HOT CURRENT LIVE PA TIMES 360 - ANG’ALULI AJAMA ZA LIPOTI YA DR SAULOS CHILIMA PLANE CRASH

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 129

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 3 วันที่ผ่านมา +21

    The truth is that this report is totally nonsense.Time will come for God to judge

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 3 วันที่ผ่านมา

      Zizungu pwilikiti ngt akuuza Joe Biden

    • @TonyMhone
      @TonyMhone 3 วันที่ผ่านมา +2

      Nonsense and stupid report indeed. Even Kwa munthu wosaohunzira yemwe akuona nonsense!!!

  • @GiftMlinde
    @GiftMlinde 3 วันที่ผ่านมา +8

    Ndipo I'm the 1st one, this is man made!!

    • @MarckChisomo
      @MarckChisomo 3 วันที่ผ่านมา +1

      Bad people will not agree once there's truth, you failed to produce envedence now you disagree with this report why,

  • @RennieChalamwendo
    @RennieChalamwendo 3 วันที่ผ่านมา +7

    Only God knows the truth, let God be God one day is one day

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 3 วันที่ผ่านมา +5

    Apa palibe report anangotaya nthawi. Mukaona report la German ndi report la equiry ndi ma report aboma ndi aderss ya chakwera pa ifa ya chilima zose zikuveka mosiyana kusonyeza chilima akuoneka anachita kuphedwa.
    Ngati amalawi tikufuna kuziwa za ifa ya chilima. Titenge chakwera ,usi ndi nduna zake zipite kwa mutumiki wa Mulungu yasini gama ose akalumbire ngati sanatengepo gawo akabera ndi moyo koma ngati anachita adzafa or adzapenga misala.

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 3 วันที่ผ่านมา +3

    Ndikhulupilira kuti inu a times ndinu momwe mnaneza zoti Mr chimwendo anakuuzani zoti ndege was full ndipo samayenera kukwera awo ndege yo so l hope kuti funso limeneli lili ndi yankho lake mu commission of inquiry imeneyi

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 3 วันที่ผ่านมา +4

    Jona amangokwera yomwe ili pa ground ndipo amafuna azitsata zomwe anzakewo akunena pomwe akuonekelatu kuti mtima wake ukuti anthuwa anachita kuwapha 😢 zachisoni momwe mwalankhulira lero on this lovely program ndipo l wish akanakhalapo a Brain Banda ndi ankolo John Kapito bwenzi patakoma apo aaa 😂😂 anyway only God knows and time will tell RIP Saulos Chilima and 8 people 😢💔

    • @SaidSamuden
      @SaidSamuden 3 วันที่ผ่านมา

      Awa alandililatu zawo anganene kuti mayakho apezeka pati muli serious koma bwanji mukanangokhala osapanga program

    • @EnockMvula
      @EnockMvula 3 วันที่ผ่านมา

      zowona

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 3 วันที่ผ่านมา +3

    Palibe what if apa mnthu sunganene kuti ndege inali yozaza ndipo ndinabwera from chimwendo Banda zimenedzo zapangidwa clarify??

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 3 วันที่ผ่านมา +4

    You can say anything you want to say you gentlemen, but truth is that malawians are watching truth shall be revealed, you are trying to shield these notorious evil people

  • @nkhomahhappy2826
    @nkhomahhappy2826 3 วันที่ผ่านมา +2

    God was there,,, he knows the truth!!!

