LIMPOPO FM WITH COMRADE KANGAUDE 15 JULY 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
  • BRAKING NEWS FROM LIMPOPO FM RADIO NDI KANGAUDE......PALI CHIOPYEZO CHOTI CHAKWERA AKHOZA KUKHALA NDI AKAZI AWIRI KU PALACE POMWE AKUCHIMUNA A MAMUNA WA VERA KANTUKULE AKWIYA KKKKKKKKKKKK🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 zambiri mporogram iyi
  • บันเทิง

ความคิดเห็น • 64

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 หลายเดือนก่อน +2

    Zafikilapa olo kungowauza achakwela kuti comryde akukhala uku mundipase 100 million akupasa 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 หลายเดือนก่อน +1

    Limpopo FM best ❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥 wina amwalira ndi Bp Chaka chake ndi chino kkkkkkk

  • @MuhammadInack
    @MuhammadInack หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂 Anatiuza kale wabakili kkkkkkkkk chakwera oyeeeeeeeeeee🗣️🗣️🗣️🗣️🗣️

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน +2

    Vera atangophetsapo amunake osalakwa apa.

  • @user-pk5xk1is9r
    @user-pk5xk1is9r หลายเดือนก่อน

    Koma mr chikangawa

  • @MerryWayson
    @MerryWayson หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkkk Koma chakwera ngat ndi ufiti kkkkk Mr Lufeyooooo Moto kut buuuuuuuuuuuuú Moni Ku office Yonse ambuye azikutetezani utsiku wabwino ❤❤❤❤

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj หลายเดือนก่อน

    Sallam alainkum MwaSwella bwanji mtanyiwwa mulungu adalise inuyyo nosse nkumene mulinko my Allah bless you always tiutseni soona sandege live in the sauth Africa estan cap ashankwela angompedwa nawosso apoo ayi mulungu awaphase missalla 👌👌👌🤛

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 หลายเดือนก่อน

    🔥🔥🔥🔥

  • @user-zf7lh1py7u
    @user-zf7lh1py7u หลายเดือนก่อน

    Where's Comrade Ntanyiwa? We miss him

  • @FrancisDay-br7xb
    @FrancisDay-br7xb หลายเดือนก่อน +1

    Lazolo sadakhalepo munthu abwino

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 หลายเดือนก่อน

    Koma kumeneko motoooooooo buuuuuuuuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @BeatrizUlanda-ht2th
    @BeatrizUlanda-ht2th หลายเดือนก่อน

    Mumakwana bos❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @KelvinMangwengwe
    @KelvinMangwengwe หลายเดือนก่อน +2

    Mumakwana popanda kumva kwa tsiku limodz timadandaula

    • @VungaQueen
      @VungaQueen หลายเดือนก่อน

      Kwambiri

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko หลายเดือนก่อน

    Mr kangaude iweso ndi dolo😅😅😅

  • @MustafaMachika
    @MustafaMachika หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤

  • @meganabigail-ye7fw
    @meganabigail-ye7fw หลายเดือนก่อน

    Mumatiimila Sir

  • @user-wb9ji3oe5o
    @user-wb9ji3oe5o หลายเดือนก่อน +1

    Kumasankha nduna mcholinga kuti azigonana ndi azikazi aweni ake.Shame( zamanyazi/ zaumve.

  • @user-ht7vs3dp2u
    @user-ht7vs3dp2u หลายเดือนก่อน +1

    Mkazi opusa athesa banja rake ndimanja ake koma mkazi iwe mamunako samakumpasa chani uziwe kut wampanga ubwezi ndi yudasi sikaloti akuperek ukapusa kkkkkkkk😂😂😂😂😂

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk😂😂😂😂😂 komakumneko chakwera😂😂😂😂komandiye ndakomoka kuseka😂😂😂😂😂😅😅

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 หลายเดือนก่อน

    😅😅😅😅😅😂😂😂😂koma mr Chikangawa zoonadi manyazi mulibe 😅😅😅😅😅😂😂😂😂komatu ndiye mukuyalukatu dairy 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅

  • @NyarineJames
    @NyarineJames หลายเดือนก่อน

    Kma Chakwera zinthu zantempwana bax... Game over!

  • @JumaKachala
    @JumaKachala หลายเดือนก่อน

    Limpopo Oyeeeeeeeee

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh หลายเดือนก่อน +1

    Penapaketu,Inu alimpopo,muziona nkhani yobweretda pa public,iyi ndi personal life esue sizikupindulira dziko kunena zoona apa mwalakwitsa,ngati ine munthu amene ndmakutsatirani bwino konzanipo pamenepo.nthawi zina not always mumabweretsa nkhani zosamaliza bwino anthu mumawasiya mmalele,ife timati mwina next audio mupitiliza yomwe munaiyanba ija,koma timadabwa kuti mumabweretsa Ina nkhani ija mwasiya,ndiye chonde nkhani ilibe umboni weniweni ndibwino osaulutsa than kuwasokoneza anthu omwe amakupangani follow up.we as malawians we love you.ngati sinthani chifukwa nkhani yabwera apa sikukhudza dziko koma ikukhudza munthu zoti dziko silingapindule kanthu,koma mukungomupanga embarrassed munthuyo.sizinakome apa.

