ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
The Dog 🐕 was awakened and started wagging it's tail when Tonde shouted DOLA 😂😂😂😂😂
Tonde wadula palibeso❤
Chisomo is a good actress
Kkkkkkkkkk gaga sazateka basi
Mwandisiya malere amfumu kkkkkkkkkk chisomo my actor no nonsense umakwana ase.Bravo team Tonde wadula ❤❤❤❤❤
Madola mulipati azimveka ayi tonde ayi mungolusila aliyense😊
Amfumuwo akumukondela gaga
I can't wait next part gaga asachenjere pakamwa choncho sikuchenjela kwabwino kumeneku 😂😂😂
Koma kodi mwati mashine okhonzera mashine ine mumawacha kuti gaga eti 😂😂😂😂😂gaga ndie mashine o
Kkkkk Gaga kuchenjela pakamwa
Koma gaga iiiiiii 😂😂😂 musiye chiso afotokoze ,ukuopa chani gaga weee
Kkkkkkkk kma gaga upole fire ,amfumu ulemu wanu inuyo mumatha
Akangomva Makwale Farao basi watha.......Ndikuwona chisomo akupangidwaso Kidnap ndi Gaga
Gagaaa gagaaa kkkkk shiii. Keep de fire burning. Ma dora eshiii fire mabomba2
Gaga chifuniro arose m'bwaro pzlz
Mmmmm chisomo umatha nosenu guy's ndimanva kukoma nanu kabasi
Watching from South Africa Pretoria mamilod Lusaka keep it up gyz ❤❤
Zili chabe bwino ,,, Nazombe moto unandi
Muwawuze amfumuwo kuti asiye kumuyikila kumbuyo Gaga
Má dolla sakudziwa chimene akufuna
Yoooo more fire guys, I'm following and watching from South Africa, Johannesburg , Alberton. Gaga amangidwe basi,,, ndiochenjeretsa kopusa ameneyo. Koma Mai Zimveka mmmm ndisaname atiphera Dorah wathu kkkkkk.
Zione my favourite ❤❤❤❤ love you zione
Nice 😂😂😂😂
Gaga wandikwanapo
Gaga aziona ife tudikirira episode inayo
Kma Gaga eeeeeee
Amayi a dola akumenyani a zinveka , koma inuyo ndinu a mphanvu simulola kkkkkk
kodi mwini wake wa galimoto sakutuluka kukaleletsa bwanji, kkkk kapena mwagula mayi adola. kkkkkkk
😂😂😂gagah ndi nkaid gyz 😂😂😂
kkkkkk a davieeee jonz jonz yavuta zed kkk
Mayi a Dolla ingovomelezani zinachitika zinachika kulibe kuchitilamwina, Dolla akhale ndi bambo ake basi..
A chiphwanya mkaziyo munasankha hahaha
27:40 Gaga kkk 28:17
Aunt a Davie mumatha
Gaga amangidwe
😂😂😂😂😂 koma gaga kuchenjela kumneku ndikwabwanji nakuuza kuti farawo azabudula memo wagulu lelo ndi uyu kkkkkkk koma afumuwa ndi makina amapanga zinthu zodekha monga mfumudi mumatiyimilila afumu 😊😊😊
Akutitu ndi amfumu enieni
Gaga wachenjeretsa iiiiiiii
Chisomo🥳🥳🥳🥳🥳
Eshiiiiii km ma Dollah chipamatu kwa a bea awo 😂😂😂😂
Kkkkkkk zimenezo ndi zomwe akukanazo😅
Dorothy sukulakwitsa atonde mulandireni mwana iiiiiiiiiiii gaga wagwidwa basitu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤ from south Africa
Next please kkkkkkkk wakuba amazigwilitsa ekha Gaga sunachenjere bwino NDE nawe Davie yakuchimwira 😂😂😂😂😂😂 chikomekome cha mkuyu
Ndipo inu kkkkkkKoma zikubeba
Koma Asiyatu phwete limenelo? Kkkk. All the same good show.
