Asilikali akuulula momwe anamuphera Chilima

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 12 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 355

  • @EnelessLundu-sn8om
    @EnelessLundu-sn8om 2 หลายเดือนก่อน +15

    Uyu akuyenera kutengedwa ndi akubanja akalongosole bwino ...chifukwa ali nawo mu gulu lakupha

  • @VictorKachulu-y3n
    @VictorKachulu-y3n 2 หลายเดือนก่อน +15

    Asilikaliwo amene akufalitsa bodzawo ndi a bodza ngati enanu bwanji sakupita ku court kukanena umboni wawo anthu mwazolowera ku pachika mayina a anthu apa cholinga wina ayipe inu mukome mukolola zomwezo bwanji osatchulako makolo anu mukunena anthu ena muferatu momwemo mu bodzamo ndiye pali phindu lanji zikuwoneka kuti ena 8 aja si anthu koma chilima basi kudafatu anthu enieni kunja kuno alikuti kili ziiii amapita kumanda nanga inu ndi ine mudzapita kuti kwa anthu andale kapena kumanda kumaganiza 😅😅😅😅😅 awa

    • @DaeyangSonon
      @DaeyangSonon 2 หลายเดือนก่อน +5

      Apite ku khoti for what? Timapereka umboni popanda mulandu? Ku khothi siku polisi tu tizidziwa zimenezo! Pakuyenera pakhale mulandu ndiye iyeyo nkukakhala mboni

    • @VictorKachulu-y3n
      @VictorKachulu-y3n 2 หลายเดือนก่อน

      @@DaeyangSonon ndiye siyani kulankhula zopanda umboni akutumani a ndale eti mukhalila yomweyio munthu anafa basi mwatsala inu ndi ine dzimvereni chisoni nanga bwanji asakatsegula mulanduwo mukungubwebweta pasi ngozi ya ndege mumayidziwa inu paja mkuyamba ku Malawi kuno eti ndiye ngoziyi yangokumaba ndi mbuli zomwe

    • @GrecianahmedMaulana
      @GrecianahmedMaulana 2 หลายเดือนก่อน +1

      ndipo apite akamange palibe zoti akunama ndizoona zinachitikadi

  • @MervisChiputula
    @MervisChiputula 2 หลายเดือนก่อน +13

    Eshiiii mulungu amakondwera ndi munthu ovomera tchimo lake inutu mwayamba bwino ingomalizani Kuti anthu tidziwe chowonadi

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 หลายเดือนก่อน +5

    Tathokodza potiudza koma usanapite machende ako bwanji unalolera kuti chilima afe chotelo iwe pokhala nsilikari nyini yamako and u chakwera nyini yamako😢😢😢😢 RIP Chilima

  • @racheallungu3939
    @racheallungu3939 2 หลายเดือนก่อน +10

    Ndaika muzimu wa malemu Chilima manja wa Mai maria. Proud katorika / Lusaka Zambia

  • @JackLuhana
    @JackLuhana 2 หลายเดือนก่อน +2

    Inusotu ndinu abodza Inu, msilikali wake wakuti? Dzitchuleni dzina ndi unit yanu, msilikali ophunzitsidwa bwino angapange zimenezo ukukamba mlayiya iwe, umawudziwa uskali iwe?

  • @StellaKChicana
    @StellaKChicana 2 หลายเดือนก่อน +2

    Mulungu amakanda munthu onena chilungamo iwe msilikali mulungu akukhululukile pazimenezi koma tikuthokoza ponena chilungamo usasiye pitabe chitsogolo oipa aoneke pa mbalambanda 😂😂😂😂😂

  • @user-xx4mt8ox8e
    @user-xx4mt8ox8e 2 หลายเดือนก่อน +8

    Tell us where is blackbox?

