Many who are encouraging us to take action on this are in the diaspora please let's be careful indeed it hurt and its difficult to bare but let's trade carefully
While I understand the concerns about acting,,,it hurts and is difficult to bear, but caution shouldn't be an excuse for inaction,ululu wachuluka ndikusavesa
Angoni from south Africa,osangonja,ndizi tsiru za MCP dzi achewa zakupha.Angoni Ndi Wanthu wozi sungira Ulemu Chilima wachita kuphedwa, koma adali Munthu wozi chepesa kumu manga kumunyoza koma iye wosayankhula kanthu mpakana kuphedwa Ndi Chitsiruu Chakwera mbuzi ya munthu pakana khala Kuti nkale,pakada khala chinkhondo chowopsya Ndi A Chewa komanso Angoni tonse takonzeka A Chewa asati zolowere yayi,unkhontho phambili,nkosi kwata ine
@@RiteRoderick braz koma mwayiwerenga bwinobwino statement yake walemba galu ameneyi ???? Akunyoza achewa kungokhalangati achewa onse ndi a MCP . Chitsiru ameneyi kwambili
Ife tamva kuti ago mani agulilidwa nyumba ku 43 ndi mcp ndi azi mfumu wonse amu ntcheu analandira ndalama ma 10 mita zikomo po kumbukila mzimu wa biyeni
CHAKWERA, CHIMWENDO BANDA, KUNKUYU, MKAKA, ZIKHALE NG'OMA, CATHERINE HARA be careful Malwians are watching your footsteps! Be very very careful. MCP is ended!
Ndizowonadi zimenezo amfumu simukunama tikumana pa 10 pano basi amfumu tipite ku mademo mwa unyinji osafowoka apolice tikawamenya sitikwafunaso apa tipanga nafeso ngati za ku Kenya 🇰🇪 apolice akumenyedwa kamba ka uchisilu ndie ifeso takozekela kumenyana nawo apolice ndipos sabale athu amenewo mcp stupid grvt
Osatopa, osafowoka, tidzafera mbendera SKC mmhh😭😭 ngati bodza ndithu may his soul rest in internal peace, and including the other souls may there soul rest in internal peace😭
I think this is warning to Mr president Kuti anthu Aku ntcheu ndiokwiya Nanu inu ndi MCP yonse ndipo if u r involved in chilimas death mulungu akukantheni
Pepani angoni, zikundinvekela ngati Biyeni wangotichokela Kaye pakati pathu akukacheza Kaye Ku dziko lina like abwelanso😭😭😭😭😭😭
.
😅😊😊😂❤ti❤ku😊😊😊😅❤😊l😊i❤❤la
A😊vice p❤😅😂resi❤de❤n😊t❤❤❤
Kuswa kuswa bas nthawi yonyengelera inapita
Angon satha onse
Zinangovuta nthawi yoti chakwera achoke pampando ndiyomweyi ino, kodi aMalawi tidzachangamuka liti let's all go Kuma Demo pa 10 pano kuchotsa Chakwera ndipo ma Demo amenewa akufunika continueos mpaka atachokapo
Pa 10 pansewu bas enough is enough
Ndipo Fortu nkhani ndiyomweyo ❤❤
Ngati bodza asaulosi chilima.munatisiya mitima itasweka.mulungu achitepo kathu koma 😭😭💔💔
Awanso muwamanga???? Zamanyazi iziii mzimu wa chilima uuse mwa ambuye
Mposo inu
Mtima wanga udzatontola pokhapokha chilungamo chitadziwika
Ndipo kwambili
Chilungamo chake ndiye ndichakuti chakwera adapha chilima that's all
Angoni olimba mtima inu tikulilira limoza saulosi chilima was a great leader was killed by jealous people.
