LIST YA MAINA OMWE APAMBANA OPANDA OPIKISANA NAWO KU CONVENTION YA DPP CONGRATULATIONS TO THESE PPLE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 185

  • @YankhoGuza
    @YankhoGuza 2 หลายเดือนก่อน +18

    Amene mukuyakhura zamwano apa mulibe nzelu osangokhala bwanji osakomenta ndinu munamupha chilima eti mbuzi za athu chalakwikapo ndichani pamenepapa agogo ndabambo ako ufune usafine peter alowanso ❤❤❤❤❤

    • @AngolanChinga
      @AngolanChinga 2 หลายเดือนก่อน

      Bro osavutik ndikuwayankha amenewo Peter kufuna osafuna akulowa bs we must know that

    • @mathewsmbaluko8522
      @mathewsmbaluko8522 2 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂​@@AngolanChinga

    • @clesheinvestments
      @clesheinvestments 2 หลายเดือนก่อน

      @@YankhoGuza Madzi akamaphwa amabwera pamodzi

    • @EdwinHowardmkandawire
      @EdwinHowardmkandawire 2 หลายเดือนก่อน

      Kodi chilima anachita kuphedwa kani

    • @languitoneelias9972
      @languitoneelias9972 2 หลายเดือนก่อน

      Nankhumwa ndi chimulirenji ali kuti kodi

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o 2 หลายเดือนก่อน +12

    Chikangawa party I think ilipompa kukomenta nao zinthu zanegative.Munyanane...Apm my vote❤❤❤

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 2 หลายเดือนก่อน +8

    Ndiye convention inali ya chani yopanda opikitsana i only support federal system of government in Malawi.

    • @AishaChibwana-b8o
      @AishaChibwana-b8o 2 หลายเดือนก่อน

      Koma ndiponso inu chinsankho chake chosekesa chopanda munthu wina aaa

  • @MercyKziphondo
    @MercyKziphondo 2 หลายเดือนก่อน +12

    Macoment enawa ndiianthu agulu lachikangawa

    • @OssmanAbubaker-k3q
      @OssmanAbubaker-k3q 2 หลายเดือนก่อน

      Kkkkkkk

    • @FatimaNakoma
      @FatimaNakoma 2 หลายเดือนก่อน

      Mcp okupha

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 2 หลายเดือนก่อน

      Umangodziwiltu

    • @fannyzimba149
      @fannyzimba149 2 หลายเดือนก่อน

      Ndipo inu moti zinthu mmene zilili kuno ku malawi anthu ena nkumati zikuyenda aaaa mulungu ndiwadongosolo atimenyera nkhondo

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 หลายเดือนก่อน +3

    Mr chikangawa 5 years nothing as Malawians achieve from him ,
    Congratulations DPP ,

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk 2 หลายเดือนก่อน +3

    Ine ndine wa UTM , koma 2025 vote pa APM ,kaboma aka kazipita please

  • @THOCCOChimbali
    @THOCCOChimbali 2 หลายเดือนก่อน

    Apm my vote

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 หลายเดือนก่อน

    God bless muthalika ❤❤❤❤

  • @MaryJefry
    @MaryJefry 2 หลายเดือนก่อน

    Koma mikundinvesa kukoma abale😂😂❤❤❤❤

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน +5

    Mcp ndi bomadi izizi ndizabwana kobveshoni ndimaona ngati amapikisana

  • @saidimwanyali8969
    @saidimwanyali8969 2 หลายเดือนก่อน +4

    Ana sangilatu Mbali yiliyonse nfichifukwa Chaka zanapikisane komaso ndi anthu omwe ndi osiwika kale

  • @PrinceMillionea
    @PrinceMillionea 2 หลายเดือนก่อน +2

    My vote APM ❤❤❤

  • @manuelrex4150
    @manuelrex4150 2 หลายเดือนก่อน

    My vote apm 2025

  • @StellaMkuzilire
    @StellaMkuzilire 2 หลายเดือนก่อน

    Ngati angoti tivote mawatu APM my vote

  • @PeterAkidu
    @PeterAkidu 2 หลายเดือนก่อน +4

    Aaaa anthu onseo ichi ndiye chibwana mcp boma

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane 2 หลายเดือนก่อน

    Tinthokoze nonse mwasankhidwa kut mupabe ubale unodzi mutiombele mumavutowa atikwana zinthu zadula kuposa chakwela❤️♥️♥️♥️♥️

