A twaib,pa zimenezi nde mwataika kwambiri chifukwa sizigwirizana nlemba,za utatu zoona mbible mulibemo,za sunday ndi sabata simungazipuruve nlemba komanso us elen white nza bodza
Abusa mukutanthauzira bwino koma pari mpingo ina yomwe imangopempera koma chowonadi chatsikuri sakuridziwa komaso za isiter kodi simungapita ndikuwadziwitsa zambiri zotere chonde monga kwa azathu omwe amapembedza Sunday
Nchifukwa chake mulungu anawauza ana a Israel kupereka hipatso zoyamba kucha pa tsiku loyamba la sabata lomweli nsunday chifukwa khristu ndi woyamba kuuka kwa lomweli linali tsiku loyamba la sabata
Abuse atwaibu mmatiyimila wosatopa amen
Ndipo amene Ali ndi tsoka anga mbulimutsidwe bwanji a bwaibu
Amen
A twaib,pa zimenezi nde mwataika kwambiri chifukwa sizigwirizana nlemba,za utatu zoona mbible mulibemo,za sunday ndi sabata simungazipuruve nlemba komanso us elen white nza bodza
Following
Uthenga ozama abusa Amen
Iwe ndiwe mwana wa mulungu nsembe yako unapha ndani taululula chilun gamo
Abusa mukutanthauzira bwino koma pari mpingo ina yomwe imangopempera koma chowonadi chatsikuri sakuridziwa komaso za isiter kodi simungapita ndikuwadziwitsa zambiri zotere chonde monga kwa azathu omwe amapembedza Sunday
Palibe yemwe angachite ndendende monga Israel nkukhalanso akulondola chifukwa anachita zonse mwa zithunzi ndipo yesu anati,nthawi ikuza ndipo ilipo kuti opembeza adzampembeza mulungu mu mzimu ndi mchoonadi kotero kuti ifenso lero tikuchita zonse anachita Israeli koma mu uzimu.
Mau oti sabata ndi chiheburi kutanhauza mpumulo ndipo ahebri ,4 amanena kuti omwe anakhulupirira khrostu analowa mpumulowo, zoona tsiku kumenelo anthu amapembeza dzuwa,komanso khristu anauka tsiku lomweli ndipo ophunzira anayamba kupembeza tsiku la Sunday koma ophunzira anayamba kupembeza limeneli chifukwa ndi sonday osati sunday