Mwandichedwesera
😂😂😂ati olo ineso zanditopetsa..davie naye watopa ndiuchitsilu wake
Koma gaga eeee
Ikwumachepa vedeo
Chisomo zoona ukamudyese Gaga maliro kkkkk😂😂😂😂
Chegaga watsala madzi amodzi
koma farao mwini film kkkkkkkkk
Kkkkkk big up guys keep it upChisomo ndi Falawo akwatilane akukhalana bwino
Amfumu awa kumulekerela Gaga aaaaa mpake episode iyi Gaga osamuonetsabe
Gaga kuchenjera paka amangidwe basi waiting next part😂😂
Agaga anachenjela mopusa kwambiri
Awiliam ndi mfumu yodekha, tione kumapeto kwa zonse kuti apitiliza kudekha?
Amfumu wiliam ndi munthu wankulu akuziwa chomwe akuchita ulemu wanu mfumu gaga la 40 lakwana lokha usanganize kuti akukusiya dala ayi.mfumu yanzeru imeneyo ikuziwa
Gud job
Gaga zamuvuta uku mavuto sakumuchoka deyile
Davie mtambwali iiiii
Koma Gaga nde mukumunyengeleratu
Koma mukuchedwesa guy timakunyadira good work
I love u asyatu❤❤❤ u are cute
Chigayo cho bwanji
Farao amatha
Chisomo yemweyo umakwana
Gaga wazingwa kkkk
Koma gaga sadzatheka
Chisomo size yomweyo osaseka umatha kma asyatu ulipama vuto ndi husband wako chiphwanya kkkkk tonde ndye walandila mbama yachi zimayi 😂😂😂 kma sanachonse zino lina
Km gaga mmm lakwana la 40😂😂
Nkazi chibwanya amandiwaza. She is a good actor
Amwalira o chifuniro
kkkk km gaga
Koma afumu mundinthandidzapo apa
Farao waiphedula
22:54 dev
Km gaga ngat uli ufit uyaluka wava
Nice acting my people 💯
Koma nyamata deya uyuuu mukuti gaga😂😂😂😂😂
Km muli bwino kwambiri tonde wadula❤❤❤❤❤❤
Killjoy koma gaga ayi zikomo la 40 likwana
Gaga watha boxa laķo wagwidwa nalo nanga chibiliti akamva poti anati chati chubwii sichinawoloke ndiye kuti uwoloka bwanji Gaga
Dave wayamba kusaka passport 😮😮, mai a Dolla kukwiya mwawonjeza, Dola asowa mtendere, Gaga! Gaga! Iwe ndi deyadi aise.
koma amfumu nawo sakumdiwaza
😂😂😂😂😂ine nganga amamdiwaza kwambili guys😂😂😂 nganga wadya wani bas
Kkkkkkkkkk mumativesa kukoma kwambili guys ❤🎉🎉🎉
Kod gaga wapambana chani amfumu akumunyabiita why?
,kkkkkkkk tonde waziwona
❤❤❤
Gaga upole 🔥😂😂
❤
0:20 Gaga ndi akatundu
😂
Amfumu mumatha ulemu wanu chisomo ndakuvulila chipewa😅😊
koma ma dollar ❤❤❤❤❤❤
Aaaa kodi zukhala bwanji mwayamba kuchoka mmodzimmodzi aaaaaaa chifuniro wazima muthinda kumangidwaa aaaaaa
Koma gaga 😅😅😅😅
Chisomo chisomo❤❤❤❤❤
Big deal
Koma ndiye kutisiya malele😂😮
zibwino gayz
Gaga ndi makina😅😅😅😅
Eeeeee gaga ndi kathyali nkhani ija wayisinthanso😂😂😂
The Dog 🐕 was awakened and started wagging it's tail when Tonde shouted DOLA 😂😂😂😂😂
Tonde wadula palibeso❤
Chisomo is a good actress
Kkkkkkkkkk gaga sazateka basi
Mwandisiya malere amfumu kkkkkkkkkk chisomo my actor no nonsense umakwana ase.
