Anyamata wa ku Airport wayamba kuulula zomwe anauzidwa ndi Boma

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 279

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl หลายเดือนก่อน +40

    Mwayakhura bwino Koma vuto umadziwa chiwembu chonse osaulura mukuulura Pano chilima wapita 😭😭😭 sangabwelelenso

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 หลายเดือนก่อน

      Amangidwe ameneyu amadziwa zachiwembuchi ndye iyeyu ali m'gulu

    • @stephanongalaukabanda2step867
      @stephanongalaukabanda2step867 หลายเดือนก่อน +1

      Eti 😢

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto หลายเดือนก่อน

      Ndipo inu osanena anthu asananyamuke Chilimaaaaaaaaa😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

    • @MussaKukada-mt9rv
      @MussaKukada-mt9rv หลายเดือนก่อน

      Mumunvesese munthuyo akuti anali odabwa osati amaziwa akanati anene then boma likanamufinya kt abwerese umboni nde zikanamuvuta ndiyeyo​@@EllinaBitto

    • @SinyoroMoyo
      @SinyoroMoyo หลายเดือนก่อน

      Mwina anauzidwa tsiku lonyamuka akanatani nanga .koma ngati anadziwa kale nde Naya amangidwe

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk หลายเดือนก่อน +14

    Mulungu ndiwa mkulu,zonse zikuturuka praise God 🙏

  • @EnelessLundu-sn8om
    @EnelessLundu-sn8om หลายเดือนก่อน +5

    Iwe opusa kwambiri...ukuulula anthu atafa kale ndiye ukufuna titani ..ngt mizimu ikukuzunza usatinyase ife apa

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g หลายเดือนก่อน +9

    amwen inuso mboza pitan ku nkhoti gt mukunena sowona mumafuna munkhale ndi maviews bas amalawi zopanda zeru😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @Ishmael376
      @Ishmael376 หลายเดือนก่อน

      Pitani Kaye classe Mr man

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน +15

    Anauzidwa,ndege isananyamuke,mpaka kuyisiya ndegeyo mpaka kunyamuka.ambwiye,mwazi wa a chilima uli manjamo.soka,kwa iye,amene anaziwa za chiwembuchi,koma kusiya osanena kathu.moto,wa sulufule ukhale pa mitu pawo,ndi ana awo.

    • @MaxwellChiwaya-tv7kn
      @MaxwellChiwaya-tv7kn หลายเดือนก่อน +1

      Inu inu musakhale ngat boma simulidziwa munthu anakawauza ndani poti oyenera kuwauzawo ndi aboma omwewo or muli inu mungatani tiyeni tidzingoziona choona chenicheni chidziwika athu ndi maso

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน

      @@MaxwellChiwaya-tv7kn munthu yu anali pamenepo ena ndikumuudza chinali chisisi cha anthuwo koma kumeneko kunalibe wa UTM, kapena,onse ogwila ntchito pamenepo amaziwa,za ichi,nanga bwanji osanena kwa munthu,opangidwa chiwembu yo kuti bwana musakwele,umu,pamene mulungu anamunong'onedza,kudzela mwa wina.uyutu,angofana ndi Judas,opasidwa, ndalama kukaziponya,pa kachichi.chifukwa,zizamuwawa paka Kale.

    • @ChristopherKamphanje-o8l
      @ChristopherKamphanje-o8l หลายเดือนก่อน

      Ok abwana mukunena zimenezo munthu atamwalila kale bwanji mukudziwa kuti kubisa chinsisi kumakhala kuti iwenso ukuvomela zoyipazo kuti zichitike basi inunsu muzigugude pamtima mwapambaso pachimenecho

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน

      Ndiye awa asamabwele,pano kumanena,zoti wina anawaudza kuti,ndege,igwa,ndipo kumamuona Vic president akulowa,mundegemo,kumaziwa pasi pa mtima akukamwalila,koma osachita kathu ndiye akubwela,pano,kumatiudza zitithangata chiyani.akufuna,kundiudza, kuti kumeneko kulibeko wa UTM ogwila ntchito pamenepo? kapena nonse ogwila ntchito ndi MCP?chinabvuta ndi chiyani kukaudza mmozi wa UTM bwana asakwele.kodi,olo unganaona bwana chilima galimoto yawo ikubwela koteloko,ndikukaima ku sogolo,sakadaima?akadafona aziwe,kuti chikuchitika ndi chani.olo,unganalemba pa katoni.akadawelenga.