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala 3 วันที่ผ่านมา +4

    Chilungamo chidzadziwika tsiku likubwela osadanda

  • @JeremiahChilenje
    @JeremiahChilenje วันที่ผ่านมา

    Mozi waiwo ndine,,,ndege yanji yovura jombo kapena zovara

  • @AviaAnalia
    @AviaAnalia 2 วันที่ผ่านมา +1

    Lipoti liyenera lizatuluke after election inshaallah

  • @DavidChapalala-k8o
    @DavidChapalala-k8o 3 วันที่ผ่านมา +1

    Osachulusa nkhani kt anthu mwaiwalise zomwe akufuna kudziwa
    Kodi mavuto monga
    (1) Nyengo yachifunga
    (2) Oyendesa ndege sanafuse
    (3) Oyendesa ndege anali ndi expires licence
    Mwazinthu ngat zitatuzi ndizimene zinapangisa kuti
    (1) Apulezidenti achedwese kutumiza anthu kuyamba kufufuza komwe kunagwera ndege ?
    (2) Apulezidenti ayimitse kufufuza komwe kunagwera ndege ?
    (3) Apulezidenti anamize mtundu wamalawi kt ndege inakafika ku mzuzu kenako ndikubwerera?
    (4) Ngat Apulezidenti anachita kuuzidwa uthenga wabodza woti ndege inakafika ku mzuzu , bwanji sanalange kapena kubweresa poyera wabodzayo kt mtundu wamalawi ukhulupirire zot wabodza siwowo?

  • @charleschij524
    @charleschij524 3 วันที่ผ่านมา +2

    Only God knows

  • @innocentkapachika6591
    @innocentkapachika6591 3 วันที่ผ่านมา +1

    Bayana, is a far spent force . No near to be a reliable person. He has been a hand clappeer ever since

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo 3 วันที่ผ่านมา

      Chitsiru chunga stupit fools

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ngati mukuopa kumangidwa mudakangosiya osayanjgulapo Kanthu Za report limeneri a times inu

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 3 วันที่ผ่านมา +2

    There is no what if Bwana.
    President osadziwa za Vice President kuti wabwera mu dziko really???????????

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mr ndevu zamwayi lelotu simukuyi tokota kwambili ya ndege mwadya chibazi 😂

  • @FidesChandama
    @FidesChandama 3 วันที่ผ่านมา +3

    Ndingoyankhapo posabwela kuzapangila umboni munthu amene akuziwa utangoti upite kukapangila umboni boma lake LA mcp likusowetsa tingodikila mulungu adzatipatsa zowona zeni zeni za ngozi imeneyi

  • @aitoniechandiyangana5421
    @aitoniechandiyangana5421 3 วันที่ผ่านมา +4

    Unfortunately, the dead do not talk...

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 3 วันที่ผ่านมา

      Very true...tikanati atiyankhure

  • @PreciousSoko-u6k
    @PreciousSoko-u6k 3 วันที่ผ่านมา +2

    Anthu timakanika kukhulupilira mulungu, ndiye sizodabwitsa kusakhulupilira anthu

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 3 วันที่ผ่านมา +1

    Air crash investigation minus flight recorders and blackbox data ...work half done....Tchutchu wankhaniyi ali mmagadgets amenewa.

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 3 วันที่ผ่านมา +3

    Sadamufunse komwe Kuli black box??

  • @PHILLIPMmwenye
    @PHILLIPMmwenye 3 วันที่ผ่านมา +7

    Koma chilima anachita kumupha ndi anthu ena onse 8 aaaaa sichifukwa cha nyengo ayiii bodza

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 3 วันที่ผ่านมา +2

    Inu amapha Ng'ombe zimenedzo dziko lake si ili lopanga munenadzo Chikangawa ngooosyatu

  • @ZaccariaPhiri
    @ZaccariaPhiri 3 วันที่ผ่านมา +1

    Sizoona kuti VP angafike mdziko muno kuchokera kunja kwa Malawi , ndi kunyamuka kumapita ku maliro a bwana ake osadziwa kuti vp wanga wafika kuchokera kuja ndinamutumaku.

  • @AbsalomKambova
    @AbsalomKambova 3 วันที่ผ่านมา +3

    Inu anchita kuphedwa awa

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 3 วันที่ผ่านมา +1

    Zonse zinali zopangana chilima anachita kuphedwa musaiwale Kuti ndi MCP

  • @LuciusKhudze
    @LuciusKhudze 3 วันที่ผ่านมา

    Komatu tiganizeponso palinkhani ya Mayi Kaliate ndi Angella . Mukawonetsetsa a Chilima sanatsate dongosolo limene GOLD papa anawauza. Coz nthawi zonse munthu akasemphetsa zizimba chinachake choopsya chimachitika , ngati kupenga misala kapena kufa basi. So kuti anthu enawo avomereze ndekuti a BOMA pangani changu nkhani ya Mayi Kaliyati. Akakhala Angella ndiwokonzeka kukapeleka UMBONI pa court.😢😢