Bravo team Tonde wadula ❤❤❤❤❤
Madola mulipati azimveka ayi tonde ayi mungolusila aliyense😊
Amfumuwo akumukondela gaga
I can't wait next part gaga asachenjere pakamwa choncho sikuchenjela kwabwino kumeneku 😂😂😂
Koma kodi mwati mashine okhonzera mashine ine mumawacha kuti gaga eti 😂😂😂😂😂gaga ndie mashine o
Kkkkk Gaga kuchenjela pakamwa
Koma gaga iiiiiii 😂😂😂 musiye chiso afotokoze ,ukuopa chani gaga weee
Kkkkkkkk kma gaga upole fire ,amfumu ulemu wanu inuyo mumatha
Akangomva Makwale Farao basi watha.......Ndikuwona chisomo akupangidwaso Kidnap ndi Gaga
Gagaaa gagaaa kkkkk shiii. Keep de fire burning. Ma dora eshiii fire mabomba2
Gaga chifuniro arose m'bwaro pzlz
Mmmmm chisomo umatha nosenu guy's ndimanva kukoma nanu kabasi
Watching from South Africa Pretoria mamilod Lusaka keep it up gyz ❤❤
Zili chabe bwino ,,, Nazombe moto unandi
Muwawuze amfumuwo kuti asiye kumuyikila kumbuyo Gaga
Má dolla sakudziwa chimene akufuna
Yoooo more fire guys, I'm following and watching from South Africa, Johannesburg , Alberton. Gaga amangidwe basi,,, ndiochenjeretsa kopusa ameneyo. Koma Mai Zimveka mmmm ndisaname atiphera Dorah wathu kkkkkk.
Zione my favourite ❤❤❤❤ love you zione
Nice 😂😂😂😂
Gaga wandikwanapo
Gaga aziona ife tudikirira episode inayo
Kma Gaga eeeeeee
Amayi a dola akumenyani a zinveka , koma inuyo ndinu a mphanvu simulola kkkkkk
kodi mwini wake wa galimoto sakutuluka kukaleletsa bwanji, kkkk kapena mwagula mayi adola. kkkkkkk
😂😂😂gagah ndi nkaid gyz 😂😂😂
kkkkkk a davieeee jonz jonz yavuta zed kkk
Mayi a Dolla ingovomelezani zinachitika zinachika kulibe kuchitilamwina, Dolla akhale ndi bambo ake basi..
A chiphwanya mkaziyo munasankha hahaha
27:40 Gaga kkk 28:17
Aunt a Davie mumatha
Gaga amangidwe
😂😂😂😂😂 koma gaga kuchenjela kumneku ndikwabwanji nakuuza kuti farawo azabudula memo wagulu lelo ndi uyu kkkkkkk koma afumuwa ndi makina amapanga zinthu zodekha monga mfumudi mumatiyimilila afumu 😊😊😊
Akutitu ndi amfumu enieni
Gaga wachenjeretsa iiiiiiii
Chisomo🥳🥳🥳🥳🥳
Eshiiiiii km ma Dollah chipamatu kwa a bea awo 😂😂😂😂
Kkkkkkk zimenezo ndi zomwe akukanazo😅
Dorothy sukulakwitsa atonde mulandireni mwana iiiiiiiiiiii gaga wagwidwa basitu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤ from south Africa
Next please kkkkkkkk wakuba amazigwilitsa ekha Gaga sunachenjere bwino NDE nawe Davie yakuchimwira 😂😂😂😂😂😂 chikomekome cha mkuyu
Ndipo inu kkkkkk
Koma zikubeba
Koma Asiyatu phwete limenelo? Kkkk. All the same good show.
Mwandichedwesera
😂😂😂ati olo ineso zanditopetsa..davie naye watopa ndiuchitsilu wake
Koma gaga eeee
Ikwumachepa vedeo
Chisomo zoona ukamudyese Gaga maliro kkkkk😂😂😂😂
Chegaga watsala madzi amodzi
koma farao mwini film kkkkkkkkk
Kkkkkk big up guys keep it up
Chisomo ndi Falawo akwatilane akukhalana bwino