OYIMBA A KU MALAWI AKUPEZA NDALAMA ZINGATI PA YOUTUBE? - TILI NDI TOP 10
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 21 ต.ค. 2024
- NOTE: Nthawi yomwe timapanga video yi tinayiwala Saint-Realest whose Estimated Monthly Earnings are at - $170 (MK294,627.68) - $2.7K (MK4,679,380.80)
Kupangira inu mukudabwa kuti Dr Namadingo sakupezeka bwanji pa list ya oyimba a ku Malawi amene akulandira ndalama zambiri kuchokera ku TH-cam....List yi yapangidwa posakatula oyimba okhayo amene ali pa "TH-cam Partner Program" kapena kuti oyimba amene anapanga monetize ndipo alibe ma strike aliwonse pa channel yawo to make money from youtube.
Malingana ndi kafukufuku amene anapangidwa pa TH-cam Monetization Checker, zikuonetsa kuti pakali pano channel ya Dr Namadingo Monetization Status yake ili off zomwe zikutanthauza kuti sakulandira ndalama kuchoka ku TH-cam pa zifukwa zomwe akudziwa a TH-cam wo ndi Dr athu.
Komabe akanakhala kuti akulandira bobo ndekuti panopa bwezi Estimated Monthly Earnings ya Dr ili pa $395 (MK678,749.83) - $6.3K (130,423,068.60) zomwe zikanawaika Dr Numadingo pa number 3 pa oyimba a ku Malawi omwe akulandira ndalama zambiri kuchokera ku TH-cam.
Check list again i wish number 1 is DR Namadingo
please revise the list DR apezekepo
Congratulations to Kell Kay. He deserves to be on # 1 indeed. Congratulations also to the departed Soldier Lucius Banda, M.H.S.R.I.P. He was a legend.
Nice promotion,Koma osati ndalama zomwe akupeza no don't lie 🤥🤥
No 7🎉🎉
🎉
Zopoila
Top 10 without Namadingo?.... simukunama inu?😂😂😂
Ndpo inuuuu😂😂😂😂kmas they don't have accurate info palibe ali below 100$ pama artist ose anenawo
I was expecting Namadingo in top 2
Where is Doc Namadingo
Eli akutipula posachedwa atha kudzakhala pa top 2. Nyimbo ya tempolale wakwapula bwino ndipo ndikuyikonda heavy masiku ano.
MAN nyimbo kulowetsa 1.5 milion kumalandira 100k zabodza izi ikudulatu apa ndi ma figure mwatchulawa
Doc Namadingo ali pa list ya Top 10 African artists osati Malawi, kkkkkkk
Uyu akunama one million views ndi 30000usa dollar or mufufuze pa net😅😅 boza
inuyo mukuyenera mufufuze ndikumvetsetsa mmene youtube partner program imayendera, 1 ma views amene amapanga ndalama ndi amene aoneledwa mmaiko omwe ali monetized ndi youtube komanso ngakhale mmaiko a monetized wo salipira content mofanana, pali mayiko ena amapeza zochulukirapo ena zochepa, pena zimatengeranso mtundu wa content yo kuti akupatse rate yochepa kapena yochulukilapo. 2 Malawi is not monetized on youtube nde olo anthu 20 million ataonela video yako mmalawi mommuno mwezi umodzi, youtube siyingakupatse olo one kwacha, youtube imawerengera ma views okhawo amene aoneredwa mmayiko amene ali monetized.
@@Factory265Media I think you don't know anything bro .... just keep lying to the people..... people nowadays the just go on net to find the truth
I hope there is enmity between u and namadingo
List without namadingo zosatheka man 😅
Saint palibe komaso zeze kumaika Jay Jay CEE 😅😅😅😅 km iwe uli chibwana et
Driemo wangoyenera kukhala pa top 3.
MOTi Namadingo uja lwangali ndthu
? Owoo koma why people doesn't wish that guy well?
We just watching broh no subscribe 😀😀😀
😂😂😂😂
Where is Dr namadingo kuti titsikimize kuti ukunena zoona
Paja bigmn Namadingo ndi mfolena
Mumakwana mam jetu❤
Where is Namadingo and Saint zosabeba
Your favorite are not our favorite
Taziwa nawo
Live
List yaboza iyi olo tay grin olo gwamba nakha namadingo 😂
the chart is based on statistics, facts not emotions
Umakwan🎉🎉🎉
waboza iwe number 1 ndi namadingo😢😢
werengani description ya video yi bwana
I think list iyiyi ndiya boza aaaa palibe ma artist ena apa
Kuyimba ndi ganyu yabwino
Basi no apa kukalamba konaeko kuchimwira Yesu chifukwa cha k173. 000..!!! Kukaotchdwera kwa Ambuye Yesu mkhristu kujahena kamba ka kandalama kake kolhaka.jetu wasankha kufa kuuzinu ndikuthupi komwe.!!😮😮😮 zoopsya tu izi
Onesmas 1
1 kell kay
Kodi namadingo siwakumalawi?
