Boma ngati liri ndi nzeru lisandutse msikawu shopping mall, awamangire anthuwa ma shop olongosoka ndi owoneka bwino, shopping mall ayipezere malo ena. Zimamvetsa chisoni ma vendor akupsa ndi dzuwa mmisewu koma amwenye ali ndi ufulu ndipo salola munthu kupanga malonda pakhonde la shop koma mukapita ku new york mukapenda ma vendor mma khonde a ma shop. Amalawi ndife ogona ndithu. Even ku Johannesburg boma linayika ma bench a ma vendor ndikuwapatsa malamulo.
Ine ndiri ndi maganizo Osiyana. A malawi tisiyanitse ufulu ndi chitukuko Cha dziko. Naperi it's part of urban, msika wa pa kamba sugwilizana ndi Area imene ija. Shopping mall ndi filling station ndi chitukuko chapamwamba. Pa kamba pamapindulira zidakwa, ma Hule ndi akuba. Kodi ma restaurant ake ati? Azimasakawo? Please a malawi tikamati Mizinda yathu itukuke ingatukuke bwanji?
@@adamusaidih8570 anzeru ndinu komano ndingokupemphani muziyenda. Mu township simumakhala ma restaurant azisaka. Opanda mzeru ndi iwe ukufuna kumayala makala mu mkati mwa mzinda. Kumasuntha ndi dziko amwene.
@@zayedmitawa8345 point ikhale yoti palibe njira yonveka bwino pa za relocation kapena compensation. Koma Malo Aja patha kuchitika Cha mzeru kuposa mmene palili panomo
Pa kamba patafika shopping mall, ma modern restaurants ndi filling station. Patha kupezeka mwai wa mbiri wa ntchito kwa a Malawi ambiri kuposa omwe akupeza phindu pano. Maganizo anga
The most important thing in life is human welfare. Mukati achoke ma vendor Mali atagulutsidwa it means sangabwererenso pamenepo coz pagulitsidwa. Amalawi tiyeni tidzikondana tokhatokha,Moyo pano walimba, ntchito kulembedwa sizikutheka pomwe katundu akukwera mtengo daily salary yomweija. Munthu uli ndi family penanso kumasamala makolo,achibale plus amasiye,ndiyeno akuthamangise pa malo a business zitha bwanji? Chitukuko cha filling station sichingasamale banja lako komanso zosowa zamunthu. Ngati kuli kotero,amange kaye msika wabwino woti mavenda apa Kamba asamukiremo pomwe akuyamba kumanga zama filling station zawozi. Boma lonyasa ngati ili sindinalionepo chibwadwireni. 2025 ilimukhonde,muzawafuna mukuwanzunzawa.God is watching you!!
To be honest ,nsika uwuwu sumapanga ndalama ndipo kuikapo shopping mall and filling station zithandiza kwambiri,this area anthu omwe amabwera apa ndiozadya ndikumwa mowa
Kodi shopping mall ndi filling station zimathandiza ndani? Msikau ulipo mpaka pano chifukwa umathandiza anthu ozungulira. Council ya Blantyre yagulitsa malowa pa zifukwa zina. Chitukuko siukambila kuseri
Khani iyi ndiyosekesa kalata yopanda siginecha so why?ndichifkwa chani sanasayinile umeneo ndiye utambwali,Blantyre city ilipo chifukwa Cha wanthu ,popanda wanthu city kulibe,Inu acity musamalakhule kt Malo ndi anu ,munawatenga kt?
This action is encouraging kuti anthu azilowa ndi Malonda nkati mwa town apezeka kuti akukagulisa Malonda pa nandos kandodo etc kenako a city azitengaso galimoto kumakalanda Malonda omweyo kumakadya makwawo are you trying to kill poor malawians
Koma Council posakhala transparent pa nkhani ngati iyi nchiani? Ngatidi akufuna kumanga shopping mall mwai umapelekedwa Kwa nzika kukhala ndi mashop awo mkatimo ndipo iyi ndi nkhani yabwino. Koma ngati kuli kupha Kwa nsikawu at least apange relocate ma vendors apititse kwina kudzera mkufotokozerana. Apa a council plus Boma akubisala mawa adzayambe kugwiritsa ntchito a police kuthamangitsa anthu ndi teargas. Mchifukwa ninji boma la Malawi silikhala ndi chidwi ndi nzika zake.Mzika zimaesetsa kuzipezera zokha zochita zomwe Boma limapindula nazo misonkho koma boma lomwero likafuna chinthu pa anthuwa limagwiritsa ntchito mphanvu osati kukambilana. This nonsense must stop. Wakawaka in Lilongwe, you're next!!!!
