ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Its giving fire...Gaga kuchenjera zochita..Maa Dola nawo ali ndi khama mu zochita zao
Ma Dora ulilitsa Muthu 😂😂 moto kuti buuuu azinveka inu pachoka nzako Pali Malo hahaha mumakhwana guys ❤️
I like uja wachoka uja uja Wamwalila ndi akuba uja my best actress 😢
mwayamba kuchedwesa koma ❤
One of the best comedie in malawi
Chilungamo gaga nkhaza zomunamizira munthu mimba mwana kufa kenaka kumakhalabe nae ufiti
Zilibwino man molen ndi chigawenga choopsa. Achiphwanya lekani nkhanza. Achibiliti mwazinvera nokha
Azimveka kulusa 😂😂😂😂mpakana kuti alemba aganyu ampwanye galimoto😂😂😂😂😂🤔naye gaga eeeee ayiiii ndithu aona polekera maboza
Kkkkkk km nzinveka chilichonse kumangodalira aganyui
Akufa akumabweleratu,chifuniro auke kwa akufa pls
Zinalakwika Chifunilo kutulukamo.Adaliso wobebetsa kwambiri
Ching'aning'ani nkadzi angomutsekera ngat chiweto😂😂
Watching from Zambia Mr chiphwanya very difficult
Kikkkkkk achipwana aonjeza bwanji,,,,, mr zanveka moto unandi 😂😂😂😂
Gaga suwuzathela ndithu😂😂😂
Chiphwanya beyond love
Kkkkkk
Nonse amene muli mu movie iyi ndi 1 palibeso ndikumva kukoma ine.
Chisomo u are so beautful
Payipa pano afumu mukuchedwatu Gaga ufumu Alanda nditu
Farao kuopa kudzingidwa ndi gaga😂😂😂
Mole mwamupha chifuniro😭😭😭😭😭😭😭 mmmmmmmm
Achibilit ndi anagumbo zitha bwanji zaulilika
Nice acting my people ❤
Gaga kuchenjera monyasa
Kkkkk Gaga sazatheka
Ndiye maliro muika bwanji ife tisanaone nkhope😢😢
Eti tinakapelekeza kah akuchikazi
Koma make dora ndi azimveka kķkkk 😂😂❤❤❤ mumakwana anthu inu
Muthinda uli ndi ma passport angati😂😂😂😂
Hahahaha. Even ma driving license kaya ali nawo angati???? !!!
@@masaukomsiska4830 kkkkkkk eeee bodzatu😂😂😂😂
mbola osati zenizeni kkkkkk@@patrickmadukani4314
Eeeeh koma Chiphwanya😂😂😂
On climax 🔥
Gaga sazatheka miseche
Zimveka chiphwanye inde
Kkkkkkkkkk gaga yeeeeee sazateka
Kodi munthinda mulindi ma passport angati na ma licence angati ma ID angati😂😂😂😂😂 zonse zonse
Zimveka wabetsa😂😂😂😂😂
nice keep up good work
🎉muthinda passport imakha imodzi
Ma dolla aponda mwala tsopano
Gaga versus Nagumbo kkkk
How can I watch this movie without chifuniro
Azimveka ndi Mai a Dora ulemu wanu
Kkkkkkkkk mr ziveka avekadi kkkk
Next more fire Zimveka😂😂
From Johannesburg
I miss chifuniro
Guys mwachotsa nsanga chifunilo please apa mwalakwitsa anayenela asafe nzanga atuluke after kuchipatala akanapitiliza
Chipwanya osawapasa mpata azanu mmmmm
Koma gaga😂😂😂
Zimveka zamuwawa
Man mole koma nde mwaphula sin yachab
12:48 chimpwanya
😂😂😂 koma banja lazimveka
Chemuthinda ma passport onse 😂 munthu amakhara ndima passport angat?😂
Nalikukute pa nthema zamveka kkkkkkk. Ma dola looks nice when u r not in make ups plz
Chiphwanyaaaa😂😂😂😂
Mr sasoka
😂😂😂😂😂😂 chiphwanya😂😂😂😂
Kuchedwa kmaaa
Koma chiphwanya sumwa madzi eeeti 😂
😂 km inuyo iiii
Zimveka walusa
😂😂😂 chipwanya ndwe kape kwabas
Chiso❤
Ma driving licence onse ma passport onse Eeeh amakhala angati chaunzika mchimodzisotu muthinda wabalalika Ku sale😂
Azimveka akwiya 😂😂😂
Kuteloko mkazi uja unapha wekha mole
Azimveka alusa 😂😂
ZIMVEKA 😂😂😂😂😂
Chisomo ndi farao angokwatilana basi
Gaga sazatheka😂😂😂
km gaga ndi katundu
Koma nde yachedwatu
Km yeah ml hard
Koma Gaga 😂😂😂😂
Vuto tikumakhala tatifupii
Amole munamumpha mkazi
guys inuyo mumatimvesa kukoma
🎉😂😂😂😂😂 chiphwa
Chiso and pharaoh is good actor's
Hahaha😅😅😅
Kkkkkkk
Guyz ❤❤❤
kkkkk ma dorah apana kapena kuti bwanji? kkkkkk Koma Gaga akujaira heavy.MUMATHA INUYO
😂😂😂😂😂
❤❤
You are prolonging maboza a gaga and its becoming uninteresting, and boring.
Achipwanya 😅😅😅😅ati kumiziyamu
Its giving fire...Gaga kuchenjera zochita..
Maa Dola nawo ali ndi khama mu zochita zao

kkkkk ma dorah apana kapena kuti bwanji? kkkkkk Koma Gaga akujaira heavy.
MUMATHA INUYO
😂😂😂😂😂
❤❤
You are prolonging maboza a gaga and its becoming uninteresting, and boring.
Gaga kuchenjera monyasa
😂😂😂😂😂
Achipwanya 😅😅😅😅ati kumiziyamu