Ine ndi khristu shaikh koyambililako mwanena bwino, munthu akafa thupi limapita pansi koma mzimu umapita kumwamba, Ndichifukwa chake tidaona mose yemwe adamwalila kale ataonekelaso kwa Yesu, that's clear example
Mkungonamuzanapo za Muhamad wanuyo coz kulibe njila ina yopitila kwa Mulungu wamoyo koma mwa Yesu yekhayo Mwana wa Mulungu wamoyo Open your spiritual eyes plz
mashaAllah
❤
Thawi ikuchepa kwambili guys bwanji muzipangako 80 munits!! Chehe akuthawila ku atumiki ena bwanji? 😂😂😂😂😂
Shekh abuze
masha Allah ❤ 🙏
Alihamdulilah brothers
Masha Allah brothers and sisters in Islam ❤❤❤
Masha Allah
Next mtengeni saidi sambia
Anthu mpakana kumamumvera Muhammad!
Ine ndi khristu shaikh koyambililako mwanena bwino, munthu akafa thupi limapita pansi koma mzimu umapita kumwamba, Ndichifukwa chake tidaona mose yemwe adamwalila kale ataonekelaso kwa Yesu, that's clear example
Shalom shalom
Allah knows
Ndichifukwa chani atsogoleli achisalamu sawauza anthu zoona kuti ndi mwana wa Mulungu
Amishek mwaonetsa kuti bible limatsutsana chifukwa bible limat ose anathawa ndie apezeka bwanji ukoko kkkkk
Pochitika chiwebu adathawa koma pamene adali kupachkidwa adalipo
Mkungonamuzanapo za Muhamad wanuyo coz kulibe njila ina yopitila kwa Mulungu wamoyo koma mwa Yesu yekhayo Mwana wa Mulungu wamoyo
Open your spiritual eyes plz
Mngati mose sanauke pomwe anali mugetseman ndi ena mwa ophunzira kunatulukira mose ndi eliya ndipo ophunzira anati ambuye mutilate timange mitsatsa itatu wina wanu wina wamose wina wa Eliya
Mungatiuze ves imenei kuti mose anaikidwa Manda tidziwe nao