaziona ataphedwa m'bale wako mwina utha kulankhula zopepelazo

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ben longwe ukufuna umugwile ndani yemwe ukufuna umupeleke kwa Yudas

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tiuzen timvetsetse zimatipweteka za imfa ya chilima

  • @ChikoMasapula
    @ChikoMasapula 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    He who this cap fits.... Let him wear.
    Ndatchula Chikangawa ngati?

    • @nyasavoicebox
      @nyasavoicebox  15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Ayi mwangodutsa simunatchole nkhani haha

  • @MadalitsoLuhanga
    @MadalitsoLuhanga 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We are following ndi chidwi ndithu