ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Much love 🔥 amen and Namiwa son of the soil 🎉🎉🎉🎉
🎉🎉🎉🎉🎉 ulemu wanu bhuro
Anamiwa ndi namiwa ❤❤ always i support you
Ndikuona kuchedwa kucha ine viva Malawi viva CDEDI viva Namiwa🎉🎉🎉🎉🎉
Namiwa ndi gulu lanu la CDEDI Mulungu azikudalitsani. Ndinu amene mwaima pa Chilungamo kuimira mtundu wa a Malawi. Osaopa, Osafooka ndipo Osatopa.
Viva comrade Namiwa viva 💪
Tisaveso zoti alepheleka Ifa takonzeka kale
Kuchoka mademo amawa kwasala oti tidzamuchose Chakwela watikwana kwambiri
Kutengeledwa kuntoso😂😂😂😂😂
Inuyo ndi one basi, more 🔥🔥
Apumedi anthu amenewa za mafuta zawakanika Kachaje must gooooo
More fire 🔥 mr Namiwa
More fire Namiwa
Pang'ono pang'ono akadati mavote amenewo mukawerengera kudambwe😂😂😂😂 wangot ku Mozambique 😂😂
Mr namiwa more 🔥
Upitako ndi alomwe azakowo inu anthu Aku Mozambique ndinu okonda nkhondo
Tiona ngat kuzakhare alomwe okha mawalo aise
Ukamati ndi alomwe ukuthandauza chani ????? Kunyoza ntundu wathu wacilomwe ndi mwikho wamva ndipo ndi Mulanje ukuputayo tsiku lina zizakutsata zonyoza ntundu wacilomwe cz uzasowa omufusa conco Ulemu ndiwofunika ndale pangani kma zonyozelana mitundu ai
Mr namiwa ulemu wanu mukutimenyera nkhondo
Am here in Capetown chakwera he must pack and go. Nothing has delivered in MalawiMaganya usatamike ku lunzu anthu akugulitsa madeya. Inu mukuba ndalama.
Sizophweka zimene ukukanizadzo
Neneli wa Malawi moto kuti buu namiwa
Kaya omagalimotinu ife timakwera kapalasa mpaka ntawn.
Ichoke kumene smart mastic yo sitikuifuna ndithudi
more fire Mr more fire
Inuyo ndabambo
Kukakamilaku Pali chinyengo akakamila bwanji
Please akuluakulu musayende cha mbuyo tiyeni tiziyenda chatsogolo. Akalepherekanso sizichita bwino.
Uthenga wina sukumveka bwino nkulu wa MEC komanso NRB akuyenela kutula pansi udindo osati azitolele or kuti asimikizire a malawi kuti systmatic machine sizagwira ntchito
Vuto Otsutsa ndinu amantha, koma izizi zot Amec asinthe sizingatheke
Marawe
Aise wina akafapo kumeneko
John Rambo iweyo namiwa
boma lopanda mwayi ili, mmene mvula ikugwela bwinomu kugawa feteleza bwezi anthu ochuluka atapindula. komatu ayi
Ndil kOnkO akanganya amnewo achoke bas
Boma likuyenera lileke kukakamila chi machine Cha simasimatikicho Pala wakutemwa Malawi wamutende
I follow you namiwa
Koma uyu tikuti namiwa ndikatundu womanga ndizitsuro bangolini weniweni
❤❤❤
Kodi bwanji kukakamira pamene anthu tisakukufunani? Kungoziwa kuti pali kanthu.
Much love 🔥 amen and Namiwa son of the soil 🎉🎉🎉🎉
🎉🎉🎉🎉🎉 ulemu wanu bhuro
Anamiwa ndi namiwa ❤❤ always i support you
Ndikuona kuchedwa kucha ine viva Malawi viva CDEDI viva Namiwa🎉🎉🎉🎉🎉
Namiwa ndi gulu lanu la CDEDI Mulungu azikudalitsani. Ndinu amene mwaima pa Chilungamo kuimira mtundu wa a Malawi. Osaopa, Osafooka ndipo Osatopa.
Viva comrade Namiwa viva 💪
Tisaveso zoti alepheleka Ifa takonzeka kale
Kuchoka mademo amawa kwasala oti tidzamuchose Chakwela watikwana kwambiri
Kutengeledwa kuntoso😂😂😂😂😂
Inuyo ndi one basi, more 🔥🔥
Apumedi anthu amenewa za mafuta zawakanika Kachaje must gooooo
More fire 🔥 mr Namiwa
More fire Namiwa
Pang'ono pang'ono akadati mavote amenewo mukawerengera kudambwe😂😂😂😂 wangot ku Mozambique 😂😂
Mr namiwa more 🔥
Upitako ndi alomwe azakowo inu anthu Aku Mozambique ndinu okonda nkhondo
Tiona ngat kuzakhare alomwe okha mawalo aise
Ukamati ndi alomwe ukuthandauza chani ????? Kunyoza ntundu wathu wacilomwe ndi mwikho wamva ndipo ndi Mulanje ukuputayo tsiku lina zizakutsata zonyoza ntundu wacilomwe cz uzasowa omufusa conco Ulemu ndiwofunika ndale pangani kma zonyozelana mitundu ai
Mr namiwa ulemu wanu mukutimenyera nkhondo
Am here in Capetown chakwera he must pack and go. Nothing has delivered in Malawi
Maganya usatamike ku lunzu anthu akugulitsa madeya. Inu mukuba ndalama.