  • @EdsonNjonjo
    @EdsonNjonjo หลายเดือนก่อน +4

    Chindele iwe, ndiweso one of them sanakupase ndalama eti

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb หลายเดือนก่อน +7

    Kalikonse tikaona pamene papita mzimu yaathu ndizovuta. Kwathu kulila abiyeni

  • @user-kj6qj1md5e
    @user-kj6qj1md5e หลายเดือนก่อน +5

    Akanika kukulipila kd uwulula lelo aaaaa km amalawi tulo take

  • @BestMtawali
    @BestMtawali หลายเดือนก่อน +1

    Zachambazo ndege snafikeko kumzuzu

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e หลายเดือนก่อน +2

    Zaboza izi bwanji sunapange kuthekela kopulumusa anthuwa ngati umaziwa zimenezi ndiwauza a Zikhale akusaketu iwe

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 หลายเดือนก่อน

    Ndipo musaope ai Ambuye ali nanu ❤❤❤❤❤❤❤❤love what you u say thanks be protect dear

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah2005 หลายเดือนก่อน +4

    Hmmm mulungu akuyendere

  • @natashamathala8715
    @natashamathala8715 หลายเดือนก่อน +2

    Utadziwa za chiwembucho, sunawauze anthu bwanji chilimayo asanamwalile kuti awone njila yina yomutetezela? Nde apa adzuka mukamaulula zanu ataphedwa kale?

    • @dysonfysonchifundo2284
      @dysonfysonchifundo2284 หลายเดือนก่อน

      Koma chomwe tingadziwe chakuti pali zina zimayendela ma level, zikanatheka iye kulankhula koma remember osauka alibe mbalume or zomwe akunena zili zothandidza sidzimaphula kanthu. Words of God imfa iliyonse Mulungu amalola koma, Tsoka wakubweletsa imfayo.

  • @AufiThera
    @AufiThera หลายเดือนก่อน +1

    Kuboma ngat kuli Munthu onyasitsinsa ndi mtima womwe Nd zikhale Ngoma iyaaaa tatopa naweee

  • @nenaningola
    @nenaningola หลายเดือนก่อน +1

    Ati ndudikira investigate😂 aah

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge หลายเดือนก่อน

    🤔😳😳😳 Mmmmmmmh 🙌 ase unaziwa kut akonza chiwembu koma iwee otsanena😢 mulungu wanga ine 😢😢 nde anthu otsalakwa apitha. iwe ukutsangalala yesu 🙌🙌🙌 mulungu akulange plz 👀

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r หลายเดือนก่อน

    Mmmmm musana weruze guys muziyamba kaye mwaganiza zitha kutheka kt ndizaboza akunenazi komanso zitha kukhara zowona tiyeni tizitenge ngati ziri zowona anakhariranji chete osaurura odindo wamunthu amene anakonza chiwembuchi ndi udindo wamunthu uyu ndwosiyana nkhuthekanso kt maumboni okwanira anaribe nkhuthekanso kt amateteza ntchito komanso moyo wake tango ganizani mmene mukumuziwira chakwera nde wina arure diru ngat imeneyo akhara moyo akwawo adarira iye mwezi ukatha kt tithandizidwa pakhomo pano nde kumaganiza guys

  • @DavieBanda-u4g
    @DavieBanda-u4g หลายเดือนก่อน +5

    Iwenso ndi modzi mwa adani Dr SKC ndakuona Ambuye achitenawe

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg หลายเดือนก่อน +4

    Nde chomasiya osanena mpaka ndege inyamuke ndi chani? Osatiuzaso basi coz miyoyo ya anthu ofunika inatayika kale ungangotikwiyitsapo l

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q หลายเดือนก่อน +1

    Mwazi wa chilima sungapite pachebe mulipo gulu muulura ndipo mzimu wake ukusowetsani ntendere

  • @user-ck7eb7tb7v
    @user-ck7eb7tb7v หลายเดือนก่อน

    Aaaah munalakwitsa... Chilima is no more

  • @mussahalfraid6395
    @mussahalfraid6395 หลายเดือนก่อน +3

    Koma anthu akupekatu eeee. Mukulipidwa zingati kodi? Anthu ndiye tili busy kugwirizana nazo zoyankhula za makapewa atangokupeperetsanipo apa. Palibe choona ngakhale cha mzeru wayankhula uyu.

