Chakwera Achotsa Ntchito Zikhale Ng'oma

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 10 ก.ย. 2024
  • khalani nafe pano pamene tizikupatsirani nkhani mwatsatanetsatane zomwe zikuchitika mudziko la Malawi

ความคิดเห็น • 20

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 6 วันที่ผ่านมา

    Zikhale kupupuluma too much 😊

  • @PhalesNotta
    @PhalesNotta 19 วันที่ผ่านมา +1

    Chikangawa chakwera ndi manganya anthu awiri amenewa akutiphera azibale athu koma mulungu kumwambako musakhale chete muchitepo kanthu ndithu

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 27 วันที่ผ่านมา +3

    Achoke basi amalawi tikuvutika munachoseranji Company yimene anayisiya a DPP

  • @ChipieWAmatthewGamah
    @ChipieWAmatthewGamah 27 วันที่ผ่านมา +4

    Bakili Muluzi TV ndi one

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 27 วันที่ผ่านมา +3

    Apule achakwela achoke

  • @DavieChiwale
    @DavieChiwale 27 วันที่ผ่านมา +3

    Kunkuyu chakutichako ndiwe chitsiru

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 18 วันที่ผ่านมา

    Mmmmm😊

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 27 วันที่ผ่านมา +3

    YYA ZIKHALE NG'OMAYI IKUTI BWANJI APA?????

  • @MikeJemus-i5h
    @MikeJemus-i5h 27 วันที่ผ่านมา +2

    Kkkkk alibe umunthu wa usogoleli achoke

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 27 วันที่ผ่านมา +1

    Nanu so a times muziona nkhani zolemba musamapange zopusa

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 27 วันที่ผ่านมา +1

    Agalu amenewa bwanji akubisabe report ya ndege achule akupha amenewa

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m 26 วันที่ผ่านมา +4

    Chakwera,kunkuyu, ng'oma ,sitikuwafuna ndi uja chenkhumba uja sitikuwafuna

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 25 วันที่ผ่านมา +1

    Zopoira zimenezo, achoke osewo

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 25 วันที่ผ่านมา

    Ndipo the last two weeks ndakhala ndikudutsa pa immigration office ya ku Lilongwe, anthu kuchita kumvetsa chisoni, anthu akuchita kukozera mitengo ya pamenepo, fungo la mkodzo. Sizikuyenda ndithu.

  • @ProsperNaison-ri7dx
    @ProsperNaison-ri7dx 26 วันที่ผ่านมา

    Achoke zikhale ng'oma

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 23 วันที่ผ่านมา

    Onse azipita kwawo kwatha, wapambana chani chakwerayo chifukwa driver ndiyeyo.

  • @Judah-zb6sl
    @Judah-zb6sl 25 วันที่ผ่านมา

    Achoke 🎉🎉🎉🎉😂😂😂

  • @MathewsMpanga
    @MathewsMpanga 23 วันที่ผ่านมา

    Our God is a good God,David is in Malawi now to take down Goliath once and for all.