I don't know why you guy hate namadingo 😢
Zaboza izii
JeTu mumakwana ❤❤😂😂😂😂😂
Namadingo bwanji?
Namadingo alikuti?😢
Where is Namadingo
Sanachite registered
🎉❤
What about saint
🎉🎉
Kelly Kay kuluza ine🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤
Ine jutu
😁 😁 😁 😁
Khaaa😢😂 namadingo siwakumalawi anasamukatu paja
Gospel klibe ?
Namadingo ndi saint njeeee
Angotenga imwe amawakonda,
Bodza iyi palibe amene angadziwe zomwe Wina amakonza pa TH-cam kupatula mwini wake fotseki
Osanamapo apa 😂😂😂 ukunena maganizo ako olo tathauzo la youtube ukuoneka sukulidziwaso ngat zili zoona ponya orignal copy yomwe watengamo zomwe ukuyankhulazo
Iwe wabodza 😂😂😂Nanga namadingo number 1😂😂😂😂
Wow...
Mwayamba mabodza kachacha iwe
Joe gwaladi bwanj 😅
Iwe ndi fisi z. Wazitenga kut iz, amenewo ndi oyimba womwe umawakonda iweyo.
Namadingo wamusiya pat.
He said top 10 sizoti enawo salandira and also those who monetised TH-cam channels
Boza iwe zimatengela nyimboyo at2 ayilandi bwanji boza adala inu🤔
Dolo kwambiri
Mmmm🙌🏾🙌🏾🔥🔥🔥
Iwe ndi ndani, Inde ndi Jetu
Koma mwapanga kafukufuku bwinobwino Mr P? Kapena Bakili Muluzi uja ndi Inu ?
these are facts chief
Kkkkkkkkkk
Ulichaboza one ndi namadingo
The list is backed by statistics and be mindful that the list is comprised of artist's whose channels' monetization status is active, and Dr's channel's monetizing status is currently off
Namadingo😢
Kelly kay 🎉
Kkkkk zosatheka iwe ndiwabodza kwambiri opanda namadingo zosatheka ndipo sizawonaso 😅😅😅😅 zaiweyo sibesa bundle Khan za bodza
Nane ndakayika
Ngati inuyo?
Lies, you can not rule out Namadingo. The guy is even amongst the top 3 best music artists in Mw. Awa ndi manyaka mwauika apawa. And your figures in terms of cash are incorrect too.
read this video's description
Uyu eli njuchi nditha kumupangira zambiri
Wawuuuu
Nanga Joe gwaladi akulandila zingat😂😂😂😂😂
Zonama izi
Panga yako
Research ya anthu amisalatu iyi 🤣
Je
Kkkk nanga chibade alikut kk
Nkhalamba yakakamila Ku jozzi😂
Where is saint releast
Wwwww
😅
Sure😂😂😂
Taygrin palibe ?
Iwe ndiwe waboza namadingo alikuti
Nane ndadabwa nazo
Waboza iwe doc Ali kuti apa
Where is Gwamba
Boza iwe
Driom yah l your songs
Izizi pali mabodza ochuluka kwabasi
Where is Namadingo?
He is not monetized on TH-cam at the moment
@@mystapresident5013 unless there is evidence but this sounds a lie, as big and as influential the guy is asadziwe zoti akufunika monetizing his TH-cam? I strongly doubt
@@PemphoMisanjo factory265 media is a professional channel, it collects data from reliable sources, TH-cam remove some content from monetization for breaching their policies...it may be the reason why his channel is not monetized now
So where is namadingo
Will unfollow you shame
Koma iwe namadingu alikut 😅😅😅
Koma jetu zoonadi wakaramba wafunadiukuoneka kasikana yaa azimai tiyeni kumazijudura
Iwe mapwalako waboza
😂🤣😅
Koy tanva nawo
Ngati izi ndizoona ndiye kumalawi oyimba ndikuwapotsa salary yangatu asa
oyimba sadalira youtube yokha ali ndi njira zambirimbiri zopangira ndalama, youtube ndi imodzi chabe mwa njirazo
Namadingo he is number one do your search properly
His channel is currently not monetized, proper research was done to come up with the list
Where is namadingo on your list don't fake us@@mystapresident5013
Mmmmmm does it mean that these are the only artist who appears on TH-cam only. Where is Patience Namadingo
There has been a fraud here and why did you leave it to him
Iweyo ukulandila zingati waziiwalatu
Nyapako sudziwa searching
We are still over you
Guy 😂😂 mbenjere bwanji
Wow I like this one 🫡
Wabodza iwe