ACHINA BRIAN BANDA ANG’ALURA ATANGOMALIZA KULENGEZA MA VOTE ONSE OGAWA NDALAMA ALUZA KU CONVENTION

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 9 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 180

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน +13

    Zikhale ngoma umayerekedwa pomanga anthu ngati ndiwe mulungu kubera mabrund musaketu bakili muluzi tv

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd หลายเดือนก่อน +26

    5 YEARS TIKUGWETSA NO CHITUKUKO CHILICHONSE...POLITICS EVERY DAY...FUCK THIS GOVERNMENT....A COUNTY WE CAN'T EVEN GET A PASSPORT..TWO PEOPLE ON ONE BED IN GOVERNMENT HOSPITALS.. NOT EVEN MEDICINE FOR POOR PEOPLE SHAME ON US A CURSED NATION.....

    • @WonganiKatchale
      @WonganiKatchale หลายเดือนก่อน

      Mulikuti?

    • @robertfrackson8814
      @robertfrackson8814 หลายเดือนก่อน

      Uli ku south africa iweti

    • @JohnmarkNazombe-hi9xd
      @JohnmarkNazombe-hi9xd หลายเดือนก่อน

      @@robertfrackson8814 it doesn't really matter kut ine ndili kut...???

    • @JohnmarkNazombe-hi9xd
      @JohnmarkNazombe-hi9xd หลายเดือนก่อน

      @@WonganiKatchale what do you mean.....? ine ndi Malawi ngat iweyoooo

    • @user-hs4bm2yj8r
      @user-hs4bm2yj8r หลายเดือนก่อน

      Ndipo ndizoona bro,ine chipani Ichi ayi ndithu chatizunza amalawi

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx หลายเดือนก่อน +9

    Kunkuyu mwatsika mu mitengo tu Allan witika munapha uja nanuso mupita ndi miyala njilamu musa male ndi zikhale ndi chithyola nonse ndi nkaka agenda mu ntcheu a kwa chilima nonse

  • @RManyau
    @RManyau หลายเดือนก่อน +8

    zikhale ng'oma zomwezo vinyo watha mujekete

  • @mwaiwaobanda2691
    @mwaiwaobanda2691 หลายเดือนก่อน +9

    Ambuye amatsitsa ozikweza ..nakweza ozisisa....tiyeni tilimbike kupemphera basi 2025 ...ambuye ayankha ndithu

    • @YusufuUsumani
      @YusufuUsumani หลายเดือนก่อน +1

      Inshaallah ambuye atiwalitsa 2025 dpp ❤️❤️

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน

      ​@@YusufuUsumani❤❤❤

    • @abbasdamsonamini4888
      @abbasdamsonamini4888 หลายเดือนก่อน

      ❤❤❤ DPP booomaa❤❤❤❤🎉🎉🎉

  • @JuliasElias-c5x
    @JuliasElias-c5x หลายเดือนก่อน +3

    Kamajekete😂😂😂😂😂😂😂

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 หลายเดือนก่อน +8

    Amchita bwino Zikhaling'omba😂😂😂😂

  • @ireenesthermbisa7200
    @ireenesthermbisa7200 หลายเดือนก่อน +6

    The DC tuluka komwe uliko uying'alule kuno 😂😂😂😂😂

    • @kekeaufi9834
      @kekeaufi9834 หลายเดือนก่อน +1

      😂😂😂😂🎉🎉

    • @lawrencemakina2882
      @lawrencemakina2882 หลายเดือนก่อน

      Wang'alula kale kkkkk

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm หลายเดือนก่อน +7

    Zotsatila za chisankho ichi zitidziwitsa chilungamo cha zimene zidachitika ku Chikangawa pa 10 paja .

