BON KALINDO THE D.C 4 JULY 2024

แชร์
ฝัง

ความคิดเห็น • 106

  • @jamusnamwino-br2iz
    @jamusnamwino-br2iz 3 วันที่ผ่านมา +3

    munthu amene amadana ndikalindo ndifiti kwambiri Kalindo amatiimirila ife amalawi

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 วันที่ผ่านมา +3

    Kuyakhula mwatchutchu bon ❤

  • @ChristopherMadulira
    @ChristopherMadulira 3 วันที่ผ่านมา +3

    The DC mwana oopsaaa kwambiri gwilan ntchito boss

    • @MosesKalenge
      @MosesKalenge 3 วันที่ผ่านมา

      💔💔💔

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 3 วันที่ผ่านมา +1

    Big up Mr bon kalindo we president 🎉🎉🎉❤❤❤❤zikuntha pa 10 zimenezo za maminazo apampa tipanga za ku kenya 🇰🇪 pa 10 si patali ai so soon ife amalawi ndife wokwiya ndi boma la chakwera never go back

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 วันที่ผ่านมา +2

    Very true The great Bon Kalindo. Opposition need to go and challenge this new rule of no 🆔 no voting.
    Otherwise, we don't need NRB in our country because they're working for MCP and not Malawians

  • @ElasonAimon
    @ElasonAimon 3 วันที่ผ่านมา +3

    Kuyankhura molikonda zdiko mowakonda a Malawi mulungu apitilize kupatani mphavu Komaso madalitso ochuluka

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 2 วันที่ผ่านมา +1

    The dc ..mwana owopsa kwambiri 🤣🤣

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t 3 วันที่ผ่านมา +3

    Ndipo apolisi amanyi nonse mukonzeke pa ten pano tikaphane basi oyamba kufa sindikhala ine ndatopa nazo mungosekelala zopsa basi kandalama kake kati komwe mukugulisila anthu osalakwa

  • @user-wu8kp7ui5j
    @user-wu8kp7ui5j 2 วันที่ผ่านมา +2

    The DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @lameckmajiga5426
    @lameckmajiga5426 3 วันที่ผ่านมา +2

    Muziko mwanthu muno mukuchitika zinthu zonyasa kwambili koma ife anthu timawopa kuphedwa kapena kumangidwa!!! Ili ndi ziko la democracy not one matparty system

  • @chirpykachingwe6802
    @chirpykachingwe6802 3 วันที่ผ่านมา +2

    Munthu uyu amenyela nkhondo Malawi it's up to you Malawians kukhala mene mulili olo kutengapo step

    • @JumaKachala
      @JumaKachala 3 วันที่ผ่านมา

      Nkhaniyo ndiyowona

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 3 วันที่ผ่านมา +2

    Mr pangolin tatulutsireni ndodo ija achinagwenembewa

  • @omanm2919
    @omanm2919 3 วันที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤❤ The DC nthawi zonse kuima pa chilungamo. Ndipo chilungamotu sichimawopsa stand with u all the time

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 วันที่ผ่านมา +1

    I support The DCs mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi.

  • @user-xc1gk6bw6m
    @user-xc1gk6bw6m 3 วันที่ผ่านมา +1

    Powerful massenge fadah ❤❤

  • @user-pf5hu2pd2b
    @user-pf5hu2pd2b 2 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwela ndi mbutuma yamunthu ndi gulu lake

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 3 วันที่ผ่านมา +2

    Ndipo message ya apolice ndi iyi mukazagopezeka mukutenga bali ya chakwera uzazima sitikuchedza pa 10 ok we need change our Malawi 🇲🇼

  • @AliciaMaphanga
    @AliciaMaphanga 3 วันที่ผ่านมา +2

    ❤❤❤❤❤ DC

  • @DONOR265
    @DONOR265 3 วันที่ผ่านมา +2

    Za ma hca zo ndee eeeeh zavuta zedi

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 3 วันที่ผ่านมา +2

    Ulemu wanu Malume ❤

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 วันที่ผ่านมา +1

    Panopa ine ndikupanga biziness koma profit ndiyaying'ono kwambiri. Mutu wanga wayima.

