ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Acisomowo siza film zokha ngovuta ndi kulolongolora ndithu in real life😅
Iyi njamoto iyi...Zimveka ngochenjeresa,,, Gaga la 40 likubwera
Ma introduction munakachepetsako we are so proud of you guys
Akachepesa ndiye kuti singayende ayi
That's true
Ndiye anthuwa tiziwaziwa bwanji..asachose ma intro
Ndipo ndiye amaonjezadi
2mins intro it's too much,maina amaoneka kumapeto aja ndiokwanira
Achibiliti ndi azimveka akumanapono osabereka okhaokha😂
😅
proudly waiting to see episode 75 I love you guys. My very best and favorite artist is Mai Phiri. All in all I love you guys you are the best.Watching from South Africa, Johannesburg Alberton.
❤❤❤😂😊❤sokosi kuvala mwendo umozi chisomo wavutatu mowa ukuyenda bwanji,,nanyoni wasopano😅
Ziveka kwa chibiliti wasiya nkhan 🎉🎉🎉🎉 waiting
Ma Dola mwayambanso nsanje? A Zimveka a chimwene anu a Chibiliti akuyenda mu mdima. Osacheukacheuka akufunani. More fire guys
Kkkkk mumakwana Gaye's thank you
Koma ziveka amvekele " allyenkha cyclia🎉🎉🎉🎉bwinotu zimveka sapanganawo chibwana
Azimveka mzeru mulibedi Inu hiyaaaaa 😂😂😂😂😂❤❤❤ achibiliti chulungamo mwakamba
Ma dorah hair style ❤😂😂
Achibili ndi mayi phiri aaaaaa 😊
Koma bwanji maa adola sakumukonda tonde koma ndimwine wamwana
Ndikumatha kuwona kuti Gaga kuchenjela kumuthela hahaha guys pitilizani mukutinvetsa kukoma❤kuno ku cape town more fire guys
Dora amayitha mwana wadzilungamo😂
😂😂😂😂😂😂 komatu zimveka akusowa mtrndele agaga akungowonjezela milandu uku wakauputaso wina kwa chisomo kkkkk mumatha guys
iweso uzandifuna zizakuvhuta - kkkk aZimveka bwanji
Timakunyadilani pitilizani ma Dora your a good example of a mother.
Ziiveka kwa Fyness paka Dola ndewu
Zinveka waionamo mwa sisiriya😅
Chisomo umandisangalasa ndi wanzelu 😂😂😂😂😂
Tonde palibenso opikisananawo muzitulutsa olo atatu pa week
Chisomo muthireni madzi Gagayu azipita asakutopetse iya
kkkkkkkkkk Azimveka kuchewukachewuka akamayakhula kungoziwa kut Tambwali weni weni kkkkkkk amandiwaza kobasi
Dola umakwana chisomo serious osaseka
Mukadasutabe fodya uja😅😅😅in Zimveka voice
Kodi gaga samwa mowa 😮😂
Amake Dora - ndimakukondani koma hairstyle yiyayi
Akuti tonde mukumudziwa 😂😂a 😂
Congrats guys
Lero mwaipatsatu fire 😂😂
21:04 mbuyache muthinda next kuti tive zambiri
😂😂😂😂 Koma Jordan yeah kkkkkkkkkkkk kumalawi
Ilove you guys
Mumakwana anthu anga ndi makunyadilani❤❤❤❤❤
Good job
Chisomo umaitha mpakana ma sokosi osiana
Pls ina mutumizeso lero timakunyadirani ma guys
Congratulations guys
Chisomo ndi munthu wolimba mtima ❤❤❤❤
Sono nganga wavala zithu zingat😂😂😂😂😂😂
Zili bwino timachosa khawa
I love you my people
Timakufran kwambili mupitilize ndi2
Mukubwera bho ❤
🥳🥳🥳apa yativesa kukoma❤
Koma afumu a William Ali ndi kazi??
Lero mwaveka ngayezi moletu apa zivuta
More fire guys
Mwatani kungotipatsa ya 1hr guys
Awa atipanikiza awa
@@mbwindinga 😂😂😂😂
Keep it up maguys
Zikukoma bwanji ❤ you guys
Zimveka zikuthelan km 😂😂😂
❤
Next
Mukuitha guys kuponya ma episode awili Lelo lokha
Mbambande❤❤
Zilibwino apa limbikilani guys
Dora keep it up
More fire guys 😂😂😂😂😂
Mmawaso tikufuna ina
Koma ma Dollar nde mmm alowere kut mwana
ZIMVEKA UMAKWANA😂😊😅😢
Shuga shuga palibe kutopa❤❤❤❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Mumandimvesa suger guys
Zili bwino zedi,
Chibiliti mabonyo
CHISOMO AND DOLA I LOVE YOUUU ❤🫣🫣🫣🫣😉😉😉😉
Mumaitha kwabasi
Koma ulemu wanu
😂😂 yomweyo
Zimveka pola moto
🎉❤❤❤❤❤❤
Tonde
Dola ndizakukwatira
Acisomowo siza film zokha ngovuta ndi kulolongolora ndithu in real life😅
Iyi njamoto iyi...