  • @AslamCassim-b7n
    @AslamCassim-b7n 2 หลายเดือนก่อน +3

    Ukhaula iwe wakuchikangawa pita uko usamaike comment sizikukhuza kapolo iwe

  • @ModesterMbendera
    @ModesterMbendera 2 หลายเดือนก่อน +1

    APM my vote 2025 Boma

  • @EthelKspito
    @EthelKspito 2 หลายเดือนก่อน

    Dan lu ati palibeso wina ife titi chan ndye chipani chantendele Ali wa DPP chala mwamba apa ziwawawe aliko☝☝☝👏👏ulum kwa Peter big man bingu muthalika nzimu wako ukuyendabe kuno phwako uja akukondedwa ndi anthu malo mwaiwe professor simunthu wamba banja LA kwa muthalika ndi akamuna amwene eehh lodala banja munayamwa apule munthu wankulu

  • @MussahWilliam-py1ff
    @MussahWilliam-py1ff 2 หลายเดือนก่อน

    Ndye kwabwinotu ,kosapikisana kkkk kkkkkkk ay aaaa kaya mwina........my vote be basi nanga mkutaaa

  • @domminicchikalenda
    @domminicchikalenda 2 หลายเดือนก่อน

    Convention and democracy has a different meaning in the blue camp🤔🤔🤔 or akanagoti akulegeza zotsatira zakumkumano waku Page house

  • @InnovativeSealing
    @InnovativeSealing 2 หลายเดือนก่อน

    Dpp my vote

  • @CharlesMasamba-m7g
    @CharlesMasamba-m7g 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂
    Ine kwanga ndikuonerela gule opanda nyimboyi 😁😁😁😁

  • @MlambeLodge
    @MlambeLodge 2 หลายเดือนก่อน

    My vote apm basi

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 2 หลายเดือนก่อน +2

    ❤❤❤❤❤ Apm

  • @CeciliaKalua-g9y
    @CeciliaKalua-g9y 2 หลายเดือนก่อน

    Kwanuko kunachuluka dyera mpake opikisana mbweee😂

  • @georgekesten3975
    @georgekesten3975 2 หลายเดือนก่อน

    Amakosana mukubowa tisaname...upgrade plz

  • @JawardBenard
    @JawardBenard 2 หลายเดือนก่อน +7

    APM my vote

    • @InnocentPhiri-o1u
      @InnocentPhiri-o1u 2 หลายเดือนก่อน

      𝙸𝚝𝚜 𝚠𝚑𝚎𝚛𝚎 𝚖𝚢 𝚟𝚘𝚝𝚎 𝚌𝚊𝚗 𝚐𝚘.

  • @TisopeMkozo
    @TisopeMkozo 2 หลายเดือนก่อน +2

    Ka sound kamene mumayambilira kutipatsa uthenga ndikonyasa kwambiri

    • @alickmustafa
      @alickmustafa 2 หลายเดือนก่อน

      Chikangawa kunukha kukhwapa

  • @EdwinHowardmkandawire
    @EdwinHowardmkandawire 2 หลายเดือนก่อน +1

    Nkhalamba APM

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba 2 หลายเดือนก่อน

    Awa ndi aja timati masanje

  • @YasinMmadi
    @YasinMmadi 2 หลายเดือนก่อน

    Mma position akuluakulu azimai awamana

  • @YusufMapata
    @YusufMapata 2 หลายเดือนก่อน +3

    k
    dpp chipani chachikulu nggati chimenechi anthu sangalemphele kupikisana wu

  • @AubreyMsusa
    @AubreyMsusa 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera paja anapikisana nd ndan ku convention?
    Paja mcp amafuna kulesa ena mpaka ku court.
    Komso nec yonse ya mcp...central region

  • @MaryJefry
    @MaryJefry 2 หลายเดือนก่อน

    Olo mumunyoze pita koma palibe chomwe mupindule ndiekhayi munthu amene anatipasa mulungu enanu ndi akupha masataniki inu fosek

  • @dennisbanda4751
    @dennisbanda4751 2 หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkk zilikomuzivoteranokha ma robot wooo

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkk kulibeko zopikisanatu kumeneko eti

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 หลายเดือนก่อน

      Ma udindo apite zigawo zonse beta bc

  • @JIMMYWATSON-ph5jg
    @JIMMYWATSON-ph5jg 2 หลายเดือนก่อน

    Iyi ndi njira ya mtanda simasankho amenewa munyanane 2025 ine ndine mcp

  • @EunceChilembo
    @EunceChilembo 2 หลายเดือนก่อน

    APM woyeeeeee Japi Mhango woyeeeeee

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 หลายเดือนก่อน

    Ndili ndichiyembekezo Kuti 2025 nyasi zomwe zilipozi zikuchoka zatiwonongera dziko lokoma lija latendere