    • @LoydKameza
      @LoydKameza หลายเดือนก่อน +1

      😂😀😂😂😂ndpodi aulura zisisi after kupsa mtima

    • @Blessingskanyinji-x7s
      @Blessingskanyinji-x7s หลายเดือนก่อน +3

      Koma apo nde mwalankhuladi tzisitsi ziululika timva ku Limpopo fm 🎉🎉🎉

    • @SamseyHassan
      @SamseyHassan หลายเดือนก่อน

      Apapa we can comfortably confirm kuti ukuku aulurana 😂😂😒

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน +4

    Kumkuyu uyangane kumwamba umuone mulungu mmene amamutsitsila munthu unaeina pomupha allan witika mzimu wake wakwiya nawe

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg หลายเดือนก่อน +6

    Zikhale ng'oma mutu uphulika mizimu yakwiya 😂😂😂

  • @ChrispinJohnson-py5ie
    @ChrispinJohnson-py5ie หลายเดือนก่อน +8

    zikhaleyoo uyooo ,2025 muziona chikangawayo agwanso Malawi siyanyumba mwanu muziona

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน +5

    Anthuso avotera prezdent wa experience 2025 achina Chunga kumeneko kkk

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu หลายเดือนก่อน +6

    Vinyo watha kamajekete

  • @gkay-striker
    @gkay-striker หลายเดือนก่อน +4

    I'm very happy chaluza chigalu chimenechi chimatumbwa Kwambiri,ndikamwe Kaye mowa apa

  • @fridaylongwe602
    @fridaylongwe602 หลายเดือนก่อน

    I like the idea "ndalama talandila Koma ife tisankha munthu oyenela"

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju หลายเดือนก่อน +3

    Tikatere tayambspotu😂😂😂😂😂😂 becareful chikangawa 😂😂😂😂

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f หลายเดือนก่อน +4

    Ndipo izitu asasangalale kwambili zikulosela zinazake chaka chamawachi😂😂😂😂😂😂

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 หลายเดือนก่อน

    1.2.3 John wick excommunicado lol

  • @ireenesthermbisa7200
    @ireenesthermbisa7200 หลายเดือนก่อน +2

    The question is Ndalama zomwe amagawa amazitenga kuti? Alibenso mphamvu pano afufuzidwe....misonkho yathu izithera izi😭😭😭

  • @AlexPhiri-in1re
    @AlexPhiri-in1re หลายเดือนก่อน +1

    Kamajekete woyeeer 😂 😂😂

  • @user-bi6pb5gc8t
    @user-bi6pb5gc8t หลายเดือนก่อน +3

    18:10 Brother bakili TV anyamata amakusaka Aja onse alephela mayeso uku tiyenawoni tiwagende ndizidina zamoto zikhale woyee witika kunkuyu woyee

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x หลายเดือนก่อน +3

    Mumba waberedwa ma vote

  • @NabeelAlie
    @NabeelAlie หลายเดือนก่อน +1

    Manganya si wawona ,kugawa ndalama si udolo,bwelelan kwanu kwawen ndi kwawen

  • @user-px9jd9co3v
    @user-px9jd9co3v หลายเดือนก่อน

    Who has won ?

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu หลายเดือนก่อน +3

    Koma Carthy mpaka ena agula ma plot koma zilipo kwambiri

  • @YamzyAmos
    @YamzyAmos หลายเดือนก่อน

    Zikhare ng'oma is strategically waluza ndithu

  • @SabinaNkhoma-sf7kz
    @SabinaNkhoma-sf7kz หลายเดือนก่อน +2

    Vote ndimumtima

  • @AishaOsman-m8x
    @AishaOsman-m8x หลายเดือนก่อน +4

    Wasala wamkuluyo 2025 akukagwaso

    • @chesterphiri7523
      @chesterphiri7523 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂😂😂

    • @DeliaKaduya
      @DeliaKaduya หลายเดือนก่อน +2

      Ndipo mmene zachitikiramu atsegule maso ake, Malawi wa lero siwipusatu

  • @owenmoses9434
    @owenmoses9434 หลายเดือนก่อน

    U always deserves bg

  • @chipiesato-ut7hx
    @chipiesato-ut7hx 29 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😅😅😅km zilibwino kwambiri chikangawa part