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 3 วันที่ผ่านมา +1

    Oletsa zoyankhula zanu munthu wamkulu,ameneyo ndiye kuti ndi mfiti.mulungu akudalitseni bwana

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 3 วันที่ผ่านมา +1

    Good Messnge my Bon Kalindo

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 3 วันที่ผ่านมา

    Mashing opangila mashin anzake D. C NUFF RESPECT TO YOU MUMATIIMILIRA 💯💯💯

  • @PatrickSamson-po7uy
    @PatrickSamson-po7uy 2 วันที่ผ่านมา +1

    Umakwana

  • @johnnyeliah4302
    @johnnyeliah4302 2 วันที่ผ่านมา +1

    That's true Mr. D.C

  • @user-jw5rx9ze8k
    @user-jw5rx9ze8k 3 วันที่ผ่านมา +1

    Olo uyankhule mbwelera, timamukondabe The DC.

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 2 วันที่ผ่านมา +2

    Anabwelatu pa shop yanga ndi nfuti akuti kuzatolela ndalamaya nsongo kkkk mpaka mfuti tiziwopa zomwezi?

  • @miraclekayira9613
    @miraclekayira9613 3 วันที่ผ่านมา

    Kalindo...The Great Man....winawe osangochoka bwanji

  • @Leo-fj6gz
    @Leo-fj6gz 2 วันที่ผ่านมา

    The Dc 👹👹👹👹

  • @FrancisGama-qb7ze
    @FrancisGama-qb7ze 3 วันที่ผ่านมา +2

    Boma lokuba kwambri

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 3 วันที่ผ่านมา +2

    Nanga munthu oti anachita kukatengedwa ku Church angaziwe kulamulira dziko? Ndinkona amangolembana mbutuma zokha zokha

  • @MisheckSenga-q4i
    @MisheckSenga-q4i 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mmakwana boss mn

  • @user-po6ir6eh4z
    @user-po6ir6eh4z 3 วันที่ผ่านมา +1

    Dc muchita bwino nkhani ma ID muitengere ku court ndikutheka a opposition anaphwisiridwa ndi agule mulumusan malawi. Ponda anthu angati unu ziko lathu likafera ku banga moyo

  • @MarthaJafali
    @MarthaJafali 3 วันที่ผ่านมา +1

    Vuto lovotela mulimi ndi kupanga president ndi limenelo munthu wakukakasiya ndikukukhala president manthongo Ali tho azasukusula liti

  • @ChrifordBiziel
    @ChrifordBiziel 3 วันที่ผ่านมา +1

    Akuluwa akufuna kusochelesa anthu iwowa akudana ndikusakhara pa udindotu

    • @lameckmajiga5426
      @lameckmajiga5426 3 วันที่ผ่านมา

      Akulu inu pamutu panu sipakuyenda bwino!! The D.C is only man come on public and tell the president true!! Ifetu tili kumbuyo kwa kalindo ndipo inu a MCP musanyengeke kuti mukalowa ku 2025 otherwise third-wool ija izayambika!!

  • @DanNzima
    @DanNzima 3 วันที่ผ่านมา +1

    The DC!!!!

  • @VictoriaWilly
    @VictoriaWilly 3 วันที่ผ่านมา +2

    Munthu wamkulu zedi, the DC

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278 3 วันที่ผ่านมา +1

    Good massage boss

  • @BashiluChimake
    @BashiluChimake 3 วันที่ผ่านมา +2

    Ife2 tikudikila ndodo ituluke

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 3 วันที่ผ่านมา +2

    Boma la anthu opusa ma savage

  • @GiftPhiri-tt7nn
    @GiftPhiri-tt7nn 3 วันที่ผ่านมา +1

    Pa ten wa police wamakani tikaonetsana ,apolice mumakhala ngati inuyo kut mukugula sugar 5hundred pomwe tonse tikuvutika limodzi ndiye mukachuluka nzeru pa ten muluza miyoyo ovutika akhala abale anu , and mufera zaini chuma akudya mabwana anu inu okathira tear gas pansewu ,muzuzutsa abale anu ndi ana .