    • @user-pt7bk1ir7p
      @user-pt7bk1ir7p หลายเดือนก่อน

      Nde inuyo bwanji osatiuza zoonazo

    • @mussahalfraid6395
      @mussahalfraid6395 หลายเดือนก่อน

      @@user-pt7bk1ir7p aaaa kuteroku inunso ndi mmodzi okhulupilira mbwererazi? Vuto lake mu mtima mwanu mwakhazikika zoti Chilima anachita kuphedwa ndiye kamba ka zimene zili mmutu mwanuzo chilichonse chokambidwacho chikumakhala choona kwa inuyo. Mudziwe kuti kagulu kambiri kamene kakupanga mislead anthu ngati inu sikalinso Ku Malawi kuno anthu ake ali kunja akungopeka nkhani inu muzikhulupilira mabodzawo.

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni1621 หลายเดือนก่อน

    Ndizoona kuti uja analankhula ndi Zodiak anaona ndege ku Chikangawa wapezeka atafa?
    Penatu musamangotero mwinadi anthu amaopa zotsatira akaulula pajatu anthu andalewa amadalira zozimitsa aliyese ofuna kuwasokoneza. Ndiye uyuyu conscious ikumuvuta ngati zili zoona

  • @AgnessKavalo
    @AgnessKavalo หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo ndiiwe galu❤ mfiti

  • @TeciaKumpitah
    @TeciaKumpitah หลายเดือนก่อน

    Kma zomaulula munthu atamwalira kalezi ndizopusa .taluza miyoyo yambili ngoz imene ija, kuculutsa umasiye nde mukamapatsidwa ma plan a ziwembu muziyamba mwalingalira atakhala achibale anu.. kma Ambuye acite nanu nose kuyambira kulikuluko poti amadziva ngt ndiamuyaya😢

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 หลายเดือนก่อน

    Chilima Adakadziwa Adakamvela Malangizo Akalindo, Nonse Amene Mukamulimbikitsa Chilima Kukhalabe Mu Aliance inuyo a UTM Ndinu zitsilu, Munamuphetsa Muthu Osalakwa Inunso Akupheni Kumeneko.

  • @user-nv3rf7bl7r
    @user-nv3rf7bl7r หลายเดือนก่อน +1

    Amalawi nanu mwanyanya kusapota zilizose ndi izo tsopano aliyese ayamba kupeka zake uko nkhani ndima sapoti ma tv nawo asegulidwa ambiri nkhani muziwalambila ichi ndiye boza lake chapala chocho akakumangani kuti umboniwo mukapelekele poyela muziti boma ndiloyipa ayi musatero guys

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

      Kuopseza ndi kwanu inu a MCP. Izi ndizomene sitinavotere 1993.

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r หลายเดือนก่อน

      @@actuarialscience2283 ineyo sindikuwophyezani mukungozivuta chabe ndipo ndilibeso chipani mukandiuze za 93 ndinaliko ine ndimakolo anga sanaganizilekoso za ndiye mukandiuze ine sorry baba zimvelani zilise muzazindikila pasogolo mverani ma post ake amunthuyo musuyanise dzana amanena kuti ndimusilikani apa akuti amagwira ku airport

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r หลายเดือนก่อน

      @@actuarialscience2283 ineyo sindikuwopyezani baba ndiposo ine ndilibe chipani or nditakhala kuti ndili kumalawi sindivotaso koma ineyo ndili ndimvuto sindikhulupilila zinthu chisawawa ayi komaso ndikudandaulila malawi wathu mukuyenela mukhale bata osati zopekazi ayi ngati mukufuna muziwe kuti munthuyu ndiwaboza muveleso audio yina ya dzana amanena kuti ndimusilikali apa akuti amagwira ku airport ndiye kuti yekha anajambula ndege ndimvalaso za usilikali kuthamangila kuchikangangawa inuyo zikhulupililani osandiwuza za 1993 chifukwa ineyo kunalibe muzindiwuxa kuyambira pa bingu nkhakhaleso ndinali mwana sinavote koma zina ndizina ndikhoza kuziziwa mwina

  • @user-vb1iq5un5p
    @user-vb1iq5un5p หลายเดือนก่อน

    Ndie ndiwe chitsiru,,ukuti umadziwa kt ndege sibwelera..mbuzi iweyo,,bwanji sunanene ku U TM members... ndie chilungamo chanji uwuze aMalawicho?