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j หลายเดือนก่อน +3

    Anthu ari pokudya ndalama mavoti ari mu mitima kkk

  • @user-ew4dm8yy3b
    @user-ew4dm8yy3b หลายเดือนก่อน

    Ambuye omva kulira kwa anthu imvan kulira kwa amalaw. Chaka cha mawa tisinthiren usogoleri bweresan mutharika ayang'anire dzikoli

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx หลายเดือนก่อน +3

    Ambuye alemekezeke kuti a zikhale aluza anapanga mwano ndikudziva

  • @LUCIAChambote
    @LUCIAChambote หลายเดือนก่อน

    Yomweyo galu iwe😂😂😂😂 uipemelereeeeeeee... Uipatse motoooooo💥💥💥💥💥

  • @user-ru6fc3qy5n
    @user-ru6fc3qy5n หลายเดือนก่อน

    Akunkuyu mwano onse uja watha dikilani nanuso muzamangidwe kukubwelaku 😂😂😂😂

  • @McfalenGola
    @McfalenGola 28 วันที่ผ่านมา

    😂Kkkkk koma kumeneko wagwanayo zikhale nkhope Ngati popayi wakhaula

  • @JoyceNkhokwe
    @JoyceNkhokwe หลายเดือนก่อน +2

    Kkkkkk koma ndiye vinyo wathaaaaa

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 หลายเดือนก่อน +4

    Bakili TV is watching you zikhale😅😅😅

    • @GloriaKaduya
      @GloriaKaduya หลายเดือนก่อน +1

      Ndipo pompano timunvera

  • @SharifChibwana
    @SharifChibwana หลายเดือนก่อน +1

    Akukanika kukopa anthu 1400 akwanisa anthu 20 million

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya หลายเดือนก่อน +1

    Convention iyiyi bola wina asaziphe yekha 😂😂😂😂😂

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b หลายเดือนก่อน +3

    Zikhale zikomo udziwe kt Mulungu amamva nkhanza zija mukapangila ndan?anthu omwe umawasaka aja lero asaka iwe dziko umalitenga ngat lako

    • @CliveChikaphonya
      @CliveChikaphonya หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂 asamuka ameneyo

    • @LUCIAChambote
      @LUCIAChambote หลายเดือนก่อน

      Kkkkkkkkkkk choipa chitsata mwini

  • @YamzyAmos
    @YamzyAmos หลายเดือนก่อน

    Ken zikhare ng'oma 93 votes 2025 boma😂

  • @ConfusedCupcakes-ke8ql
    @ConfusedCupcakes-ke8ql หลายเดือนก่อน +2

    That is erosion package to ZikhaleNg'oma

  • @user-ru6fc3qy5n
    @user-ru6fc3qy5n หลายเดือนก่อน

    Azikhale ng'oma ndi akumkuyu munatchukatu 😂😂😂😂 mwakhaula

  • @user-pp3zd5zb2h
    @user-pp3zd5zb2h หลายเดือนก่อน

    Kmtu zikhale ng'oma ndisakumane nawe ndikuthira duka iwe galu mbuZi😂😂😂😂

  • @daviskamonde4882
    @daviskamonde4882 หลายเดือนก่อน

    Missed opportunity for MCP in the north. Vitumbiko was a perfect piece of jigsaw for Lazarus in next year's elections. Vitumbiko could replace the void SKC left in the north.

    • @beinhardkausiwa7107
      @beinhardkausiwa7107 หลายเดือนก่อน

      Very true and he could have come with a good vibe

  • @JamilMchakama
    @JamilMchakama หลายเดือนก่อน

    A times mukulephera kutchula mayina bwanji?