  • @SiceloNgiba
    @SiceloNgiba 2 วันที่ผ่านมา

    Inuso musakhale mbali ya okuphawotu ndikukudabwani mukubakila a president

  • @charlesjimu6054
    @charlesjimu6054 2 วันที่ผ่านมา

    It is not possible for the president didn't know the arrival of the vice president, he was the one who assigned him to wherever he went

  • @kenmasta
    @kenmasta 3 วันที่ผ่านมา +1

    They will repay

  • @JoiceNkhoma-s1m
    @JoiceNkhoma-s1m 2 วันที่ผ่านมา

    Lero mwayakhura ngati ku interviekoo mwadyako ndazi coz mukananena kuti amalawi mafunso amafuna live kuti tixiyimba nkufunsa plus azodiak on dat day anayakhuramna ndi mzibambo yemwe ati anayetsetsakuimbira anthu kodi amene uja anamuitana?? Nanga anthu anawatchura iyeyo aja anaitana kuti azayakhe kuti amazengerezeranji??

  • @tvprospernews
    @tvprospernews วันที่ผ่านมา

    Komatu nkhaniyi ikuloza ku chinthu chimodzi or titazungulira motani, the way anthuwa anafera is not normal something happened and someone took part. Koma nthawi ikubwera chobisika chidzaululika,and those who took part pa imfayi will pay, anaononga miyoyo komanso kutionongera ndege.

  • @InnocentBanda-ze8de
    @InnocentBanda-ze8de 2 วันที่ผ่านมา

    Mwayakhura Mpwara mpwara mpwara 😮

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 3 วันที่ผ่านมา

    Kodi chifukwachani chimwendo sanafusidwe kuti anamulesa ndani kukwela ndege
    1 anawavula tai achilima ndani
    2 anatenda ma phone ndindani
    3 zovala zachipima anawavula ndani
    4 black box kunkuyu anati ilipo
    Ndizambili zofuda koma sitingakwanise

  • @PRECIOUSKK-c9j
    @PRECIOUSKK-c9j 3 วันที่ผ่านมา

    This report is so .... Is it possible the Vic president kubwela kuchokela kunja president mkukhala osaziwa mmmm ayi report iyiilingati thaw ya Bingu timkati wafika ndege azikwelamo yekha ,kutabwela Joyce anango oky kugulisa

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu 3 วันที่ผ่านมา +1

    Chifunga sichigwetsa ndege musanamizidwe adachita kuphedwa?

  • @catherinekadwala3839
    @catherinekadwala3839 2 วันที่ผ่านมา

    Ngat mwadya banzi nanu ingokhalani chete

  • @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb
    @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb 3 วันที่ผ่านมา

    Kodi ikadakhala kuti ikupita ku nkhondo akanayang'ana ma license adani akumwera ? Osasokoneza ku usilikari kulibe zimenezo

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani 2 วันที่ผ่านมา

    Simunapemphere, mchifukwa chake mwangobvinyabvinya😂😂😂😂

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 3 วันที่ผ่านมา

    Kodi nanga k5000000 imene anatenga a Chilima yokapepesa ngati pamalopa pamalopa sipanafike aliyense ndege itapanga ngozi inayenda bwanji?

  • @KenKananji-v7h
    @KenKananji-v7h 2 วันที่ผ่านมา

    Apa nde zikupweteka mtima kusiyana mpoyamba coz a chitetezo Nthawi zambiri even pa ngozi ya galimoto ndalama za anthu sizimapezeka. Ma galimoto ambiri amoyenda popanda zoloredza kod malamulo mmagwiritsa ntchito ndi adziko liti? Tilibe chitetedzo cha chilungamo.

