Mmene Anthu awa Otchedwa 'OMENYERA UFULU' Amatipusisira a Malawi?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 44

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 8 หลายเดือนก่อน +2

    Kumalawi tilibe omenyela ufulu waanthu ayi, tili ndi ma hippocrates basi anthira kuwiri monga redson munlo, timosi mtambo, ben longwe , gift trampez, just mention a few, ndikutyipa maina awo ndi ma small letters coz dey don't deserve our respect

  • @BashiruBanda-f5j
    @BashiruBanda-f5j 8 หลายเดือนก่อน +3

    Boooni kalindo number one basi palibeso

  • @GEORGE-yr7nx
    @GEORGE-yr7nx 8 หลายเดือนก่อน +2

    Only BONI KALINDO ndiye amayimila amalawi basi

  • @lyiemax
    @lyiemax 8 หลายเดือนก่อน

    Bon kalindo is the only true and trusted activist in Malawi and not manyaka ngati awawa

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 8 หลายเดือนก่อน

    Peter Muthalika called this group, a Terrorism group and now I come to my senses that it was true. A traitor shame on you Mtambo.

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu 8 หลายเดือนก่อน +2

    Kalindo ndiamene amamenyera ufulu amalawi mtambo amkangofuna udindo

  • @Uncle_B265
    @Uncle_B265 8 หลายเดือนก่อน

    I like Bon kalindoo the Bc bola naye asazasitheeee

  • @PromiseKhenzo
    @PromiseKhenzo 8 หลายเดือนก่อน +1

    KU MALAWI KULIBE OMENYERA UFULU🎉😂

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 8 หลายเดือนก่อน

    Uyu ndiamene atiwonongera malawi kwambiri, munthu oipa uyu

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 8 หลายเดือนก่อน

    Ntambo si mmalawi so we all knows about that bwanjiso Pano sakuzuzula MCP pantumbo pake ndithu

  • @georgekchimwaza6838
    @georgekchimwaza6838 8 หลายเดือนก่อน

    Ku Malawi kulibe omenyera ufulu amangofuni kuwonekera patsogoro ngati chilungamo kwinaku matumba awo akukhuta... Tamuoneni manganya anazachuka pa tikufelanji koma pano bwanji mmmmm

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 8 หลายเดือนก่อน +1

    Chitsilu cha munthu Mtambo, galu wachabe chabe.

  • @owenmajoni-d3n
    @owenmajoni-d3n 8 หลายเดือนก่อน

    Bon kalindo ndi wa chipani dpp ndipo nthawi zonse amangokakamiza kuti chakwela atule pansi udindo. Kwa ife anthu timangomuthandiza kupeza zomwe akufuna basi

  • @chisomochavula
    @chisomochavula 8 หลายเดือนก่อน

    Inuyo amene mudzintcha omenyela ufulu mudzidziganizila nokha coz mukupweteketsa anthu

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 8 หลายเดือนก่อน

    Kupusa basi kumakhala ngat omenyera ufulu koma ali achipani,antambowa nde ulemu unatheratu....anthu alibe nawo ntchito

  • @tiunzanenganimunomwaafrican
    @tiunzanenganimunomwaafrican 8 หลายเดือนก่อน +1

    😂 apa aa❤ atipanga tabwa basi 😂my Malawi 🎉 anafa.asala andale wokha.

  • @ladymart-mw723
    @ladymart-mw723 8 หลายเดือนก่อน

    Nice 👍 more more

  • @BenardBanda-d1f
    @BenardBanda-d1f 8 หลายเดือนก่อน

    Kalindo number one

  • @zephasibanda4462
    @zephasibanda4462 8 หลายเดือนก่อน

    Omenyela ufulu amalawi yemwe alipo kumalawi ndi boni kalindo basi palibenso wina kaya enanu mukuona bwanji

  • @StandeyJanafordKandaya
    @StandeyJanafordKandaya 8 หลายเดือนก่อน

    awa a HRDC amafuna zawo ziwayendere afiti.

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 8 หลายเดือนก่อน +1

    Zilimo zakatanngale koma kuyankhula kwake sayankhula ngati kalindo amadana ndi achakwela chifukwa choti anawamana udindo koma awa ankapeleka ulemu kwa mtsogoleli

    • @user-lf8zb4mo1g
      @user-lf8zb4mo1g 8 หลายเดือนก่อน

      Mau mbale wanga ndimene inenso ndimaonera ndi kjmva

  • @DoreenSkova
    @DoreenSkova 8 หลายเดือนก่อน

    Amangofuna aziti namiza kutipepelesa amakhala akuzimenyela khondo okha athuwa

  • @RaphaelHara-tr9iy
    @RaphaelHara-tr9iy 8 หลายเดือนก่อน

    Bora mutambo sanalowe zipani Ngati kalindo anali wa DPP atuluka alowa UTM atuluka chisisi chake anawanama udindo sopano Kuti ndiwomenyera yoooo

  • @charlesmartin6990
    @charlesmartin6990 8 หลายเดือนก่อน +1

    Vuto chifukwa cha u mphawi,they always act pofuna kudzithandiza okha

  • @AidinMponda
    @AidinMponda 8 หลายเดือนก่อน

    Ndikape ameneyo

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 8 หลายเดือนก่อน

    koma yemwe anganyodze kalindo kuti siomenyera Ufulu.ameneyo ndi mfiti komaso ndi mdani wa kalindo ...Why I'm saying that. kalindo wamangidwa 15 times mu ulamuliro wa ch
    mcp.

  • @bashirnanga
    @bashirnanga 8 หลายเดือนก่อน

    Mtambo amapanga zasogolo lake basi

  • @abdullahkazembe6340
    @abdullahkazembe6340 8 หลายเดือนก่อน

    Ntambo wamisala

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i 8 หลายเดือนก่อน

    Mtambo watha ngat makatani😂😂😂 bolaso bon kalindo

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 8 หลายเดือนก่อน

    Panyapako ufuna akunkhendani pantumbopo funsolakolo kafunse amako tchanel chakocholankulazozizila

    • @smokeestery1101
      @smokeestery1101 8 หลายเดือนก่อน

      Iwenso pa mtumbo Pa makoo pa Gazi

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 8 หลายเดือนก่อน

    Bon kalindo ndi amene akumenyera ufulu a dpp chifukwa Ali ndi nkwiyo pot sanamusankhe unduna

    • @DeveliousMasinja
      @DeveliousMasinja 8 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂mwayiwalakale kuti anachita kunena yekha kuti zimamuwawa coz adamanidwa udindo??😂😂

  • @miltonmiltons
    @miltonmiltons 8 หลายเดือนก่อน

    Munadya kageyeni

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 8 หลายเดือนก่อน

    Mtambo chitsilu cha munthu

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery 8 หลายเดือนก่อน

    Tikukuonani

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 หลายเดือนก่อน

    Useless people anthu oipa mxeuii

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 8 หลายเดือนก่อน

    It's possible that he is still receiving his monthly salary who knows what this government is a joke

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 8 หลายเดือนก่อน

    Amtambo anali wanthu imebyeead uffulu akabwela pamseu ananena zifujwa zomwe azipangila mademo not akalindo kunabwe bweta ngati agalu

  • @amosChataika-e8h
    @amosChataika-e8h 8 หลายเดือนก่อน

    You are too slow.