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 หลายเดือนก่อน +1

    DPP boma 💙💙

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba 2 หลายเดือนก่อน

    Iyi si convention koma kuzaitana mayina

  • @FredLiwonde
    @FredLiwonde 2 หลายเดือนก่อน

    APM Boma we are praying for Malawi my mother land 2025 Boms ilo osawopa In God we win

  • @RuthBinali-b8c
    @RuthBinali-b8c 2 หลายเดือนก่อน

    Ndimava mawu ambiri azibambo pansi pansi kusonyeza kuti chipanichi chilindimphavu kwambiri

  • @AustinChazuma
    @AustinChazuma 2 หลายเดือนก่อน +3

    Zopusa masankho amapanga choncho uchitsilu

    • @MCAnthonyNdau
      @MCAnthonyNdau 2 หลายเดือนก่อน

      Ndipo inu

    • @alickmustafa
      @alickmustafa 2 หลายเดือนก่อน

      Galu iwe ukuti chani ana achikangawa inu anyalugwe

    • @spargomw
      @spargomw 2 หลายเดือนก่อน

      Zamunyasa ayanike ufa pachingwe,

    • @HamitonFrank
      @HamitonFrank 2 หลายเดือนก่อน

      Ana okupha achikangawa Inu

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 2 หลายเดือนก่อน

    Well organized

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s 2 หลายเดือนก่อน

    Nde convention wanji sanasithebe akanakhala awawa eti mbalame za wathu mzimu wa Dr Chilima uziusabe mumtendere mukananya nose mcp ndi dpp

  • @blessingschimwala229
    @blessingschimwala229 2 หลายเดือนก่อน

    Chipani Cha nkhalamba,a dad kukakamila mpando yet akukanika ileven kuzutsa dzanja,Malawian politicians they are too greed for power

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 2 หลายเดือนก่อน

    Congratulations DPP.... Convection yayenda bwino.

  • @dennisbanda4751
    @dennisbanda4751 2 หลายเดือนก่อน

    Ana anjoka mukuona ngat mungaloweso m,boma kut muzizamenyaso anthu ma bar iwalani zimenezo zaana adad kwanukomko

    • @AgnessMatchado
      @AgnessMatchado 2 หลายเดือนก่อน

      Galu iwe pita uko

  • @Emmanuel-o9y
    @Emmanuel-o9y 2 หลายเดือนก่อน

    dpp Boma 2025

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 2 หลายเดือนก่อน +2

    Masanje mipando yonseyo anthu sakuifuna?

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 2 หลายเดือนก่อน

    Akumva pain apaseni panado!

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 หลายเดือนก่อน

    Taona maboma ife koma nyasi izi za kaboma aka ka chikangawa sindinaone

  • @khwimamtonga954
    @khwimamtonga954 2 หลายเดือนก่อน

    Azimai Kulibe Ku dpp or gender kulibe

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 2 หลายเดือนก่อน

    Tikufuna tichose nyasi izi za MCP, kulibe kuwima MCP kwawo kwatha ndipo chipani cha MCP chathhera popo ali ndi zeru akuwona sichingazalowenso boma mpaka mathero adziko lino.

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zokungola ❤❤

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 2 หลายเดือนก่อน

    Pepani amcp musalowelere sizikukhuzani izi ndi za dpp full stop

  • @Chikwina
    @Chikwina 2 หลายเดือนก่อน

    Too much osapikitsana no democracy. Or rubber stamp democracy .

  • @FaysonChimbalanga
    @FaysonChimbalanga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Chipani chamakape cha dpp kuyambira President mpa mipando ina yochuluka opanda opikisana nawo ku phangila basi makape awa

  • @HagEva1
    @HagEva1 2 หลายเดือนก่อน

    Dpp tipulumutsen ku nkhaza ,!!!

  • @MosesNgombeyayera-tc3ru
    @MosesNgombeyayera-tc3ru 2 หลายเดือนก่อน

    Ma unopposed achulukatu kusowa anthu chani?