Zimveka ngochenjeresa,,, Gaga la 40 likubwera
Ma introduction munakachepetsako we are so proud of you guys
Akachepesa ndiye kuti singayende ayi
That's true
Ndiye anthuwa tiziwaziwa bwanji..asachose ma intro
Ndipo ndiye amaonjezadi
2mins intro it's too much,maina amaoneka kumapeto aja ndiokwanira
Achibiliti ndi azimveka akumanapono osabereka okhaokha😂
😅
proudly waiting to see episode 75 I love you guys. My very best and favorite artist is Mai Phiri. All in all I love you guys you are the best.
Watching from South Africa, Johannesburg Alberton.
❤❤❤😂😊❤sokosi kuvala mwendo umozi chisomo wavutatu mowa ukuyenda bwanji,,nanyoni wasopano😅
Ziveka kwa chibiliti wasiya nkhan 🎉🎉🎉🎉 waiting
Ma Dola mwayambanso nsanje? A Zimveka a chimwene anu a Chibiliti akuyenda mu mdima. Osacheukacheuka akufunani. More fire guys
Kkkkk mumakwana Gaye's thank you
Koma ziveka amvekele " allyenkha cyclia🎉🎉🎉🎉bwinotu zimveka sapanganawo chibwana
Azimveka mzeru mulibedi Inu hiyaaaaa 😂😂😂😂😂❤❤❤ achibiliti chulungamo mwakamba
Ma dorah hair style ❤😂😂
Achibili ndi mayi phiri aaaaaa 😊
Koma bwanji maa adola sakumukonda tonde koma ndimwine wamwana
Ndikumatha kuwona kuti Gaga kuchenjela kumuthela hahaha guys pitilizani mukutinvetsa kukoma❤kuno ku cape town more fire guys
Dora amayitha mwana wadzilungamo😂
😂😂😂😂😂😂 komatu zimveka akusowa mtrndele agaga akungowonjezela milandu uku wakauputaso wina kwa chisomo kkkkk mumatha guys
iweso uzandifuna zizakuvhuta - kkkk aZimveka bwanji
Timakunyadilani pitilizani ma Dora your a good example of a mother.
Ziiveka kwa Fyness paka Dola ndewu
Zinveka waionamo mwa sisiriya😅
Chisomo umandisangalasa ndi wanzelu 😂😂😂😂😂
Tonde palibenso opikisananawo muzitulutsa olo atatu pa week
Chisomo muthireni madzi Gagayu azipita asakutopetse iya
kkkkkkkkkk Azimveka kuchewukachewuka akamayakhula kungoziwa kut Tambwali weni weni kkkkkkk amandiwaza kobasi
Dola umakwana chisomo serious osaseka
Mukadasutabe fodya uja😅😅😅in Zimveka voice
Kodi gaga samwa mowa 😮😂
Amake Dora - ndimakukondani koma hairstyle yiyayi
Akuti tonde mukumudziwa 😂😂a 😂
Congrats guys
Lero mwaipatsatu fire 😂😂
21:04 mbuyache muthinda next kuti tive zambiri
😂😂😂😂 Koma Jordan yeah kkkkkkkkkkkk kumalawi
Ilove you guys
Mumakwana anthu anga ndi makunyadilani❤❤❤❤❤
Good job
Chisomo umaitha mpakana ma sokosi osiana
Pls ina mutumizeso lero timakunyadirani ma guys
Congratulations guys
Chisomo ndi munthu wolimba mtima ❤❤❤❤
Sono nganga wavala zithu zingat😂😂😂😂😂😂
Zili bwino timachosa khawa
I love you my people
Timakufran kwambili mupitilize ndi2
Mukubwera bho ❤
🥳🥳🥳apa yativesa kukoma❤
Koma afumu a William Ali ndi kazi??
Lero mwaveka ngayezi moletu apa zivuta
More fire guys
Mwatani kungotipatsa ya 1hr guys
Awa atipanikiza awa
@@mbwindinga 😂😂😂😂
Keep it up maguys
Zikukoma bwanji ❤ you guys
Zimveka zikuthelan km 😂😂😂
❤
Next
Mukuitha guys kuponya ma episode awili Lelo lokha
Mbambande❤❤
Zilibwino apa limbikilani guys
Dora keep it up
More fire guys 😂😂😂😂😂
Mmawaso tikufuna ina
Koma ma Dollar nde mmm alowere kut mwana
ZIMVEKA UMAKWANA
😂😊😅😢
Shuga shuga palibe kutopa❤❤❤❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Mumandimvesa suger guys
Zili bwino zedi,
Chibiliti mabonyo
CHISOMO AND DOLA I LOVE YOUUU ❤🫣🫣🫣🫣😉😉😉😉
Mumaitha kwabasi
Koma ulemu wanu
😂😂 yomweyo
Zimveka pola moto
🎉❤❤❤❤❤❤
Tonde
Dola ndizakukwatira
Next