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f 3 วันที่ผ่านมา

    The DC chimwana cholimba mtima kwa osauka more 🔥🔥 Mr Kalindo Tell them😅😅

  • @user-ul1fb4yn5o
    @user-ul1fb4yn5o 2 วันที่ผ่านมา

    The DC mwana woooopsa kwambiri

  • @user-ji4xn6me8d
    @user-ji4xn6me8d 2 วันที่ผ่านมา

    Indeed it's bullshit a MRA the DC ayankhula

  • @Enock-c9l
    @Enock-c9l 3 วันที่ผ่านมา +1

    A opposition afasa ngati Chilima

  • @MarthaJafali
    @MarthaJafali 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo inu a China pharaoh amenewa Sali bwino mulungu wa Israel awayendele

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 3 วันที่ผ่านมา +1

    The DC koma otsusa akudziwa chilichotse chimene aboma koma ndele ndidzimenedzo akufuna aboma adziwona ngati zawo dziyenda chifukwa chachinyengo chomwe NRP ikupanga pa kalembela wa ma ID muthalika chihana atupele mayi patelo ndi akaluwa ndianthu oti angalole DZOPUTSA ZA ID ALEMBANA CHIGAWO CHAPAKATI CHOKHA AAAA AKADZALENGEDZA KUTI ALEMBETSA VOTE NDI AMENE ALI NDI MA ID WOKHA NDIPAMENE AMALAWI OTSE KUMWELA KUPOTO DZIWONETSELO PAKA PAKA TIZAVOTE NGATI MBUYOMU ADZATSINTHE NDIPAMENE TIDZASIYE KUMANTCHA KUPANDA APO CHITSANGO KUDZAKHALA KULIBE KOMA CHAKWELA NDI MCP YAKEYO ADZACHOKA PAPANDO ASATITENGA NGATI AMALAWI DZISILU CHAKWELA NDI MCP AYAKOYO NDINU AGALU KWABASI

  • @user-ty4pq5ub3q
    @user-ty4pq5ub3q 3 วันที่ผ่านมา

    The DC. Chimwana choopsa kwambiri ..ine buzines wanga anaduka kale kale.

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 3 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 3 วันที่ผ่านมา

    The DC mwana olimba mtima

  • @rachidecaundealy8335
    @rachidecaundealy8335 2 วันที่ผ่านมา

    Assani,keti

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 วันที่ผ่านมา

    Wi love you ❤❤ bon kalindo

  • @JingaleMwafulirwa
    @JingaleMwafulirwa 3 วันที่ผ่านมา

    Proud of DC

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni 3 วันที่ผ่านมา

    D c ❤️❤️❤️❤️❤️

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 3 วันที่ผ่านมา +1

    Munthu ukuzitama wekha iwe ndiwe chitsiru chenchen

    • @ZionekaMember
      @ZionekaMember 3 วันที่ผ่านมา

      Iwetu akupasazo ukabweza

    • @dalitson3558
      @dalitson3558 3 วันที่ผ่านมา

      Chitsiru ndi wagule akulephela kuyendesa dzikoli, kwacha kumangogwa siku ndi siku

  • @YusufuKaifa-fr4wt
    @YusufuKaifa-fr4wt 3 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤ great full story poor DC

  • @oscarchafulumira3127
    @oscarchafulumira3127 3 วันที่ผ่านมา

    Dangerous child ❤

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 3 วันที่ผ่านมา +1

    The DC

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 3 วันที่ผ่านมา +1

    Audio iyi yandikhudza kwambiri.

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f 3 วันที่ผ่านมา

    Morning the DC

  • @user-wb3us4pg4b
    @user-wb3us4pg4b 3 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤ The Dc

  • @MartseMichael
    @MartseMichael 3 วันที่ผ่านมา

    Mwana owopsa kwambili

  • @user-eb2yo9bc9k
    @user-eb2yo9bc9k 3 วันที่ผ่านมา

    Akudziwana onsewatu

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 3 วันที่ผ่านมา

    Powerful!!!!

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 3 วันที่ผ่านมา

    Powerful 👊

  • @LimbikaniKadzongwe
    @LimbikaniKadzongwe 3 วันที่ผ่านมา

    Amalawi tiyeni tikhale maso osalola zimenezo zoonadi ndikuba poyera

  • @GiftKananji
    @GiftKananji 3 วันที่ผ่านมา +1

    Timakunyadiran bg

  • @macDonaldKuwani-zo3nv
    @macDonaldKuwani-zo3nv 3 วันที่ผ่านมา

    💪💪💪💪💪 Bon K

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 3 วันที่ผ่านมา

    Timam'konda Dc,,,iwanawe ušamalimbane ndi Dc

  • @lameckmajiga5426
    @lameckmajiga5426 3 วันที่ผ่านมา

    Kod ma track ndi zida zoopya zomwe zinalowa m'muziko mwanthu zija zikuzatani! Kapena boma linagula zida zankhondo za M.D.F? Tatifufuzileni mr kalindo please! Otherwise chakwela atha kutigulisapo apa!!