  • @Kira-r3z9k
    @Kira-r3z9k วันที่ผ่านมา

    Kodi ndekuti license yanga ya galimoto ikapanga expire ndekuti experience yanga yoyendesa galimoto yathanso?!?
    This report aaaaaah only God knows

  • @chifundokumbali-nv7fz
    @chifundokumbali-nv7fz 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    I still don't believe of ngozo

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 3 วันที่ผ่านมา

    U can see himself he hiding something and knows truth

  • @GoodMindozo
    @GoodMindozo 3 วันที่ผ่านมา

    Izo ndo zithu zoyesana iwo anazikoza kale

  • @GraceMwase
    @GraceMwase 3 วันที่ผ่านมา

    You guys mumatiimilira ndipo ndimakunyadilani koma ya ndege yokhayi isiyeni mungadzachite manyazi pamawa chifukwa chilungamo chenicheni chizadziwika tsiku lina. Iyiyi nobody can convince me otherwise it was man made. Diso la Yehova lungoyang'ana

  • @ManzyNgoleka
    @ManzyNgoleka 2 วันที่ผ่านมา

    Even inuyo nonse pamenepo kupatura andevu zamwayi mukulankhura moopa komso mwandale mwa mantha mantha choncho kuonesa kuti boma lilipori ma solution awo ndikupha thats why mukukankhura moepula

  • @jafaliKazembe-v3f
    @jafaliKazembe-v3f 3 วันที่ผ่านมา +7

    Sikuti anthu safuna kunena ayi koma vuto lakumalawi ndiboma lake ilili likhoza kukupha

  • @tinalialfazema2366
    @tinalialfazema2366 3 วันที่ผ่านมา

    Angodyapo ndalama za ulere apapa

  • @reubenngambi-x5r
    @reubenngambi-x5r 2 วันที่ผ่านมา

    Kod sitingagwiliseko ntchito mankhwala zinthuzi tione zenizeni

  • @LivaneMsyamboza
    @LivaneMsyamboza 2 วันที่ผ่านมา

    Mulungu ndamene akudziwa zonse ubwino wake Ali yense akudikira ifa yomweyo

  • @RenaldMawindo
    @RenaldMawindo 2 วันที่ผ่านมา

    Ndangoonongapo bundle yanga apa iyaaa

  • @YohaneChipande
    @YohaneChipande 3 วันที่ผ่านมา

    The answer is no

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis 3 วันที่ผ่านมา

    Poti Ndendeyo sidayake nanga ndalama za chipepeso zidapita kuti olo nanga ziduswa za foni olo tsono ngati adazipeza ndi liti adauza a Malawi kuti pa ndege tapeza izi izi ngat inaoneka Boxer ya Chilima ndeno foni mwaimodzi ikadapezeka koma awa achita kuphedwa

  • @MichaelHastingsGodfreyMvula
    @MichaelHastingsGodfreyMvula 3 วันที่ผ่านมา

    Aliyense amene wataya wapamtimu wake sangavomere kuti wakeyo sanalozedwe. Ngozi yiliyonse anthu amakhala obalalika machitidwe ndi mayankhidwe. Omwe anachita withdraw ku Inquiry anatilakwira a Namiwa a Malawife. Azingolimbana ndi ma DEMO osakathàndiza zomwe akuziwa bwanji? Amaopa chiyani? Ndizosathandiza kutsutsana ndi mbusa atadalitsa kale ukwati.

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 2 วันที่ผ่านมา

    Ndemvu za mwayi aamalandila ndalama

  • @AshrafMussa-x8q
    @AshrafMussa-x8q 2 วันที่ผ่านมา

    Ngati abale akasambala anawona kuti nyengo sinali bwino oyendetsa ndege anazikakamiza ulendo wachiwiri kuyendatso bwanji

  • @AbelSibale-b4v
    @AbelSibale-b4v 3 วันที่ผ่านมา

    Akulu akulunu yesesani kuyankhula straight nanuso mukuwoneka kuti mukuwopa ndithu

  • @LonexWataya
    @LonexWataya 3 วันที่ผ่านมา +1

    You guys your analysis is obviously non critical. I think you are out of steam in critiquing issues. Or you are partisan

  • @GiftMlinde
    @GiftMlinde 3 วันที่ผ่านมา

    Report iyiiii, ngabozaaa, ndipo, they spent alot of weeks to write this!!