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp หลายเดือนก่อน

    Iwe ukunenapano Moyo waahndu wwachedwa Big men

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo4493 หลายเดือนก่อน

    Bwera poyera usamanamize anthu ngati akunamuza agalu akowo ingokeanitsa kuwadtera zomwe akupatsazo. Ndimtere line lija ndiye lero vuziti nyooonyoonyoo ?wamisala galu iwe

  • @SlyviaPhiri-bd9uu
    @SlyviaPhiri-bd9uu หลายเดือนก่อน

    Koma antha mumaiwala Kuti inutso muzafwa ndipo pompheza Mau amanena Kuti zodisika ziza kululika Kuti ukulu wamulungu uziwike kumpha anthu osalakwa ndipo muli ndi nthembelero pamoyu wanu ndipo aliyese amen ana panga chiwembu chimenechi apanga kofesi padziko pano

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 หลายเดือนก่อน

    Mpaka mwandilembeza zozamveka APA chifukwa mandiwontcha ntima kukonda ndalama kotani Koti mpaka kulolela anthu awonongedwe ndiwe mbusi yamunthu nde mwapindula chani ?

  • @eunicethokomanda8911
    @eunicethokomanda8911 หลายเดือนก่อน

    Abale Pena tamaopani Mulungu pofuna kuyankhula zinthu

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf หลายเดือนก่อน

    Ndiwe opusa ukuwulura lero? Ulibe nzeru anzako ukuwawona akukafa bwanji osaiphedura nthawi yomweyo kuti chilima atsikemo? Opusa iwe nchawa

  • @antonsam40
    @antonsam40 หลายเดือนก่อน

    Ndinu wopusa Inu kwabasi bwanji simunanene ndege isananyamuke anthu akanapulumuka onse aja,muli gulu lopha anthu khalani chete basi muzidya ndarama za magazi

  • @user-pt7bk1ir7p
    @user-pt7bk1ir7p หลายเดือนก่อน +2

    No secret under the sun

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni1621 หลายเดือนก่อน

    Nkhani zovuta ngati mulidi ogwira ki airport komaso ngati muzalankhule report ya mdf ikatuluka

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani หลายเดือนก่อน

    Ulibe chikondi ayise,chiwembu umachidziwa koma osadziwitsa mmodzi wa okwerawo bwanji nawenso ndiwakupha basi

  • @user-nz1qo5tn3b
    @user-nz1qo5tn3b หลายเดือนก่อน

    sizikupindula chilichose zimene ukulankhulazo Bola ukadalankhula kale

  • @MaprinceKasiyah
    @MaprinceKasiyah หลายเดือนก่อน

    Anthu ndinu olimba mtima kuwalora anzanu kuti anyamuke mukudziwa kuti sakabwera amoyo padziko lapansi palibe chisisi

  • @JOSEPHPHIRI-ve6ls
    @JOSEPHPHIRI-ve6ls หลายเดือนก่อน

    Linali ndibodza anakhala kt amadziwa akanaulula kale kwa chilimayo ngat amamukonda

  • @josephchitsulo5882
    @josephchitsulo5882 หลายเดือนก่อน

    Bwanji sunakangon'goneze Chilima ndi anzake zazomwe unauzidwazo? Lero ndiye ukunena anthu aja ataphedwa kale, ndiye ukuti ife titani?

  • @MollenMponya
    @MollenMponya หลายเดือนก่อน

    Osanena Ndege isananyamuke bwanji, tikati ndwe modz mwa Iwo ukana

  • @user-sr5dx8fw1x
    @user-sr5dx8fw1x หลายเดือนก่อน

    Wachibwana uyu , Munthu wafa kale olo utawulura ndiye abwera, iwe ndi mbudzi ya munthu

  • @user-cw6jg6xg7h
    @user-cw6jg6xg7h หลายเดือนก่อน

    Atulutsa bwanji chilungamo atapanga iwowo😂

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 หลายเดือนก่อน

    Palibe chifukwa chodikilila kunena,, iwe waphesa nawo anthuwa,, ukhala utachedwa usazatiuzenso

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc หลายเดือนก่อน +3

    Waiting

  • @user-bu7ut2gb7o
    @user-bu7ut2gb7o หลายเดือนก่อน

    Mphaka weniweni iwe. Ndiwe chisilu wanva? Umadziwa kuti imfa imene ija imatiwawa kwambiri? Vuto ndiloti ambilinu mumangowona pa a Chilima basi koma enafe pano tilibe potsamila. Ndiwe galu kwabasi