Khani yomanga mnsika pliz ndiyofunuka,ma new models akufunika kt mzinda .ndi ma toun zizioneka bwino.kma pakufunika ndondomeko kt anthu ali mmenemu apasidwe Malo ena ,kupanda kutero simunthana nawo chifkwa ndi m'badwa ndi mzika zamalo ao.nthaka ya amalawi ndiya wo kma ulemu ndi ndondomeko zikhalepo.
Funso mkumati kuyambila litiro kuona malowo ndi akulu ? This government its too much corruption ndeno akagulitsa malowo what is your benefit you will get ?
Koma if its redevelopment and malowo si amunthu, i dont see any problem, we need standard things, enawo akhoza kukayala panyumba pawo, or apeze pena akayambise okha
Abale a Malawi anzanga ngati timafuna dziko lathu kutukuka ngati Maiko ena, tidzakwanitsa bwanji kutero ngati pano tikukana shopping mall mu urban? Kaya akumanga ndi a Mwenye kaya ndani koma tidziwe kuti zikumangidwa mu dziko lathu, ndipo olembedwa ntchito pamenepo ndi abale athunso
Boma ngati liri ndi nzeru lisandutse msikawu shopping mall, awamangire anthuwa ma shop olongosoka ndi owoneka bwino, shopping mall ayipezere malo ena.
Zimamvetsa chisoni ma vendor akupsa ndi dzuwa mmisewu koma amwenye ali ndi ufulu ndipo salola munthu kupanga malonda pakhonde la shop koma mukapita ku new york mukapenda ma vendor mma khonde a ma shop. Amalawi ndife ogona ndithu. Even ku Johannesburg boma linayika ma bench a ma vendor ndikuwapatsa malamulo.
Abale athuwa sakudana ndi chitukuko, koma dandaulo limveke. Nthawi ili yachabe. Apatseni 5 years notice kudzanso alternatives.
@@lastonmasoatenganji-bs5gf 😅😅😅malo ndi a khonsolo not awo..chikuvutani kumvetsetsa ndi chan kod?? . Umunthu ukatichulukila sittitukukapo apa
Ine ndiri ndi maganizo Osiyana. A malawi tisiyanitse ufulu ndi chitukuko Cha dziko. Naperi it's part of urban, msika wa pa kamba sugwilizana ndi Area imene ija. Shopping mall ndi filling station ndi chitukuko chapamwamba. Pa kamba pamapindulira zidakwa, ma Hule ndi akuba. Kodi ma restaurant ake ati? Azimasakawo? Please a malawi tikamati Mizinda yathu itukuke ingatukuke bwanji?
Amwene mwangokula mulibe nzeru
Chitukuko sitibisa,momveka bwino anthuwa akuti nthawi yosamuka ikuchepa komanso kosamukira sanauzidwe.
Zomanga shopping zilibe umboni ndimphekesera chabe.
Udzifunse Mchifukwa chiani BCC siikulankhura zomveka pa izi?
@@adamusaidih8570 anzeru ndinu komano ndingokupemphani muziyenda. Mu township simumakhala ma restaurant azisaka. Opanda mzeru ndi iwe ukufuna kumayala makala mu mkati mwa mzinda. Kumasuntha ndi dziko amwene.
@@zayedmitawa8345 point ikhale yoti palibe njira yonveka bwino pa za relocation kapena compensation. Koma Malo Aja patha kuchitika Cha mzeru kuposa mmene palili panomo
Pa kamba patafika shopping mall, ma modern restaurants ndi filling station. Patha kupezeka mwai wa mbiri wa ntchito kwa a Malawi ambiri kuposa omwe akupeza phindu pano. Maganizo anga
Inu ntchito amalembana okhaohka mutsavutike kuti anthu akhodza kugwira ntchito
@Slivia Awiri atatu amapezeka abale athu
Maganizo a shopping mall ndi abwino koma pali vuto mpoti BCC siikutsindika zomanga shopping mall komanso siikufuna kukambilana ndiochita malonda munsikao.