  • @kumbukaningambi4943
    @kumbukaningambi4943 2 หลายเดือนก่อน +1

    Only JAH knows....everyone shall get paid according to works he has done🔥

  • @DeliseNtenje
    @DeliseNtenje 2 หลายเดือนก่อน +8

    Udye ndalamayo usaope usachite matha nyani iwe unatani kuulura zisanachitike mwana wanjoka iwe

    • @MsondaBanda
      @MsondaBanda 2 หลายเดือนก่อน +1

      Iwe tiye uko vyaboza

    • @goodmhone3308
      @goodmhone3308 2 หลายเดือนก่อน

      Fake news

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 หลายเดือนก่อน +8

    Example kenya , anthu aku kenya anasiya kupembeza boma lakuba ,
    Ife amalaw wachuluka ndi umbuli .

    • @user-cy9zp4fb2m
      @user-cy9zp4fb2m 18 วันที่ผ่านมา

      Ndpo sukunama I don't kod mdziko mwathu mchan chnachtka ife tisakuchidziwa kut tiziona zinthu zikungochtka mosakhala bwno mkumangozisiila choncho bas

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y 2 หลายเดือนก่อน +12

    Pitani ku TIMES TV on live interview ndi Brian Banda amwene

  • @carlosZiyadi
    @carlosZiyadi หลายเดือนก่อน +2

    Bwerani poyera basi osaopa chilungamo chioneke 😭😭😭😭😭😭 ineyo
    Ndiwa kk umudzi koma ndikumamva kuwawa ok Allah🤲🤲🤲 protect marawi prize

  • @WycliffNkunika
    @WycliffNkunika 2 หลายเดือนก่อน +5

    Limenelo ndi bodza lochita kupeka. Iweyo bewanji upite ku Police nkukaperekela umboni umenewo. Chimene ukuopa nchani? Wasowa chonena!

    • @paulinekayuni1621
      @paulinekayuni1621 2 หลายเดือนก่อน +1

      Olo zimakhala zoona sangamusiyesiye atanena komano ndioipa yekha atinanalandira ndalama

    • @DanMwatchipitsa
      @DanMwatchipitsa หลายเดือนก่อน

      Kkkk kma zitakhala kut ndizoona police yake ya a yolamu
      Bola kungoisunga mkhaniyo

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koma munalakwa kwambili munapha muthu ofunika kusiya zitsilu komaso ndale zophana zinatha kale kale kupusa kumeneko adzakuvoteleni ndi Amanu😢😢

  • @WitnessPhiri-zr9uf
    @WitnessPhiri-zr9uf 2 หลายเดือนก่อน +3

    Kabwezeni ndalama zo pemphelani pemphero lolapa lonsweka tima mulungu akukhululukirani mupite poyela kukabweza ndalamazo 😂😂😂😂😂

  • @humphreykalolo976
    @humphreykalolo976 2 หลายเดือนก่อน +1

    Malankhulidwe anu zikuonetsa kuti ngakhale 8 simunafike, mumagwira ngati ndani ku airport?

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula 2 หลายเดือนก่อน +1

    MUZIDZIWA MULUNGU.. ZITICHEDWERSA IZO. MUBWERETSE UMBONI MWACHANGU... TIMVE # YANUYO. YA ZOMBA. PRAISE GOD

  • @DavidNundwe-k8r
    @DavidNundwe-k8r 2 หลายเดือนก่อน +1

    Thanks for providing us you service

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 7 วันที่ผ่านมา

    Eeee akulu akulu, ai bora.... tinkangova komaso kuwelenga KUT MCP ndiyakupha koma ai ndithu

  • @JosephKavalo-yx6xb
    @JosephKavalo-yx6xb 2 หลายเดือนก่อน +7

    Uchitsilu mukananena anthu asanafe ndinu m'Modzi mwakuphawo

    • @PRECIOUSMKUTE
      @PRECIOUSMKUTE หลายเดือนก่อน

      Wapha Kenako mkumayankhula za Mkutu apapa mapazi ndithu,,infact whats his name?? Killing VP just for 10 mita mmmmm it's a shame,,ndalama yot olo mansion sungamalize 😢

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 2 หลายเดือนก่อน +3

    Akulu zopanda nzeru izi.