  • @stuartbonga5060
    @stuartbonga5060 2 หลายเดือนก่อน

    Magogozeni akonzeka kukaba mboma
    ndi kutsekanso njanji ndikukayimitsa kumanga misewu munya agalu inu

  • @dennisbanda4751
    @dennisbanda4751 2 หลายเดือนก่อน

    Chipani Chama robot vote palibepo pamenepo

  • @HaswllLyford
    @HaswllLyford 2 หลายเดือนก่อน

    Ine olo nditamwa delunde siningadzavotere m'kwadzamba

  • @CharlesMpinga
    @CharlesMpinga 2 หลายเดือนก่อน

    Asiyeni anthu akuphawo ife zanthu ndizau Christu pamene inu zanu masiku onse ma plan anu ndiongoganiza zopha anthu basi..... Mukufunanso kuti mupitilize kulamaula kuti mutipherenso anthu ena basi inu anthu Achikangawanu

  • @PeterWillard-o3d
    @PeterWillard-o3d 2 หลายเดือนก่อน

    Zilibwino 🎉

  • @ElisyIweni
    @ElisyIweni 2 หลายเดือนก่อน

    Achikangawa ali mommuno zanu izoDpp woyeee

  • @LovenessMaluwa-c4x
    @LovenessMaluwa-c4x 2 หลายเดือนก่อน

    Amen

  • @BrianJoe-z7u
    @BrianJoe-z7u 2 หลายเดือนก่อน

    one kuva kukoma mutima mwe

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน

    Koma mwati ndikobveshoni nanga bwanji anthu sakupikisana tiziona

  • @GeoffTchezan
    @GeoffTchezan 2 หลายเดือนก่อน

    Za chibwana zimenezo agalu inu kkkkkk

  • @LiznertScissors
    @LiznertScissors 2 หลายเดือนก่อน +1

    Sizankasatu izi 😅😅😅😊

  • @jameskavina197
    @jameskavina197 2 หลายเดือนก่อน

    Aaaah kodi dpp bwanji kupondereza u president osawapatsa ena mwai bwanji?

    • @CharityChanzah
      @CharityChanzah 2 หลายเดือนก่อน

      Term ikubwerayi muona mnkhope za chilendo but for the time being tilolen tikunthe uyu kaye

    • @SamsonJuma-w6y
      @SamsonJuma-w6y 2 หลายเดือนก่อน

      😂😅😂😅😂 ndpo kukutha ngt pang'ono ​@@CharityChanzah

  • @ChisomoLester-h7x
    @ChisomoLester-h7x 2 หลายเดือนก่อน +5

    Anali atasankhana kale uku ndie kutha kwa chipani uku

    • @CharityChanzah
      @CharityChanzah 2 หลายเดือนก่อน

      Mmmmm manyaz bwanj

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@CharityChanzahspa ndiye corvetion mukatani olowa ndi miyendo athu 20 aaaaa mugotaya thawi

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 2 หลายเดือนก่อน

      Iiiiiii kkkkk chikangawyo

    • @ibrahmdoka7486
      @ibrahmdoka7486 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@kingsleyhopematchaya5184amakhala kut ndi abwino ndikale...no change...even enawo amadziwa kut sangawine olo atapikisana enawo

    • @HanifiYaumu
      @HanifiYaumu 2 หลายเดือนก่อน

      Wachikangawa iwe inja

  • @ERICBISHOPJERE
    @ERICBISHOPJERE 2 หลายเดือนก่อน

    This is nonsense. what's the meaning of having convention when there is no one to complete on the positions. Aaaaaaa eish what a drama.

  • @Jele-mk9ip
    @Jele-mk9ip 2 หลายเดือนก่อน

    DPP dzitsilu they worship a person instesd of party.

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 2 หลายเดือนก่อน

    APM ndi DPP tengani bomali amalawi alandire ndalama zao za pension zomwe alipowa akulephera kupereka mpaka, zaka zitatu anthu akuvutiikabe

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq 2 หลายเดือนก่อน

    Chikangawa watani kumabwera ndima comments achabe apa wakhaulatu

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน

    kunena zoona apa dpp yatha sindikuona munthu oti angapange kampeni ai ine ndi wa dpp koma zomwe ndikuona mmmmmmm