Msika is under district council not government. School ijaso pena imathandiza kudziwa omudandaulila.
🎉Kudesa town ndizimasaka zanuzo, iyaaaa. BCC gulisan malowo
The most important thing in life is human welfare. Mukati achoke ma vendor Mali atagulutsidwa it means sangabwererenso pamenepo coz pagulitsidwa. Amalawi tiyeni tidzikondana tokhatokha,Moyo pano walimba, ntchito kulembedwa sizikutheka pomwe katundu akukwera mtengo daily salary yomweija. Munthu uli ndi family penanso kumasamala makolo,achibale plus amasiye,ndiyeno akuthamangise pa malo a business zitha bwanji? Chitukuko cha filling station sichingasamale banja lako komanso zosowa zamunthu. Ngati kuli kotero,amange kaye msika wabwino woti mavenda apa Kamba asamukiremo pomwe akuyamba kumanga zama filling station zawozi. Boma lonyasa ngati ili sindinalionepo chibwadwireni. 2025 ilimukhonde,muzawafuna mukuwanzunzawa.God is watching you!!
Thats wat we call development...pena timakakamila zopanda tsogolo
Development sabisa.Kuwafotokozera anthu momveka bwino zimachepetsa mikwiyo.
Zikuoneka kuti malowa agulitsidwa pa zifukwa Zina osati kumanga shopping mall.
@zayed munakamva zomwe ceo wa bt anayankhila b4 kutiyankha
Inu fatsani ngati kuli kukuchotsani akupangirani ndondomeko yabwino . Musachuluke nzeru . Dziko lizioneka bwino
Ndipo asachoke nsika umene uja umathandiza Maka ukakhala ku chipatala kuja
Ayi tikufuna chitukuko amangebas akupasani pena
To be honest ,nsika uwuwu sumapanga ndalama ndipo kuikapo shopping mall and filling station zithandiza kwambiri,this area anthu omwe amabwera apa ndiozadya ndikumwa mowa
Kodi shopping mall ndi filling station zimathandiza ndani?
Msikau ulipo mpaka pano chifukwa umathandiza anthu ozungulira.
Council ya Blantyre yagulitsa malowa pa zifukwa zina.
Chitukuko siukambila kuseri
Abale athu kozekan bs boma ili siligonjatu paja azabwera usiku kuzachosa zimenezo
Ma senior a Blantyre city council ndi makape akatero apeza mwenye kuti amugulitse
Accept development
Osachoka akamange kwawo kwa zimayi awo zachibwana
MCP kubesa mavoti....
Amwenye ali ndi malo opangira malonda mwa ufulu, ayini ake adziko akupsa ndi dzuwa mmbali mwa misewu, amalawi ndife ogona.
Khani iyi ndiyosekesa kalata yopanda siginecha so why?ndichifkwa chani sanasayinile umeneo ndiye utambwali,Blantyre city ilipo chifukwa Cha wanthu ,popanda wanthu city kulibe,Inu acity musamalakhule kt Malo ndi anu ,munawatenga kt?
Musalore akufuna musowe zochita anthu oipa awa, kongeresi iyo ikufuna anthu aku Blantyre avutike
Mmmmm komano anthu akuchipatala azizagula kut zinthu zawo
This action is encouraging kuti anthu azilowa ndi Malonda nkati mwa town apezeka kuti akukagulisa Malonda pa nandos kandodo etc kenako a city azitengaso galimoto kumakalanda Malonda omweyo kumakadya makwawo are you trying to kill poor malawians
Koma Council posakhala transparent pa nkhani ngati iyi nchiani?
Ngatidi akufuna kumanga shopping mall mwai umapelekedwa Kwa nzika kukhala ndi mashop awo mkatimo ndipo iyi ndi nkhani yabwino.
Koma ngati kuli kupha Kwa nsikawu at least apange relocate ma vendors apititse kwina kudzera mkufotokozerana.
Apa a council plus Boma akubisala mawa adzayambe kugwiritsa ntchito a police kuthamangitsa anthu ndi teargas.
