Koma nde Wonder Msiska wabwera mozizilatu bwanji? Is everything ok with you my brother? Ndiyetu mukatero nonse mumafooka aaa anyway love the program and you guys ❤❤🔥🔥🇲🇼🇲🇼
100% program ❤, kunena chilungamo akulu akulu, MCP ndi Chakwera wawoyo watikanika, bola APM ndi DPP., eish! Moti George kasakula pa MBC aziti boma ndi lomweli😅
Zalakwika Koma Vuto ndi boma zikumavuta kwambili akachita otsutsa pamene olamula khani Yao siyipita patali a police ofunika alingalire bwino kut Azi balance bwino 2 Malawi ikuenela kukhoza malamulo Kuti ngati president akulephela kuchita zomwe analonjeza pasamakhale kudikila ma vote ay Kaya walamu two years azichotse ndikupeza ogwilizila
Komano a police man apapa mpaka akanjate? Kkkkkk angowalangiza Basi. Pena so Anthu tuonjeza eeee eee. Izizi sizoona di. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkk. Pamkuku iyi nde kuikwezatu volume nawe eeee kkk
"Chakwera trust thieves" this got me into laughter how he delivered the statement
❤❤❤🎉
These people MUST be arrested. However, the first to be arrested must be the panga carriers in Lilongwe.
In Zambia that's why we love hh
Mindset charge Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Koma nde Wonder Msiska wabwera mozizilatu bwanji? Is everything ok with you my brother? Ndiyetu mukatero nonse mumafooka aaa anyway love the program and you guys ❤❤🔥🔥🇲🇼🇲🇼
100% program ❤, kunena chilungamo akulu akulu, MCP ndi Chakwera wawoyo watikanika, bola APM ndi DPP., eish! Moti George kasakula pa MBC aziti boma ndi lomweli😅
This is my 5th year now I don't listen MBC 1 coz of its stupidity.
Kodi zimayamba bwanji 😢😢
Kuonetsa kuti MCP anthu atopa nayo 😮😮😮😮..
Times ndimbava basi 😮😮😮😮
Mabwana mumatha kuyankhula bwino kwambili mu hot current
Ku Lilongwe ndi chigawo chapakati , congress imapanga chipongwe anthu adzipani dzina popanda odzudzula , ku ndirandeko kwapambana bwanji ?
Mcp aonjeza
Ufa paka 50kg 100
Frower 50kg 110
Kuona tomato wa K100yo, masamba a K400 oh Lord😭
Anyamata.ochena.mumakwana❤❤❤
Vuto olo a pule atadziwa kuti anthu akuba sachitapo kanthu,he will give it a deaf ear
Malawi 🇲🇼 wanu ameneyu....boma langusingitsa order basi
Siine wa DPP koma izizi anapanga anyamata awazi sizabwino olo pangonotu mmmmmh 😢😢 kuvulako mwavula azimayi anunso ndipo musadzachitenso izi chifukwa mzimayi akakutembelelani simudzakhala ndimtendere
Timanena kuti mafuta yathu niyochipa until akunja amabwela kugula kuno koma ineyo sindiwona kuti ndiyochipa koma ndalama yatu ndiyopanda mpamvu ni chifukwa amagura kuno kulingana ndi ndalama ya kuno yopanda mpamvu.
Foreigns inayamba kusowa nthawi ya MCP maboma yena sikasowa bwanji?
correction palibepo wa UTM...
Koma asayiwale kutitorera azikwanjewo plz
Zalakwika Koma Vuto ndi boma zikumavuta kwambili akachita otsutsa pamene olamula khani Yao siyipita patali a police ofunika alingalire bwino kut Azi balance bwino
2 Malawi ikuenela kukhoza malamulo Kuti ngati president akulephela kuchita zomwe analonjeza pasamakhale kudikila ma vote ay Kaya walamu two years azichotse ndikupeza ogwilizila
Ine sindisapota chipani koma ndimazifusa chimene anadanira ndi DPP!! Mugafuna kuti DPP izapanga chani muzinena kuti inawononga chani ili pa ulamuliro.
APAC mwachedwa kuzuzura ndipo a pac mulibe ntchito tavutika kale tavutika kokwana
Palidi nduna zina komanso mapredencial advisor ambiri a President mumachuluka kunamiza a president. Ndiye bodza lanulo mukuononga nalo president komanso kuyipitsa mbiri yachipani. Pempho langa ndiloti a president ntchito zammaunduna ambiri ziyenderani n̈nokha chifukwa mumanamizidwa muzambiri.
athu amamangidwa chifukwa chongooneka nawo mu video........ ndilande why??
Nawonso amawapanga a DPP kulilongwe nkhanza mwayiwara tidule malire basi
Koma azibambo awawa hahahaha anabwera
Onsewo ndimkwiyo wa zikwanje zinatuluka ku ku Lilongwe Kuja zotsatira palibe mmodz anamangidwa kkkk
Amasikini andilande akufunika kunyongedwa akutiwonongera dziko
Ngati aku Lilongwe anjaso entiin...azikwaje anja
Inde munthu Ali ndi ufulu osankha koma ndimomwe zinthuzili MCP sichipani pano chochisankha avulidwe ndithu amenewo.iweyo lwayna ndi wa MCP
Timakutsatirani ndithu
Boma ili siliva malangizo zukhalangati ava koma ayi nthithudi palibe chimene ava
Aaaa nanunso bwanji attv ayambe amanga kae azikwanje aja kae mmesa adangonama kuti awamanga? Zaziii
Inu boma LA mcp silingamve chongochoka apakicho popo popo ka2ndu kukwera ndiye kut amva
MCP yatikwana or salu yawo sitikuyifuna
Sukunama. Mlongo waga yatikwanadi
Komano a police man apapa mpaka akanjate? Kkkkkk angowalangiza Basi. Pena so Anthu tuonjeza eeee eee. Izizi sizoona di. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkk.
Pamkuku iyi nde kuikwezatu volume nawe eeee kkk
Chipani cholamula chinatha mphavu chifukwa chosava chidzudzulo asinthe kumanga ayambile azikwanje
Muauze kt ku bagamoyo kulibe mbusa.
Akhulepera kunena zoona apopo a TTV 😂😂😂😂..
Nthawi zonse mumadzudzula MCP 😅😅😅..lero ndi izo,nenani zoona kuti zinthu zayamba kuchitika 😂😂😂😂..koma apo ayithawa 😮😮😮😮
Mcp ndiyakupha
Amfiti a mcp