  • @soulkanyinji982
    @soulkanyinji982 หลายเดือนก่อน

    They could have said before they could told chilima not to go the problem is hard to reach him

  • @user-lz4kc5ob1t
    @user-lz4kc5ob1t หลายเดือนก่อน

    Nde zipindula chani galu iwe uziwa zot chilima wanga anafa unakanika bwanj kunena isananyamuke

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s หลายเดือนก่อน

    Kodi athu inu munakhla bwanji?lmeneyi ikuyakhulayi ndimbuzi yotheratu

  • @AlfredMtukula
    @AlfredMtukula หลายเดือนก่อน

    Murungu popanda njira amaika njira zobisika zidaonekera nkuwara

  • @steviekhonje4606
    @steviekhonje4606 หลายเดือนก่อน

    Mumagwila ntchito yanji ku airport ko kaye😂😂😂

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke หลายเดือนก่อน

    Zikundiwawa kwambiri mukamaulula pano pomwe mumadziwa chilichonse anthu asanamwalire inunso munatengako gawo pa imfa ya anthu aja

  • @ChifundoChicco
    @ChifundoChicco หลายเดือนก่อน

    Akulu akulu anthuwa aakhuta nsima akusowa chochita you ndi waboza apite uko anatan kuulula nthawi yomweyo akuuluna pano taluza kale ifee

  • @MaryNgwira-s5z
    @MaryNgwira-s5z หลายเดือนก่อน

    Ndiye ku mafotokoza zimenezi anthu atataya miyoyo yawo sibwino a Malawi

  • @MasegoModukanele-xg2hj
    @MasegoModukanele-xg2hj หลายเดือนก่อน

    Umbuli wa athu ena ndiumenewu mosemuja pano uzikati kati mwango funa kuthila mchele kuti zikome ndiye simunazitenge bwino mwaphonya

  • @SekkoAgrobestMw
    @SekkoAgrobestMw หลายเดือนก่อน

    Wausiru Uyu angosiya asakambeso,B4 ngozi samanena bwanj?Osatilola aixe

  • @berthamigodi6529
    @berthamigodi6529 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkk ganyuwaboza kkkkk inutuinu mmmm boza bas

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 หลายเดือนก่อน

      Akuchita kumveka kuti wakumangochi kikikikiki

  • @FauzaTabu
    @FauzaTabu หลายเดือนก่อน

    Musamatukwane yinu plz munthuy mizimu yikumuvuta

  • @EnockNgozita
    @EnockNgozita หลายเดือนก่อน

    Zidalizovuta kuti alimbane ndi boma nthawi imeneyo komaso sadaliko yekha kumeneko akadangoyelekeza kuyankhula kanthu akadaphedwa kapena ndiiyeyo muziyamba mwaganiza mutsadayankhule

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 หลายเดือนก่อน

    Chilima Munamupha Uja Nzimu Wake Ukukudandaula Iwe Chichakwela, Chinchewa Chakupha Iwe Umanama Kuti Ndiwe M busa , U president Wanji Okupha Naye Nzako? Iweyo Suzafa? Sitikukufuna 2025 Chitsiru iwe

  • @RabeccaMpunga
    @RabeccaMpunga หลายเดือนก่อน

    Why mukunena lero zitaonongeka? Inu agalu kwabas nde zipindula chan miyoyo yapita kale 😭😭😭😭

  • @user-lf6qf2tw5o
    @user-lf6qf2tw5o หลายเดือนก่อน

    Mkudikila chan abale ingoyankhulan.kumutundu wa Malawi kt anthu amve km mkamakhala chete chonchi mkudikila chibanz

  • @user-hk3hg1to4e
    @user-hk3hg1to4e หลายเดือนก่อน

    Mmmmm ndye waphanaotuu bwanji sunane isananyamuke ... Unbelievable

  • @user-tn4xm2dc2n
    @user-tn4xm2dc2n หลายเดือนก่อน

    Ndikuona ngat anyamatawa amangidweso akudziwapo kanthu bwanji amabisa

    • @rapkenthindwa9240
      @rapkenthindwa9240 หลายเดือนก่อน

      Awa2 ofunika kumangidwa kuti akafotokoze bwino, nanga munthu zoona kuuzidwa zimenezo basi chetee... Mboni yoyamba akhale iyi basi