  • @elizachisanga2671
    @elizachisanga2671 หลายเดือนก่อน +2

    Mkakawo ausungunula ndi mchere kuti usanduke madzi 😢😢

  • @CatherineKamsare-cy3yo
    @CatherineKamsare-cy3yo หลายเดือนก่อน

    Matama onse aja Kamajeke,Kunkuyu ndiogawa money aja aluzaso🤣🤣🤣🤣🤣

  • @user-jb5hr4rz2s
    @user-jb5hr4rz2s หลายเดือนก่อน

    Azikhare ngona mwachita bwino kuluza ndi akukuyu muli ndi mitima yo nyasa kwabasi

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko หลายเดือนก่อน

    Iwe kamajekete mpaka 93 😅😅😅😅😅😅

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂😂dziko Lima zungulula

  • @FosterSuwedi
    @FosterSuwedi หลายเดือนก่อน

    Ndi ka network kako ka 2G ko ndye wabowa😢

  • @RichmanIssah
    @RichmanIssah หลายเดือนก่อน

    😂nde mwati nkhani ndiyazikhale
    Ndengati anthu akuchipani sakukufuna umangoziwilatu pakaipa😂zikhale

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol หลายเดือนก่อน +2

    Nde nyama zikuluzilulu pano mkumanati chani

  • @WonganiKatchale
    @WonganiKatchale หลายเดือนก่อน +1

    Yes indeed

  • @HajjAmadu-e1u
    @HajjAmadu-e1u หลายเดือนก่อน

    Zikhale sangawine wasala mbale wakeyo anthu okuphawo

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg หลายเดือนก่อน +1

    Bakili tv naye zikhale ndi kunkuyu 😂😂 anya manyi uku

  • @khumbotembo302
    @khumbotembo302 หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu amatsisa ozikweza ndipo anyamula ozichepesa

  • @MosesKamtndo
    @MosesKamtndo หลายเดือนก่อน

    Kalandeni ndalama akuthyoleni miyendo anthu adakwiyati

  • @getrudeminikwa9636
    @getrudeminikwa9636 หลายเดือนก่อน

    Tili mu nthawi ya zikhale ngomaaaaaaaaaaaa waionatu

  • @CliveChikaphonya
    @CliveChikaphonya หลายเดือนก่อน

    Ndpo Wina akadativuta akadawina ndthu stikadayenda Ai.azipta azikalima fodya ukoo😂😂😂😂😂

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde หลายเดือนก่อน

    Chete watching from khotakota😂😂😂

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂 wamphwasamuka zikhare pathakopo kkkkkkk

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo imfe timakhala tikunena kuti ndalama siyigula chikondi mamuna wabwino amaoneka ndi mtima wabwino awa azikhale ng,oma koma kulimbana ndi wa bakili muluzi uleke zimenezo

  • @RichardChirwa-em6qj
    @RichardChirwa-em6qj หลายเดือนก่อน

    Mkaka ndi zikhale mmazimva uchi ngati mcp munayambitsa ndinu akuchotseni indiana lazalo vmyaluke ndi kunkuyu anthu akupha in ndll

  • @manasemaposa
    @manasemaposa หลายเดือนก่อน

    Come 2025 another shock is coming

  • @LysonMkomadzinja
    @LysonMkomadzinja หลายเดือนก่อน

    Mzimu wa anthu aku chikangawa uja osauphweketsa

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b หลายเดือนก่อน +1

    Azikhale ng, oma achita bwino kuluza amazimbva kwambiri

  • @mikaeelmumba2408
    @mikaeelmumba2408 หลายเดือนก่อน +1

    Andevu za mwayi ali kuti?Amenewa amafotokoza bwino kwambiri....apit bull.

  • @josephnyirenda1683
    @josephnyirenda1683 หลายเดือนก่อน

    Osewa achita bwino osawina akupha wanthu ukachita choyipa uziwe kt chikudikila kumbuyo mizimu ya anthu 9 simasewela BP yikukomola nanuso

