JESSIE KABWIRA WAYAMBAPO YAKE IJA - EEH WAYANKHULA IZI ATAWINA MPANDO WA U PUBLIC SECRETARY

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 9 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 61

  • @user-bl2ee4zk4n
    @user-bl2ee4zk4n หลายเดือนก่อน +7

    More fire mayi Jesse kabwira,mumayitha komanso kukwanila pa ground.A opposition ali njenjenje mmazi chifukwa cha kusankhidwa kwanu.Level ya inu 2025 mcp ndi boma kale,zosachita kubisa ayi!!!❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-nj4ob8jw6y
    @user-nj4ob8jw6y 29 วันที่ผ่านมา

    My favorite woman in Malawian affairs, Dr. Jessy Kabwira, you made me to leave Malawi congress party, but now a'm back with fire, coz of sister Kabwira. Tiyeni tiyambe tapita kwathu ku Mua tikakondwere.

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi หลายเดือนก่อน +8

    ifetikuziwa kuti Chakwera anapha Chilima ,,,

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 หลายเดือนก่อน +1

      Kkkkk ndie ku court upita liti umboni ndi omweu

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 หลายเดือนก่อน +1

      ​@@damianokachingwe3531funso labwino😂😂😂

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 หลายเดือนก่อน

      @@GraceZumazuma usachedwe thamanga ku court umbon ulinawo

    • @GraceZumazuma
      @GraceZumazuma หลายเดือนก่อน

      @@damianokachingwe3531 ku court ndi September 2025 kokavota osamasekelera chibwana mdziko lokhala lathu ana athu adzakahala pa moto

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 หลายเดือนก่อน

      @@GraceZumazuma kkkkkk maloto achumba amenewo bwana mukulephera kuwina by-elections mphamvuzo zilipati

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h หลายเดือนก่อน +7

    Zaziiii mcp ukuchoka mu Boma 🤞🤞

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y หลายเดือนก่อน +5

    Kusiya ntchito mkukakhala pa udindo opanda ndalama Ku chipani? Anthu inu andale mumatitenga anthu ngati ife zitsiru. Muzinva manyazi benefiting over the poor.

    • @kingsleyChisenga-i8g
      @kingsleyChisenga-i8g หลายเดือนก่อน +1

      Amenewa zawo ndizoyera kale m'bale tingocedwanawo tizingopanga zathu bas

    • @user-iq5xk6ju7y
      @user-iq5xk6ju7y หลายเดือนก่อน

      @@kingsleyChisenga-i8g M'bale ndizoona ukunenazo. Koma akamaononga kwambiri ife oyesela patokha timatchingilidwa Pena pake.

  • @hudsonheadsonidanah9474
    @hudsonheadsonidanah9474 หลายเดือนก่อน +4

    Opportunist Jersey Kabwila

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 หลายเดือนก่อน +1

    Kabwira went to UTM out of frustration. She is an MCP bona-fide.

  • @hendresonsande5156
    @hendresonsande5156 หลายเดือนก่อน +3

    Ndikumva nyimbo ya dpp kuseliko ija amati pangono ndi pangono a Peter akubwela tiyendee😢😢😢

    • @user-xt2ic5gg1g
      @user-xt2ic5gg1g หลายเดือนก่อน

      Satha kupeka nyimbo a MCP

    • @GraceZumazuma
      @GraceZumazuma หลายเดือนก่อน

      Aba nyimbo DPP ija

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 หลายเดือนก่อน +2

    All the best Jesse...

  • @edsonphangula5817
    @edsonphangula5817 หลายเดือนก่อน

    Indeed more power MCP she understand politics

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw หลายเดือนก่อน +2

    Komatu Jessy adaotcha msalu za congress ndiye pano tizinji kodi

  • @divaisonjickson5281
    @divaisonjickson5281 หลายเดือนก่อน +1

    Oh Ajessy mwatero moti fetereza uja muxitiuzanso kuti tigula K4,500 kapena mubwera ndi ina

  • @PledgeBanda
    @PledgeBanda 28 วันที่ผ่านมา

    Agalu achabe Chabe kusiya ntchito zanu kumakapaga zaziii mitu yanu

  • @user-mm3wq8qp2q
    @user-mm3wq8qp2q หลายเดือนก่อน +1

    mau ngati chigayo😂😂 koma nzimai

  • @user-ty1vq9lq6w
    @user-ty1vq9lq6w หลายเดือนก่อน +2

    Ovotera magazi party ndani

  • @peterdanie4684
    @peterdanie4684 หลายเดือนก่อน

    Machine Jessie Kabwira

  • @AlcidioManuelGabriel
    @AlcidioManuelGabriel 9 วันที่ผ่านมา

    NDIZOONA NZIMAYI UYUYU AMATHA NYALE YA MCP INALI YOVINDIKILA.

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 26 วันที่ผ่านมา

    Anthu akupitirako ndalama basi..ine kulowa lero mawa millionaire..APM by vote

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 หลายเดือนก่อน +1

    Viva Jessy Kabwila, I like this woman but not MCP

  • @SherryJiya-c1u
    @SherryJiya-c1u 29 วันที่ผ่านมา

    Mission ikuchokela patali Malawi wake up

  • @AllanJentala-g6h
    @AllanJentala-g6h หลายเดือนก่อน

    Boma ndi lomweri ❤❤❤

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani หลายเดือนก่อน +1

    Koma mayi uyu ndikatundu

  • @BragaDeeh-j1x
    @BragaDeeh-j1x หลายเดือนก่อน

    Zadyera kumalawi

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o หลายเดือนก่อน +1

    Munva kuning'ina ndi Jesse kabwila

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 หลายเดือนก่อน

    Mistake imene anapanga a MCP Anapha Chilima Koma Anasiya Nkazi wake wamoyo

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v หลายเดือนก่อน

    Richard Msowoya alipo?

  • @IsaacKulongwe-ol5mx
    @IsaacKulongwe-ol5mx หลายเดือนก่อน

    MCP 2025 Boma mufune musafune enanu dzavotereni opanda manoyo

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 หลายเดือนก่อน

    Wachita bwino kutuluka. ,,ndiwamilandu ndikusokoneza

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 หลายเดือนก่อน

    Opusa ndiyamalawi

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 หลายเดือนก่อน

      Chokani apa, mulibe nkhani inu.

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms หลายเดือนก่อน

      ​@@tamalangoma2765lwe uli ndikhani yanji chifukwa nkhani ili pose pose.

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole หลายเดือนก่อน

      Ndege singagwe 10 koloko mmawa kuyamba kusaka 4pm asilikali 8 nkhalango ikulilenj ndege yogwa mphepete mwa nsewu ndege osayaka adaphadi chilima.

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 หลายเดือนก่อน

      ​@@SolomonNjolomoleMuchedwa nazo bwana thamangan ku court ngt mukufuna ziyende

    • @anthonynkhoma4265
      @anthonynkhoma4265 หลายเดือนก่อน +1

      Chakwera my vote

  • @IrvinejuniorJere
    @IrvinejuniorJere หลายเดือนก่อน

    Chipani chauchitsilu

  • @user-zr5oc3rg2c
    @user-zr5oc3rg2c หลายเดือนก่อน

    Zoooonadi

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 24 วันที่ผ่านมา

    Jessy Kabwira "A FAILURE"? Useless academic.

  • @mcdonaldmuyombe4380
    @mcdonaldmuyombe4380 หลายเดือนก่อน

    Voice yako yimapanga irritate. Uyisinthe nzanga

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y หลายเดือนก่อน

    Ife ndiamene tingachose nyasi izi za mcp 2025