Kodi nde mukuti akuluwa akuti chani? Ine sindikumvapo kanthu... kodi kabamba ali ndi mphamvu zomuyitanitsa Usi kkkkkkk koma sukulu zakumalawi Manganya ali duuuu uku ena mayooo mayooo heeeee
Kunena zoona dziko lanthu la Malawi satana watenga Malo kwambiri paliponse Pali chisokonezo palibe chamzeru chomwe chikuwoneka Ndipo ambuye atinthandize (Usi your days are numbered.)
Gyz mangochi akunena zoona inu ma presdent a o position tauzani ma sapota anu tonse tipite kumsewuku.Mupange mmene mumacitila mukamapanga misonkhano ya zipani zanu.comrade mangoci tili tonse osadanda.
koma dzikoli lathu lilindimatenda matha atichulukila kwambili inu anthu ochepa koma kumatiopsyeza zoona ayi tiyeni tidzuke wakumsewu
😊😊
Activist oonetsa party colors- what a joke
Proud of you Lyton Mangochi ❤❤❤❤
Ena mungotengerapo mavuto muvutisa nazo ana anu azibare anu omwe akudalira inu uchitsiru wokha wokha womwe mukuchita mukufuna udindo or chani zitsiru za anthu izi apapa wosokoneza ndinu osati omwe akupikisanawo
Iwe nd garu eti ndizokamba zimenez ndiwe wa mcp
Ndikuwuzeni azitsoleri athu kuti tayesetsani kuti mupelekeso mayendedwe kwa anthu ose amene ali ma ose kuti adzatheso kufikaso ku mademo
Ng'alulezetion 😅Lyton Mangochi.
Dyera manganya likupha ufuna usangalasa order from above
Nankhumwa ndi wogudwa ndi MCP musamukhulupilile
Kkkk km kamanganyaa😂😂
Zoonadi brother Mangochi chilungamo
Koma zoti Akhara Lolemba ndiye amene mumakakamira Kwa pephawo amazikweza kuti a DC agwirizananazo Kodi chikangawatu ndimafiya mumene ananenera bon kalindo ziko laolala ndiyetu tazingo khalani musamatimvutise kumalowa pa TH-cam mukuziwa kuti namapwalalo simungakwanise siyani
This guy aliboh heavy pambuyo panu
Mr Mangochi tayesani enawa akuchita mantha
Kodi nde mukuti akuluwa akuti chani? Ine sindikumvapo kanthu... kodi kabamba ali ndi mphamvu zomuyitanitsa Usi kkkkkkk koma sukulu zakumalawi
Manganya ali duuuu uku ena mayooo mayooo heeeee
Inuyo ndamene simukuveka. Kamsnganya mudzingoksyang'ana mukawona kuti Kali mbali iti
Iweyo ndamene sudziwapo kalikonse ussi ali pansi pa kabambe kuchipani cha UTM malingana ndi constitution
Inuyo ndamene yakuvutani nanga si mukumvera mutavala mamaka Mcp
Dyelatu mkuluyu any way viva Dr kababe ❤
Kunena zoona dziko lanthu la Malawi satana watenga Malo kwambiri paliponse Pali chisokonezo palibe chamzeru chomwe chikuwoneka Ndipo ambuye atinthandize (Usi your days are numbered.)
Fire Burn
Uyuso ngwamisala akadya ndalama za andale amapusa
Ku malawi kulibe wolimba mtima azikuonelelani
Mangochi....❤❤❤❤
Koma mangochi ndi 1 panopa sakuphweketsa
DC wopusa kwambiri nkhumba yamunthu
Gyz mangochi akunena zoona inu ma presdent a o position tauzani ma sapota anu tonse tipite kumsewuku.Mupange mmene mumacitila mukamapanga misonkhano ya zipani zanu.comrade mangoci tili tonse osadanda.