Apart Afumu mudapalamula ndipo imfa yanu mudzafa ngati galu wachiwewe pazomwe mudapanga pa Achilima 👌🏽☝🏽️🙏🏽
Many who are encouraging us to take action on this are in the diaspora please let's be careful indeed it hurt and its difficult to bare but let's trade carefully
While I understand the concerns about acting,,,it hurts and is difficult to bear, but caution shouldn't be an excuse for inaction,ululu wachuluka ndikusavesa
Osakhara Bata ayi chakwera achoke
Mfumu yalila zosakhala bwino
Angoni from south Africa,osangonja,ndizi tsiru za MCP dzi achewa zakupha.Angoni Ndi Wanthu wozi sungira Ulemu Chilima wachita kuphedwa, koma adali Munthu wozi chepesa kumu manga kumunyoza koma iye wosayankhula kanthu mpakana kuphedwa Ndi Chitsiruu Chakwera mbuzi ya munthu pakana khala Kuti nkale,pakada khala chinkhondo chowopsya Ndi A Chewa komanso Angoni tonse takonzeka A Chewa asati zolowere yayi,unkhontho phambili,nkosi kwata ine
Iwe ndiwe chitsiru kwambili . Chifukwa chani ukuphatika achewa ndi MCP . Siyanitsani pakati pa Chipani ndi Achewa . Mapwala ako ndithu
@@edenngoma8214mesa big inuyo achewa Ndi apa central Ndipo mumakonda MCP chipani chokuphachi. Ndinkana iyetu watero coz anthu aku Lilongwe mukumaona kuti dziko likuonongeka koma mukumapopabe MCP big. Ndie sizokuti mutukwaneyi onani Malawi wanunkhiramu boss😢😢😢
@@RiteRoderick braz koma mwayiwerenga bwinobwino statement yake walemba galu ameneyi ???? Akunyoza achewa kungokhalangati achewa onse ndi a MCP . Chitsiru ameneyi kwambili
@@edenngoma8214 Big pakunyoza achewa ndikulakwitsa tisalimbaneyi Ndi Ntundu komano tilimbane ndiulamuliro oipa okuba, okupha ulipowu boss. Apopo basi khululukani ingozisiyani ndithu braz
Olira salakwa
Zibonga ndichatunga zigwire ntchito tsopano.Chisoni chikuphesa nkhwali yapa
Zimu wawo unused mutendele . Koma apa chakwela anapanga chipongww
Ndipo mistake
Painful 😭😭😭😭
😭😭😭😭😭koma kulira a mfumu Eeee koma Mulungu yekhayo alowelelepo mwava My Mr Saulos Chilima and all other souls Rest in peace
This just proves how great SKC was. May his soul rest peacefully and may God comfort his family
Ing'alure iwe aaaaa
We are watching from the united kingdom
Kuswakuswa angoni atiphera chilima kumene.
CHAKWERA MUST GO ✊✊ on the 10th July I will be on the front 😂😂
The revolution is now🔥💪✨
Watching from united Kingdom 🇬🇧, am pure Ngoni from Ntcheu. Viva Viva All Ngonia
T/A kwataine kungoying'amba
Mwamba ukuchitikira pa old depot eti home is best always
Proud to be Ngoni ❤
More 🔥 🔥 angoni 🎉🎉
I sympathize with you Ngwenyama Gomani the fif th .Malawi has really lost the adept political hero Dr.Chilima.May his soul RIP
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Dr SKC and other 8, forever in our hearts 😭😭😭😭😭 Ambuye atonthoze Mitima ya aMalawi😭😭😭😭
We need Mafumu olankhula ngati awa! Kulankhula kopanda mantha!
Pepan kwambili
Ndipo asakuophyezeni afumu
Zikutiwawa zikutiwawa zikutiwawa tsiku lina tidzadzuka
Ine chilima bodza inu anamulakwira kwambiri
Ife tamva kuti ago mani agulilidwa nyumba ku 43 ndi mcp ndi azi mfumu wonse amu ntcheu analandira ndalama ma 10 mita zikomo po kumbukila mzimu wa biyeni
Aaaaaa asithana ndi moyo wa chilima
Kuswa kuswa bas madala amwela mazi mwa nkhwiyo awa
CHAKWERA, CHIMWENDO BANDA, KUNKUYU, MKAKA, ZIKHALE NG'OMA, CATHERINE HARA be careful Malwians are watching your footsteps! Be very very careful. MCP is ended!
❤
Speak without fear, tell the government to understand
Powerful speeches from Ngoni chiefs
Chakwera wakupa chilima wapa chakwera patenipa 10 July kuvuta chakwera achoke
For sure we're coming pa 10 enough is enough guys our hearts are bleeding
NA NGONI OKAVOTERA CONGRESS NDIYE KUTI MUTU WAKE SUGWIRA.
not only ngoni but malawian, angoni ndi atonga sfunidwa ndi MCP
Orton chirwa
Ralph kasambala
few examples of tonga plus ngonis matenje
Mcp chipani cha kupha ichi
A Biyeni kuphedwa mwankanza kwambili aaahh 😭😭😭😭💔💔..RIP SKC
inu maumboni ndi okwanila ndithu kuti munthu uyu adachita chokoza there is evidence
Simukunama apopo
MCP ndiyakupha ndipo chakwela mulungu amuwone ndithu
Umboni mulinawo pitani police mulinayo pafupi mukapeleke umboniwo to show kuti anaphedwa
@@Muhwimialiyense akudziwa kuti anaphedwa
Ndipo sitiopa kuntcheu aliyese wa MCP tinathetsa chipani cha MCP tidzaphophola
Pepani Amfumu mmmm zokhudza kwambiri eishiiiiiiii Chilima akause mu mtendere mmmmh❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Tili limodzi angoni zikhale ng'oma ,Moses mkukuyu,chimwendo,nkaka ndi chakwera akufunika zikwanje basi kuphakupha
Peace doesn't mean that the truth should be compromised
Its really sad
We need peace not igniting civil unrest otherwise who will suffer are women and children malawi need unity not tribalism say no to tribal conflict
When peace fails use what?....
