Nyimbo njabwino koma message sili bwino. God is sovereign ndipo amadziwa zonse simungamuuze zochita. Verse 1 mukunena kuti Mulungu sangadziwe mbava ndi ndani ndi bodzatu limelo. Mulungu adzabwela pa tsiku la chifuniro chake komanso amadziwa chilichonse. Komanso, kupulumuka ndi chisomo ndipo Mulungu amadziwa kale zochita za wanthu ndipo mukamachimwa samadabwa nazo ai. Mulungu si size yathu to be used to entertain. Take an example of Skeffa Chimoto or Grace Chinga pa nkhani yopanga compose nyimbo rightly ndi mau a Mulungu.
Yooo this hit is catchyyyy. I will come again mukapanga like comment yangayi😂🎉
This song deserves million views, ndizomwe opembedza ambiri ife tikumachita including leaders and Pastors 🤔🤔🤔🤔
fact,,,vuto amalawi pano tupanga support zinthu zopanda pake,,
Nice song 🎉🙏
What a nice tune, idzikhala pa repeat
Odala amene amawamva mau nkusintha, apa nde tadzudzulidwa .may the lord bless you more
Ijust watched aclip of this song on my friend's status i had to come on utube to watch the full song the is a strong massage in this song..
Same here...I had to watch the whole song
Muli ndi mphatso ya maimbidwe. Yehova akudalitseni achimwene
Nice song ❤ taphuzilamo zambili mulungu azikudalisani siku ndi siku ❤❤❤❤❤
Keep fire burning zikutheka basi
Mulungu apitirize ukudalitsani it is good song
Amen And Amen!
Lets make this song to million views beautiful piece ..
Nyimbo njabwino koma message sili bwino. God is sovereign ndipo amadziwa zonse simungamuuze zochita. Verse 1 mukunena kuti Mulungu sangadziwe mbava ndi ndani ndi bodzatu limelo. Mulungu adzabwela pa tsiku la chifuniro chake komanso amadziwa chilichonse. Komanso, kupulumuka ndi chisomo ndipo Mulungu amadziwa kale zochita za wanthu ndipo mukamachimwa samadabwa nazo ai. Mulungu si size yathu to be used to entertain. Take an example of Skeffa Chimoto or Grace Chinga pa nkhani yopanga compose nyimbo rightly ndi mau a Mulungu.
Powerful
Amen
. Bingu remains a legend.
Indeed campaign imkakoma, ili the warm heart of Malawi.
Zikanamatheka tikanayambiransoooo
Why this songs 🎵 doesn't catch 1m views
Nice song
ok
Munapha ndi amwenu chilima ndikupaka chakwera tiyeni tilimbilane ufumu wa mulungu mateyo 24vs 35
❤❤❤❤❤❤josephy this song l like it ❤❤❤ good work focus brother l hope u sing more nice brother
Ife tili kujon azatipeza tili zitchitotu koma azabwere loweruka ndi sundy kujoni kuno eee mayi koto
Kana musuudzwa kuti munogona vanhu iwawo vane Jerasi
Iyiyi nde mwalalika kwambili timakhala ndichizolowezi Ambuye atinthandize
Listening to this every moment🎉 ❤
I love the Guy composes his songs
Azitumik ambili ndizmene akupanga masiku ano ambuye azikudarisan amwene mulindi luso
😂😂😂😂😂😂Jetu apa ndayamba kuvuna ku tchito jetu andichosesa tchito 😅😅😅😅
Kodi nyimbo imeneyi ukuzembela ndani? Akutuma eti? Akupwetekesatu
I love this song... Imakhala pa repeat
Share
Wabwera ngati coming kuzakhazikika pa nsika
Iyi wayiphulà bas chilungamo chenicheni wanenachi bro
Watching live in capetown pa Boma nice song
Yes mnsansi is playing a pivotal roles on most fate issues on
Wumakwana Zidazamotho❤❤❤
Anagogodatu🎉
Love your songs. Powerful massages. Keep up the good work 💪🏻💪🏻💪🏻💪🏻
Nice song
Akupaseni zelu zochuluka muposele pamenepa😊
Very nice. 👏
I'm Lesotho 🇱🇸 lady but the song is very powerful
Nice warning song
Moto kut buuu
Mupitilize achimwene ndithu ndichoncho
Mikozi akuyenera amudziwe munthuyu ndi dolo ndithu
Why do I like this guy songs .. chilungamo
Amen in the name of God and God bless you with this song
Nyimbo yaphedwa iyii,,, umatha aise
Nice song brz
Zoona brother
I wish you all the best good talent
I like this guy.....
Eish nice song
I love the song ,thank you brother man
Powerful song
Ndayikonda
God knows better even anthu atazibisa
U are blessed brother nice song
Powerful song
Wawoo amen end amen nyimbo yabwino kwambiri 🙏
What a nice song 🔥🔥 wow on repeat
Nice gospel song with touching message ❤️
You have done much continue sister
Kodi inayimba ndiwe nice song🔥🥰
Meaningful song
Excellent hit. Keep it up. I have liked the sing
Mmm zopanda mbali mumath boss
There is talent in this guy....
Powerful message amen
Wow powerful song
Chilungamo chokha chokha 😢
Why do you ask that question
Mumakwana koma eeeeeee my favorite songs ❤️🤩💕
Iyi ndi more yaposa ya chiovololo umainena ija😂😂
Beautiful song
Kachilungamotu 😅
Beautiful song🙏
Akuluawawa ndikuwapatsa ulemu
nkhaniyi ili mu black n white
Ndipo wangoti khaaaa!😂😂😂
Yilibwino love it❤❤❤❤❤
Iyiyi munayipha ❤❤❤❤❤❤
Uthenga okwanila timanamadi
Ili bwino kwambiri nyimboyi
Upitilize braz ukubwera
Asazabweledi Sunday
Very nice one
Nice song
Katundu wapsya bwino uyu
Splindeed song
Ma umboni onama achulukila
Sound iyii unaswaa ❤❤❤❤
Oyimba uyu adakoza kkk
I like the song
Good one
What a nice song!❤
A touching song❤
Nice song ❤❤
Masterclass 🔥🔥🔥🔥
Amen amen amen ❤❤
Nice song
Ndaikonda et
Koma ndizoona mmh
This is a very nice song.