  • @gregben7657
    @gregben7657 2 หลายเดือนก่อน +1

    MA CADET MULI PA CHINTCHITO CHA SATANA MDYEREKEZI KWAMBIRI KOMA DPP CAN'T WIN BECAUSE OF PLANET CRASH OF VP.
    WE ARE STILL RECALL WHAT EVIL WORKS DPP HAS DONE TO INNOCENT BLOOD OF ALBINISM.
    GOVERNMENT VEHICLES WERE MISUSED TO AS POLITICAL PROPERTIES TO KILL THE OPPONENTS.
    SHAME ON YOU CADETS.

  • @user-dq8iq9bk7i
    @user-dq8iq9bk7i 2 หลายเดือนก่อน +2

    Zopanda ntchito tonse timaziwa kuti tidzafa koma sitikuziwa mmene tingazafere

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 2 หลายเดือนก่อน +5

    Zaboza ngat nkazi wako ndiwopemphera uma chitiranji zimenezo

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 6 วันที่ผ่านมา

    Amalawife ndife mbuli , tikudikila john chilembwe azatimenyelenso ufulu

  • @ThokozaniJenala
    @ThokozaniJenala 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ambuye akuyendere mwapaderadera kuti unene zoona zokhazokha.

  • @GulliverTower
    @GulliverTower 2 หลายเดือนก่อน +2

    Stop taking weed +Ambuye ntengeni Bro

  • @christophergibson72
    @christophergibson72 2 หลายเดือนก่อน +3

    Looking for 1M viewers

    • @Blessings31
      @Blessings31 2 หลายเดือนก่อน

      Eish desperation is real

  • @PriscaChapsa
    @PriscaChapsa 2 หลายเดือนก่อน +2

    Kkkk msilikalli opusa wapha nawo

  • @user-lg1mc2ze2g
    @user-lg1mc2ze2g 2 หลายเดือนก่อน +2

    Waboza kulankhula ngati wakurundi bwerani poyera kuti mumangidwe munthu oyipa iwe kumakapanga chiwembu

  • @DANIELMAGANGA-j7z
    @DANIELMAGANGA-j7z 2 หลายเดือนก่อน +1

    mukusowa zochita mmene mumvekeramu mungakhale ten million kulira ndi umphawi

  • @MackzainWhite-rj9tx
    @MackzainWhite-rj9tx 2 หลายเดือนก่อน +2

    Ndiwe chitsilu kwabas bwanji sukwatchula anzakowo nanga

  • @MbandaPrimarySchool
    @MbandaPrimarySchool 2 วันที่ผ่านมา

    Bodza ili, simsilikali uyu. Bodzatu silisowa kwa munthu wanzeru. Mvetsetsani zomwe akunena.
    1. Sakunena kuti ndege inagwa bwanji
    2. Asilikaliwo anadziwa bwanji kuti ndege igwera pano
    3. Akuti ndege itagwa inaphulisidwa. Ndege ingaphulisidwe koma osayaka?
    Mfundo zokhazi ndizokwanira kupeza kuti munthuyu ndiwabodza. Mbuli ndi zitsiru zokha ndizomwe zitakhulupirire pakuti bodza limakoma mkhutu la chitsiru.

  • @markseniorkamoto4844
    @markseniorkamoto4844 2 หลายเดือนก่อน +1

    Sakupita kukhoti ndimaumboni awowa bwanji

  • @JemimaNyirenda
    @JemimaNyirenda 2 หลายเดือนก่อน +1

    Why is the government busy ku anga a Kaluw kusiya athu ngati a wawa why

  • @BESTERMAYESO-r4v
    @BESTERMAYESO-r4v 2 หลายเดือนก่อน +1

    iweyotu ukunama ndipo palibepo chikumveka panfundo zakozo usanamize ndipo usasokoneze anthu ndi bodza lakolo

  • @WysonJalamu
    @WysonJalamu 2 หลายเดือนก่อน +3

    Boza ili, paja nvula ikagwa kuchuluka zoliralira, nanga ndege inachita kutela kapena kuphulisidwa? Mesa inagwa kusowa choyakhura eti amalawi tili ndi khwiyo pa ifa ya anthu amene aja ndiye osamatiuza boza ngati limeneri.

