ndikumvano kuwawa ndi nyengo ya Berthia 🥺😭😭😭🥺🥺😭😭, yomwe ikumamuonetsa ngati ndiye Hule komano asali nchoncho.👀👀👀🥺🥺🥺🥺🥺 am not happ true speaking. Berthia may almighty God bless you and remember you in all necessary ways good for your life through in Jesus name. Amen
Kodi pa mibawa tv mumaonetsa lit and nthawi zanji ,,,,,guyz mmatha Sellina mmokonda❤
Maranatha ndiwe obhowa
Maranatha uli nd macheza opoira sure mchifukwa Bhima amadana nawe now I understand him😮
ndikumvano kuwawa ndi nyengo ya Berthia 🥺😭😭😭🥺🥺😭😭, yomwe ikumamuonetsa ngati ndiye Hule komano asali nchoncho.👀👀👀🥺🥺🥺🥺🥺 am not happ true speaking. Berthia may almighty God bless you and remember you in all necessary ways good for your life through in Jesus name. Amen
Nthwi ndye ikuchepatu.....tamaonjezakoni guys
Benard mpaka ku studio😂😂😂😂
Maranatha ali ndi mdede kuposa wa selima pa tokotani amayi wakumaan nazo selina
Kumapetoko ndiye inayamba kukoma ...koma koyambilira kuja anthu amakhalitsa pa scene kwambiri
Komansotu Maranatha🙌🙌
Scene yikumakhalitsa,,, zafika pobhowa
Ati ndimakhala kwa Landlord
Ayiboooo Bethia ali mmavuto sure😂😂😂😂😂😂
Amene anavula malayao ndi mzakeyo sanali serious aaaa
Big mn adye selinah sopano 😂😂😂
4 tone kukasamusa bed lokha? kkkkkkk koma munthu uja mwamubeladi
Ndiye mwangoponya komweko ka Ben 20 kkkkkkkkkkkk
Cross mwanvunga ya Ben 20 😂😂
Yafupikatu kwambiri bhima alikut sakuoneka kapena ali busy ndikulandidwa ATM card
Siben ten akut ndiben 20 Koma Selina polamoto😂😂😂😂
maranatha kuzavunga cross😂😂🙌🔥
Mayoooo yatha ikupita kokoma
Selinah wapita bus kkkkkkkk
Piliz chonde muzipangako tatitali please please I berg of you
Berthia wakumana ndi level yake Benard amamudelera😂😂😂 love it
Ben 20 yemweyo😜
Nthaw yumachepa please😩😩
Komabe kuchoka sachoka chomchobe. Bethia azivere basi😆
Kkkkkkk koma sellina eti kwa landlord
Koma a org ndimoto
Why Chakwera Ndi chilima Akufuna kupha Peter Muntharika ndi Born Kalindo yeti Nawonso Anatenga dziko through Demonstrations?
Pelekani basi number yo a Selina musamphweketse mupeze ben 10 Bhima apsye mtima
Ma places anu 2 minutes inayake
Tchimo lamuzuza Tadzi
Kkkkk Ben 20 😅😅😅😅
Maranatha wabwera 😂😅
🔥 🔥
It's too short 😔
Koma ndiwonere kae kuti tiwone zitha bwanji
Kuchoka sachoka choncho Mamie ndidikireko 😢
Ben 20😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
🤣🤣 ben20
Kkkkkk ben 20
ben 20 😂😂
Ben 20 🤣🤣🤣🤣
Cham 2am
😂😂😂😂 Mesa unachita kumuthamangisa
Not interesting ..you can do better guys
Chi mbombo😂 kuyankhulira chilichonse
Zalowa umbombo
Nthaw yumachepa please😩😩