  • @FelisterHunter-b7h
    @FelisterHunter-b7h 3 วันที่ผ่านมา

    Nonse mwalandila ndalama

  • @chisomophiri-m7k
    @chisomophiri-m7k วันที่ผ่านมา

    Magy wa anadya banzi ndithu

  • @ZaccariaPhiri
    @ZaccariaPhiri 3 วันที่ผ่านมา

    Ndi tsiku limodzi chidzadziwike chilungamo.
    Ndipo wins adzazifunsa kuti tinkapangiranji izi atayamba kumagwa khunyu.

  • @SaidSamuden
    @SaidSamuden 3 วันที่ผ่านมา

    Ndipo sindivelaso npaka kumapeto ndakutulukani

  • @FrankKamundi-l1s
    @FrankKamundi-l1s 3 วันที่ผ่านมา

    Chilima anachita chotafuna cholinga satanayu ayimeso 2025 koma wawuponda kumupha nzako weni weni upresident utafikano ponona mfiti yachebe chabe iyi

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 3 วันที่ผ่านมา

    Mafunso alipo ambiri Koma ngakhale tifunse pano mayankho sitiwapedza mpaka chikangawayu achoke chaka cha mawa

  • @LucyKnight-v5w
    @LucyKnight-v5w 3 วันที่ผ่านมา

    Zinakhazikikatu mu mtima ya Malawi kuti chilima anachitidwa tintini, apapa zomwe anthu zingawagwire mtima ndi confession basi , apo bii kkkkk

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 วันที่ผ่านมา

    Azimai obereka kupanga nawo report labodza mwana wamzawo ai ufumu wa Mulungu watikanika chfukwa chokonda dziko lapansi ndi ndlama

  • @SandfourKatambo-r4v
    @SandfourKatambo-r4v 3 วันที่ผ่านมา

    Inunso mwarandi nao ndalama et zapatumbo zokhazokha bas

  • @CatherineMsaya
    @CatherineMsaya 3 วันที่ผ่านมา

    Amaphang'ombe apa ndiye mwa ig'alura chilima ndi ena ana chitakuphedwa tamva basi

  • @JosephineLongweSelolwane
    @JosephineLongweSelolwane 3 วันที่ผ่านมา

    Tidzazindikira bwino patsogolo!

  • @aaronbamusi9802
    @aaronbamusi9802 3 วันที่ผ่านมา

    Anthu amaopa kunena chilungamo even if chilungamocho akuchiziwa kuopa kusowa monga mene anasowela bambo chilima

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 3 วันที่ผ่านมา

    BIYENI mukanayankhula.... kuti tidziwe chinachitika

  • @simeonbanda4240
    @simeonbanda4240 3 วันที่ผ่านมา

    Amawavula malaya Ndani?
    Where is the Blackbox?
    Why did the search start late ?

  • @MarySelenje
    @MarySelenje 3 วันที่ผ่านมา

    Palibe zomveka zomwe mukukambiranapo apa kagoneni kwanu.
    That's nonsense

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 3 วันที่ผ่านมา

    Vuto atolankhani akumalawi mumalambalala pofuna kuzukuta nkhani mantha too much

  • @ChristopherMatemba-m4g
    @ChristopherMatemba-m4g 3 วันที่ผ่านมา

    Tiyakhule motele okuba saitana a police

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala 3 วันที่ผ่านมา

    Nfipo ndege ija anachita kuphulitsa ndi Bomba mpake anthu amamva saund

  • @jamesmwakayoka7586
    @jamesmwakayoka7586 3 วันที่ผ่านมา

    License ya chani anthu oti anakhoza kale mayeso oti atha kuyendesa ndege.