Wozerezeka iwe mademo achiyan 😂
Osangosiya mademoo bwanji
awa amandivesa chisoni bwanji😂😂😂😂😂😂 kufuna kutchuka kutionesa zosaona
zipangani mademo anuo mkuona ngat zikhala ngat zakale zija hilichose chili ndi nthawi yake zinadusa zija bas
Kkkkkk kamanganya
Inunso mumangobwebweta zilizonse ahhhhh
ZAMADEMO SIYANI MUNAYAMBIRA LITI MADEMO KUMALEPHERETSA IYAAA KUMALAWI MADEMO SAZATHEKA , MANTHA ACHULUKA, KUOPA CHIKANGAWA
Kamanga sikazatheka
Panopo Layton Mangochi kuyakhula Za nzeru Ngati munthu tayanba kukusatilanso
Manganya wazisiya kale analibe azimayi ake opusa ajatu
Ndazikonda izi asazolowere avp ndimunthu wachipongwe
Usi opusa kwambiri
😂😂😂😂😂 yes bwana Mademo ankhareko
Indee amanganya khalidwe alibe
kuyitanila ngat malonda amangochi kkkkkk
I don't think MCP will give us chance to demonstrate on Monday ,
I don't think malawians will fight back our freedom
Manganya kasiyeni katopa kokha kalibe.nzeru mungoti phee mcp imutengesa
kd inu a mangochi mulibe zeru galu kachaso mau atha Kusatsa😂😂😂😂😂😂😂😂
Yomweyo Tiyeni Tiyeni nazoni😂😂
usi ndiwachamba
APM mwamuiwala atsogo
inu tamakambani yamafutayo basi!!!!!!!! koma ikakhala ya smartmatic a mec akuzani kale kuti a opposition onse ali komweko pofufuza zimenezi
🤞🤞💪
Mademoiselle kulibe tiyeni kumunda basi .anthu away zoawo zidayera kale
Enawa bwanji sukuwatchura? Peter profesa siotsutsa?
Apm apite kumademo akataniko? Ali ndi anyamata ake apita kumeneko not Big man himself kuthamanga pa nsewu ngati Chakwera the Chikangawa President.
Manganya ndi mfiti uja sua
Osaopa,osatopa,osafooka
❤❤❤
Ugoka zapatnubo😂
Ngat ulibe zoyankhula bola kumngokhala osayikirapo molo
Phanani mesa nonse atatu ndinu aku mwela anthu adyela inu tamuwoneni kuchikamwa tamawawuzeni anthu kumwelako azipita kumunda osamangolimbana ndi ndale kenako mzizati anthu akudya chiteze chaka chamawa ana asatana inu fotsek.
Panya pako
Naweso panyelo pako mwana wa hule mwana opanda bambo iwe chimwana chapantchile ndimwambo omwe ulibe coz ulibe ukulangiza
Ka munthu kameneka kamanganyaka😂😂😂
Lyton mutu sukugwira
Mademo boma lidaletsa nde mupita kut a police akukhala busy nthawi ya mademo ngat nokha simungadziteteza,za mademo zokha siyani chifukwa chiyambilen mademo sakuchitika nde ife masapota anu tisakunamizeni tatopa kubwelera kumademo
Ati munthu wausatana😂😂😂
Chisilu iwe mphawi wachabechabe
Kukhlala wachuma opanda nzeru nde vuto
Komaso asakayiwale chisango
Koma akuluwa ma ARV auwazunguza bongo mutu mwawo sukugwira
Mukunama inu.
Yes Kabambe Ali ndimphamvu kumuyotanisa Usi chifukwa kuchipani Michael Usi ndimunthu wamba president ndi Kabambe
Kkk
Zopanda mchere
😂😂😂😂
Mangochi palibe chomwe ukulankhulapo chanzeru apa. Ukhala bwanji ndi bodyguard iweyo uli bodyguard kale.kape iwee peza zina zochita olo utayamba using anga
Achitsilu Inu moti ana amati adad alipantchito kunena imeneyi shame on you
😂😂😂😂😂😂 koma guys
Michael usi abwere ku commit yaikulu apasidwe mwambo apoo aaaaai achotsedwe Dr Dk mphamvu mwapasidwa ndi ma derigates