Namadingo ndi one Mr kungoti inuyo atola nkhani ndi amene mumafuna kuyipitsana nthawi zambiri ndi bwino kumavomeleza I munthu wina akakhala kuti zake zamuyendela adoko adavaya 👌👍
That means if namadingo is compared to any new hit artist any time he is a very good artist of all times so no one can be compared with him. Namadingo you're always good note this bcz even if they can hert u they always point u also the whole world 😂😂😂 proud of you
ine sindikuonap vunto ndisanje yokha komaso muthu sangakonde oyimba ose chachikulu osaziyang'anila pas enawo ndiathu amene ama ngogemula bas ndiy tchitu yaw
Zina zose nchabe, namadingo trying to draw competition between himself and Lulu is what led to most people believing wfika pozimva kwambiri and that was the genesis of the amass hatred towards him. Akanafuna kupikitsana ndi amatama anzake, the likes of onesmus, I don't think bwezi Pali vuto but he went after the coolest guy odziwika ndikupanda ma vuvu in the industry. He gave the impression to be the morden and more successful version of the outdated Lulu which angered most fans as Lulu has a LOCAL fan base more than namadingo chifukwa za chikondi anayamba nkale namadingo akadali ku gospel. Namadingo lost most of his LOCAL fans when he changed to become a circular artists and was still in the process of capturing the heart's of new fans at the time whilest Lulu's local fan base was intact hence he stood no chance beefing him.
If they compare each and every upcoming artist with namadingo that's means namadingo is forever star and he's rocking and he will rock now and then 😂😂😂
Namadingo ndi star💥🎉 ndipo amene timamukonda ndife ochuluka😍🎉, iweyo samu ndamene umadana naye mhmm
He's one of my favorite artist
I don't know what you are saying because namadingo is the most followed artist l don't see hate anyway you are doing your business
Namandingo is one of greatest musicians here in Malawi that's why Mikoz compares him to other artists how are HOT at the moment not Mikoz hating him
Ño one
timamkondabe namadingo olo muzidana nae kungokhala ndimoyo wanyemba kufuna kutha nkhuni🙌🙌🙌
Namadingo anthu olephela amamuchitila nsanje chifukwa Dr Namadingo is a man of his words.
Namadingo ndi one Mr kungoti inuyo atola nkhani ndi amene mumafuna kuyipitsana nthawi zambiri ndi bwino kumavomeleza I munthu wina akakhala kuti zake zamuyendela adoko adavaya 👌👍
l like him
That means if namadingo is compared to any new hit artist any time he is a very good artist of all times so no one can be compared with him. Namadingo you're always good note this bcz even if they can hert u they always point u also the whole world 😂😂😂 proud of you
My artist Doc
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Till today l don't know reason why most Malawians hate Namadingo but Doc Ali pa top
I like Namadingo he is so unique when it comes to music ❤ keep pushing bro
The Fact
Me2 Ndimakonda Kadzi Onenepa Ndipo It's Ma Favorite 😊
Hahahaha
Auze namadingo kkkkkkkkkkk wandifikapo God bless you
Namadingo ndi king inayo ndi sanjee chabe ❤❤
I like namadingo enawo amamuda patience chifukwa chot anzawo akumudanso
Imagine hate yoyamwila
Amakwana ameneyo palibenso
Phazi lako Sam ifetu Doc tinayamba kumutsata kuyambila kale
Watching from Milange Moz🇲🇿
Ankazi onenepa ndiwochapa zovala osati oka njoya nawo🤣🤣🤣
Nkazi azikhala ogwilika sanalakwitse
Doc anavaya ❤️🔥🔥🔥
Boh kulimbikitsa
❤❤
ine sindikuonap vunto ndisanje yokha komaso muthu sangakonde oyimba ose chachikulu osaziyang'anila pas enawo ndiathu amene ama ngogemula bas ndiy tchitu yaw
That's great
Ndidolo doctor ❤❤❤
I love 💕 namadingo
Man I love Namadingo
Ngat ine ndimakonda onenepa mene ndilili
Mumakwana mandala Sam ukali wanu mandala
Kungoti amalawi sitimafuna kutukulana kapena ndinene kt kulemekezana munthu akachita chabwino walakwisa akachita choipa nde nanji eish😢 amalawi let's respect each other plz kusesa munthu sumayambira kusesa kunja kumalizira mnyumba tiyeni takonde oyimba akwathu ndameneso akupitisa dziko lathu pasogo. Ndikakhala ine nde ndimakonda oyimba aliyese wa Kwanthu ku malawi 😅
Namadingo ndi Dolo kuposa makape enawa iyaaaa then Namadingo amayankhura zilungamo zokazokha
Kod video yoyi mwalandila zingat kwa doc
Zina zose nchabe, namadingo trying to draw competition between himself and Lulu is what led to most people believing wfika pozimva kwambiri and that was the genesis of the amass hatred towards him.