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 2 หลายเดือนก่อน

      Zowona ndiye ndiziti malume?

    • @user-nv3rf7bl7r
      @user-nv3rf7bl7r 2 หลายเดือนก่อน

      ​@mishecksipolo71 mukavele yomwe watumiza lero mukhulupilila kuti ndiwaboza apa anati ndimusilikali anali kuchikangawa lero akuti anajambula dege ndiyeyo ku airport amalawi tiyeni tiseguke chonde anthu azikusewelesani chochi koma ambuye amukhululukile sakuziwa chomwe akupanga

  • @ChiccoMabvuka
    @ChiccoMabvuka 2 หลายเดือนก่อน +2

    Zikundimvekela ngati zaboza mukufuna kungotipusisapo

  • @AaAa-qy9id
    @AaAa-qy9id 4 วันที่ผ่านมา

    Asilikari mukutani mukurephsra ntchito yanu nanga zinthu zikuonon geka mukungoyanganira
    Vuto mumandira ndarama basi zoteteza anthu mwayiwara anzanu asilikari akunja akanachitapo kanthu
    1993 pa Operation Bwezani panari General Manken Chigawanbwenzi izi kulibeko anali olimba mtima komanso okhurupirka kt agwira ntchito kuteteza anthu a dzimo lza Malawi osati chipani

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 2 หลายเดือนก่อน

    Simunati mutuluka mizimu ya anthu amene Aja ikudzuzani zedi ndipo muulurana wat is 10 million after all ndalama malo moyendesera dziko mukupangira uchigawenga inu agalu kwambiri.

  • @EversonGeorge
    @EversonGeorge 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chomwe mukuopa kut umbon ngat umenewu kukapereka poyera mukuopa andare coz aliyese Ali ndi mantha

  • @augustMag
    @augustMag 2 หลายเดือนก่อน

    Mulungu wanthu sazagona tulo mpaka mwazi wa anthu omwe anafa pa ndegeyi utaonesa Chilungamo Romand Catholic Les prayers so hard mpaka Mulungu atationesa choona

  • @user-et1tl1qs2j
    @user-et1tl1qs2j 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mulungu salephela tidziwa zonse pompano mu ukulu wake alibe othandizana naye

  • @ChisomoKalimba
    @ChisomoKalimba หลายเดือนก่อน

    Komano ngati ukunama iweyo kufuna kuipitsa mbiri ya anzako ,ndikukutembelera komanso kulengeza matenda oopsa ndipo udzazuzika ndi 3:23 nthenda yofa ziwalo,ndipo sipapita zaka zimenezi zikuchitikila by fire by force,,, komano ngati ukunena zoona ambuye akudalitse ndikukutetezera 3:23 3:23

  • @GenitojosebingalaJosebingala
    @GenitojosebingalaJosebingala 8 วันที่ผ่านมา

    Kampeni silikaliyu ku zomba umboni wokwanila uwu

  • @SamuelMthengo
    @SamuelMthengo 2 หลายเดือนก่อน +2

    Ngati ukufuna kukhululukilidwa,bwerani poyera.

  • @chrissyamanda5510
    @chrissyamanda5510 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kupusa kwako galu iwe mxiiiii😢

  • @PreciousKatsokwe
    @PreciousKatsokwe หลายเดือนก่อน +1

    Ng'alula iwe😭

  • @GodfreySibale-ry9ig
    @GodfreySibale-ry9ig 2 หลายเดือนก่อน +1

    10 mita kupha munthu za Bodza ngat izi 😂😂

  • @GenitojosebingalaJosebingala
    @GenitojosebingalaJosebingala 8 วันที่ผ่านมา

    Amalawi chakwela ndindani kuti azunze malawi nde silikaliwe pita ukasume live pulumutsa malawi

  • @authenticmedia24
    @authenticmedia24 8 วันที่ผ่านมา

    BOMA Linapha CHILIMA full Stop 🛑 .