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 2 หลายเดือนก่อน +4

    Koma kuti chakwerako wapya mutima kwabasi

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 2 หลายเดือนก่อน

      Wapenga ndichiya kape iwe

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 2 หลายเดือนก่อน

      Wapenga ndichiya kape iwe

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 2 หลายเดือนก่อน

      Wapenga ndichiya kape iwe

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 2 หลายเดือนก่อน

      Wapenga ndichiya kape iwe

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 2 หลายเดือนก่อน

      Wapenga ndichiya kape iwe

  • @RonaldTchapo
    @RonaldTchapo 2 หลายเดือนก่อน

    More bpp 2025 boma basi osati chikangawa😂😂😂

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 2 หลายเดือนก่อน

    Aliyese akwera yake

  • @GeoegeGRSHala
    @GeoegeGRSHala 2 หลายเดือนก่อน

    Nkhalamba zokha zokha yooo

  • @robertkabade5011
    @robertkabade5011 2 หลายเดือนก่อน

    Kubwera zikufunika chocho 2025 boma basi tichokeko kuno ku South Africa tikapange zathu ziko LA mtendele

  • @LimbaniJohn
    @LimbaniJohn 2 หลายเดือนก่อน

    Tikulowanso boma 2025

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 หลายเดือนก่อน +1

    Apa zilibwino Kwambiri.zosangalasa Mayina amene kumwamba Kwa vomereza .osati kumawagulila anthu zinjinga kugawa ma million kupita Kwa azising.anga Kuti muwine Inu nokha nokha kuphana ..izi sizamagazi zamtendere ..ana achikangawa munva madzi ..😂😂😂 APM Moto Kuti buuu❤❤❤❤

  • @PreviousStanley
    @PreviousStanley 2 หลายเดือนก่อน +4

    Ndiye chochitira masankho ndichani apatu ndichimozimozi kumapita kuchipatala mutaziw Kate Kuti munthuyo watuluka kare

    • @FatimaNakoma
      @FatimaNakoma 2 หลายเดือนก่อน

      Ndie vuto lako nchani galu

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@FatimaNakomazamanyazi mukanagokhala ku magochiko mesa munasakhana kale

  • @ElizabethSawenga
    @ElizabethSawenga 2 หลายเดือนก่อน

    Adadi omwewo

  • @LazarousKasambala
    @LazarousKasambala 2 หลายเดือนก่อน

    Kozani admarc 2025 bwana.

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 2 หลายเดือนก่อน

    Tsamafuna za ndewu nchifukwa anasankhilathu

  • @EllieMvoso
    @EllieMvoso 2 หลายเดือนก่อน

    Suleman alikuti

  • @clesheinvestments
    @clesheinvestments 2 หลายเดือนก่อน

    Tanthauzo leni leni la dpp ndi lakuti
    "DONA PAMTUMBO PAKO" (DPP)

    • @JhdaLifi-vu9sd
      @JhdaLifi-vu9sd 2 หลายเดือนก่อน +2

      Kutukwanatu sikupindula limbikila kusaka ndalama nzanga anthu andalewatu ndiamozi timangozivutisa anphawife kutukwana

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@JhdaLifi-vu9sd zooona

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 หลายเดือนก่อน

      Koma manyazi mulibe, inu ngt muli amcp sibwino kumagwela za a zanu kumatukwana. Ulemu ndi ofunika

    • @mcsellahntv6896
      @mcsellahntv6896 2 หลายเดือนก่อน

      Pajatu Chikangawa Party ngodya zanu ndi zimenezi. Kutukwana, Kupha ndi Kuba. Sitili odabwa nanu.

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq 2 หลายเดือนก่อน

      Chikangawa utonyapo apa

  • @LaitoneJefitala
    @LaitoneJefitala 2 หลายเดือนก่อน

    Chipani cha nkhalamba

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 หลายเดือนก่อน

    2025 kuchema

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 หลายเดือนก่อน

    Boma ilo

  • @SellinaSanena
    @SellinaSanena 2 หลายเดือนก่อน

    💃💃💃

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya 2 หลายเดือนก่อน

    Zilibwino

  • @DorothyKamanga-l9j
    @DorothyKamanga-l9j 2 หลายเดือนก่อน

    Adad the great

  • @YamieManda
    @YamieManda 2 หลายเดือนก่อน +1

    Mukanangopatsana mapozishoni osati kupanga convesione,,iyi siconvesion awa ndimasanje ndi azigogowa.

    • @AubreyMatress
      @AubreyMatress 2 หลายเดือนก่อน

      Mwana wa nyau kagwere uko, ukuyetsa ndi chikangawa party iyi
      Komanso kumuona munthu wakeo omvetsa chisoni_ sukugona kwanu ndi njala iwe

    • @AndersonBishop-i2t
      @AndersonBishop-i2t 2 หลายเดือนก่อน

      Iwe si nyau imeneo wamva mapwala ako agulewo

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 2 หลายเดือนก่อน +1

      Awononga nzanu kodi?