Character ya Selina in the play ndi yoopsa and such women amawameneyera nkhondo ndi Mulungu. Amakhala pheeee sikuti amakhala kuti apusa koma kumakhala ija Amati khala chete nkondo ndimenya ndine. The repercussions which follows are always dangerous. Azibambo let's not take advantage of such innocent women one day is one day God will fights for them.
❤❤❤❤nice gyz zikubeba izi kip it up glory be to God ambuye azikhala nanu nthawi zonse pomwe mukupanga ma pg anu,malawi on fire
It's a song for me ❤️❤️❤️❤️❤️
Bhima ndi moooo 🔥🔥🔥
Keep fire burning guy's watching from Capetown ❤
Character ya Selina in the play ndi yoopsa and such women amawameneyera nkhondo ndi Mulungu. Amakhala pheeee sikuti amakhala kuti apusa koma kumakhala ija Amati khala chete nkondo ndimenya ndine. The repercussions which follows are always dangerous. Azibambo let's not take advantage of such innocent women one day is one day God will fights for them.
Ndipo nde ndi zoona wamva amakumenyela nkhondo ndi Yahwe iwe uli chete
Eshiiiiiii kkkkkkk Akazi pá ndalama huuuuuu Anakonza
nice guys koma chepesani kugwilisa ntchito mawu ena osakhara bwinowo
Zoonadi ofunika mau Ena azisefedwa ndithu
Celina umatha and umandivesa kukoma,Hanna peza wako mamuna usatengeke ndi kadora ndika Celina kkkkk
This is nice guys however try make sure khuti ti ma elements ta drama tisamaonekhere
Otherwise the characters wow
I loved it
Bertha ndidolo km😊
bima stop lookin at the vamera wen actin bro
I thought that is told to them before acting?? How come he still does it
Izi nde ndazikonda sure guys inuo nd 1
Koma Bhima ndiwa bodza iiiih, ndeamanyengerera iiiih 🤣🤣🤣
Azimai akaona MONEY, 😂😂😂
BP yonse pa LOW…
Koma DUmbula mmmmm hiaaa mpaka pa nsana pake kkkkkkkkkk thumbs up
Ilipo bho heavy
the girl has a beautiful voice
Celinna athaa kukudyetsa poison, 😂😂😂
Silent killer
Iziz ndiy ndizoon amapangil uhul ndalama zaakaz awo
So nice guys u always make me happy
😂😂Km ngat kuli azibambo onyenga ngat uyu asaaa 🎉😅😅
😂😂😂😂😂 Inu munalikut thawi yoseyi wawooooo 😅
Km bima mmm kmso selina ndiwe udenkha
Koma Bima umatha komatu bwino angakumenye akaziwa ukawapusitsa kwambiri
How much
Koma Sellina ndiwe odekha bp ulibe
Koma ndi boma lit kuli ma bullet ku
At mpasana Pako kkkkk
Hannah uhule 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣ndalama zakunyenga
Sellina ndidolo
Cellina ndiwe number 1
Bima you are coming nice bro. Zapamwamba
We love you Hana dear
bhima ndimakina 😂😂😂😂
ndalama zakazi anu muli ndindalama 😂😂😂😂😂😂😂😊
Ati pansana pako😂😂😂
Pa nsana Pako....😂😂😂😂😂😂
I like ma guys ama reality plz😂😂😂 ati zakazianu
Zili bwino koma chepetsani mawu otukwanawo chonde!
true
This is nice
😂😂😂😂ukagona wekha 😅😅
Za ma blesser zokhazo atsikana simungathane nawo, Chilembwe wabvuta😂😂😂
Kkkk koma athu mumalimba tima iii 😅
Bhima ndi kuchikweza 😹😹😹🏃
Woooow❤
Ati ine ndili pa number chani
Uli pa nambr 0 kkkk ameneyo nd bima
uyu Nde original tambwali
Money is the ruti of all ivo 😂😂😂 mhu
123
NDALAMA NDALAMA NDALAMA
Iiiiiiiiiiiiii
🔥🔥🔥🔥🔥💥💥💥🔥🔥
Kkkkkk❤️❤️
Ofuna kudya nawo makobili😂😂😂
Ndalama zakazanu 😂😂😂😂 Tadala
Bima machine😂😂😂😂😂
Selina ulibhoo ukadekha la40 limakwana thenks guys
Iweonso pansana pako
Celinah umalimba mtima iiiih
Kkkkkkk Selina Amatha
Akazi odekha ngat Selina alipo angat dzikoli
Tilipo ndithu
Koma kuno kuno esh😂😂😂
Eshii game yokora kale yavutaso 😅😅 bhima
Akuti pamsana pako koma Selina adah
🤣🤣🤣 MG1 uyu ndi shasha😂😂
Pasanapako🙄😂😂🙌
At pano ndabwera pa number chanino kkkkk
Relationship between money and women ,, mmmmm
Selina umatha kudekhatu 😂😂
Pasanapakedi 😂😂
😹😹😹
fire💥
Koma mwabwela guys
sellina wadza🤣🤣🤣🤣🤣
Mulibho maguys
😂😂😂😂😂 mada umatha ati ndalama zakazanu
Selina eshiiiiiiiii
MG1 yu ndi odekha.
😂😂😂😂 kma adha iphone bas watheka
Kmatu ndalama 😂😂
Mbambande
I phone 14😊
Bhima umaitha🤝👍
Hana
Pasanapako mula😂😂😂
pliz Guyz musasiye kutisangalasa
Zovuta bhima anakoza
Big up guys keep on inspiring us izi za blesser zafikapo and zikuwononga achinyamata ochuluka zedi.
Ukunenad zoona sizilibwinod
Bhima wanyanya😂✋
Guys mumatha km mibawa ndi 1
bodza lokha lokha
Iiiii komaso bhima😂😂😂😂😂 ayi ndithu
Bhima machine 😂😂
Umakwana bhima 🔥🔥🔥🔥
Zosangarasa
Bima umakwana
Tadala
Umatha selina
bhima Koma 😅😅
Celinna umayitha kkk
b man mumathe
Bhima😂😂😂
Kuno kuno kuno kuno kuno kuno kkkkkkkk Bima
Ndalama zimenezo bhima ndiza iPhone 8tu😂😂😂 Nanga ikukwana ya 11 imeneyo