Peace cometh, where there is justice.... A grand revolution is coming ☀️🔥💪✨
Ngati pakuchitika zauchitsilu zikufunika ma Demo kumene no justice no peace ✌
Next time you must think before casting your rubbish ok?we the ngoni we will do what ever we can
Useless chief, angoni alipo angati iyambeni muone polekela
😢😢😢 Live km bata livuta mpaka liti
Rest well skc
Zomvesa chisoni a senior chief akulira zawakhuza kwambiri SKC anali machine
Ulemu wathapo APA kungobwera ndikuing'alura basi
Am feeling very tearful ndkamamva mawu ngat awa okhudza malemu chilima😢😢😢 amalawi tiyen tidzuke pa siku lamademo
Kumpoto konse chinali chiyembekedzo chathu timaona Ngati chakufwa Chihana anatibweletseraso munthu kunena Chilima otsati fitodzo dza MCP chakwera👿👹👺
Angoni atopa
Angoni sife zitsiru .one day you will see. Anthu amafika potopa
😭😭😭😭😭😭😭
Adaputatu Angoni aziona
Mafumu tikulira Nanu limodzi koma sunganibe bata.
Inuyo mayankhulidwe anu akhale obweretsa mtendere osati nkhondo ai
Bata ndiye chani iwe
Ng,alulan bs
Kunena mosabisa ayi Mcp ndiyokuphadi kwambilii😭😭😭😭😭😭😭
And i wonder y bcoz zikhale is from ntcheu y he never protect his home boy
MCP is evil, may the lord expose their wickedness at at all cost
Panganipo kanthu afumu osasiyilira zinthu zikukupwetekani ntima dzukilani mwamba
Well speaking king 😎
Quachema
Kkkk...."akuti tisunge bata"..mukanawasiya amfumu athu atulutse zonse zakukhosi mitima ikuwawa iyi
Ndizowonadi zimenezo amfumu simukunama tikumana pa 10 pano basi amfumu tipite ku mademo mwa unyinji osafowoka apolice tikawamenya sitikwafunaso apa tipanga nafeso ngati za ku Kenya 🇰🇪 apolice akumenyedwa kamba ka uchisilu ndie ifeso takozekela kumenyana nawo apolice ndipos sabale athu amenewo mcp stupid grvt
Bt why mcp😢😢😢
Uyu wadya ndalama koma aja alakhula poyamba paja ngachilungamo
Osatopa, osafowoka, tidzafera mbendera SKC mmhh😭😭 ngati bodza ndithu may his soul rest in internal peace, and including the other souls may there soul rest in internal peace😭
Zaphamvu afumu
Kodi mesa chakwerayo amati ndi m'busa oziwa mawu amulungu ndiye umulungu ulipatipo apa, wayiwala kuti mawu akuti chani m'buku loyera
I think this is warning to Mr president Kuti anthu Aku ntcheu ndiokwiya Nanu inu ndi MCP yonse ndipo if u r involved in chilimas death mulungu akukantheni
koma ndikunva kuwawabe mpana pano vuto tikumakhala monga opanda zeru bwanji kut pade pade madzi satsuka tiyeni tigwirizane chimodzi achewa azilamulana kwaoko ifeso zathu
Pepani angoni amzathu zowawa izi watching from dedza tikulira limodzi😢😢
Amen osaopa angani enough is enough
Chiyembekezo chathu
Am watching from South Africa taking true
Kom mwandifikapo zomwe mwayakhula ip mwayakhula bwino zedi pamenepa osafooka osawopa ayi
Us Malawi anthuwa atitola tsopano ngati kuli kunvara mabomba nkukaphukitsa pandokhano or kumaofesi chikhara ku irac tikadathana nazo kare
Eish koma imfa ya chilima ndi anthu 8 aja mmmm amalawi tapwetekeka koma ndege imene ija
Tiyeni tikathane ndi chakwelayo
Khara nae iweo
Motor
Rest in peace chilima
Very painful chilima aaa shanil amayo ine 😢😢😢😢
Akuntcheu akutipezera kwambiri bata lachan agaru awa mzimu wachilima ndi anthu anaaja iwakathe amene anapanga izi ndikut iwakathe adziweso kut mzimu yakwia zedi
Bafwetu asiwachayen laba bayasijwayela ba mcp
Osawopa 😂😂😂😂
😭😭😭😭😭😭 RIP SKC
Amfumu awa ndawakonda kuyankhula kopanda mantha kusunga bata pomwe angoni akutha. Abiyeni mudaphera dzikoli mukhale nawo .ndipo munthu adapha abiyeni naye afe
Angoni to the world. Yob 13:13
Osaopa nthawi yoopa yatha
Ndizimenezo mudzimva
Tamubwezerani chakwera chipongwe chake abale
Angoni mozambique tiri limodzi abale
Imfa 😢😢😢😢😢😢😢
Tiyeni panseu ndipo ayao tili pambuyo panu angoni agalu amenewa achoke
Si angoni okha Koma Muthu aliyense okhala ndi mzimu akulira