We don't want politics of killing Malawians just because they support other parties not MCP. We want all Malawians to develop our country together. Mulungu alange adani a chitukuko,onse amene akuba ndalama za boma ambuye muchite nayo kwakukulukulu.Anthuwa aba kwambiri. Our hope is in UTM.
Point of collection asisi SKC sakuyang'anila moyo wanu..even family yake alibe mphavu mu Dimension yomwe ali kut he can able to protect them..ndi wakufa ali ku Dziko la akufa.. Jesus Christ yemwe anaigonjesa imfa ndiyemwe akukutetezani
Komatu muziona Kaye nkhani zokopera anthu.Let us moan our beloved late SKC and remember him in prayers. But if you make his name as a road to campaign, you failing yourself.
Trust me, if this woman was still a minister she could have been supporting usi. These are politicians. Michael Usi is Malawi first that’s what every Malawian needs.
Kweni.... ukhale pomwepo pa u secretary general. Apa a utm akulimba mtima... Uziyankhula kawiri kawiri... Believe me you. Usi... He will never come to utm. sazabwelako
Ase remember chilima atamutenga peter ngt running mate anthu amkat alibe molaro then how sudden he changed to be a strong politian ,kabambe ndi candidate wabwino ase
Mr usi should know where he belongs if he keeps on being used by a certain party,he is lost, dead and buried, sorting out UTM matters through media that's childish, Mr usi talk to madam SG. Otherwise you will not finish what u have started
It is very amazing to see Usi going around in markets pretending to be intelligent and more close to the people. I have the following questions 1. Where was he when SKC was alive . Why couldn't he go around the market and buy bananas Manda's etc . Why couldn't he make misonkhano ya UTM that time while SkC was a live. When SKC died he was no where to be seen neither call the people for comfort. Generally we have no hoe in him.
We don't want politics of killing Malawians just because they support other parties not MCP. We want all Malawians to develop our country together. Mulungu alange adani a chitukuko,onse amene akuba ndalama za boma ambuye muchite nayo kwakukulukulu.Anthuwa aba kwambiri. Our hope is in UTM.
wakufa samva sayankhula mwatani Kodi Pangani za sogolo
UTM MOTO & LOVE kuti bhU For EVER WE ARE GROWING.KUNO SITIPHANAAA
Manganya unangowona kuziyamba and ndiwe mwana mundale,akutsukuluza akweni ndipo sunati unya.
Mumatha mama. I salute you
Zoonadi a kweni a Chakwera anaputa nkhondo imene sangawine
*Maso patsogolo mulungu simunthu ❤❤❤❤*
Yomweyo Akweni !!!!!!!!!
Kaliati ndi machine
Manganya sanali wandale anangomtola penapake ndie sangakwanitse kuyendetsa chipani and ameneyo Siwa utm
K🎉🎉🎉koma kaliat ndi katundu
Just believe in God . Musiyeni wakufayo palibe chomwe angakuthandizeni. Nde or mutakagona pamthumbila wake kwazaka zaka . Is dead is dead.
Ndipo wakufa sadziwa kanthu...komanso palibe chomwe angachitire anthu amoyo monga mwa malemba.
UTM FOR LIFE ❤
Akweni more fire 🔥 ❤❤❤
Kaliati ndi a katundu si munthu womba....Kabambe nkungoyamba kukubwera zambiri....musaope mesa nanuso kukubwera anthu anuso??? Kabambe ndi cream....
❤❤❤ Akweni zabwino zose
Regardless of the constitution of UTM but his actions are for MCP. Am not a lawyer but my analysis tells me that Usi is for MCP not UTM.
Ulemu wanu Mai mkulu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
UTM moto 🔥🔥🔥
Point of collection asisi SKC sakuyang'anila moyo wanu..even family yake alibe mphavu mu Dimension yomwe ali kut he can able to protect them..ndi wakufa ali ku Dziko la akufa..
Jesus Christ yemwe anaigonjesa imfa ndiyemwe akukutetezani
Koma ndipo
Kabambe his capable &fine
Manganya banchala kkkkkk uziona umayenda mbali masewero😂
Koma please Ngati mukudziwa Kuti ndale zakanika ,tiyeni tivomereze , zikuwonetsa Kuti zipani zonse zosusa ,Palibe chipani chomwe chili NDI maziko woti chikhoza kuchosa mbamva Za MCP
Komatu muziona Kaye nkhani zokopera anthu.Let us moan our beloved late SKC and remember him in prayers. But if you make his name as a road to campaign, you failing yourself.
Man this lady is matured she knows what she is doing
Ma concerned citizen letter writers awa
Pepani anapamtumbo a MCP. Kanyereni
Mcp manyi okhaokha
@@chesterkumwenda Uli ndi nzeru zambiri
This is the journey to destroyed utm
More fire mai guru❤❤
UTM boma. Kabambe boma. You have my vote. Usi kanyere uko=kagwere uko.
Adzipha okha asiyeni Mulungu awakanthe achina chikangawa amenewa
Trust me, if this woman was still a minister she could have been supporting usi. These are politicians.
Michael Usi is Malawi first that’s what every Malawian needs.
