Ayankhula za Mai Joyce Banda mosabisa mau or kumuopa zoti anali mtsogoleri wadziko

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 72

  • @ZikhonaPantshwa-qs6jn
    @ZikhonaPantshwa-qs6jn 7 วันที่ผ่านมา +5

    Keep it up brother from Capetown

  • @EmmaEmma-q4u
    @EmmaEmma-q4u 4 วันที่ผ่านมา +6

    Amayi awa ayi muli boza ndipo ndi ampeni kumphasa

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 3 วันที่ผ่านมา +3

    Brother saro mukunena zoona mayi Ameneyo ndi oipa satanic walemera lemera and zomwe anenazo ndi kuthedwa mzeru chifukwa amalawi awasiya pa mbala Banda afuna awoneke ngati amzeru ajoice Banda a kondwani nankhumwa mwendo wawo umodzi uli ku MCP

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 4 วันที่ผ่านมา +3

    Atupele adalephela mp ku balaka
    Upresident sangauthe

  • @jacquelinecunningham363
    @jacquelinecunningham363 4 วันที่ผ่านมา +2

    Welll said brother very true 👏👏🔥🔥💯

  • @hermeschapola3583
    @hermeschapola3583 3 วันที่ผ่านมา +2

    Chilima yekhayo musiye CHITSILU iwe

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 7 วันที่ผ่านมา +3

    Ma hule ose aku malawi president wao ndi Joyce Banda

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 4 วันที่ผ่านมา +1

    Malawi is no longer at comfort.We have many misleaders in religions and politics.May God intervene !

  • @Royhauya-uw2kr
    @Royhauya-uw2kr 4 วันที่ผ่านมา +1

    If she had listened to the people Joyce Banda had listened before the elections against mutharika she would be here now

  • @MasterChilangiza
    @MasterChilangiza 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ben longweyo ndiye ukulakwitsa kumawa nyoza ase amene tikumvera nkhani zambili ndikwa Ben longweyo iweyo sumatha

  • @SmithBlessco-v8t
    @SmithBlessco-v8t 2 วันที่ผ่านมา

    Zoona brother

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 4 วันที่ผ่านมา +1

    Take it or leave it
    It's true brother sallo

  • @JoshuaXambo-oc8yq
    @JoshuaXambo-oc8yq วันที่ผ่านมา

    Nkozi Nanu muzipita direct pa zifundo

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma วันที่ผ่านมา

    Zoona zake mau

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 3 วันที่ผ่านมา +1

    Zoona Atupere mulibe utsogoleri,,,Mai Joyce ndi a kuwiri kuwiri

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 วันที่ผ่านมา

    ALUFUNA KUTI MUDZAPESE MCP MAVOTI AKUWONEKA NGATI SALI KU MCP KOMA DZIWANI AFTER KUVOTA MAVOTI JOYISI BANDA ADZAPATSA CHAKWERA SAMALANI NDI JOYISI BANDA

  • @NobuhleHlabati
    @NobuhleHlabati 3 วันที่ผ่านมา +1

    Takuziwani inuo ndi Adppp

  • @HajjAmadu-e1u
    @HajjAmadu-e1u วันที่ผ่านมา

    Kodi bon kalindo atangoti aimire u pre anthu angamuvotere

  • @ZakariasintidomathengaMathenga
    @ZakariasintidomathengaMathenga 4 วันที่ผ่านมา +2

    It's true story

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 วันที่ผ่านมา +1

    Kusowa zochita kumangokhala kunamiza anthu

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 5 วันที่ผ่านมา +1

    Mai Joyce Banda akulamulira anali woipa kwa a malawi..amazunza ma civil servants ndipo ife ma civil servants tinawapangira m demo kuti achoke ndipo afe !@ ife ma civil servants tinawaika mu coffiñ ndimaluwa .ife nkumaimba nyimbo yolira kutì amai wa akutizunza iÿeyu ndi mfiti kwambiri ndipo mulungu mdzina la Ambuye Yesu Mnkhrustù anaĺephera zisankĥo .!! Aaah akagwère ku gehena

    • @vitujames53
      @vitujames53 4 วันที่ผ่านมา

      Komatu mukulankhula za bodzatu...Malawi yake yomweyi anazunza ma civil servant???? Ndale zikukupengesanitu.
      Munene zina mwina mumawada osati mwanenazo