  • @AdamNapwanga-ff2wm
    @AdamNapwanga-ff2wm หลายเดือนก่อน

    Big chilungamo chibwele❤❤

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon หลายเดือนก่อน

    Aaaaaaaa ndiwenso wakupha bwanji sunaulule zisanachitike unalola kuti anthu afe then udzibwera ndi mabodzawa musatenge ngati chotchukirapotu iyaaaa ukanakhala wanzeru ukadaulula kuti anthu asakwere ndegeyo

  • @shupikayintuwaluwa-5899
    @shupikayintuwaluwa-5899 หลายเดือนก่อน

    Km2 mukungobwata ayao inu! Shiiii umagwila ku airport yake ya usku or kapena zomwez tuziziwazi . Zsyen this z serious issue, uyu ndwaboza.mboli yakonxo

  • @user-nr4mi7pt8g
    @user-nr4mi7pt8g หลายเดือนก่อน

    I didn't believe that this was a plot, koma nditaona mmene wina amajambula ndenge mobisala ndi pamene ndinayamba kukhulupirira, kuti chiwembu chinachitika

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di หลายเดือนก่อน +1

    Mukanawapangako tip Dr Patricia Kaliat akanauza a Chilima eee mh . Mulungu analolelanji

  • @user-qm1qb2jp4s
    @user-qm1qb2jp4s หลายเดือนก่อน

    Skc has gone forever inu mumadziwa ndithu God should intervine malawi wants to know the truth of what was actually happened

  • @AllanaChiphazi
    @AllanaChiphazi หลายเดือนก่อน

    Bwanji sanazitchule dzina lake mmmm

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e หลายเดือนก่อน

    Eish Chakwera kupha chilima cholinga apitilize kulamula koma adziwe ndidziko ili awafuse anzake alikuti pano Mulungu akuona zonse.palibe chinsinsi padziko pano chakweraso akuyenera kuphedwa okupha nzake nayeso aphedwe

  • @JumaKachala
    @JumaKachala หลายเดือนก่อน

    Kusanenako imawopa kufaa kapena ndeee uziwulula anthuu atapita kale mmandaa

  • @OssmanAbubaker-st7pu
    @OssmanAbubaker-st7pu หลายเดือนก่อน

    Mulungu ndi wamkulu .brother mwachitabwino kunena tiyenitidikile kut MCP ikambachani paifa ya anthu 9 amenewa

  • @felixkambewa8294
    @felixkambewa8294 หลายเดือนก่อน

    Akuchita kuwerenga 😂

  • @wezzieneba9238
    @wezzieneba9238 หลายเดือนก่อน

    What is it going to benefit now? We have lost a legend, a father of many, a husband to someone, a future leader in whom we had hope. You should have been in the forefront kupulumutsa moyo wa a VP ndi anzawo enawo. At least, kulolera kuchotsedwa job and save them. I wish you would have broken the protocol, run and kneel in front of the VP as he goes to board the plane and then talk to him so that he doesn’t board the plane. Guys this is painful, indeed.

  • @martinsailesi1731
    @martinsailesi1731 หลายเดือนก่อน

    Nkamwa mukuchita kumveka kuti chiyawo chikulemera. And malongosoledwe akao akuchita kumveka opanda confidence. School yochepa koma kukhala wodziwa kwambiri , ndinakuuzani musalekele standard 3

    • @user-hm9nc7lz6e
      @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน

      Tisayakhule zambiri tiyeni tidikire tidzave zambiri muthaw yake

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 หลายเดือนก่อน

    Ndie ukuyankhula zinthu zitachitika kale

  • @jameschiwanga
    @jameschiwanga หลายเดือนก่อน

    Inu Nanu osapusisa anthu inu munayamba liti kugwila ntchito Ku airport inu 😂😂Koma Malawi nde boza timaliziwa Koma eeeee

  • @user-zr5oc3rg2c
    @user-zr5oc3rg2c หลายเดือนก่อน

    Awawa akuyankhula zopusazi lero ankalekeranji akuyankhula nthawiyo zisanachitike lero akubwebwetuka zimenezi ndiye akabwebwetuka chilima adzuka madevil nonsenu mumadziwa chiwembu osaneneratu muona Mulungu akuotchani mukuona ngati ndiimfa yabwino imene ija