  • @user-zg6mn8qr4m
    @user-zg6mn8qr4m 3 วันที่ผ่านมา

    🔥🔥🔥

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 วันที่ผ่านมา

    Wenawe ngati wadya ndalama za eni tuluka usamanvele apa ife ndi bon ❤ wagwana nayo pita ukabweze ndalamazo cos apa walephela 😂😂😂😂😂😂

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 3 วันที่ผ่านมา

      Amutuma kuti azasunzumile kuno Ha😅😅😅😅😅😂😂😂😂wanya nayo wadya ndalama zaulele

  • @IssahTchakato
    @IssahTchakato 3 วันที่ผ่านมา

    Ndipo Ine andikhomela pa shop akut ndisokhele 80

  • @user-nq7yv2lm6k
    @user-nq7yv2lm6k 3 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤

  • @LazarusEvasonchafachaola
    @LazarusEvasonchafachaola 2 วันที่ผ่านมา

    D.C ukhalise umatiimilila kwambil

  • @JunaKananji
    @JunaKananji 3 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤karido

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 วันที่ผ่านมา

    Mcp boma lakuba kwambiri.

  • @kondwaniwhite2871
    @kondwaniwhite2871 3 วันที่ผ่านมา

    Auzeni chilungamu

  • @Wellingtonphiri-op8pp
    @Wellingtonphiri-op8pp 3 วันที่ผ่านมา

    ❤❤

  • @AnnoyedFallingLeaves-zp8dy
    @AnnoyedFallingLeaves-zp8dy 3 วันที่ผ่านมา +1

    Nde mwati Yosefe anali wa number chani? Nanga Benjamin? Pilizi chonde!

    • @user-xt2ic5gg1g
      @user-xt2ic5gg1g 3 วันที่ผ่านมา

      Joseph wa 11 Benjamin 12 walakwitsa pati munthu

  • @user-ec3xh4pc6t
    @user-ec3xh4pc6t 3 วันที่ผ่านมา

    Anganga

  • @MasterHeadson-ki7ji
    @MasterHeadson-ki7ji 3 วันที่ผ่านมา

    📌

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 3 วันที่ผ่านมา

    A DPP ADYA BANZI NDIIIIITHu!!?

  • @MussahSmart-wn5ue
    @MussahSmart-wn5ue 3 วันที่ผ่านมา

    The DC umakwans

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s 3 วันที่ผ่านมา

    Tingopita ku cort basi

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 3 วันที่ผ่านมา

    Dc

  • @AdamYas-ec9oc
    @AdamYas-ec9oc 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mumakwana kunena dzoona the dc

  • @user-uj9st8zp7v
    @user-uj9st8zp7v 2 วันที่ผ่านมา +2

    Ndili pambuyo pako bon kalindo the D.C

  • @homeremedys3748
    @homeremedys3748 3 วันที่ผ่านมา

    Rest in peace Redson Munlo 😢😢😢😢😢.
    We love you the DC

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 3 วันที่ผ่านมา

    Boni kalindo watha basi

    • @TopoTopo-bm4vw
      @TopoTopo-bm4vw 3 วันที่ผ่านมา

      Iwe usamalimakimbane ndi DC ukutaya thawi

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 3 วันที่ผ่านมา

    I stopped listening to this nonsense frm coz I don't see any profit

    • @MarthaJafali
      @MarthaJafali 3 วันที่ผ่านมา

      Who told you to listen get out

    • @EllenPhiri-xt8pt
      @EllenPhiri-xt8pt 3 วันที่ผ่านมา

      Iwe ndiwe chitsulu osangatuka bwanji ndani akukukamiza kuti uzimvela zomwe akunena bon kalindo musiyeni akutokota za nzelu zothandiza ife iwe unalandila ndalama kuti uzifowola anthu choka galu

  • @IsmailRahim-yy3yr
    @IsmailRahim-yy3yr 3 วันที่ผ่านมา

    The DC

  • @GiftKananji
    @GiftKananji 3 วันที่ผ่านมา

    Timakunyadiran bg