Akanafuna kupikitsana ndi amatama anzake, the likes of onesmus, I don't think bwezi Pali vuto but he went after the coolest guy odziwika ndikupanda ma vuvu in the industry.
He gave the impression to be the morden and more successful version of the outdated Lulu which angered most fans as Lulu has a LOCAL fan base more than namadingo chifukwa za chikondi anayamba nkale namadingo akadali ku gospel.
Namadingo lost most of his LOCAL fans when he changed to become a circular artists and was still in the process of capturing the heart's of new fans at the time whilest Lulu's local fan base was intact hence he stood no chance beefing him.
Mwanena bwino inuyo
I see sam mavita hates Namadingo
Makonda makonda buy the way Doc anavaya
I like namandingo🎉🎉🎉
Ngakhale amandinyasa nyimbo zake zathandizila kuwononga zikondi za anthu including me
How
Ife sitimamuda ayi
Anthu akamakamba za lulu ndi namadingo kunena zoona namadingo amatha, jelasi amalawi tisiye zoyamwila kapena magazi akumakolo
I like namadingo
Inuso mufuna mutchuke et mtopola bas doc Nd dolo
Am sorry to disappoint you... Koma I always try my best to bring unbiased content
🎉
Hate him, komabe i support him, Team Doc 🔥
Hate and support at the same time
Kunenepa Kuja ithink inali mimba evin chovala mudachiona ,mwana uja akuonesa 3 years
Zikhonza kukhala moterodi
@@sammalvitha ndipo or muone pic yachikhoswe zikuchita kuonesa koma sadafune kumayankhula zija ena amapanga
Ife timamukonda namadingo nsanje tilibe ife.
Mas força mano namandigo💪🤏🥰
Sanje nd nthenda ku Malawi kuno anyway Namadingo amayankhurà zoonã zokha zokha
Nchifukwa chake Zili pa national anthem,,, njala,nthenda NSANJE . Munthuyu amamudalanji?
More life Doc
Kuyankha kwake sakuyankha mwamwano. comparison ya namadingo ndi onesmus ndi yomwe inakwiyitsa namafanzyu mpaka kulengeza kuti amalawi sakumukonda
Pamene anabowera panali pamenepo sizinachitike zabwino btwn Onesimus & Namadingo himself
Therefore...Doc anavaya
Ambiri or ena?
my 🐐🐐
Namadingo amakwana
Iweyo ndi amene umadana naye
Ndiwamatama namadingo osati timamudana chifukwa cha akazi ai koma chilungamo amaziyika pamwamba ena pasi
& anatiwuza kuti wasamuka he is no longer a Malawian citizen
INEM ndi makonda, a thupi
P
Namadingo ja é moçambicano.
Ndiwamatama uyo
Amamuda ndani Namadingo? Odanitsa ndinu.
Mmamukonda?
If they compare each and every upcoming artist with namadingo that's means namadingo is forever star and he's rocking and he will rock now and then 😂😂😂
U r an amateur in commentary komanso zoti a Malawi ambiri amadana naye research yake munapanga liti? & What was the sample?
😂😂😂
The most hated musician to be the most followed Malawian musician kkkkkkk
Namadingo is arrogant, in fact you don't have to say ndinavaya but let the people prove it.
Doc anavaya
Ndiwodzimva uyu
Namadingo samayakhula bwino pofuna kunena ndi anzake
Ndiwamatama Namadingo