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r หลายเดือนก่อน

    Five moba yaku Malawi ili pa social media pitani ku Court mukanene umboni wanuwo because anthu opusa akumverani koma ozindikila kuti Satana akugwilitsa ntchito social media sakhulupilila zonena zanuzo ndiye ngati muli a nzeru pitani ku Court musawope, Ngati mukuwopa kutenga mabodza anuwo ku court mukuwopa chiyani mudiwuza mbuli zimenezo inetu ndine wa DPP koma si zonse kumangowombera mmanja ndi nyasi zomwe ayi ndinu omvetsa chisoni manyazi bwanji DPP wooyeeeeeee Mulungu amayika munthu pa mpando wotsogolera komaso amachotsa yekha ndi cholinga ndawonera a Dad (APM) koma savomereza kuti Mulungu analanda ndilo vuto lili ndi atsogoleri athu 😊😊😊😊awa ndi maganizo anga ndimmene ndikuwonera work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die

  • @AlufeyoBanda-cv2we
    @AlufeyoBanda-cv2we หลายเดือนก่อน

    Choka iweyo ndiye mfiti yotheratu ngat sulapa ukapsa iwe,why kunenana pano satana weniweni iwe

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 หลายเดือนก่อน

    Ululani pano asanakumangeni mukachedwa kuwulula musanga akumangani
    Phone yanga data yanga ndiye nkhumba zina zizinena musayakule tikumanga ngati zinakugulira phone misala kapena cha. Boma liyambe kaye kugula ma phone ndikupasa anthu ndipamene aziyuka malamulo opepera

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos หลายเดือนก่อน

    Iweso ndiokupha bwanji sunamuuze chilima kuti asikemo

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q หลายเดือนก่อน

    Zazi munasiyirangi kuurura poyamba paja mukuurura rero chirima wapita kare ndarama munadya kare ingokharani chete apa

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 หลายเดือนก่อน

    Nanu boma lonena chilungamo ndilimeneli?? Boma la boza ngati likuchita kukhala ngati mtsogoleri si busa koma zonvesa chisoni zedi.

  • @KandisonKonyani-iz8pc
    @KandisonKonyani-iz8pc หลายเดือนก่อน

    iweso ndi fiti ungamadilile afufuze osaulula bwanji😢😢😢 pano pano chilima kulibe

  • @KhebranConnections
    @KhebranConnections หลายเดือนก่อน

    Aaaa kkkk wokhulupilira izi ndi zoba wenweni a dpp mwapezela mwai koma simungawine chisankho

  • @SimeonPhiri-uq8uf
    @SimeonPhiri-uq8uf หลายเดือนก่อน

    Iwe ndiwegalu kwabasi

  • @user-gg9hw4oj2v
    @user-gg9hw4oj2v หลายเดือนก่อน

    Mmmm mulungu akuyendele

  • @johnmalupia1754
    @johnmalupia1754 หลายเดือนก่อน

    Ndiwe chitsilu usapusitse anthu sugwila ntchito ku Airport komaso ndiwe galu, kodi achawa bwanjinu bwanji mumachuluka mbuli? Osamangopita ku mzikiti ku ka swala bwanji a galu mi dyomba inu dzitsilu

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 หลายเดือนก่อน

    Ndiye zopoilazo osangonena bwanji ngat ukudziwa chilungamo

  • @AmujeMwamad
    @AmujeMwamad หลายเดือนก่อน

    Aaaa, inu muulura anthu atafa, bwanji simudauze kut asanyamuke? kma mmapemphera inu 🤔

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga หลายเดือนก่อน

    ndiwe waboza ojambula anamangidwatu lwe ukufuna ktchuka

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 หลายเดือนก่อน

    God bless you

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y หลายเดือนก่อน

    Anthu awa awiliwa alisiya dziko lawo ndi kuthawa ku tsiya dziko lawo likukoma chifukwa cha chibwana chomwe anapanga pokupa chilima

  • @abdulhameed7808
    @abdulhameed7808 หลายเดือนก่อน

    Aaaaaaa nde mbwereratu iweyo bwanji unali chete before ndege kunyamuka

  • @EliasKawuwa
    @EliasKawuwa หลายเดือนก่อน

    Ma propanda yake mmmm ma bodza ake please, akuoneka ndi munthu osaphuziraso nkomwe, Airport yake amangwira iyeyo, akudikira investigate ndekuti chiyani!