  • @SlyviaPhiri-bd9uu
    @SlyviaPhiri-bd9uu 2 หลายเดือนก่อน

    Koma zovesa chisoni kwambiri kumpha anthu wosalakwa chifukwa chandalama Koma ndi zoonadi Kuti pamene pamphedwa munthu osalakwa mulungu amaulula zitsitsi. Zobisika 🙆🙆🙆🙆💔💔💔😭😭😭😭

  • @chinyanjephiri9236
    @chinyanjephiri9236 11 วันที่ผ่านมา

    Jusas Iskariot anatumidwa ndi satana kukapha Yesu Christu osachimwa ndiye iwenso ndi mmodzi wa satanic wapha SKC ndi anthu ena mundege. Ndiwe munthu wovetsa chisoni ukuyenera kulapa machimo ako

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 2 หลายเดือนก่อน

    Sunanene dzina lako bwanji kodi maliro mukuona ngati chithu choseweretsa kod atakhala bambo ako ungakambe zopusa kumanama ngati ukudziwa kathu uli jufuna kusikoneza athu iwe ngati unapha ndiwe osapita ku police kukadzipereka uzilakhula zophwisa apa malilo mukuyesa zoseweretsa kod

  • @MuhammadKazembe-ot8sc
    @MuhammadKazembe-ot8sc 2 หลายเดือนก่อน +2

    Alakhulayo panyepake

  • @JemimaNyirenda
    @JemimaNyirenda 2 หลายเดือนก่อน +1

    Nde iweso uli mugulu lokuphalo

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 หลายเดือนก่อน +1

    Tell us more about the death of chilima, wat else dd u c?

  • @TitusGoba
    @TitusGoba 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ndikuzimva mwabodza

  • @bamusilabana6423
    @bamusilabana6423 หลายเดือนก่อน

    Komanso munthu uyu Pena kumumvesa ngati akunamatu chifukwa akanadzichula dzina

  • @DanielLio-c6n
    @DanielLio-c6n 2 หลายเดือนก่อน +1

    10million mungagule moyo wa munthu mulungu akukanthen nonse asasiyeko or modzi

  • @LindaMoffat
    @LindaMoffat 2 หลายเดือนก่อน

    Nde osangozitchula dzina ngat mukunena zoona bwanj. Ndege yoti inaphulitsidwa ingawoneke chonchija? Komaso ndege yoti inatela inganyenyeka chonchija? Campaign yabwanj kod tiyiwone chaka chinoyi mwati

  • @AudetterMaganisha
    @AudetterMaganisha 29 วันที่ผ่านมา

    Inuyo ngt mukunena zoona tazitchulani dzina koma zomangoyakhulazi aaa zosakhulupililika

  • @JaneNthala
    @JaneNthala 26 วันที่ผ่านมา

    Mm mm only God knows everything,continue rest in peace SKC

  • @NonduduzoNxumalo
    @NonduduzoNxumalo หลายเดือนก่อน

    Mulungu akuddalitse chifukwa chonana chilungamo

  • @augustMag
    @augustMag 2 หลายเดือนก่อน

    Ambuye landilani mizimu ya abalewa amene mwawayitana kubwera Kwa Inu chitilani chifundo midzimu Yao pamozi ndi vice president Chilima Mulungu wamphamvuzonse landilani mizimu

  • @OusteriaDogo
    @OusteriaDogo 2 วันที่ผ่านมา

    Komat zombesa cisoni zinachitikazo ndithu kumupha munthu osarakwa bwanji

  • @SophieBanda-el8ri
    @SophieBanda-el8ri 2 หลายเดือนก่อน +1

    Wabodza uyu, palibe chilungamo pamenepi

  • @Certified-Mbudede04
    @Certified-Mbudede04 2 หลายเดือนก่อน +2

    Ngati mukufuna kutchuka muneneee

    • @PRECIOUSMKUTE
      @PRECIOUSMKUTE หลายเดือนก่อน

      True this is nosense

  • @highcallingglobalministries
    @highcallingglobalministries 2 หลายเดือนก่อน +1