    • @mwale86
      @mwale86 4 วันที่ผ่านมา

      Mmmm abodza inu mayi Joyce Banda anawonjezela malipilo ma civil servant kawili konse kuzuza kwake kuti kunama basi siinu APA mukhulu inu which Malawi

    • @mwale86
      @mwale86 4 วันที่ผ่านมา

      Ukagwele kugahena ndiwe kuwano akuyamkhulawo nkhope ngati kugehena komweko kkkkkk

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 4 วันที่ผ่านมา +1

    Bro mukamba zoona atupele ndi odontha

  • @McfirozMcAdam
    @McfirozMcAdam 3 วันที่ผ่านมา +1

    Wabwino ndiiweyo ndi banja lako

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 7 วันที่ผ่านมา +1

    As a country let's do away with family political dynasties .

  • @Friday-o4u
    @Friday-o4u 2 วันที่ผ่านมา

    Usatanic muwauze mai joyce kt amalawi panopa ndiochenjela sakusatila zilizonse km sikulina muzamuthawa malawi amalawi atatopa nanu

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 2 วันที่ผ่านมา

    Eya zoona

  • @ChimwemweNicholas
    @ChimwemweNicholas 4 วันที่ผ่านมา +1

    Machine ako aye

  • @kingslygwedezamajor6780
    @kingslygwedezamajor6780 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ya achilima uyisiye wamva usatchukire pa iye chifukwa anaphedwa wamva,???

  • @AnnastanziaMhango
    @AnnastanziaMhango 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiwe osokoneza poti wati ndi maganizo ako koma palibe chomwe wanena iweso ndiwe wonyasaso kwambiri ulibe khalidwe

  • @RobertCosmas-bo1uo
    @RobertCosmas-bo1uo วันที่ผ่านมา

    Chitsiru iwe wa DPP

  • @NobuhleHlabati
    @NobuhleHlabati 3 วันที่ผ่านมา

    Ajoce bada asowe

  • @GiftJulius-ro9ev
    @GiftJulius-ro9ev 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Galu lwe ndi gogo wa dpp

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 3 วันที่ผ่านมา

    Ndiye poti amalawi timafuna tione Kaye zoopsyazo

  • @FarookYahaya
    @FarookYahaya 2 วันที่ผ่านมา

    Zoona mayi uyu ndi mbuzi

  • @JamalTambula
    @JamalTambula 3 วันที่ผ่านมา

    Musamathe mau pa Joyce Banda muzitha mau kwa chakwera Joyce Banda apepese chifukwa chani osanyoza Joyce wathuyo

  • @ChrissyPhiri-q8b
    @ChrissyPhiri-q8b 2 วันที่ผ่านมา

    Mai JB ndi akuba adatibera ndalama chakachatha potinamiza kuti atipatsa ngongole dziko lonse lamalawi adazungulira kutolera ndalama mpaka kutitsekulitsa ma account up to now kuli ziiiiiiii tikuchita kusowa kokafunsa voti asaione

  • @phindiswatshibo7101
    @phindiswatshibo7101 8 วันที่ผ่านมา +2

    😂😂😂😂😂 komaditu

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 7 วันที่ผ่านมา +2

    Chilimayonso ndi amene anabweretsa mavuto omwe amalawi akulira lero lino koma amalawi sakuona zimenezi ndipo timamulilabe ngati mmalawi zathu koma tikudzi kuti anatisiyila mavuto ndiye plz mulekeni atupele muluzi

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano 3 วันที่ผ่านมา

    Mayi awa Malawi akuthandizila Kuti tizivutika kufika pomwe tilipa kuvutikaku chifukwa chamayi ameneyi ndimuuza JB awathile ma phuzo

  • @McfirozMcAdam
    @McfirozMcAdam 3 วันที่ผ่านมา

    Wabwino ndiiweyo

  • @hermeschapola3583
    @hermeschapola3583 3 วันที่ผ่านมา

    Ukawawuze agogo ako ZOPUSA zako ukamaGalu

  • @user-wi8xw9qh7n
    @user-wi8xw9qh7n 7 วันที่ผ่านมา +1

    Joyce banda upepese ndithu

    • @Blessings31
      @Blessings31 4 วันที่ผ่านมา

      Apepese kwa iweyo ngati ndani galu iwe

    • @mwale86
      @mwale86 4 วันที่ผ่านมา

      Za ziiii apepese kwa iweyo aaah koma anthu ndinu osekesa

  • @MedayiMtambo
    @MedayiMtambo 3 วันที่ผ่านมา

    Kaya ndioipa kaya ndiotani akunena zoona, wayenda nawo ndipo waona kuti ndioipa ndiye asanene ,Atupele yenkha ndiye ai ndizoona alibe ulamuliro,