  • @MariaKhowoya-lu5yc
    @MariaKhowoya-lu5yc หลายเดือนก่อน +1

    Yomweyo galu iwe😂 waluza mavot kamajaketi ng,oma

  • @RashidJohnphirigombwa
    @RashidJohnphirigombwa หลายเดือนก่อน

    Munthu WA mayi unamulanda Malo uja apo ndiye umenyedwa ndi Ana galu iwe

  • @LuskaMoses
    @LuskaMoses หลายเดือนก่อน

    Mulungu alipo ndipo alipo imfa ya chilima ikukathani😢😢😢

  • @SibahleThoko
    @SibahleThoko หลายเดือนก่อน

    A mcp gawaniso ndalama ku tundu wa amalawi kaya ngongole gawaniso komano ziwani kuti chidikhodikho chili mu mtima

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt หลายเดือนก่อน

    Ken zigone /ziyime/zikhare ng'oma/mabatcha/màmbilira walephera mongàso maudindo ake akulephelera 😂😂😂😂

  • @RosinaWakuthera
    @RosinaWakuthera หลายเดือนก่อน

    Aviator 1.00x flex away 😢

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o หลายเดือนก่อน +1

    Ife pheee kudikila wa Bakili Muluzi TV zikhale Ng'ona ndi Kunkuyu kuti akumva bwanji mthupimo

  • @PeterHuckilin
    @PeterHuckilin หลายเดือนก่อน

    Check out aspairant mps next it's you moto umapita kwatsala tchire

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v หลายเดือนก่อน

    93 keni zikhale ng'oma chimutu chikulile mwano😅😅😅😅

  • @WitnessKamoto-bf4pu
    @WitnessKamoto-bf4pu หลายเดือนก่อน +1

    Zovuta kwambir 🤣🤣🤣🤣

  • @user-pv8dg6fc5y
    @user-pv8dg6fc5y หลายเดือนก่อน

    Muudziwe moyo achina ujen 😂😂

  • @GubuduLungtone
    @GubuduLungtone หลายเดือนก่อน

    Mulungu simunthu azikhale Ngoma mwanva muzifuse

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu หลายเดือนก่อน +1

    Nanunso2 network yanuyi ndie ndi manyaka2 nanga ikungoduka duka ofunika muzitolere

  • @chcmzuzudiocese5916
    @chcmzuzudiocese5916 หลายเดือนก่อน

    Seems Brian Banda wakulira ku mudzi .Ali ndi moyo wa magemu

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 หลายเดือนก่อน +3

    Zikhale Ngoma mulungu alemekezeke unapha Chilima ndi Kunkuyu .agalu ino

  • @haroldfodya7071
    @haroldfodya7071 28 วันที่ผ่านมา

    Oooooo mkaka😂😂😂😂😂

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u หลายเดือนก่อน

    Mizimu ndiyokwiyabe mpaka 2025

  • @AdamMpalira
    @AdamMpalira หลายเดือนก่อน +2

    Diesel watha

  • @AfickDaud
    @AfickDaud หลายเดือนก่อน

    ankamwaza dala anali nd plan yokaba,ankadziwa kut akawina azakabwezeretsa kkkkk sorry kwammbiri koma

  • @Jele-mk9ip
    @Jele-mk9ip หลายเดือนก่อน

    Zikhale Ngoma.

  • @wilsondairi5459
    @wilsondairi5459 หลายเดือนก่อน

    Who is this guest speaking?

  • @user-ov7yw4bq7y
    @user-ov7yw4bq7y หลายเดือนก่อน +1

    Apa wabakili muluzi asakidwabe kapena zapita ndi kama jecket

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkk aja amati ndi eni Malawi akhara pansi😂😂😂

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q หลายเดือนก่อน

    Carthy iwe wawina takuona upange chitukuko kwwnu chamiseu osati kumadura anthu ziwaro yayi chepesani rekani kudumura virarowawanthu

  • @chimwemwekamwendo3701
    @chimwemwekamwendo3701 หลายเดือนก่อน

    Eeesh

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 หลายเดือนก่อน +1

    Amuchita bwino kamajekete ndi satanaso kwambiri amuchita bwino

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 หลายเดือนก่อน

    Chi network chake ndiye manyaka eni eni basi

  • @LindiweMamwene
    @LindiweMamwene 28 วันที่ผ่านมา

    Muziwe kut onse alepherawa nd oyipa mtima