    AM PASTOR CHRIS PLEASE BROTHER GIVE THEM BACK THEIR MONEY,

  • @RobertKingsleyMarevon
    @RobertKingsleyMarevon 2 หลายเดือนก่อน

    A mukanazitchula dzina ndikanakhulupila koma simunaziulule . Coz olo ine ndithanso kupanha audio yanga kunena kuti ndinali mmodzi owamakizitsa pamene kunalibe
    Mukungofuna mupitilize kumatiliza tisiyeni mitimai ibweletemo

  • @hopekandle6707
    @hopekandle6707 7 วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅😅 bas mukakhuta uko muzipanga ma audio abodza aaaa tsek mbuzi dzawana

  • @LouisAndrew-jr1yj
    @LouisAndrew-jr1yj 2 หลายเดือนก่อน +3

    We wish you well🙏

  • @Brighnut
    @Brighnut หลายเดือนก่อน

    Ndiwe mbuzi chitsiru iweyo ndichifukwa chiyani unalandila ndalama chosecho unali ndimaganizo okana ndiye kuti iweso unapha chifukwa iweyo ukanalorela ufe Koma achilima apulumuke

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo4493 2 หลายเดือนก่อน

    Galu wachabe chabe uyu iwe umakatani kuchikangawa kuchoka ku Zomba? Bwanji osanena nthawi yomwe ija anthu tikusowa Mtengo ogwira? Ukamanama chonchi ukupempha tsoka kwa mulungu

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni1621 2 หลายเดือนก่อน

    Ngati mukunena zoona kuti ndi nsilikali mukuyenera kukanena ku malo oyenera. Komaso munena bwanji kuti amalawi tisamale pomwe inu amene mumayang'anira za security of people mukupanga zimenezo? Kodi mesa olo anthu atapanga protest ndinu nomwe mutawapange chipongwe chifukwa cholandira ndalama

  • @user-nv3rf7bl7r
    @user-nv3rf7bl7r 2 หลายเดือนก่อน

    Ichi chawoneka kuti ndichaboza apa akuti ndimusilikali analikuchikangawa lero akuti amagwira ku air amajambula nthaawi yonyamuka ambuye akukhululikile ndithu

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 2 หลายเดือนก่อน +2

    Tiutseni soona sandege live in the sauth Africa estan 😢😢

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj 2 หลายเดือนก่อน

      Thank you so much for replying me your welcome

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj 2 หลายเดือนก่อน

      Tell me all story from you soon side please I am Malawian

  • @bernardnambwe7753
    @bernardnambwe7753 17 วันที่ผ่านมา

    sanamalize ataiphulisamo anatani anene zonsetu mesa anakipo

  • @preciouskhombedza4456
    @preciouskhombedza4456 2 หลายเดือนก่อน

    Bwanji wangotchula kuti ukupezekera ku zomba Barack while ku zomba kuli air wing kuli cobbe kulinso changalume and rank number Yako sunatiuze and why sunanene early because iweyo izizi ndekuti unazidziwa zisanachitike nde utha kuwauza anthu za Zina zimenene zikufuna zitadziwidwa kuti zili pati and zinaenda bwanji anatenga ndi ndani mafuso ngati amenewa utha kuyankha?

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 2 หลายเดือนก่อน

    Ngati mukunena zoona amwene ndinu opusa coz munakanika kupulumutsa miyoyo ya anthu ngati Inu nsilikali, panthawi imeneyo munkayang'ana za ndalama not moyo wamunthu.mukudziwa kuti infa za anthu amenewa zinatiwawa motani?idyani ndalamayo mpaka masiku a moyo wanu isadzathe

  • @sothinimwale3405
    @sothinimwale3405 2 หลายเดือนก่อน

    Iwe ndichitsilu opusa ngati ukunena zoona pita poyera kuti anthu aziwe, komaso bwanji osanena anthu asanafe ndiwe galu

  • @patrickscott9086
    @patrickscott9086 2 หลายเดือนก่อน

    Tabwelani poyela2 nanga mukulekelanj kuwulula?

