Misunderstandig the rasta livity is rampant even in Jamaica.Sellasie himself said he was not God.The events of today's world are not in line with what the bible said will take place after the second coming of Jesus.
Mmm..Funso kwa Ras GALAWANDA ..Mwati Yesu ndiye Mulungo yo: Ndiyeno nchifukwa chiyani 'Yesu ku Munda wa Getseman kuja adadzapemphera pemphero yili". ILAHI ILAHI LAMASABA KATANI ,, MULUNGU WANGA MULUNGU WANGA MWANDISIYIRANJI..Apapano Yesu yo ankapephera kwa Mulungu wake wutiyo. Komanso pomwe ankanyamuka Yesu kukwera kumwamba iye adawatsanzika wophunzira ake ponena kuti ; NDIKUPITA KWA ATATE WANGA NDIKUKAKUKONZERANI MALO ...kodi atate wake wa yesu yemwe ankamunena apayu anali ndani.?
Koma penapake aChakhaza zoona mungalephere kufufa zamatathauzo a makaka owowo omwe akuzungulira I mean red, black, green and yellow, inu basi busy kufusa have u killed chicken before?
A Chakhaza panopo tili mu stage of Kingdom, we have three stages, stage of Law, stage of Grace and stage of Kingdom. Ma Raster akunama the second incarnation God now is in China not what what he is talking. Jahena is there, the new Jarusalem is there
I always proud of you joab frank
What I like most about Joab, kudziwa nyimbo eeeh
I love this interview please next time have another raster 😂😂😂😂🤜🤛
Joab umatha kucheza
This is nice Joab
Damn..I paused the video to verify about Marcus Mosiah Garvey...Ras Gwalawanda chimene akunena achikudziwa...the man is on point!SALUTE
92
2h6ju6udd😢
Ndaphunzirapo,sindimadziwa kuti yesu anabwera kale
May the lord open your eyes rastamen.......am touched
Koma zoti Yesu anabwera kale kachiwiri through Haile Selasie nde nzachambadi
😂😂😂 uyu asatisocheletse ife ndipo chambachi aah azitsuta bwino ndithu
Werengani masalimo Chapter 24
bwana could you do a cruize 5 with DR KEN ZIKHALE NG'OMA, it woul dbe epic i suppose
Is he a doctor?😂😂😂 how ?
Mmmm rastar uyu akukamba zachamba
Inu ndamene simukudziwa
Kuteloko ma Rasta amakhulupilioanso utatu oyela wa akatolika ndiye nzausatanansotu Mulungu ndi mmozi ndipo mwana wake ndi messiah
programme ya Cruise ndimayikonda kwambiri,imandisangalasa kwambiri kuno ku Zambia
Kkkk koma joab,akuti oohh eee paja ndimulungu eti kkkkkkk
Rasta uyu m'mutu mwake simuyenda bwino
😂😂😂😂
Ndigalu kwambili uyu
Uyu atha kukutengela ku uchimo sure
Koma eeeeh chambadi
What is the quencequence of uchimo if there is no Gehenna?
Imfa
😂😂😂 ati Yesu sanali wa mpala iiiiii ,,,anthu awa🤣🤣🤣🤣
Mumativesa kukoma achakhaza
Komanso banja ndichilengedwe kuti mwamuna amayenera kuzitengera mkazi wa iye yekha
Misunderstandig the rasta livity is rampant even in Jamaica.Sellasie himself said he was not God.The events of today's world are not in line with what the bible said will take place after the second coming of Jesus.
Rasta akunama tsikulinalake adzakumana naye mulungu maso ndi maso
Joab akut sungasambire ku toilet bath lilipo... watero galawanda 😂😂😂😂😂
Kani 😂😂 😂😂🙌🤣🙌
Rasta
Eeeeh zithu zake
Mmm..Funso kwa Ras GALAWANDA ..Mwati Yesu ndiye Mulungo yo: Ndiyeno nchifukwa chiyani 'Yesu ku Munda wa Getseman kuja adadzapemphera pemphero yili".
ILAHI ILAHI LAMASABA KATANI ,, MULUNGU WANGA MULUNGU WANGA MWANDISIYIRANJI..Apapano Yesu yo ankapephera kwa Mulungu wake wutiyo.
Komanso pomwe ankanyamuka Yesu kukwera kumwamba iye adawatsanzika wophunzira ake ponena kuti ; NDIKUPITA KWA ATATE WANGA NDIKUKAKUKONZERANI MALO ...kodi atate wake wa yesu yemwe ankamunena apayu anali ndani.?
Inu khulupulirani yomwe mukumudziwayo osati za ma arguiment ambwelera apa
Uyuyu ndi wa chambadi , mpaka mtumiki wao ndi mulungu.
I think mu pange more research on Bobo Ashanti.
Koma Joab ndiwe dolo, nyimbo iliyose umaidziwa
Munthu sungaziwe nyimbo iliyonse..iwee😂
Ndimbambande mamunayu ❤❤
Ndie mukuti tizilima chamba mulimbe.
Awadi ndi chamba , chikhulupiliro chopanda pake ichi
raster iponden fada
Oiv
Chifukwa ngati akuti chiweluzo nkumwamba bwanji tikulangana pansi pompano??😂😂😂😂
Mu chamba muli ntchitooo
Nde yesu anasutapo chamba ?? 🙄🙄🙄 inu ndachambadi heet. 😂😂😂
Misala ndi nthenda ya ku makololo ngati asima, bpp ndi matenda ena ambili
Bwanji zimene iwo anakana azungu mubaibulo ndizomwe akupanga..kumalemela,,ifeyo osatira baibulo nkumagwirila ntchito..
Anati sokoneza mutu
Koma penapake aChakhaza zoona mungalephere kufufa zamatathauzo a makaka owowo omwe akuzungulira I mean red, black, green and yellow, inu basi busy kufusa have u killed chicken before?
🤣🤣🤣🤣
Munthu sukumbuka kapena kuganuza zonse atleast watiimilira 😊
This is stupid to be honest they praise Ethiopian president
Ena chamba chimawapasa nzelu ena ayi uyu chinamupweteka uyu
A Chakhaza panopo tili mu stage of Kingdom, we have three stages, stage of Law, stage of Grace and stage of Kingdom. Ma Raster akunama the second incarnation God now is in China not what what he is talking. Jahena is there, the new Jarusalem is there
Koma MA Rast eeeeeeee zamba zimapweteka hvy 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Christianity is a propaganda
*nde mukufuna kundiwuza kuti nthaw ija Yesu anali m'manda for 3 days Dziko linakhara lopanda Mulungu??*
*Chambadi sichabwino🤣🤣🙌*
Bible ndi nsete...