  • @KinziWindasoni-h4b
    @KinziWindasoni-h4b 2 วันที่ผ่านมา

    Wondara sinsia ngati wadya chibanzi khala chete .ripor siyili bwino iyi

  • @SueWahna-y8m
    @SueWahna-y8m 3 วันที่ผ่านมา

    Or titapanga debate iyiyi sinali ngoz ngoz kom chiwembu why report likusiyana inaija inapanga blame ndege ndi zina zotero iyi ikukamba zina chilungamo chidapita bas Amalawi tivomereze kom chilungamo chilipo pangatalike amalawi azaziwa

  • @arnoldchikopa2611
    @arnoldchikopa2611 2 วันที่ผ่านมา

    Za black box palibe bwanj

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 3 วันที่ผ่านมา

    Anthu umboni ali nawo koma akuopa ng'ona za MCP

  • @chifundochiwaula998
    @chifundochiwaula998 3 วันที่ผ่านมา

    Tikanakhala kuti taitanidwa nde tapeleka umboni nde atimanga akanadzationa ndani?

  • @LufaniAhamadi
    @LufaniAhamadi 3 วันที่ผ่านมา

    Where is black box ansaa

  • @WilsonMbendela
    @WilsonMbendela 2 วันที่ผ่านมา

    Madolo program yokhai mwanyika palibe chomwe

    • @ManzyNgoleka
      @ManzyNgoleka 2 วันที่ผ่านมา

      Ndipo straight kunyikira2

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 3 วันที่ผ่านมา

    Akunama zinali bwino bwino anachotsa black box

  • @blessingsgonani6243
    @blessingsgonani6243 3 วันที่ผ่านมา

    Ndizumvuta kuti munthu abwele Yakhule zomwe akuziwa kumapetokwake amagindwe

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 3 วันที่ผ่านมา

    Kkkk ngozi yardage ingaombere mutual mwa a chilima ndi amai Shania muluzi ?@ ndipo ngozi yardage ingaombere a chilima chipolopolo.munthiti? Ndipo.ngozi ya ndege ingadule dule miyendo yonse iwiri ya a chilima ndi kudula nkuchotsa mutu wa lady pilot Nginjiri ? Whence has chakwera put madam ngwinjiri's head that she was put in the coffin without her head . ? So chakwera ate her head..mcp is too wicked

    • @RuthChilobwe
      @RuthChilobwe 3 วันที่ผ่านมา

      LADY MADAM PILOT NGWINJILI HER HEAD GOT CUT OFF AND ITS WHEREABOUTS IS NOT IN THR COFFIN. STATED THE COMRADE NTANYIWA IN HIS AUDIOS NTANYIWA IS A NEPHEW OF MADAM.PATRICIA MULUZI. AND THESE ARE GRNUINE FACTS .

    • @RuthChilobwe
      @RuthChilobwe 3 วันที่ผ่านมา

      Chakwerayotu abwere poyera ngati adzatha kukana

    • @RuthChilobwe
      @RuthChilobwe 3 วันที่ผ่านมา

      Absurd point is.the commission of enquiry was nominated or appointed by the killerman himself..thar is chakwera himself..and him.gave the commissioners .areas to disclose to the public.bug this extreme areas do not tackle them.and expose or publicise cos they are portraying me chakwera.the killer.

  • @PatrickWhite-mo4nd
    @PatrickWhite-mo4nd 3 วันที่ผ่านมา

    Tagwirani makinawo yasiya kuulusa mau kuno ku muzernberg cape town

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 3 วันที่ผ่านมา

    Munthu wanzeru anganene kuti anali careless munali zianthu mmene muja

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 3 วันที่ผ่านมา +2

    TIZANENE 2025 UMBONI. USELESS HOT CURRENT ZA NZIIIII

  • @PiriraniNasiyayah-yl5mn
    @PiriraniNasiyayah-yl5mn 3 วันที่ผ่านมา

    Pakanakhala kuti palibe otuluka tikanawakhulupirira

  • @daviekachali9481
    @daviekachali9481 3 วันที่ผ่านมา

    Ok

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 3 วันที่ผ่านมา

    MWADYA MA BUNS ETI ZITSIRU

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 3 วันที่ผ่านมา +2

    Anthu amaopa kupangidwa tintini kapena kuona kiyama or kuphedwa and the trueth will come in 2025 and this enqiry was well planned so that they can decieve people.

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 3 วันที่ผ่านมา +2

    Mwayambatu kuida hot current agang'a inu........ mumafuna akuuzeni kuti anakhapidwa

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 2 วันที่ผ่านมา

    That is fake report angotionongera our tax money