Mchifukwa ninji boma la Malawi silikhala ndi chidwi ndi nzika zake.Mzika zimaesetsa kuzipezera zokha zochita zomwe Boma limapindula nazo misonkho koma boma lomwero likafuna chinthu pa anthuwa limagwiritsa ntchito mphanvu osati kukambilana.
This nonsense must stop.
Wakawaka in Lilongwe, you're next!!!!
Osachoka ndipo osaopa
Khani yomanga mnsika pliz ndiyofunuka,ma new models akufunika kt mzinda .ndi ma toun zizioneka bwino.kma pakufunika ndondomeko kt anthu ali mmenemu apasidwe Malo ena ,kupanda kutero simunthana nawo chifkwa ndi m'badwa ndi mzika zamalo ao.nthaka ya amalawi ndiya wo kma ulemu ndi ndondomeko zikhalepo.
Osatopa osawopa osafoeoka
The govt should be non profit business allow its citizens to conduct business
Inde chokani pabwere town pachuluka afiti kwa kamba kkkk achokepo basi
Chilungamo ndichofunika kuwaudza anthu mcp why your doing this to Malawians
Osamangakaye wenela bus deport bwanji instead kumalimbana ndi misika yamuma location
Ati wagula ndi faizo matama basi ndi ndalama
Shopping Mall basi .pitani ku mukakhala kwa Manje inu basi
Chipani cha mcp sichisamalila osauka as a lankhule mozembazemba apa tilongosola zonse 2025 kovota muziwona
Chokanu panenepo malondi abima akupatsan chipepeso
Koma tiyeni tlikinde dziko akamanga shopping Mall paonekabwino tauni idzisintha matemba tidzikagulabe kuseli kwa shopping Mall,, pano pa queens hospital padadzadza ma hawker palibenso amapita kwa kamba kukagula zinthu
Sakufuna kumanga shopping mall nchake anthuwa akuti sachoka.
Malowa Council yagulitsa pazifukwa zina.
Council iyenera ipeze malo kwina ikaike anthuwa
INU CHITUKUKO CHA CHIYANI BOMA ILIRI NDI LAKUBA LIKUKONDA KILANDA MALO NDIYE NGATI SINUSAMALA IZIZI ZIKUVUTANI ANTHU AKWAKAMBA MYSAVONEREZE AYI A CITY NAWONSO MUWAKUNTHE ZIMENEZO MUWAUZE AZIKAPANGA KU LILONGWE KWAOKO OSATI BLANTYRE ASATIONE KUPUSA OSACHIMA AKAFUNA NDEU IBADWE ZAUTSIRU INU AMENE MUKUIKIRA KUMBUYO KUTI MUKUFUNA CHITUKUKO BOMA LIKUKANIKA KUKUGULIRANI FETLIZER MAFUTA KUDOWA NDIYE MUKUONA NGATI ANGAMANGE NSIKA WA KAMBA? BOMA ILI NDI LAMANYI KUTEROKO ALIPO AMENE AKUFUNA KUGULA MALOWO WAMBOMA MUNDIKHULUPIRIRA
Funso mkumati kuyambila litiro kuona malowo ndi akulu ? This government its too much corruption ndeno akagulitsa malowo what is your benefit you will get ?
Koma if its redevelopment and malowo si amunthu, i dont see any problem, we need standard things, enawo akhoza kukayala panyumba pawo, or apeze pena akayambise okha
Komatu
Abale a Malawi anzanga ngati timafuna dziko lathu kutukuka ngati Maiko ena, tidzakwanitsa bwanji kutero ngati pano tikukana shopping mall mu urban? Kaya akumanga ndi a Mwenye kaya ndani koma tidziwe kuti zikumangidwa mu dziko lathu, ndipo olembedwa ntchito pamenepo ndi abale athunso
Kuchoka ndizotheka kma situation ku Malawi sikuli bho powachotsa pamafunika ndondomeko yoyenela at least kuwapititsa malo ena
@@ChikaNation-g8j ndizoona
Ma comment onse iweyo wabaya osat nzeru zozaza soda mutu@@ChikaNation-g8j
Ndipo.musachokedi.khaza.bas
Chilungamo ndichofunika kuwaudza anthu mcp why your doing this to Malawians