    • @LamieTiger
      @LamieTiger หลายเดือนก่อน +1

      Osaikira kumbuyo zoputsa usi sufuka popanda Moto nkhaniyo ndiyaumbon why mamuna wankaziyo wanyanyala iye chakwera akaz opanda amunawa sakuwaona ana ambili mbili opanda amunawa sakuwaona nkaz wakeyo wasiya kukoma kod

    • @CharlesChagudubuka-rm6bh
      @CharlesChagudubuka-rm6bh หลายเดือนก่อน

      @@LamieTigernkhani ndiyakuti ife sikutikhudza ngati dziko tiyeni tizikhala ndi malire tikafuna kuyankhula, chifukwa munthu alibe ufulu ophwanya ufulu wanzake.

    • @LamieTiger
      @LamieTiger หลายเดือนก่อน +1

      @@CharlesChagudubuka-rm6bhzikalakwika kumayakhula ukakhala ufulu wamuthu nde chakwera ndioyamba kusalemekedza ufulu waaliyense muno m'malawi ngat mumaziwa ufulu wamuthu nde mundiudze ngat chakwera amalemekedza ufulu waamalawi ngat mumamukonda ngat mwayandikananaye chakwera mumuudze Kut aphudzile kulemekedza maufulu aamalawi ndikulemekedza akaz ayen

    • @CharlesChagudubuka-rm6bh
      @CharlesChagudubuka-rm6bh หลายเดือนก่อน +1

      @@LamieTiger 😅😅😅 ndipo ine sindimukonda olo pang'ono koma a it's okie

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 หลายเดือนก่อน

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣chigololo mpaka ndapulesedeti omwe nyasi zokazoka kumalawi kkkkkkkkkk

  • @DownRolly
    @DownRolly หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂koma chifukwa chani mwamuna akakhala kt ali ndi ndalama sagona nyumba imodzi,mmm amafuna kukhala ndi nyumba zambiri🙌🙌

  • @EsnalaThomas
    @EsnalaThomas หลายเดือนก่อน

    Mumakwan alimpopo fm

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 หลายเดือนก่อน

    😂🤣🤣🤣🤣ochakwera! Mpaka mwana wayeni.

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 หลายเดือนก่อน

    Atakanika kuyendetsa boma angoganiza kuti ayambe uhule 😂😂😂

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน +1

    Kkkķkk yalakwa

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl หลายเดือนก่อน

    Limpopo moto kuti 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥😂😂😂😂😂😂

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana หลายเดือนก่อน

    Khanizo osamabisa zawo nde zobisa zidzibwera nde bwino paribe zobisa ayaluka ndazikonda kwabasi😂😂

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkk koma kangaude suzatheka oooooooh chakwela kutosatosa et ife nganga pano pa limpopo

  • @uzaleuzale8603
    @uzaleuzale8603 หลายเดือนก่อน

    Basi angodalitsaso nanga atani wakula watha ameneyo galu wa munthu 😂😂

  • @feehasaidid.r.d
    @feehasaidid.r.d หลายเดือนก่อน

    Mmene walionongela dzikoli ayambanso uhule kuonongano mabanja anduna zawo 😂😂😂😂😂😂 koma kumalawi kuno abale😂😂😂

  • @TonyMpate-by9gp
    @TonyMpate-by9gp หลายเดือนก่อน

    Iyi ingokhala own goal 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @louismagongwa
    @louismagongwa หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂 koma kumeneko

  • @HashimNyirenda
    @HashimNyirenda หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkk umakwana bigy.
    matosatosa nawonso iiiiiii

  • @DisireDokotala
    @DisireDokotala หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤❤❤

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 หลายเดือนก่อน

    Komredy ntanyiwq khunda mumadya agogo anga akufuna akupaseni

  • @Leo-fj6gz
    @Leo-fj6gz หลายเดือนก่อน

    Tsano kunjaku akapita limodzi mdala uja amathila batile 😂😂😂 eeeeish chigololo anakonza ndithu that’s why mayiwo watemetsa mutu pa mwala sachoka kuli makobidi uku 😂😂😂😂🙌🏾

  • @stevovosalimu5443
    @stevovosalimu5443 หลายเดือนก่อน

    ❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-mf5ce9wj4m
    @user-mf5ce9wj4m หลายเดือนก่อน

    Atule udindo hule lamamuna kukhala kuno ku john anakamva madzi ndi aphungu osusa

  • @SaniJonathan
    @SaniJonathan หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂 koma kuli zinthu tiuzen zoona

  • @user-uj9st8zp7v
    @user-uj9st8zp7v หลายเดือนก่อน

    Tiye nayo kangaude

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z หลายเดือนก่อน

    KOMA ZOVUTA NDITHU NO PAIN NO GAIN CHAKWEL KUKWELA KWELA😅😅😅😅

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu8402 หลายเดือนก่อน

    Iiiiiiiii manyasiapite kubanja lachakwela koma ndichifukwa chani abusa ubusa uja ulikuti achakwela chonde koma dzinthu dzinazi abale???????

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 หลายเดือนก่อน

    Koma comredy asalile aziyamba okha

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 หลายเดือนก่อน

    Mumasuleni Nkasa Nyimbo Ija Anaimbila Amalawife

    • @ShorishKenneth
      @ShorishKenneth หลายเดือนก่อน

      kasa wamangidwaso

    • @mcsellahntv6896
      @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน

      ​@ShorishKenneth is this true??

  • @crosbeygondwe5403
    @crosbeygondwe5403 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂 yalakwa

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r หลายเดือนก่อน

    Koma izi ndi zoona 😂😂??

  • @StanleySabantinegamah
    @StanleySabantinegamah หลายเดือนก่อน

    Kd abakha mumadya kkkkk

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂

  • @BeatrizUlanda-ht2th
    @BeatrizUlanda-ht2th หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkkkkk🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @HanaNyasulu
    @HanaNyasulu หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂 mmmmm koma chakwera