Kaliyati akanapanga resign she's utm bones
maganya wangoona ataziyamba
More fire
Mwadzipha kale nokha mai
Ifeyo ndi UTM basi welcome DK
Ause mutendere Dr saulos chilima
Utm my vote
Kweni 💪 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Sitizakuyiwaran chimwene paka muyaya
Amen
50+1 😂iteketsa anthu DPP musasunthikike chipan sipa media ai koma maboma Onse chikhalemo ndekut ndichipani Chen chen
Koma musatenge munthu wochokela Ku MCP Ayi akuonongelani chipani
Kod ku magochi awina a utm kod
Ndiye mwati samakuonani kogula chinangwa eti kkkkkk wamva ameneyo ndiwamkulu
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😂😂😂UTM my vote
Koma kumeneko😂😂😂😂😂
A VP mwava kt munathawa Nd nthiko wa ndio km kwen iweo #1 palbeso aphuzitsen ndale a VP
Kkkkkkk
UTM ❤ mbambande 🔥🔥🔥
Akwen more fare Manganya aziwaso
zachamba basi mwasowa chonena inu simungawine zitavuta zitatani mwachepa
UTM yomweyo tili nganganga
Komatu kweni amabwata.....🙌
😂😂😂😂😂😂amabwatatu ngati nyemba zogonera 😂😂😂
Kugawikana patatu kokhako mwapangitsa kulowesa minyama chipani tikuonerani
Mbeu ya chilima yayamba kubeleka zipaso
Yomweyo galu iwe, usampase ndi mpasa
Mai kaliyati 🔥🔥🔥
Manganya ndiwadyela chitsilu
I get fredokiss
Machine
Usi musamuumilire mulekeni apange zache za dramazo akuchedwesani
Utm woyeee
Apapa UTM yatha, ngati pali mwiniwake Chilima ma MP 4 nanga apaaaaaaaa
Kafuseni kumangochj mudziwa chomwechidameta nkhanga mpala
Iyi si nkhani palinso Zoti maganizo anu ndiotani si debate iyi. Osapotoza zinthu. Inu maganizo anu mukhonza kuikapo ngati mulinawo
Chinkazi chooneka ngat chigagalala iwe
Awa akulira ndi mtima chipani chikutha ichi, musamangowombera manja zili zonse
The end
Mukuthetsa ndinu???
@@AngelinaMzowa Just wait and see...
Akweni machine
Kweni.... ukhale pomwepo pa u secretary general. Apa a utm akulimba mtima...
Uziyankhula kawiri kawiri... Believe me you. Usi... He will never come to utm. sazabwelako
😂😂😂😂 nkhani yavuta ndi yamtiko
Koma kweni sazatheka😂 kuyipasa mototo kumeneko,iwe ndimakina
Wallocome
Akweni amudya manganya😂😂😂😂
Ma by election mungokhalira kuluza zachisoni kulakhula kosakopa anthu
UTM yatha yatenga munthu yemwe alibe molaro. Kabambe satithandiza loko pang'ono ku UTM
Ase remember chilima atamutenga peter ngt running mate anthu amkat alibe molaro then how sudden he changed to be a strong politian ,kabambe ndi candidate wabwino ase
Kwaterera 😂😂😂😂😂😂😂😂 mcp yili m'madzi
Kaliati ndi Cynthia lofiloko katundu madzi
Utm bas
Utm hoyeeeee. Chakwela mulibe vot koma mpata wokhala kundende ulipo 😂😂😂😂
Kkkkkkk politics woyenda ndi mtiko ndi bachalala
Akweni ñdi dhilu kkkkkk
Yomweyo UTM
❤❤
Akuti ena pamene akugula chinangwa m'misika ife tili pa ground 🤣🤣🤣🤣
Anthu akubailana awa😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
Inu inu mmmmmmm
Kutha Kwa chipani ngat katani
Uyu wadya ndalama asakupusitseni wagulitsa chipani chija kwa a DDP
Hule wa zipani...apa ulendo wa ku DPP wapsa kaliat ukanakula lija ndi kale
Mr usi should know where he belongs if he keeps on being used by a certain party,he is lost, dead and buried, sorting out UTM matters through media that's childish, Mr usi talk to madam SG. Otherwise you will not finish what u have started
Continue uplifting the party UTM leaders so that the spirit of SKC should rest in peace
😢
Eeeeeeee koma MCP eeeeeeeee ai ndithu Kaya anthu munaganiza bwanji kuvotera okuphawa mmmmm
Kuipa kwakaliyati kumkabisika ndi chilima pano kuipa mtima kwawo mwayamba kuoneka
Utm yatha basi
UTM pano yalowa dyela chimene mukufuna ndichani Chakwela ana kulemekeza kutenga a Usi pano simukukondwela eeeee guys polani Moto
Analemekeza ndani usi anapangak liti za utm?? Anadzilemekeza okha pomusakha kt akhale go between wao not zomwe ukunenazo
Utm bomaa 2025
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Akweni ndi mkani
It is very amazing to see Usi going around in markets pretending to be intelligent and more close to the people.
I have the following questions
1. Where was he when SKC was alive . Why couldn't he go around the market and buy bananas Manda's etc .
Why couldn't he make misonkhano ya UTM that time while SkC was a live.
When SKC died he was no where to be seen neither call the people for comfort. Generally we have no hoe in him.