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs 4 วันที่ผ่านมา

    Palibe chanzeru chimene ukukamba apa za nzeru ndizokhazo za ma bridge zo

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 วันที่ผ่านมา

    Wangokhala ndi udani ndi Mama JB...ulibe manyazi kunyoza kumeneko ngati sunabadwe ndi mzimayi.
    Munthu womvesa chisoni iwe

    • @Friday-o4u
      @Friday-o4u 2 วันที่ผ่านมา

      Nanu achisilu mukukambait

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 4 วันที่ผ่านมา

    Kulibeko mp komwe kulibe ma bridge ko

  • @CyprianoSandalamu
    @CyprianoSandalamu 5 วันที่ผ่านมา

    Ndizoonadi atupere muluzi simunaganize bwino,ukaoneka wabwino kudziko Lina osapepesa kumwalira Kwa chilima?

  • @PeterMbata-bw2xx
    @PeterMbata-bw2xx 3 วันที่ผ่านมา

    alibe utsogoleli mayi banda

  • @MathewsSande
    @MathewsSande 7 วันที่ผ่านมา

    Julie mavuto Ku Malawi mavuto ali mnyumba mwako chifukwa cha ulesi wako kuzolowera kupmpha

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 3 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi

  • @BrightonStorey
    @BrightonStorey 4 วันที่ผ่านมา

    Zaziiiii

  • @Royhauya-uw2kr
    @Royhauya-uw2kr 4 วันที่ผ่านมา

    Be brief

  • @SimeonAbraham-u2j
    @SimeonAbraham-u2j 4 วันที่ผ่านมา

    Zowona

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 7 วันที่ผ่านมา

    Bambo iyetu amangozuzula ntchitedwe umene ukupitilira kupwanya democracy mu Africa atupele amalankhula ngati mu Africa nzawo kodi umene chilima boni kalindo wakhala akulankhula naye kangati koma mumamumvela boni kalindo chaka chatha analankhula ndi Bryan banda kuti ngati chilima sanganene any statement kufika January chilima is finish ndiye sanathe iye amadziona kuphulazila kwambiri komanso palibe angamuwunze zochita ndiye asalo musiyeni Atupele muluzi ngati mwasowa zochita nanu

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe 5 วันที่ผ่านมา +2

    Ndiwe wa DPP iwe.Ukunamiza ñdani?

  • @mwale86
    @mwale86 4 วันที่ผ่านมา

    Ati ndiyizukute za ziiii asiyeni masten ati ndimangomuswa tinakupempha ife

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma 5 วันที่ผ่านมา +2

    Machende ako kape ndiwe wa dpp

    • @BawulenLuka
      @BawulenLuka 4 วันที่ผ่านมา

      Mapwala ako mr chikangawa

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 วันที่ผ่านมา

    Tapezani zina zochita osamangokhalila kunyoza zinthu zopanda pake...
    Ena akupatsani ndalama kuti mugundike kutukwana that one will not change that Mama JB changed Malawi within 100 days.. Ndimtsogoleri yekhayo anthu ammidzi ali mumtima mwawo

  • @jimapo
    @jimapo 4 วันที่ผ่านมา +1

    Iwe ndiwe chisilu kwabasi

    • @vitujames53
      @vitujames53 4 วันที่ผ่านมา +1

      Wopanda nzeru uyu..

  • @Blessings31
    @Blessings31 4 วันที่ผ่านมา

    Find other things worthy to do other than being busy tarnishing other people's names for the sake of useless views

    • @vitujames53
      @vitujames53 4 วันที่ผ่านมา

      Kupusa kweni kweni...ndipo muzawonesetse amanyoza ali kunja zopusa akupangazi sangapangile ali mdziko muno..kufuna kutamika ndi zinthu zopusa

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 5 วันที่ผ่านมา +1

    iweyo ndi wa DPP galu 😂😂😂😂😂😂😂