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera munthu wakupha uyo izi zayenera kuyamba ndinu bomwe asilikali.Mukusekelera zinthu zopusa kupha anthu amtundu wanu womwe mkwiyo wa Mulungu ukukanthani ndithu,Muuzane inuyo asilikali muyambe kukantha Lazaroyo ndi akubanja ake onse

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 26 วันที่ผ่านมา

    Ndiwe chitsiru kwambiri mene umalandila ndalama kuti ukachitse dzimu wa azako umati iwe ndiokhalitsa dziko lino Ambuye akukatheni bambo ngati zomwe munena zili zoona ndipo muthadi

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 หลายเดือนก่อน

    Munalakwisa kupha ose komanso ndiwe chisilu

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h หลายเดือนก่อน

    Koditu ndizoziwika kale kuti chakwela anapha chilima

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zikomo kwambili chifukwa Cha kuzipeleka kwanu pofuna kulapa chimo lomwe munalomwamo chifukwa Cha anthu ena mulungu akuyang'anileni ndi kukutetezani kuti oyipayo asatengeko gawo pa inu
    Chomwe ndingaphembe amalawi azanga tiyeni tiyime njiii ngati azathu aku Kenya tichose mbuzi imeneyi

  • @GRACIOUSCHIDZANJA
    @GRACIOUSCHIDZANJA 2 หลายเดือนก่อน +2

    Wow

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 2 หลายเดือนก่อน +2

    Following 🙏

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 2 หลายเดือนก่อน

    Mudatani kumuthawitsa osamupha inu asilikali zovetsa chisoni😂😂😂😂

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 หลายเดือนก่อน

    NDIWE MUNTHU OPANDA CHIKONDI BWANJI SUNADZIWITSE NTHAWI YOMWEYO KUTI ANTHU APULUMUTSE MIYOYO YA ANTHU? KOMANSO IWEYO ULI NDI UMBONI OKWANIRA BWANJI OSAYITANA MABANJA OFEDWA NDIKUWAUZAKUTI TIYENI KU COURT NDIRI NDI UMBONI? MUNAPHANAWO CHIRIMA NDI ANZAKE,BAMBO MLANDU MULINAWO

  • @franklinnyirenda8126
    @franklinnyirenda8126 2 หลายเดือนก่อน

    Aaa 10 mita kandalama kochepachepa, kupha president kumafunika ma 50 mita

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh 17 วันที่ผ่านมา

    Uyu azakhala mboni 2025 likachoka boma lilipoli

  • @Noelbanda-j1l
    @Noelbanda-j1l 2 หลายเดือนก่อน +1

    Wa Dpp iwe

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 2 หลายเดือนก่อน

    Nawe camba chakukwana, tinzakhulupilira ukapita ku khoti kukasuma mlandu wakupha, udye ndalama yo, ukananena time yomwe amakokedwayo😂 ndie kut iweso akanakupha, ndie ndipamene tikananziwa kut wafa bwanji pomwe ndege munakwela athu 9, iweo kukhala WA ten, zaziiiii

  • @Owenmalunga-jo4iq
    @Owenmalunga-jo4iq 2 หลายเดือนก่อน

    Vuto Kodi president ngati sakupanga zabwino osapanga Kuti achoke bwanji pa mpando

  • @jonathandaimon7996
    @jonathandaimon7996 2 หลายเดือนก่อน

    Koma Chakwera why? Achewa ndithu ndinu oipa ndawonela Chakwera koma mulungu akukantheni tikuona ndithu

  • @CharlesMakuluni
    @CharlesMakuluni 2 หลายเดือนก่อน

    Mabodza oyambanitsawa mumapindula Chani?

  • @user-em6cm1mw4g
    @user-em6cm1mw4g หลายเดือนก่อน

    Ambuye akusamalireni ndipo akutetezeni